Ken Msonda People's Party Joyce Banda

Msonda azitaya, atuluka PP

Chipani chija chikutha anthu akuona. Mneneri wachipani chostutsa cha Peoples’ amene anakakamila ngalawaya chipanichi ngakhale mtsogoleri wake atachithawa, a Ken Msonda, alengeza kuti basi iwo alekana nacho chipanichi. A Msonda analengezaizi pa tsambalawo la pa… ...
Malawi Patricia Kaliati

A Kaliati agwila a Nankhumwa ufiti

Ziwanda zandeu zinabisala kuchipani chotsutsa cha Kongeresi chija tsopano zavumbuluka ndikupita ku chipani cholamula. Malingana ndiu thengaumene ukufalitsidwa, nduna yoona zama boma aang’ono a Kondwani Nankhumwa ili ndivuto loti ikumankakunena mabodza nduna zimzake ndicholinga choti… ...