A Mutharika akufuna aphe ine ndi Chakwera — Chilima
Zina ukamva, mutu mpaka kupweteka mwa ching'alang'ala. Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima walengeza kuti akudziwa za upandu umene boma la a Mutharika likukonzekela kuchita pa moyo wawo. A Chilima amene tsopano… ...