Boma latsindika ku mtundu wa a Malawi kuti limanga mabwalo amasewero a matimu a Mighty Mukuru Wanderers komanso FCB Nyasa Big Bullets mu mzinda wa Blantyre. Nduna yoona za achinyamata ndi masewero mdziko muno a… ...
Articles By Ben Bongololo
M'modzi mwa anthu omwe athamangitsidwa mchipani chotsutsa boma cha DPP, Mark Botomani, wati zoti iye amuchotsa mchipanichi akungowerenga m'masamba amchezo ndipo iye wati akudikira kalata yochokera ku chipanichi yosonyeza kuti amuchotsa asanapange chiganizo chake pa… ...
Phungu wa nyumba ya malamulo mchigawo chapakati m'boma la Salima watsekulira chipinda chophunziliramo ndi kupereka mayunifolomu kwa ophunzira okwana 100 pa sukulu yapulayimale ya Demera yomwe ili mdera la mfumu yayikulu Maganga m'bomali. Malingana ndi… ...
Mnyamata wina opanda dambisi wazaka 18 wavekedwa zibangiri ndikusungidwa mkambolimboli ndi apolisi m'boma la Thyolo kaamba komuganizira kuti adagwililira ana akazi atatu a zaka zinayi zakubadwa.. Nkhani yonse ikuti nyamatayu yemwe dzina lake ndi Milwad… ...
Mtsogoleri wadziko lino a Lazarus Chakwera akuyembekezeka kuboola mtambo lero pa ulendo opita mdziko la Democratic Republic of Congo (DRC). A Chakwera akukawonelera mwambo olumbilitsa mtsogoleri wadzikolo a Felix Tshisekedi Tshilombo yemwe wangosankhidwanso kumene komanso… ...
Jetu walira chokweza pamene bungwe la Copyright Association of Malawi (COSOMA) silidamupatseko yachipuputa misonzi pamene bungweli lapereka makobidi kwa oyimba osiyanasiyana mdziko muno ndipo iye akufunsa kuti a COSOMA akumusala bwanji? Jetu wayankhula izi kudzera… ...
Malingana mkuona kwa a Sylvester Namiwa yemwe ndi mkulu wa bungwe la CDEDI, ati ofesiyi ya mtsogoleri wachiwiri mdziko muno siikuwoneka ntchito yeni yeni yomwe ikugwira kotero iwo ati mpofunika kuti dziko lino liwunikenso ngati… ...