Onse onena kuti Mutharika wamwalira kapena akudwala amangidwa
Ndende ikudikila anthu onse amene akufalitsa nkhani yoti mtsogoleri wa dziko lino, a Peter Mutharika, akudwala mwakayakaya mu dziko la Amereka. Malingana ndi nduna yofalitsa nkhani imenenso ili mneneri wa boma, mtsogoleri wa dziko lino’yi… ...