Chikhulupiliro cha anthu chili mwa UTM – atelo a Kaliati
Pomwe masiku akusendera ku chitseko kuti dziko lino lichititse chisankho chaka cha mawa, mlembi wa chipani cha UTM a Patricia Kaliati ati ndiothokoza kuti chikhulupiliro cha anthu ochuluka mdziko muno chili mwa chipani chawo koma… ...