Bwalo la milandu ku Lilongwe lalamula a Arafat Goman kukakhala kundende kwa zaka 63 pa mlandu wakupha a Cecilia Lucy Kadzamira azaka 82 amene adali mchemwali wa a Tamandani Kadzamira, mthandizi wa mtsogoleri wakale wadziko… ...
Articles By Ben Bongololo
M'busa wa mpingo wa Bua African Abraham ali m'chitokosi cha apolisi ku Mchinji kaamba koganizilidwa kuti adaba mawaya amagetsi wa ndalama zokwana K297,000 a bungwe lopereka magetsi la Escom. Mneneri wa apolisi m'bomali watsimikiza zankhaniyi… ...
Bambo wina wazaka 49 wa m’mudzi mwa Binya kwa mfumu yaikulu Kwataine ku Ntcheu, watsikira kulichete atamwa matoti 42 akachasu pampikisano wazidakwa opapira bibida omwe unachitika dzulo mbomali. Nkhani yonse ikuti dzulo lolemba pa 11… ...
Fostina Mbemba ndi amene wathamanga kuposa atsikana anzake mu mpikisano wa Mzuzu City Half Marathon lero. Mtsikanayu analibutsa liwiro ngati kulibe mawa ndipo iye anathamanga mtunda okwana 21 kilomitazi pa ola limodzi ndi mphindi zokwana… ...
Chikondi Mwanyali ndi amene wapambana masewera a Mzuzu City Half Marathon atathamanga mtunda otalika makilomita okwana 21 pa ola imodzi ndi mphindi zokwana zisanu ndi chimodzi. Mkulu wina amenenso wakonkhomola lekodi ndi Chancy Master pamene… ...
Zachitikanso lero mumpingo wakatolika ku Lunzu pamene wansembe wathira bakera kukamwa oyambitsa kwaya kamba koyambitsa nyimbo ya Aleluya mu nyengo ino ya lenti mpaka mapemphero kusokonekera. Nkhani yonse ikuti a Edward omwe ndi oyambitsa kwaya… ...
Mpikisano othamanga wa Mzuzu City Half Marathon wayambika pamene ma athletes ayamba kuthamanga mtunda okwana 21 kilometres kuchokera pa St John's munzinda wa Mzuzu. Kuno kuli liwiro lamtondo wadooka pamene anyamata komanso asungwana akulikumba liwiro… ...