Maanja 28 ali kakasi kamba kamvula ya mphamvu yomwe yawononga katundu osiyanasiyana
Maanja okwana 28 akusowa mtengo ogwira kamba ka mvula ya mphamvu yomwe yawononga nyumba komanso katundu osiyanasiyana kwa gulupu Mawawa, mfumu yayikulu Chulu m'boma la Kasungu. Mwakatundu wina wawonongeka kamba ka mvula ya mphamvuyi ndi… ...