Patangotha masiku mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika atapempha kuti mtsogoleri opuma a Joyce Banda abwele, Apolisi nawo alengeza kuti akufuna kunjata mayi Banda.
Malinga ndi chikalata chimene asayinila Bambo James Kadadzera amene ndi mneneri wa Apolisi mu dziko muno, mayi Banda akufunidwa kuti azayankhe milandu ya cashgate.
“A Malawi ambiri mwakhala mukudabwa kuti nkhani imene anthu ena anatchula kuti amatumidwa ndi mayi Banda kuti asolole ili pati,” alemba motelo Apolisi.
“Tsopano tikufuna kukudziwitsani kuti tamaliza kafukufuku wathu okhudza mayiwa ndipo akuoneka kuti ali ndi mafunso angapo oti ayankhe,” chikalatacho chikutelo.
Apolisi ati m’mene iwo afika potelopo, tsopano ndi okonzeka kunjata mayi Banda.
“Tatenga chikalata chotipatsa mphamvu yoti tinjate mayi Banda ndi kuwasakasaka kumene ali kuti azayankhe mafunso,” atelo a Polisi.
A Banda anachoka mu dziko muno ataluza zisankho mu chaka cha 2014.
Chichokeleni sanapondeko kumudzi kuno ndipo mbiri ati iwo ali ku Amereka.
Mmbuyomu akhala akunena kuti akubwera koma mpaka lero kuli chete.
Sizikudziwika ngati mayiko amene akusunga a Banda ati awatumize ku Malawi kuzayankha milandu yawo.
Before you do that you must first arrest Kamuzu Banda,Muluzi,Bingu and then JB don’t jump
Which police are talking about? Bcoz all police,soldiers,lawyers,judges are full of corrupt including all wicked politicians under DPP may fire upon you all
ACHAPONDA ATAMANGA MMAVINA KUKONDWELA LELO MUKUTI NDALE AMALAWI AMALAWI
Kutapa-kutapa bola osagwi zosiyirana izi Kamuzu…Bakiri…Bingu…Joice…Peter…kumapeteko sitikudziwa kuti adzatapa ndani.
Fearing 2019 elections g instead of creating jobs what you know is to arrest people go to hell
Bwanji sanamange uja anapezeka thumba la mabilion munyumba mwake thawi imeneija?
Munabela limonx ndi amayiwa et muziulula nokha apa iyaaa bom mpaka kusauka chifukwa cha amaneyu ee shi iiiii
Mzimayi ogulisa ndege ndalama zake mkugulira chimanga,,mayi ameneyi ndimakina
Tikadali kuvutikila ziko lathu azathu akunjoya mayiko ena
Musamuwonele kt ndikaz
Kusowa zochita eti
Apite nkonko ku USA
Ndizopusa zimene mukukhanzazo awoso achimwene awoke ananbaso ndalama mukatambe mwawamanga amenewo wava ife amalawi tukumalila ndinawusogoleli apanopawo ndiye asiyen amayiwo kod mukawamanga mukufuna uzikawagona zachibwana ayi mwava
zaziii , leave jb alone
Kodi mayiyu waipalero ayambe afufuze ndalama yomwe adamangila ndata ija abwela liti abingu kt alemele choncho,muyamikeni mayi chaka chimodzi adakuwonjezelani malipiro kawiri yamikani.
Comment is loading
Akamaramula kut amangidwe uziganizile iweyo nawe ukazatula udido iwe ndiye ulikale papen kkkkkkkkk
Ngat mwasowa zochit aboma pezan zona osat zomanga amai
Mumakwana amai zosatheka kukumangani amai
Mmmmm ku malawi kumeneko
Anjatiwe basi.
president opanda masomphenya nsanje zokhazokha
Nanuso apolisi mukalila kununkha misewo basi sachamba bas
Kkkk oooowoo?
Osamanga chaponda bwanji
thawi ikakwana yakwana basi
amalawi unachuluka ndi umbuli…very cheap.munthu samangidwa asanalowe khoti,akapezeka olakwa nobody is above the law SHE WILL BE ARRESTED.the current president is innocent for now.some of u guys are indeed being childish.ngati makolo anu anadya nawo dolayo mukonzeke kumakasiya za kudya ku penitentialy
Tikulila ndalama zanthu za sonkho ife kumasamba opanda soap ngati simagwila Ntchito.nde alekelenji kumangidwa palibe mmalawi amene ali okondwa pazimene maiwa b ndi gulu lawo anachita.Mangidwani mai ulendo wa kundende wa bwino mulungu Akulangeni ndithu.
what about “unyolo wa chaponda” alibe?
Law must take its course.
Guilty until proven innocent.
Let
ZIKUWONETSE KUTI KHOTI LILIBE PHAVU KOMA PETER B…………
Any party which was in government did the same thing
Aliye ndiwakuba
Ithink if u look at the comments its either writters are mad, insane, drunk, ignorant, childish , etc.
This is corruption case, if u are a beneficiary sory for u…. She will be arrested
NKHANI YAYIKULU
Boma lililonse ndilokuba nde mot tindalama tilipoto agwilise mwanzelu km nkhan ndalama izingothera mumabwalo umenewo nde umbuli ngt malaw ndalama zachuluka bwanj osamangowathandiza anthu onsewa akuvutikawa km tizingomva zopoyira bas .Bakili adaba ndalama zaboma even kamuzu same Bingu same Amayi nawonso ndechavuta ndichan? Milandu yabakili ikuthandalama zambili kuma bwalo amilandu km kumangokakamira zaziiiiiiii .Asiyen may JB osamalimbana ndizinthu zopita kale pomwenso zikusakaza ndalama zaboma .kuli maophaz care ambili omwe akusowa zithandizo km kumangokokana zaziiiii malaw zizachita bwino chifukwa cholimbana ndizinthu zopanda phinu .boma lililonse ndilokuba tiyen tiziyang’ana zakusogolo osat zambuyo ndizopita tikatero malaw tizachita bwino (Palibe wabwino )
tinaxiwa Ife kut Chaponda’s arrest was just a trick but amafuna Issue JB…..but enywy thus a nice development mangani mbanva zonse
Mukamugwira nde abweza ndalamazo?
Abwere basi adzammange mmai ameneyu mpaka kutchyola lock nkumaonetsa kuwanthu kut ndathyola khomo latseguka!! Amagidwe basi kkkkkk
Mam musabwele dziusani asakuvuteni awa zanu zinaela kale awanso kuno akutinzunza kuno naonso akuba kuno iwo asakhale ngati angelo kuba kunayamba kalekale kamuzu bakili bingu peter chaponda nduna zambili ma mp ma cansala ndiena ambili musade nkhawa mayi imwani khofi ku america
Mam musabwele dziusani asakuvuteni awa zanu zinaela kale awanso kuno akutinzunza kuno naonso akuba kuno iwo asakhale ngati angelo kuba kunayamba kalekale kamuzu bakili bingu peter chaponda nduna zambili ma mp ma cansala ndiena ambili musade nkhawa mayi imwani khofi ku america
e tv RSA maiwa khani ilikamwa
yabwatata
Palibe chimene ndikudziwa, koma kuno nkunja kumayanja lichelo
Mbamva zikamaba umagwira yemwe wampenzayo sumalimbana nd munthu osangwira ndye mmai amenei mangidwe basi wadziwika ku adatchyola lock wa ndalama nd ameneyu adachitaso kumujam bula pa malaya atatchola umboni ulipo
Amangidwe kumene
JB, God should clean your hands ,Peter kuno boma lamutonda, maji,maizegate 2019 achokapo ameneyu
INE PHEEE, NDIUMPHAWI WANGAWU KUMADYA SIMA NDI NDIWO BASI NDILIBE PROBLEM.
Muahahaha!! amafunika unyolo special?
kukhuta soya pieces basi ndemwati mnkhuto wanuwo i want the former president to return home hhhhhhhhh koma abwana amenewa mmalo momumanga chaponda afuna kuwayamba kaye adan? nazoso mbuzizo mkumati unyolo wa jb ulipo kkkkkkkk answer upolisi wake uti?
Joel Chinkhanambwa
Mmmh mwaona kt nthaw yasar yochepa nde bas muzivute nde mukufuna mundiuze kt peter sadadyepo ndalama za boma pot fuel akuchoka paife nde ngt amai adachosapo ndalama alekeni kod nthawi yonse ija mudar kut kut mpaka muziwauza kut abwere nawe iwe wa police mwapeza mpata pot przdent walowapo nde nyomi nyomi kod kithakhar kut Dpp yazagwa kod mungatani kod zanu zija zomwe mukubisa sizizaululika kod nanga ifa za athu ngt mfana uja wa school uja mesa mudapondeleza cz ndi nkulu wanu adapanga zonse kd chulungamo mumafuna kt chizafike pat nyasssss
Ndale chabe izi
khani ndiyoti amangidwe akayakhe mafuso kodi bakili mukunenayo mesa nayeso khani yake ilipo ndipo azayakha komaso mukuziwa kuti bakili ndimatenda amsana aja ikatulu kalata yofuna kuti akayakhe ake mafuso muzava kuti dokotala akumufuna kunja klklk
misokho yanthu imatipweteka jb amangidwe basi.mukakhala enanu ur tym is coming.chikolopa chiyendetseni nanu mukudikila kukolopedwa
agwidwe bs..
Atsogoleli apamalawi kuba basi,amuluzi anaba,abingu anaba,amayi anaba awaso awa alipowa nawoso akusolola,mind you God is watching,malawi shall never develop if our leaders will not change,kulira kwamuthu wakumudzi mulungu akumva,muzilandira zilango modzimozi.
Mwasowa zopanga a Dpp instead of fixing mavuto azachuma alipowa nkulimbana ndikumanga anthu, you are bizy digging old cack, focus on our things. Watch this iweso tizakumanga ukazachoka pa mpando en thats a time you will feel the same pain.
Ukudziwa chani iwe?
Palibe, koma mawa ndi wina
Mr kananji are you assuming kuti munthu akaba asamangidwe? Potengera kuti ndiwandale kapena ndalama?
Asanakunamizeni amenewa analephela kutumiza Vincent mulekeze
Kkkk amai awa ndokuba bas shaaaaaaa!!!!!
Akuona ngati akubisala mmasamba
asamatipuse agalu amenewa this government mbava zokhazokha mxiiiiw
Since multiparty Malawi has seen corrupt leaders, let us go back to MCP in 2019
PETER ali bixy kupereka madzi ku mpoto pano ndpo mmmmm za jbzo zinatikwana patdogolo ndi chitukuko,chilungamo
KODI ANABA CHIMANGA UJA WAMANGIDWA? MAYESA ANAPHA ATHU OSAUKA
Lamulo ligwile ntchito kumalawi. Kkkkk
Zimanganani kumalawiko ife tili phe kudya marands pajoni
Ndale zakumalawi all the leaders we vote into power end up embezzling the money from donors intended to help poor malawians, please our leaders God is watching
kkklkk kuteroko kumuitana kuja sikunali kwa ubwno? kkkk
Nanga wa Bakili mdausiya pati paja during his leadership their were rumours that he was making fake K50? Pangolowa chidani chabe with pita
Nde yake
stupid government go to hell!
Polowa Boma ndikutuluka ndipamene amapeza mwai wakuba,Kamuzu potuluka Boma adaba naye Muluzi adangokafikila kutapapo, a DPP potuluka Boma adaba Joyce Banda naye adangokafikila kutapapo potuluka adabaso,DPP polowa idangokafila kuba kukwatisa maukwati,5yrs yomaliza ulamulilo wa Muluzi adapha mwana wa sukulu ,ulamulilo wa Bingu adaphaso mwana wa sukulu palibe adaimbidwa mlandu ,I Wadi adachosedwa ntchito chifukwa chofuna kumuimba mlandu Muluzi .Ife zosowa zathu sizomangana zanuzo mudalonjeza muzapanga chani zatheka zomwe mudalonjeza
Zoonadi manfestal a Dpp sanatiuze kuti azamanga JB, nde ofunika apange kaye zomwe analonjeza zija then adzipanga zawo..
Mumangeni komaso inuso ndi mbava enawa mukuwasiya bwanji? ?
For what reason?
kkkkk peter wabalalika,
Mumuyambe chaponda
Acc for what??
Angofuna kuti wanthu awapange confused amaziwana andale ndimodyera mwawo amen
ndalama zinabedwakalekale zakazosezimumataniosamumanga?chifukwamwawonakuti masankho ayandikila kuti muwonekengatiabwino? musatipusise amalawife mwanva
DPP u are too let
Mujamunayambilamu osagwira anthu awa ndi amodzi.
Agalu inu mwaona kampen ayamba eti MbuZi mix Peter yemweyo
Asabwele a joyce bandá ñaoso apeter asowa zochita thàwi yoseija osamuitànisa akamutañe paño?àķufunà amuipisiĺe cv mzaoyoooooo.sithawi yakampeni ikuyandikila.inu mukuoná bwaaaaa!!!!
Zandale Zokhazokha Kukhala Mmalawi Mkulimba Mtima Akuba Nose Mbuzi Azitsogoleri Ose Mbuzi Pita Mbuzi Chaponda Mbuzi Zikutiwawa Mmalomonthandiza Anthu Mukudzilemeretsa Nokha Pamtundu Panu A DPP Mwava?
corruption pa Malawi ndie kudya kwawo even peter mukumunenayo mukuziwa komwe akusunga ndrama zobera dziko? kungoluza peter this s round muzamuona sazakhala kumalawi azizapita kwao komwenso Ali ndi Green card ID
palibe Ku mW anamangidwa chifukwa waba ndalama za boma ayi kma wakuba zovala ndiye tiyeni timuwoche were guyz ziku pwetekesani mutu iyiiiii ndi goverment mission panja imadya pamene ayimangilila amw azanga tiyeni tisekule maso amw tiyeni tilibike kungwila ntchito kuti ana sakhale ndi njala
Kkkkkkkkkkkkkkkk
ana a primary strike..ana a chanco strike..prison warders strike.. jugdes on strike..nurses on strike.
dpp zero pa 10
Teachers strike, MYP strike, Min bus drivers strike kkkkkk
area 18 residents in lilongwe on strike
A munthalika khondo mukuiyambayo simuimaliza?
Kkkkkkkk
Dpp want to divert peoples attention from Chaponda’s case to Jb’s. Politics is being played here.
George chaponda
APM akusewela ya nyambo pamenepa. Akuonetsa kuti akutchera msampha wogwira mai Banda
Asiyeni Amay Apume. Muyambe Kaye Mwa Tsegula Milandu Yobisa Ndalama Ku Dzko Lina
Akutumani eti? Akupweteketsa 2019 ili pafupitu.
amumanga opanda kulakwa kwenijweni bwanji ayambekaye atapanga zitikuko akapangapo ndipamene aziwona Zolakwa za mayi uyu
Welcome back
Chisoni
Ngati muwamange amai ifeo tiyenda chaponda mwamumanga
Palibe muthu angalamulile popanda cholakwika
kkkkkkkk
Abwele Basi Ngat Anaba Aone Zingwe Why She Is Hiding Outside The Country?Corrupt Woman We Need U Here Come Come U Left Us On Fire
Unyolo umenewo adzimanga ekha muthalikayo iyeso ndimbava dziko silikusintha ndalama zikulowa mwa acount yake not acount no one yaboma amusiye JB alibe tchimo
asowa ntchito, mbava zina zikutibela panozi
Koma Amai anaba mowonetsera kwambiri ndi mwana emwe kuchita kuziwa achina bakili ndi bingu amaba koma fans simadziwa koma Amai anaonetsa kuti ndiamayidi….
mangani 7 minister owolawo
never the less to arrest mama jb zopanda mapiko zifika yesani
Jb musiyeni ife timamukonda mtsogoleri wathuyu padziko lapansi pano palibe woyera.inuso zanu ndi zomwezo
What a rubish gvt. Instead of initiating development projects in the country wasting time with the former president. Malawians are not after that , pItAlA be wise! Fight the current corruption scandles. why blindfold Malawians?
Is arresting those involved in corruption not fighting corruption? Mukufuna gvt itani pothana ndi corruption? After all, JB is still innocent until proven guilty by the courts
JB and Peter are corrupt leaders. Report says Malawi is the BEST corrupt country in the world. Peter remove a log in our eye and do to others.
Musaiwala a DPP amalimbana ndi amene anal M’boma paja Malemu ankalimbana Mlatho wawo a Muluzi, lero ndi izi… Dere ayiwala kale za Maize-Gate
Bakili after pocketing 1.7 billion kwacha Ali phee now akukalamba mlandu uli kukhoti.mmmm.Malawi
kodi kampeni yayamba kodi?
Komatu ma comment enawa kumalankhula mukudziwa kuti kulinso mawa.
Musayese zija mwadala mayi alakwanji?
Atumidwa amenowo azafera zaeni
Asowa chochita alakwanji jb apolice ndinu zitsilu pamozi ndi munthalika ngati mufuna kumanga bwanji mutamanga chaponda mbava yeniyeni,munthalika kuntha mano mukamwa ndi zelu zomwe fuck you stupid wali
Inali keep change
Osati kuba
Koma zoona akuluakulu anzelu zawo kumapanga ma plan oti mu mmange mzimayi? Mkazi ? Aaaa za ziiiii
Watani Kuti Amumange?Kodi Nesa Wonsewa Ndiakuba?Iwe Peter Usatengere Poti Ukulamula Ndalama Zija Zimapezeka Kwanuzi?Ukusokosa.
musaiwale kut pamene mulipo ena akubweraposo muzalira nanu ndikuba kwanuku inu mukulimbana ndi mayiwa bwanji amene angakugweseni simayiwa ayi akubwerapo chakwera mbunzi za anthu. inu.
Joyce b! She’s free live her alone she’s a good person!
This News Is #Fake The Police Hav Nothing To Do With JB, Maybe If U Were To say ACB We Would Hav Agree With U.
Lamulo limaposa mphamvu ngat ali olakwa akuenera kulandila chilango
Don’t come mama
Ohh yaaa ma lawyers adye dollars tsopano, kumangokhala nazo kujako ndalama zathu, come and start paying legal fees
Malawi wa lero
Kkkkkk ndiye Malawi ameneyo za ziii mmalo molimbkira kupanga chitukuko kulimbana kulumbutsa nkhani za kalekale
pakut nd malamulo a dziko koma cholinga ndichakut abweze ndalamazo kapena kungozunzana chabe!? naga mukut a pita muthalika anawaitsnisa kut azayankhe muland! kapena anawaitanila zao ndikudabwa inu apolis mukut mwatengelapo mwai onjata amaiwa ndiye kut mwagwilizana nd bwanao titelo kkkkkkk inuso ndiye mbava zokhazokha manyaz bwa hahahahahaha
If u have tried to open account but u failed, and u still want to have account don’t worry, am here to help u just call/WhatsApp on 0604945171. No need Work permit. No need Proof of address. We based in Capetown
M’bomamu mwasowa chochita m’malo mokweza Nandolo mukulimbana ndi dzaziiii makape inu
Apindula chan
Malawi too much ndale ake
Eee Zatipasa Chimbikiso. Muwanikhe Ka 50yrs Poti Akalamba Kale .Kanaka Chaponda Ka 60yrs.
She Deserves To Be Arrested, She Stole Our Resources And She Ran Away, She Is A Thief.
Sipping My Dry Gin
Machende wanu apolisi opusa inu!
What we need is the Truth and they should not arrest her bcoz of politics but if it is true that she overused her office, then let the law work.
Mtharika is the head police, he is the one doing all this, but be careful you can go where your brother is before Joyce arrested.
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk umakwana
ONLY GOD KNOWS WHO DIES FIRST NOT VAIN INTIMIDATIONS
hahaha wayamba ufiti wayaluka ase amangidwa basi ameneyu iyaaa demet
watenga ufiti wa ambuyache
musatsogoze moyo wamzanu Mbuye asanalole,this issue has nothing to do with HE rather its the MPS who have secured that warrant of arrest to the former head of state
andale onse ananadwa banja limodzi …kumangoti kumanga komamusaganizile kuti zingafanane iweyo ndiine .kumanga kwake kongofuna kuti phimphamaso komweko.kutsuliko mkumamwela tea limozi. .ngati simuziwa amapanga anthu amenewa..dzuka malawi
Mwayamba kuulukapo apa etttttt kkkkkkkkk
Kkkkkk ufiti at its best hahaha
Simungamuthe Peter mufa ndinu nd chimbamvacho kkkkkk
Kodi muthu akaba ndiekut as asamangidwe? aMalawi munatani kodi kususa zilizonse basi
#Caffy chakuti chamako
mufun mukuona nokha et? hahaha Mukhala #team
Zitsankho zikuyandikira tiyambe kumva za milandu
Za ziiii
Aliyense ndi mbava ndiye palibe zomangana apa
Ndrama zomwe mukufuna kukamangira Joyce banda chonde chonde wonjezerani ma salary a apolisi kapena gulani ma jombo amasoja kamba koti milandu ya corruption kumalawi siimatha nanga Bakili muluzi boma linawononga ndrama zingati
jb is not coming to Malawi she will stay outside the country until Peter and his DPP come out of power, bingu anaba ndalama wamanga ndata bakili anabaso bwanji kulimbana ndi mayi banda gulisani ndata ndiposo mangani muluzi and then arrest banda don’t jump bcoz she is a woman
kkkkk
Kkkkkkkkk naweso Gondwe iwe ndiwe mtumbuka Wa 0 it shows like umadya naye JB wakoyo
Wasekachi Gondwe? Kkkkkkkkk hahaha
KKKKK Kasi mwati ndinadya naye jb
With a warrant of arrest issued by police it means she can be arrested wherever she is
A Gondwe mwawoya makala chomene wamange wakwambilira na.
Atumbuka siamalawi muziwe
Imwe baboma mukukhumba kumanga mama nine month munthumbo mulije chitima Eti sono mukhumba kuti mama a fye na BP Eti kkkkkkkkk
Kkkkkkkkk kuti wapereee wana uhawuu imwe namwe mwamadoda hw u can allow mzimayi wamubereninge mukubeka nthena?kkkkkkkkk kwalicha mwekha ohoooo nafwaaa naseko kkkkkkkkk diiiii!
Which is which. The president said she is not going to arrest her.Now the police says they have warrant of arrest. Malawi is very confused state.
Apolisinu mapazi anu kwabasi
Kod Mukufuna Kumanga Jb Nanga 577 BILIYONI Yomwe Anaba Bingu Ilipati?
Si zonyengelera apa. Si zandalenso apa. Okuba nkhuku ndie amangidwe?? Akapezeka olakwa amangidwe basi. Amathawa chani?? Wakoma lero?? Chifukwa ali kuja ndie basi akumulakwira?? Abwere basi. Lamulo lisaka ukalipalamula. Si zolowesapo ndale apa wapalamula walalamula basi
Check 577 billion
Amangidwe basi ….i cant wait!!!
Mxiewwwww!!
She was our mother ,amene sanachimwepo ayambe kumugenda miyala mkaziu kkkkk. palibe angamange mai ake or utakhalakuti unasainira polowa tchitoyo she Will remain our mother forever.Ngati sititha kukhululuka ndipovuta kuti Mulungu azatikhululukirenso.
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkwidzingani
nde za 577 biln bwanji? We don’t have good leader to fight against Corruption even he himself is a thief. Why is he shielding those 7 roten ministers???
Zaziiiii kusowa ntchito apolice eti.
Imeneyo ndale kumukola mzako agwe basi kkkkkk
Kkkkkk mavuto
aaaaa politics will naver change,,,, kaya it
aaaaa politics will naver change,,,, kaya its non of my business
Onse akuba amangidwe, osaiwala wakuba chimangayo!!!
Zopusa unyolo ukudira wachani makape inu xwiiii zopusa mwasowa zochita
Shupit pitala ndi apolice ako mkanjateso bingu or ai njatani pitala yomweyo anadya madola aja ops apitala ndi mapolisa eeeeeee mlibe cash kkkkkkk muisovenge
Mawa ndi iwowo
arresting her or not nothing will change in my life…politicans they birds with same feathers..
Unyolo umenewu umachedwa pati?..
I can’t wait to c amayi kumuzikuno since 2014…
#teamJB_must_fall
Mwachedwa
Machende anu nonse
Death penalty chilango chake simasanje omangananso adzikapitilidza kutitheranso misonkho pokudya ngaiwa kundende
Kkkkkkkkkkkkk,bwanji amalawi tsazavote palibe wabwino…..
Awandi akumba, akhaza, tziona mathero
Boma Manyaka mxiwwww
kulengedza koyamba??? kkkkk kma abale
Koyamba ndi ukwati?
Kkkkk zangondisekesa
Ndaonanso
Eaa
Aaaaaaa mukuona ngati anthu angaiwale za chaponda?malawi wake siwaleroyu amene mungamupusitse.zakukanikani basi,sakani plan ina.
Nanga chaponda palibe unyolo wake. Mwina mulibe ndalama zogulila ndikuthandizen one
apolice onse paminyelo pawo
Ngati ali olakwa amangidwe basi, kwa inu mukuwaikila kumbuyo mayiwa kodi anakugailani ng’ombe nthaw ijayi eti.. Hahaha
Ayi man, mayiwa anaba zochepa kusiyana ndi pitala ndi malemu bingu!
Ndiye mukufuna mumange m’tembo
kkkkkkkkkkisiting alibe mfu mfundo akulankhula mozemba ngati ife timadziwa zoti ukaba ndalama aziti cashgates scandal tinamvera mayiwatu ayini ake kusolora
What can we expect from a swine like you offspring of stupid Lundu. If I may ask you, how much was stollen during Bingu’s reign? And how many has this fool called Peter admimistration arrested. Malawi doesn’t belong to one group of ppl. Ndipamene mzayalukile tsopanoQ
mbava ndi mbava kaya yaba zochepa …… Anthuwa analandila ng’ombe hahahahahaha
Hule JB #amangidwe
Jb azakhara mfulu mpaka kale kale.
Deal with chaponda first mthele JB
Bwanji simuzimanga nokha ndalama mukubazo
nthawi yonseija munari kut zazi
Penati penati penati(#singing penalty)
Aaaaaa zaziiii
Kkkkkkk Melvin Malikebu
jb cisiilen dzikoli chanzeru /chitukuko chachikulu boma lachitapo ndiku chosa achaponda pounduna bassi!
Akamumanga tidzamu votela 2019 adzatenge boma ali mundende
Nanga kale lonseli amatani??amangidwe basi enaso amu nthawi ya Bingu amangidweso asakondelepo apa kutibela kwa onjeza atsogoleli ukula kuzikupindulirani!!!!!!
Muyambire wakuba ndalama za chimangayo
Akuziwana awa asatipusise
Ndipo alibe ndi manyaz omwe
Zawo ndizimodzi
Zaziii kusowa zoti atiuze
yeap sukunama
kkkkkkkkisting G Chaponda alraedy arrested don’t u know?
Kumangidwa kwa chaponda it is just kungofuna kupaka tuvi amalawi m’khutu kt asave zapatali.koma choti adziwe amalawi atsekula maso and atalephela apa! kaya tiona
Mungomusiya
Zachamba bas et apolisi wo asowa chochita
Kkkkkk malawian politicians
2019 ikuchedwa kuti mulilamulire dzikoli mwaubwino mosayang’ana mtundu wa munthu,mosaba ndalama za msonkho wathu,wodi uko Aphiko adutse!!2019 phiko boma
amange basi, asamangodya dollar zathu kumenko, m’bale wake chaponda nde aliku khoti,
Hahahaha tione mumene zitathele mwaona poti 2019 yasala pang’ono eti kkk
osamanga peteryo bwanji zazii
Mxiiewhm!! Zazii!! mwaona ndalama zakutherani zachina mphwiyo muli tidye za JB tsopano….mukhaulatu…
Kaya zanu izo, mesa kulengezako ndikumuchenjeza munthu ndiye angabwele. Apolice nawo akukanika ku njata chaponda ali phe .
Amusiye asamumange , ngati atamange then Nkhalamba Bakili Muluzi amangidweso chifukwa zonsezi ndiyeyu adalephera kuphunzitsa anthu za mfundo zabwino za Democracy
leave story of demo bro,the story z progression,how we can boost our country..there’s no need to waist time some1 instead of dealing with our povert,they just remind us that they ar playing their duty as politicians instead
Tell Ur Politicians That We R Tired Of Their Stupidity.
Aaaa amalawi kusamva! Malemu kamuzu banda adanena ndi pakamwan pake kt democracy ndi khondo, koma amalawife kusamva
Am dead
Heeeedee !
nde choncho angabwere, zopusa eti …
Kkkkkkk kumalawiko zli choncho
malawi woyeeee
Hahahaha!wanyuwani kapena wakale?
Wanyawanitu