Pakufunika kukambirana kuti tithetse kusamvana – Nankhumwa
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha DPP mchigawo chakummwera, a Kondwani Nankhumwa, ati iwo akufuna pakhale kukambirana kuti kusamvana komwe kuli mu chipanimu kuthetsedwe. A Nankhumwa amayankhula izi lamulungu pa Nyamithambo Arts Palace m'boma la… ...