Boma kudzera ku nthambi lowona za anthu olowa ndikutuluka m’dziko muno la Immigration latsimikiza kuti posachedwapa likweza mitengo ya ziphaso zoyendera. Poyankhula ndi nyuzipepala ino mneneri wa bungweli a Joseph Chauwa anati mphekeserayi ndiyoona koma… ...