Akugulitsa chithandizo analandila chija
A Malawi24 tatsimikiza kuti Anthu ena amene anakhuzidwa ndi kusefukila kwa madzi mu boma la Lilongwe, tsopano ayamba kugulitsa wina mwa katundu amene anapatsidwa ndi Anthu akufuna kwabwino. Malinga ndi kafukufuku wathu, Anthu amene anapezedwa… ...