Malawi24.com
Mtsikana wina wa zaka 17, Mercy Phiri, wafa atawombedwa ndi mphenzi kwa Khosolo madzulo a pa 18 February, 2024 m'boma la Mzimba. M'neneri wa polisi ya Jenda Macfarlen Mseteka wati womwalirayo ndi Mercy Phiri ndipo akuti… ...
M'mbelwa speaking at an event in mZIMBA
Mfumu yaikulu ya angoni  ku chigawo chakumpoto Inkosi Ya Makosi M’mbelwa Ya Chisanu yayamba yaimitsa kaye mafumu asanu kamba kothandizira kuwononga chilengwe. Mfumu Mbelwa yayankhura izi pa mwambo wobzala mitengo womwe unachitikira pa sukulu ya… ...
Inside Malawi Radio station MBC radio 2
Anthu okwana pafupifupi 7,200 okhala m'madera ena akumidzi  m'boma la Nkhata-Bay alibe mwayi opeza mauthenga osiyanasiyana kudzera pa wailesi popeza mawayilesi samveka kumaderawa kuyambira nthawi ya atsamunda. Madera monga Thotho, Mangw'ina, Musinjiyiwi, Chisangawe, Masasa, Chitundu… ...