Chakwera, ndiwe tate wa mbava – watelo Mutharika
Ati mukamayenda mumseu ndi kumuona mtsogoleri wa dziko lino muzikhala kuti mukuona tate wa akuba onse ndithu. Watelo mtsogoleri opuma a Peter Mutharika. Polankhula pa msonkhano wa atolankhani ku nyumba yawo ku Mangochi, a Mutharika… ...