Alliance for Democracy (Aford) President Enoch Chihana has taken an injunction restraining other party members from holding a convention on Sunday. There are wrangles in the party over the date of the convention with a… ...
Articles By Kondwani Mkhalipi-Manyungwa
President Peter Mutharika has declared that he is not voluntarily quitting to pave way for his younger Vice President Saulos Chilima. Speaking upon his return from the United Kingdom, Mutharika said that he will be… ...
Just days after the CCAP Nkhoma synod issued a Pastoral letter, the Catholic Church in Malawi has issued their own. The letter which has been read in all Catholic Parishes in Malawi this morning has,… ...
Ngati muli akuluakulu a bungwe lija la Sulom, ati chonde lero zipumi zanu zisaoneke ku Bingu National Stadium kumene maule apalane mamba ndi nyerere. Malinga ndi chikalata chimene a Malawi24 anapatsidwa chosayinilidwa ndi mkulu wa… ...
Kaya muli chani m’chuinomu choti mpaka ndi kufika poimitsa maphunziro kenako sukulu ndi kutsekedwa ndithu? Ma lipoti amene Malawi24 yalandila aonetsa kuti sukulu ya za ulimi ya Mwimba ayamba aitseka kaye. Ati akulu akulu a… ...
Nkhani ija ya ndege ija, zija anamutchula a Lutepo zija, mwinanso zija adanena a Kasambara zija. Mneneri wa a Polisi mu dziko muno a James Kadadzera ati chilolezo chomwe a Polisi adatenga chowapatsa mphamvu yonjata… ...
Kwanuko akukamba ya ndani? Kunotu anthu nkhani ndi ya Amayi. Atakhala kunja kwa dziko lino kwa zaka pafupifupi zinayi, Mtsogoleri wa kale wa dziko lino Mayi Joyce Banda ati akubwera. Malinga ndi chikalata chimene atulutsa… ...