Joyce Banda will be arrested – Malawi Police

Advertisement
Joyce Banda

The Malawi Police Service (MPS) has obtained a warrant of arrest against former President Joyce Banda in connection with the cashgate scandal.

MPS National Spokesperson James Kadadzera has confirmed to Malawi24 that the warrant of arrest has been issued against the former president over cashgate cases.

Joyce Banda
The Most Wanted

According a statement issued by MPS and signed by Kadadzera, the law enforcers using through its Fiscal and Fraud Section conducted investigations on the suspected involvement of Banda in cashgate cases and unearthed credible evidence.

The statement says the evidence gathered raises reasonable suspicion that the former president committed offences relating to abuse of office and money laundering.

“Since there is a need for investigations to question the former president on the suspected offences, a warrant of arrest was issued against her. This warrant of arrest is in force and necessary legal formalities are being pursued,” reads the statement.

According to Kadadzera, the warrant has been made public because the issue of cashgate is in the public interest.

Banda who was Malawi leader from 2012 to 2014 went into self-imposed exile after losing 2014 tripartite elections. An independent audit analysis funded by the German government established that over K550 billion was unaccounted for during the period that Joyce Banda was president.

She has been named as the Chief Cashgate architect by different people who have been convicted over cashgate.

Advertisement

359 Comments

 1. it sounds ambiguous to see ACB which is responsible for handling of such profile corruption case are quiet and it didn’t issue warrant of arrest itself. The procedure is not even there. She has never been incredibly ACB to be investigated. PAC has never summoned her yet. Who is the complainant at this stage?who is the witness at this stage?Police is acting as a defendant and prosecutor,yes? Was the police self-employed to gather the evidence gathered?at what challenge?Is this a fiscal or corruption challenge?JB wasn’t a bank. This is why all warrants for those arrested on corruption were instituted by ACB..I don’t know

 2. Ndalama zili mamnyumba mwawo anthuwa.atangoti tiyeni tiseche manyumba anduna ndi pulezidenti amene.mutuluka ndalama zankhaninkhani.Dziko mpaka kudabwa kuti koma ndalamazi zinali momwemuno? Zamisonkho ya anthu.

 3. Hahahahaha!!!!!!! Mukumuopa mzimayi hahahah!!!!!! Mumadikira Chisankho? Mwachedwa palibe kumangana muyambe mwazimanga nokha kaye ndalama mwaba ndinu pano ziri m’manyumba mwanumo za chamba

 4. Ngati boma lakukanikani kuyendesa siilani anzanu odziwa bwino osamatiuza za m’bwelera pano jb walakwa chani, iyeyo ndioyamba kuba?mbuzitu imadya pamene ayimangilira, pankholo panu agalu inu

 5. Muphe anzanu ndi ma BP mwaiwala BINGU keep lot of money while dziko likuvutika Busy with nothing that’s why we can’t develop because of that mindset think twice

 6. If u have tried to open account but u failed, and u still want to have account don’t worry, am here to help u just call/WhatsApp on 0604945171. No need Work permit. No need Proof of address. We based in Capetown

 7. Don’t worry mama, you will be arrested and within a short period of time you will be out of jail because in Malawi prisons were meant for the poor people only mmmmmm.

 8. Why u people still against the innocent person, who didn’t do sin among u?leave her alone mind ur business we want to hear other stories not that,kupusa eti zoyipa zanu zili thoo agalu inu amichira.

 9. Ndikaona ngt anthu azeru mugolemba zachibwana basi ,muzizifusa musanalembe ,chomwe anachokera ndi chani ,ndalama zomwe akudya bwanji adye kuno ,ndalamazo ziziyenda momuno , zimakusangalasani akamacheza ndi bushir ,mmmmmmm ooooooooo

 10. Mumangeni ngati wakulakwilani ku Dipipi ko…. kumanga munthu mpakana publicity? Kulephela ntchito basi… APM akukanika kugula galimoto lothana ndi mavuto wodzimitsa moto ku Balaka and other districts koma ndalama kudyera ma party and kuba …Dipipi must be ashamed of itself for failing malawians who are drowning in deep poverty

  1. #Sapangwa ndiye wati thupi la chaponda liri mu cell kutiko? ndikamupase nsima ya dothi chimanga anadya kale.

 11. First arrest Comrade Chaponda and other six rotten ministers, end Bakiri Muluzi corruption case, arrest the killers of Chasowa & Njauju. We’re anxiously waiting!

 12. WHAT SURPRISES ME IS THE FACT DAT IT IS THE SAME JB THAT INITIATED THE FORENSIC AUDIT ON CASHGATE SCAM. WHAT DID THAT MEAN ?

 13. Kmalawi kuba ckudzatha inenso ndkangowina 2019 ndidzaba coz zkuoneka kt kwathu kuno kuba ckoletsedwa kkkkk. tyambe tamanga kaye apolisinu coz nanunso ndinu mbava

 14. Ngati izi zili zoona ndiye kuti mkwatuloso uli pafupi. Akhilistu konzekani. Nthawi imene Joyce Banda adzamangidwe ndiyomweyonso kudzachitike mkwatulo. Yemwe ali ndi makutu auzimu amve nachitepo kanthu.

 15. Lamuro ligwile tchito ngakhale titalalata bwanji komangati odziwa malamulowo afufuza palibe angatsutsane nao atengedwe basi zimatha ndikukambilani izi ngakhale winawe udane nane undinyoze komaine sndinyenyeka lamulo ligwile tchito basi

 16. Zalowa ndale y ppp in malawi, talowelela amalawi ymuthetsa mpingo y mukut amangidwe ine cndikunopo zifukwa zoveka bwinit ap. U shud do thingz kut amalawi akondwe not kut muzilimbana ndi ena atsogoleri akumalawi oliz change

 17. Malawi Police Service,do ur work professionaly without favour,political interferance,all those concerned should face the law accordingly.Malawians want all those on the list to be tried wthout fear or favour,We want Bakili Muluzi to be tried no matter his sm Atupele is in the ruling party,late Bingu no matter is dead but truth should prevail,brutal deaths of Chasowa,Njaunju,Chaponda maize gate and JB,failure to do these honestly,i doubt if Malawians will HAVE TRUST in MPS

 18. they are in fear of losing elections in 2019.Jb is an inocent woman,why are failng to arrest muluz?Thoz who are involved in the 579billion shld also be arrested too.

 19. Boma ili sindilivetsa..Chaponda akulephera kumangidwa chofukwa chani??? Pali nkhani zambiri zomwe amalawi tikuguna mayankho..ndiye mupeze kaye mayankho a izi. Kuphedwa kwa chasowa, kuphedwa kwa njeunje, kupezeka kwa ndalama zambirimbiri mnyumba ya Chaponda,komaso kuotchedwa kwa ofesi yake mpaka pano kuli ziii munangoti mumamgot fufuzabe chosecho mukupanga replace zinthuzo ndi misonkho ya a malawi.. Apa mwati mufufuza za kuphedwa kwa ana ku stadium ya Bingu koma phaka lero kuli ziiiiii…akapezeka wolakwa munthu wambali ya boma nkhani imathera pompo..musiyeni JB apume inuyo mumange kaye nduna 7 zija!!!!

 20. Joyce banda sanabe ndalama ayi, koma anthu amene amagwila naye ntchito ndi amene amaba ndalamazo, coz ziazi bambo zimene zinamuzungulilazo zinali zanachokera ku MCP zomwezonso ku UDF zomwezonso ku DPP zomwezonso zina bwera ku PP, chipani cha amayi, zimbava zigawenga zi afiti zolumila ku mchila, nde lero mukulimbana ndi amayi bwanjiii??

 21. Amalawi Al Ndi Vuto Nkhani Yakalekale Bwanji Osamanga Bingu Ndi Muluzi Ndalama Zoti Mukuziona Kale Kt Amanga Nyumba Ndikukumbilatu Manda Ake Pa Ndalama Za Amalawi Mukulimbana Ndi Munthu Wa Phee!Mayiso A Peter Ndinu Ofoyira Mwina Mumamufuna Ndiye Akukanani Ndi Chifukwa Mukulimbana Naye

 22. Boma la Malawi ndi bomadi lopusa,kotero kuti Joyce Banda sakumangidwa kaamba koti alikunja,,sumuziwako komwe amakhala, Osamuyitanitsa bwa?? ndiye ngati sazabwera basi nkhani itha choncho??? Boma la Mbuzi

 23. Bakha amangidwe basi..akanatha kuyambitsa ziwawa mdziko lino Bakha..kumakana kuti election results atulutse…satanic evil

 24. Mmmmm ine zandalezi zisanditayitse nthawi ndili ndizochita ine kkkkk tiyeni tikasake chakudya chalero osamalimbana ndizitsilu zandalezi zimamadyera limodzi

 25. Warrant of arrest for cashgate cases only? Why? They should arrest her for trying to set the country on fire after she tried to nullify the ballot! During elections, no candidate must be powerful save for emergencies to sitting presidents and not otherwise!

 26. Amangidwe osamusiya mwina mukumuwopatu auzen azanu athandizile aaaaaa chinathawa iye ndichan kamutengen iye akawona ngat wathawa ,,chamba kamutilen zingwezo ,,,,azayange kuno

 27. Ine ndinadziwa kuti pakhalekhale azagwira chachikulu kuchithothola mapiko lero ndi izo amai waku Maula mudzikadya pa tsiku kamodzi mukaphwera konko kkkkkkkk

 28. Ngati kukumawatalikila kunyumba ya chaponda ku Malawi komkuno, ndiye ku america kutalika motani? Mmene munayambira za Joyce banda muja, zaka zikukwana zitatu sopano, ndiye ngati mukumuopa mmayi wabwinobwinoyu mungathe kusaka Islamic state itayafika wathu kuno. pezani ganyu wina Malawi police, ndakatulo tatopa nazo

 29. At first it was former president Dr Bakili Muluzi,he comes Bingu wamuthariKa here we go now is JB ,they stolen billions n billions of poor Malawians. Can some of tell me who have been arrested by those so called malawian police n ACB? Instead to keep on wasting Governments money by taking those people to court and nothing has happened,stop fooling us because all these President comes from the same mother and nothhing will happeny. Political at its best finish and kraller

 30. All these years passed. Why now? Who instructed now. Is police formed now. If they were there why didn’t arrested her that time? Is this campaigning strategy? What about Chaponda threatening to bring the house down if they lock him down.

  1. OK then it’s unfair to other citizens when other cases are moving fast with a speed of lighting. What jeopardise justice is political interfere and orchestral to gain morale. It funny in Malawi for politician to get arrested that then after 3 yrs they say lack of evidence. The justice system is captured and its not independent. Right now Chaponda threatened that don’t dare treat me like trash. I will speak out and high profile people will be implemented.

  2. Man Chimene Mungadziwe Chilungamo Ndi Ndalama Siziyendela Limodzi Ai.Mkazi Ndi Mamuna Ndi Osiyana Kwambili Timaganizaso Mosiyana Amaiwa Kukhala Musogoleli Wa Dziko Sikuti Iwowa Amaganiza Kuposa Ali Yese Ai Koma Ndi Tsogolo Lomwe Anakonza Namalenga,anakakhala Mamuna Sanakathawa Koma Poti Ndi Mkazi Ndichifukwa Anathawa,kumangidwa Kumeneku Koma Sangagone Mu Ndende

 31. Thats the problem of malawian politics full of ironic Malawi wil never dvlp with such issuels DPP Kuseka anthu kumaso kuiwala zomwe iwo akuchita mbuz za mino kusi ,,,,,,

 32. Umbava wavuta kuno kwakatuli boma lamangochi bwanji apolice ngati mwasowachochita osabwela mutatenge anthu amenewa tikuuzani nyumbazawo

 33. Cover up pa nkhani ya chaponda just to divert People’s attention that means all presidents from South are thieves

 34. Cover up pa nkhani ya chaponda just to divert People’s attention that means all presidents from South are thieves

 35. Cover up pa nkhani ya chaponda just to divert People’s attention that means all presidents from South are thieves

 36. Ine boma lathuli limandimvetsa chisoni kwambili kale lonse lija now mwaona kuti mutha kumumanga ysopano poti zisankho zayandikila? Just cout how much money have we spent on investugation process over this so called cashgate zithanso kumayandikila ndizomwe zinabedwazo. Ndeno muyambe process yoti mumumange tiononga ndalama zingati? Remember that this is not just an oldinary person woti mungopitia kukamunyamula kuti mwamumanga there will need for some money to do everything dziwani kuti ndalama zake zimwchoka mmatumba mwathu momwemu. Leave her and focus on development period.

 37. just to west time kodi migwanya ya ku Malawi yasowa chochita eti mpamodz ndi mgwanya wamkuluyo amati commando za ziii, kodi nanga ndalama zimene zinampita ku Ndata zili mpati? Tisamawone chitsotso cha diso la zako chako chikukuknika kuchotsa chitani manyazi ndi munthu wa mayi uyu mukulimbana nayeyu

 38. Akuyenela kumangidwa unless atalankhula za chowona chake amathawa chani, inalipo nthawi imene anawona zolakwika mwa apitala ndipo anawakwizinga yakwana nthawi naye azione .chaona nzako chapita mmawa chili kwa iwe malamulo ligwile ntchito , ngati mwadyela limozi izo ndi zanu ndi nthawi yoti tidziwe kuti ndalama za misonkho yathu inayenda bwanji ? That’s my comment whether you like or not

 39. Interesting that they can find evidence of mismanagement of government finances by JB but, unable to do the same on Bakili Muluzi and Bingu.

  Oh, did the same Malawi Police solve:
  – Robert Chasowa’s murder case?
  – Njaunju’s murder case? Life is wealth more than the $200 plus millions mentioned here. Isn’t it?

  Yes, JB has to come to book however, I would love for the Police to bring justice to Chasowa and Njaunju families first and, have Bakili and Bingu pay back the stolen government money.

  JB should be prosecuted later after 2019 elections – mlandu suola!!!

  1. Then we can start with the imfa of Aaron Gadama,Sangala and the likes,even ng’ombe zomwe amkalanda anthu zija zinakafufuzidwa,Politics aside

  2. Gertrude I support this your idea there is no point letting others free and we fight one case. We have maizegate which is latest. Miseu yosakonxeka bwino but very ecpensive why not investigate these as well

  3. This is politics, you may come up with a good argument to defend JB, but you forgot 1 thing,in this game, who has the power calls the shorts. #ArrestJB

 40. kkkkk koditu anthuwa amawelengela mwanbi woti nbuzi imadya pomwe ayimangilila … ndiye poti amalawi kkkk pepani tiyeni tiphunzile kuchangamuka .. kodi mmene anthu munayanbila kuvota muja pali amene mungandiuze kuti bola uyu? zonvesa chisoni kukuyikani panpando zili nbava zokhazokha

 41. Good move !!!! izi ndizomwe ndimayembekezela. kamzimayi aka kanabweletsa mavuto oti amunamuna sangawapange solve in short period.

 42. M’malo momanga zipatala, school zabwino ndi misewu yolimba komanso kuchepetsa umphawi wa anthu, boma lili busy kumanga anthu.

 43. Amalawife mmmmmm tili ndivuto.Apa zayambikapo anthu tikhala busy ndi zimenezi kwinaku akutibera.Ino ndi 2017,2019 chisankho anthuwa akupanga dala ndi njira imodzi yosokonezera anthu ovota.Tizichenjera anthufe kumbukira za Bakili 2009 last minute anthu anasokonezedwa.Ndiye tikamati amangidwe amangidwe tikamadzalira kutsogoloko titasankha omwewa ndizofuna.

 44. masten ndi deal ,,,,he left the country quietly is at peace with Truph hahaha wasting time issuing arrest warrant adzabwera after regime change where ur are mum be at peace amange Kaye awa lol,,,,,involvement is not the case please use another language

 45. Akanangokhazikitsa lamulo loti Prezident asamafunsidwe za kusowa kwa ndalama ie. cash gate, stealing, bribe, misuse or what ever you call it if the money is less than 10 billion kwacha otherwise no Prezident will come out clean

 46. Boma lolamulidwa ndi zitsiru, mkumakwera pachulu `timanga Joyce Banda`
  Chaponda mwamutaya. Kwinaku mukungowononga ndalama zathu.
  Mukamayamba zinthu muzimalizitsa komanso muziganiza kuti mumadya kamba ka chala chathu, mbuzi!!!!!

 47. Kodi amayiwa anathawila kuti Kumwamba kapena ali pa dziko pompano? Ngat ali pa dziko pompano nanga bwanji osangomutsata komwe aliko ndikukamunjatila konko inetu mzimayi ameneyu amandipweteketsa mtima ndisaname

 48. thats fine, tidikiranso 577 billion ija idasowa before joyce banda komanso 61 billion mwayamba bwino ndipo tikudikira mwa chidwi

 49. Kkkkk iiiii ndiye pano,iiiii amaiwa samwanso khofi uja!! Iiiii ndiye aaaaa aaa ndayamba chibwibwi wina athandidzile chonde.

 50. Zaziiiii leave her alone wodya zake alibe mirandu anatenga gawo lawo komano ngati kuli kumangana ayambe kaye chaponda konkuno pafupinso

 51. Am in support of it..many challenges we r going thru now as country r direct side effects of her involvement in famous cashgate ie delaying to employ our teachers after graduating,no medicine in hosptals…but speed the trials of chaponda & other well known cashgaters

  1. Honestly though late Bingu also get invoved in such kind of immoral behaviour bt many things changed 4 good in his first term & plus a yr of term 2 ie hunger ended,,construction of BICC,MUST,BNS,MBWERWA UNIVERSITY(in advance) to mention bt a few..now lets turn our attention to Dr.J.Banda, 2 yrs in office bt she plundered alot of resources wth notable effects like linkage of MSCE,delay in recruiting our teachers,no medicine in hospitals,freeze aid by donors,mob justice rate incrieases,devaluation of kwacha, the list is endless…she shud face the arm of law, am backing it.

 52. “and then entered the same river paraded the sails, instuted the nets but never caught any fish- Simon Peter-Jesus Disciple”….

  People we are talking of ex president here not a mare person like me……do you recall Bakili muluzi case?…..,u will parade evidence ,present all documents depicting Dr Banda as a theif ….but later u will hear the state closing the case after failing to file a case against her…..watch the space………it will end as that of Bakili……..

  1. go n ask kasambala n his friends they goona tell u who is peter muthalika, cant u see since him the government has never lose a case? u gonna see it bro

  2. ahahaha …..unless wisdom changes its thin line ………This is cashgate ….not murder gate ……compare and contrast the two…thus y u see anthu convictedof cashgate are given lessier sentence …some times releasd on political grounds…….. u recall od senzan, nd this recent one pardoned on 6th july?……cant put a question… mark…..mlandu wa mphwyo…..ukuwavuta…pati…..nanga wa jb azaukwanisa?…………Peter is not court himself court…..to convict people……see how much we coughing prosecuting anthu a cash gate …..nanga jb…..les seee as u hav said

  3. Japierl u r tru jus wait n c.n tis z matter of waistng time its better to focus on our future than busy 4llowing tis wich wil end without final judgement

  1. The funny thing is they actually have no evidence at all, a smoke screen to deflect their failures to fix our economy.

  2. sanathawe JB mumafuna mumusowetse ngati chasowa ndi njaunju.kodi inuyo auncle anuwa akazaluza azkhala muno?green card yaku america ili nthumbayo

  1. Should the whole country stand still simply because ku area 18 kunatuluka bibi? What kind of reasoning is this, baboon? Zaziii!

 53. Mangani chitsilu choba chimangacho first zaugalu basi police yake iti yakumpanje yopanda even njinga yakapalasa

  1. Kunena zoona mayiyu musamuone ngati anali kape ayi ilike this woman too much uzane ndi kape wako wakwagoliatiyo nonse agalu

  2. A John Ndinu Opanda Mzelu Mukhala Mu Shop Yama Somalia Musanyoze Dziko Lanu Inu Popita Kumeneko Munayenda Panjinga?? Maiwatu Tiwamanga Mufune Musafune

  3. Iwe ndiye chitsilu ndinzako opasuka mphunoyo wamva ndipo chakuti chani ndi peter wakoyo wamva kodi ndale zakumalawi akudziwa ndimwana emwe kuti zavuta pomwe iwe mavizi ali tho mkabuludula ukulephera kuona zautsilu za mbwiyako wakwa goliat yo

  4. Ndipo mamuna ngati iwe sinamuone jb ndi mmodzi yomwe kwaine amalamula bwino lero uli kumudziko chifukwa passport ili pa 48 grand ungoononga mitengo uli phee ndiye ukuti fwefwefwe peter ndi boma aaaaaa akulu mwayenera kuvala skert mzeru zanuzo mukufunika muzinyengedwa ndinu mkazi

  5. Check ku ma post anga kapena utenge number yangayi ngati uli pa WhatsApp ndikuonese zomwe ndimapanga 00277632803966 then ndikuuza wamva usalimbane ndine police yampanje ndinasiya kale kuiopa amkafuna kundilanda kabudula ati wa silikali kodi zovala zolandila kumawasata amzawo ngati ndiokha amalandila

 54. UnFearful Dog go for bite not barking coz if it bark the person will think of defence Simuwapeza masten or muli inu mwachita kuuzidwa kuti tikakupezani tikumangani mungayandikile??? Thanks….

  1. shut your mouth Noah.are you amalawian? it seems your from bulundi…umboni upose kuthawa akuthawaku.agwidwatu makoyo.ndiye matupi ake amenewo zima BP zili thooo.akakhale nyapala basi tizikamuonera pawindo

  2. A DPP nonse muli mmadzi chifukwatu dziko lonse likudziwa kuti mbava zazikulu ndi inuyo,ndipo munthu amene mumamunjenjemera pa ndale ndi JB basi.Pano mwaona kuti chisankho chikuyandikira nkona mwayamba kumusakasaka JB kuti mwati amangidwe asazayimenso,but mind u JB sali nazo chidwi za ndalezi mchifukwa chake mukamabwebweta samayankhayi.

  3. Noah kazinga tili limoz fundo zabho ife tzngopanga zot ztithandize milandu yanj yomatluka near nd zsankho nthaw yonsey anali kt?aliense akalow m’boma amamupezela mlandu oti waba ndalama nanga mapeto ake amakhala otan?munamva kt wina wakhala kundende evn zaka zokwana ziwiri?amalawi tachangamukan mu ndale mutha kumangoyamban kma stngapindule.focus on our future MULUNGU pasogolo aztisogolera

  4. Why now hahaha pezani chifukwa china, chomumangira JB kupanda iyeyu kuvumbulutsa mbava mukanaziziwira kuti? Muziyamika

  5. Siza Allahzoxo Apapa,mumabera Limodz Eti? Munthu Anachita Kuthawa Atatisiyira Mavuto Kuno Ndiye Muziti “no Ant Weapon Formed Against Her Shall Prosper”, Wakubayo?

  6. Viva JB,tikukumbukira mu 2009 pomwe DPP imanjenjemera ndikumanga Dr Muluzi koma mapeto ake masankho atadutsa mulandu wake unathera pati ndipo pano uli pati? A DPP mulungu azakulangani….

  7. Hahaha kape noah Mlandu wa Bakili unatha chifukwa anagulisa chipani, koma makoyo sitimusiya. Amangidwe Mbava

Comments are closed.