Kulibe mphenzi yogulitsa – atero azanyengo
Nthambi yowona zanyengo yatsutsa mphekesera zomwe zimamveka kuti anthu ena amatha kulenga mphenzi m'matsenga ndipo ena amagula pa mtengo wa 30 kapena 50 kwacha kuti aphe anzawo mwamatsenga. Izi zadziwika pamene nthambiyo inali ndi nkumano… ...