Private Schools Association of Malawi (Prisam) say they will this week launch the Lilongwe chapter which seeks to help improve education in the city's private schools. Disclosing the development was Prisam president Amon Tafya who… ...
Articles By Archangel Nzangaya
Forty-eight Ethiopian nationals have been arrested in Rumphi for allegedly entering the country illegally. Rumphi Police station spokesperson Sergeant Tupeliwe Kabwilo says the migrants were arrested in the wee hours of today at Chiweta area.… ...
Kulibe kupuma ku Malawi; ina ikamatuluka, ina imakhala ikulowa, nkhani sizimatha. M'busa wina uku akuyenda chewu chewu kaamba koganizilidwa kuti wakhala akuchita kusaweluzika ndi mkazi wa nkhosa yake yomweso yakhala ikumupatsa chithandizo chochuluka, inde kuluma… ...
Blantyre Seventh Day Adventist (SDA) church has organised a fundraising music show this weekend ahead of this year’s celebrations marking 100 years of the church’s existence in Malawi. In an interview with this publication, Chairperson… ...
Pomwe akuluakulu a kampani ya Ichocho Power Security (IPS) anali kuwunguzawunguza kuti nsuzi uzipezeka bwanji ngati kampaniyi ingalandidwe chiphaso, boma labweza ganizo lake pa nkhaniyi. Nkhaniyi inayamba sabata imodzi yapitayo pomwe mkulu wa IPS a… ...
Zina ukamva ndithudi kamba anga mwala. Bwalo lamilandu ku Netherlands lalamula bambo wina wa zaka 41 yemwe akumuganizira kuti anabeleka ana pafupifupi 600 padziko lonse lapansi kudzera mukupereka umuna kuti asiye kupereka. Malingana ndi malipoti… ...
Apolisi ku Monkey Bay m'boma la Mangochi akusunga mchitokosi mzimayi oyendayenda kaamba kobaya kasitomala wake malo obisika pa nkhani ya malipilo. Malingana ndi ofalitsa nkhani pa polisiyi ya Monkey Bay Sergeant Alice Sichali, mzimayi ogulitsa… ...