I am ready to be arrested – JB

Advertisement
Joyce Banda

Former President Joyce Banda is ready to be arrested in light of the warrant of arrest that the Malawi police have issued against her.

According to her press officer, Andekuche Chanthunya, the former President will cooperate with the Malawi Police whenever they want to arrest her following the warrant which the police have obtained.

Joyce Banda Politics Malawi
Banda says ready for her arrest.

According to Chanthunya, they are yet to receive the warrant despite the issue going hot on local media but he assured Malawians that the former president will cooperate when all proper procedures are followed.

He said police have not yet made any formal communication on the matter. Chanthunya yesterday visited police headquarters in Lilongwe to gather information on the case only to be frustrated.

He was quoted as telling a local radio station that while at the headquarters, he was being directed from office to office. The former president’s mouthpiece went on to say that he did not even meet National Police Spokesperson James Kadadzera.

Malawi’s first female president is subject to the arrest warrant over her alleged involvement in the massive looting of public resources dubbed cashgate, during her tenure of office. She left the country having surrendered her presidency to Democratic Progressive Party’s Peter Mutharika in 2014.

Since her departure, she has been a wanted person as some people suspect her of having had a hand in the corruption scandal.

Advertisement

584 Comments

 1. DPP YASOKERA MAMA AWASIYE APUME BASI, NTHAWI YA BINGU ANAZUZIKA KWAMBRI, APASO AZUZIKESO? A DPP ONSE ALIBE YESU MUMITIMA MWAWO, MALO MOTI AKOZE DZIKO UKULIMBANA NDIYA AMAYI, ATANI? A PETER ZAWAVUTA

 2. Mwezo umene umuyeza nawo nzako uziweso kuti iwe nso uzayezedwa ndiwomwewo: Amai asiyeni Mukawamanga muziweketi Voti ya 2019 Iwapeza komweko

 3. Come Beloved Mother We Miss U Mum,u Deserve Respect Mum,nthawi Yozunza Mzimai Siyino Only If U Wish Kuti Zako Zikudele Ndiye Uzunze Mzimai Komanso True Malawian Like My Self Wont Accept Kumangoonelela Mukuzunzida

 4. Am here to share my great testimony as a member of the most richest club on earth called Illuminati. I am so happy today ,to share my great testimony to the entire world. I almost killed myself because of level of poverty in my life and my family, until I saw post Lady sharing her testimonies of being a member of illuminati, and she drop the number: +2347085503341at that
  particular time, I did not believe it, but I decided to give it a try
  because I was hopeless, but since I became a member of the BROTHER HOOD CALLED ILLUMINATI, there is a great turning point my life and that of my entire family.

  I USE THIS OPPORTUNITY TO WELCOME YOU ALL TO THE GREAT TEMPLE OF ILLUMINATI. JOIN US TODAY AND become rich and famous in life and be like other people and your life we be totally change.

  The great Illuminati is an influential club or society formed by a fervent Academic, Adam Weishaupt in Balvaria, 1776. The club as its name suggests, was a group of intellectuals who came together to in still discipline in themselves, infiltrate government agencies, and create a new world order. Are you a business man or business woman, politician, musical, driver, banker, student and you want to be very rich, powerful and be famous in life. You can achieve your dreams by been a member of the Illuminati. With this all your dreams and heart desire can be fully accomplish, to be a member of the great Illuminati then you can contact our
  Supreme Leader +2347085503341 what so ever you need in life, contact our Supreme Leader on
  +2347085503341call and whatsapp contact: +2347085503341

 5. i cant believe someone is barkinģ âround claiming joyce chitsiru banda is nt guiĺty!.utsi sufukha opanda moto..let her come…if u thinķ peter will jst stare at her…COMEEEEEE!!!..JOYCE!! COME WE HUNGRY FO U!!!

  1. You could have made a point without the “chitsiru” word you know. …n it would have made a whole lot more sense

 6. Yes,indeed malawi police r not investigating properly that case,chifukwa mtsogoleri wina aliyense mmalawi muno akachosedwa paudindo mumati amangidwe,kodi umakhala umphawi kapena kusaziwa ntchito yanu? mama asiyeni apumule. paja kumalawi kuno amangolembedwa ntchito asilikali ndi apolice cholinga azingotisokoneza mmakwalalamu kuno kudziko lopanda nkhondo.

 7. Pepani malawi! Mukhululukireni mayiyu,mkazi olo angakule bwanji amaganiza ngat mwana mwina sankadziwa kuti adzachoka pa mpando

 8. Nothing to fear mum, i think dis government now is seaching de way hw they can steal our money. So they want to use you us money transfer 4m government. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk… Mukunamatu ine pambuyo pa JB nganganga……………..

 9. If arrested,what will the common people get.What about former presidents and other ministers?Nanunso mudzafufuzidwa nthawi yanu ikadzakwana.Zopepera,musandipusitse wakhatene.

 10. I Hope dat JB she cnt come home again cz she haz evry where she iz staying n tzingovutika ndfe an2 amene timakavota but de main problem chipani chikalo mu boma chimangoti chapeza ndalama mulibe mtsogoleri yemwe adzatiuze chilungamo palibe ovutikafe tzingovutkabe enawo ndkumangopitilirabe kulema

 11. don’t start poluting da enviroment as we go closer to the coming elections its dere right to.if u r worthy to stand steedy for de battle kkkkk check t out

 12. ndale zafika pamwana akana phala bingu anaba zingati? Bwanji tikumangeni inuyo ngati bale wake? Siyeni munthu

 13. police ya malawi timaidziwa imayamba zinthu koma osamalizitsa,Mlandu wa Dr Bakili Muluzi udathera kuti?ndipo patha zaka zingati kuti uthe?mai Banda sakuopa olo kuteketseka ndi mbwelera zanuzo poti mbava zambiri mwazibitsa kuchipani chanucho,nanga mukampeza osalakwa muli okonzeka kumulipira ndalama zankhani khanizo?

 14. it gonna be a very long jouney for audience to understand the fact,kampen sapanga through kulimbana kumanga atsogoleri,show your ability through your intelligency,oh a pitala mwapenga

 15. Tikufuna 572 million irukutu angaru a dpp atipase maromokoza ziko mukuyambazamurandu chocho kumatizikoratu ndirosauka mukurisaukizandiabomanu ife turemera ndarezanuzo zopusa tajozani ziko maromokwera rikutsikalasikirabe mbuziyanu pitayo wachitachani chazeru chazeruvhakesi kumangorimbanandiazao mbuziyandu kashinget mese inachokera ku dpp jb wayionesapoyera kuti adpp asowesandrama pomuonakutinsi mzimayi kaya alenemuziza votanu ine chupanichangz ndi mulungu basi sindizavotaso moyoyangaose voti yangasumuzaiona mpaka murungu azaweruze

 16. Ndalama zathu mudamangira NDATA tikuzifuna.NDALAMA ZA KAYEREKERA MINE ZIKUPITA KUTI?2019 Tionana tizachita kukumangirirani Ku galimoto mku MAKUKOKANI.
  TAONANI KUKAMWA

 17. Kumanga Jb Or Kusamumanga Palibe Chosintha,bolaso Boma Lake Despite That She Was Somehow Clever,malo Momayesa Kuthana Ndi Ma Current Situation Problems Muli Busy,kuganiza Za JB,BINGU MUMUMANGA LITI? Malawians,icry That Am Part Of Them,anthu Okonda Timilandulandu Ee Kukanika Kuthandizana.Inuyo Mumangidwa Liti? Sikutitu Simusolorapo

 18. zinthu zakuvutani pano mwngonganiza zomubera zimayi nthaw yonsei munali kt smumutha zimayi ameney ur just wasting ur tym nd zinthu zot sztithandiza ife amalaw welcome back mam

 19. Ready to be arrested wen you are living in a self imposed exile? If you are trully brave and innocent, this is the tym to come back home

 20. Africa’s problems is fighting themselves,,,,,
  Do you know how much cases obama,hillary clinton have?
  Respect our formers!!!!

 21. Hahahahaha!!!!! Voti ikayandikira mumafuna mudzichuluka nzeru. Apolice nthawi yonseyi munali kuti? Mwalephera kumanga mbava zikulu-zikulu zachina Kamuzu,Bakili, Ndata and their followers nde mukufuna muonetse udolo pa mzimayi? Police inatha kale ku Malawi pano iriko G4s. Hahahahaha!!!! Joice simum’manga Hahahahahaha!!!!! Ngati mumangomva kuti mwala wa legeni umapha munthu muona nthawi yake ndi ino yopherana m’mitochi we are going to see where you are going to arrest her!! Mum ngati mukundimva don’t be shaken enjoy your life izi ndiza chamba azingomwerera ku America komwe amathawirako akaba ndalama

 22. Aaaaa abwele azamangindwe pepani nose amenesi simukukondwakuti azamangindwe pazakaziwilipalibe chimene ananga kukanika kumaliza chipala chakwaokwa amuna ake kumaliza bank kumuzuzu Peter wamaliza pano akukoza museu opita nkhata bay to mzuzu koma iye anangoba ndalama olo chitukuko

 23. So it has really shown that out police is the worst police in the world that can’t perform its duties with speed.
  We had the death of Chasowa up to now no progress
  Three years since JB left government and you tell us you were still investigating and once she is arrested, it will take another five years to conclude her case yet you say you have all the event.
  Vuto ndiloti polices service is not yet reformed and it is being moved around politicians and also headed by old JCE officers

 24. I guess this woman is significant citizen, that is why everyone is missing her. Dpp, ikungoti why masten is away, Kumudzi akutinso why masten is away, pa bawo ya munsika akutinso why masten is away. Every one is missing masten. Achina Peter akhala zaka zambirimbiri ku america palibe anawafunsa, koma amzawo angokhalako 3 years yokha ayamba nawo kunena why masten is away, bwelakoni mwina ndale zingazakomeko kuno masten

 25. i dont c any benefit being get during and after the arrest of this woman…..apolisiwo akungofuna azabepo mafuta agalimoto kmanso azanyamure matora pasikuri….Xausiru basiiii….Bingu nde akammangira kt nanga bakili maruzii?????

 26. Kaya mutani or munenebwaji koma zanuyo ndiwandalama zizampulumutsa pamene iwe ndi ine aphawi kampopa adyela kumtiko tikulimbana ndizinthu zomwe sitingapeze mphindu izi ndindale mmene zizathele simuzaziziwa chifukwa ndalama

 27. IT’S UNFAIR TO AREST OUR FORMER PRESIDENT DR.JOICE BANDA.WHAT’S WRONG WITH HER?IF YOU WANT TO A REST HER,YOU MUST ALSO A REST BINGU WA MUTHARIKA INCLUDING HIS WIFE CARISTA,

 28. Koma mtchona uyu wasowa zochita Kogulitsa chimanga anthu kumachita kugona ku adimaki komweko koma osagulitsanso.JB abwele usamumange koma umupatse boma kuti atigule chimanga. Umange chaponda ndiye mbava

 29. Sindikuona po chomumangiri coz ndi ambiri mbiri omwe anaba ndalama zaboma ,,nde olokumumanga nde kupindula chan ndalama zinabedwa kale ,,,malo molimba ndikuteteza ndalama zatsalazo kt awo alipamenepowo asabe …mukulimbana ndi zaziii …mavuto onsewa osalimbanana nawo bwanj …komaso kuli amuna ambiri mbiri enaso Ali m’boma momwemo mpaka lero osawa manga bwanj koma mulimbana ndimunthu wamayi nokha manyazi mulibe monga?!!

 30. They will get you in Pretoria,where you’re hidding through Interpo….. have seen you in Pretoria west for several occations…. you must be in jail!

  1. this thing so called Bushiri have failled to protect you in true God “Almighy God whom I save Has done so…….. to hell where you belongs to ypu must go…… think about our mother Malawi how poorer is today and you’re outside chips and baggers while the people of Malawi remain poor and homeless…… you will end up in hell mum. ypu must be arrested by Intrpol or else will hit you right here in South Africa!!!!! be warned!!!!!!

  2. Gerald Davies Mbewe ur bitterness will not take u anywhere and u are contracting urself. Why not hit her before coming to social media since u have seen in several occassions. Am sure u are among those kind of people who are just only clever on Social Media but cannot act upon. Dont blame her or anyone for ur poverty, no president cannot make u rich if u dont work hard. U left Malawi for RSA should we say u run away from ur country? Lets be reasonable sometimes and let the court prove her guilty. This type of mentality is what is killing Malawi, we stop working and start minding other people’s business while they are progressing and we are becoming poorer.

 31. Osamanga jb kung’owafusa kuti anthu amamba mmnjira yanji .kenako nkutseka njira zimene anthu amamberazo.(mundipange add pa whatsapp yanu ya malawi 24h nambala yanga ndi>0997241587.

 32. Jb Akaba Amamangira Manyumba A Anthu Osauka Koma Inu Mudya Nokha Mkumalemela Amphawi Akutupa Chifukwa Chosowa Zakudya Mthupi Kkkkk

 33. Mudali kuti? Pano pomwe mukuona kuti kampeni yayandikira nde mumvekele “ndikubwera” Ooo teroni poti kuno ndi kwanu koma musaone ngati muzasowetsanso mafuta kusekeleza chitukuko cha doko ku Nsanje mmm sadzakusekelerani Pitala poti ndinu yemwe mudayamba kumunjata nzanuyu nde nanunso muzanjatidwa Mama kuno

  1. Yaa komanso palibe anadya zochuluka choncho in 2 years 250 million dollars. She is not mom anymore but we call her now a big criminal.

 34. Koma Zinaz Ndizopanda Nzeru, Olo Kum’manga Zopanda Phindu, Mayi Joyce Banda Ndi Munth Oganiza Heavy Osat Mbuzi Zinaz Nanga Bwanj Akanam’manga Chaponda.

 35. munthu akamangidwa amabwezanso ndalama?koma zinali bwino nthawi ya amayi koma pano akuti mutu wa ma degree kulephera kulamulira hehehe! shame!

 36. Amakapuma nzoopweteka zimene zinachitika zija kumubera ma vote Ali pampando zikakhala zakubazi mbava tonse taziona tokha.

 37. Musiyeni Jb Coz Ur’e Failing To Arrest Chaponda , Bakili. Insted Of Developing This Poor Country Ur’e Buzy Againest Oppoz Leaders. Amai Anali Amasophenya Osati Americano Futsa Wa Ntambe , Bwampini Ameneu

 38. Sichifukwa kukhala munthu wa mkazi ai nanga amunawo mukuwaoperanji? Amakuopsyani eti? Bakili ndi Joice adayamba ndindani kuba ndalama? Mumamuopa eti? Osamayang’ana mtundu ai. Tiyeni chilungamo chiziyenda ngat madzi AMALAWI OSAMAYANG’ANA NKHOPE.

 39. Mukanankala momo bwedzi ziliko bho koma kuba nkuthawa nkukatukula maiko aanzanu, pano nkumati am ready 2 b arrested, kkkkk kwanu kwanu,or no police warrant mumakufuna kumudzi.

 40. Zatani kut mumange lero?. Thawi yoseyi munali kuti? Nanga Bakili amangidwa liti? Nanga ndalama zinapezeka ku NDATA zija munuwake adzamangidwa liti? Nanga maize get adzamangidwa liti? Kodi tinene kuti poti muli mu m’BOMA ndie kut chilichonse chilibwno etiii? Ayi osamatero yambani mwayang’ana zanuzo.

 41. AMAI MUNALAKWITSA KUTHAWA!NO SECRET UNDER THE SUN!APA DZIKO LAKUCHEPELANI!!!PEPANI!!!!!PEPANI!!!!WELCOME BACK TO MALAWI!!!!MRS PRESIDENT!!!!!

 42. Boma pammawa lizalipire Joyce mwammanga opanda milandu misonkho yathu izalipire? Ndale zaziiiii inu olo ine ndikutumeni kuba inu kugwidwa ine ndingavomere, ndikukaniranitu chifukwasimunandigwire sono president samagwira ndalamatu

  1. kkkkkkkk iwe osekesa eti? akummanga opanda mlandu monga haaaaa suli kumudzi kuno ase cashgates scandal mwini wake ndameneyutu anthu angapo anatchula mayiyu kuti ndamene anapindula kwambiri ndi scandal imeneyi. pepani ngati nkhani siukuiziwa ndi bwino cheeeteeeeee mpaka uyitolera nkhani ija

  2. eeeee a China Lutepo achina Kasambala anatchula abiti Mtila kuti ndemwe anapindula zedi ndi cashgates scandal sono iye amakana ati iye ndamene anapangisa kuti nkhani ipite poyera ngati ku court ,pali nzeru apo

 43. Kodi munthu akalamukila dziko ngati waba amamangidwanso, musiyeni musamumange. Tsogoleli afree kuba ndalama zaboma musiyeni musiyeni ndiyo democracy imeneyo .

 44. What obout Bakili Muluzi, Bingu Wamuthalika, and Green card himslf, problem ya Malawi Police imagwiritsidwa tchito ndi ma politians, Mulandu wa Bakili, Bingu sizikidziwika kiti zilipati mukutulutsanso mlandu wina what for

 45. WITHOUT U MAMA, BWEZI TILI MU MDIMABE, UR THE ONE WHO INTRODUCED US TO CASH GATE & WE THANK U FOR THAT MAMA
  BT B4 U GET ARRESTED MAMA,
  #MAIZE_GATE
  #EIGHT_MINISTERS
  #CAPTAL_HILL_FIRE
  #NJAUJU_DEATH

  MUZIMANGIRE LIMODZI INU A #DPP

 46. Talimbaso,come And To Give Us Makwacha Anthu,tikayesa Simudzabwera Your Most Well Come Amama Athu, But Dont For Get To Bring Makwacha Athu Munatitengerawo.

 47. ndizazii mungofuna kumuchotsa tindalama alinatoto tidatopa nazo zomati munthu akaba ndalama ndikumalemba nkhani kt mumanga kapena wamangibwa mission yanu ili yofuna kumubela naenso ndi #zazii..

 48. You can’t arrest JB that one is third powerful woman in Africa,and that one she is not just a person in Malawi but she is former head of state you can’t compare with other bullshit that you talking about n she is ready for any attack,if you remember that time she was arrest you bcoz you were not the president n full of sheet that is why she was doing like that,,,,,she musn’t come home bcoz of what??????

  1. Malawi is a democratic country n there is no life president in our country Malawi it was happen dat time coz we were not in under federation rule,,,,,,you can’t just arrest JB never she’s got right to explain with no fear and nothing wrong to JB but DPP is sorrounded by misguided who just want to enrich themselves,,,may fire upon you all of DPP government and all corrupt police men,soldiers,cabinet ministers,lawyers,judges,including you Malawi 24 ur real foolishness

  2. Pepani Baba Poti Mumawakonda Mamawa Koma Poti Analakwila Dziko Akuyenela Kumangidwa Basi Anakakhala Osalakwa Sanakathawa Osabwelela Bwanji Kwawo Ngati Ali Aphanvu Kuposa Malamulo A Dziko.Abwele Adzalongosole Zomwe Akudziwa Kuno Ku Malawi,ndipo Musaiwala Tikangwila Wakuba Timaocha Atisamaletu Mamawa Aotchedwa

  3. ngati ali osalakwa anathawa chani? iyeyo anamulowetsa mzakeyu mu cell naye akalawamotu. mphamvuuuuu siziposa lamulo

 49. To be honnest the gorvemen would have started with the issue of 72 b case coz its where of the whole issue begun, and am no dout our presdent pro. A .Munthalika can be involved we start counting by 0,1,2,3 so on and so fourth. Why just jumping to 3 its long they have failed

 50. The way Malawi is now… Even her arrest will mean nothing… Nothing will change… How many people have misusing our money is these governments,,, and now because she is a woman then you want to be perceived as if them are innocent…

  Kwanga NDIFUSO,,,, KODI ALIPO AMENE SANABE NDALAMA ZA BOMA, AMUMANGE MZIMAYUU? Concentrate on issue that can help to build Malawi, unless you are telling that she has to come and give all the money you think she got. But putting her behind bars, what will the national benefit. Waiting to see wat will happen soon

 51. Ha! What a shameless and heartless woman…..Malawi is indeed poor since time immemorial but you deliberately hammered the last strong nails to the coffins.Apart from the famous cashgate,”the kwacha devaluation is another sector i beg not to ever forgive you.You must hasten up you coming,maybe we can get consolation and covered from the wounds that you caused in our hearts

 52. Put your hands up mama & don’t move. You have the right to remain silent.
  Anything you say can and will be used against you in a court of law.
  Inu wakundende baxi mayi

 53. Mphwiyo ndiamene watchura amayiwa, koma phwiyo ukangolimba mtima , anachita kukupana chamtundu wanji, anyway palibe di chifukwa choti ukavundire kundende wekha pamene ndalama anadya zambiri ndi abiti mtira yu

 54. munjateni bas monga mwamchtira chaponda ine nilibe na polobulemu ndzdyabe denje langal kod mukumuykra kumbuyo inu anakunyemeran et kkkk wher did v cashgat take place?..amangdwawa ndzislu? shut up! amangdwe bas

 55. Mmmm kaya ndi ndale kaya ndichani mmene ena munganeneremo koma nkhani ndiyot ngat anabanawo amangudwe basi amzake ndi awo mpaka ziwalo zikufera kundende konko iyeyo nde akhale ndani ngat aki osalakwa zizaziwikira pa court basu koma abwere basi

 56. Mxiew….poor Malawians…so every former president will have to answer questions and be jailed??? Noooo its almost every head of state in every country they might have a misuse of funds and made afew wrong decisions…. Take an example in America…. When did they accused their former heads of states?? After so many things and decisions that have caused so many deaths…..Joseph bush,did he ever get arrested?? So why here in Malawi? When Mrs banda took over the government there was a lot going on,bingu government spoiled everything and she only tried to pick up from there,one could leak the cashgate saga and its now all her blame….so if she will be arrested,will all that money return back to the government?

 57. Arresting JB will be a grave mistake DPP have ever done , we have to admit that this woman is highly blessed and she is untouchable, remember when you she was fired from your party , people were having heart attacks and Cardiac arrest , try her this time someone will have Yellow fever , when the Judiciary will issue the warrant of arrest for the whole cabinet.

 58. Zachamba basi…anthu onse amamutchurawa samamukonda?abwere aonetsedwe sesemile ndimbava nanga anathawachani kuno?2014 ndikubwera koma kuri ziiii,2015 ndikubwera koma kuri ziii,2016 ndikubwera koma kuri ziiii pano 2017. Osamangoti zirizonse ndale zirizonse ndale iyahh abwere adzafotokoze kuno

 59. Mr President Sir penan pake mutu wanu unaphwanyika mbali imozi. Zoona kusiya nduna zakozo pamozi ndi iwe wekha pa 5 hundred billion ija munaba kulimbana ndi amai? Anthu Oyipa inu. Bwanji mungotipha tonse chifukwa mwatizuza kwanthawi yaitali ife amalawi.

 60. Komatu kufufuzaku tamafufuzani zonse, zophana zijaso tidakakonda tikanazimvankuti ziri pati, anaphao ndani and the like, osamangofufuza zimodzi zokhai

 61. Komatu kufufuzaku tamafufuzani zonse, zophana zijaso tidakakonda tikanazimvankuti ziri pati, anaphao ndani and the like, osamangofufuza zimodzi zokhai

 62. Kkkkkk tisathe mawu amalawi Muluzi anaba ndalama zambili mbili Ali kut pano ndiye Amayi atan stop dreaming manyasa panjatu tikuyandikilatu zisakho panja

 63. Politics is a game I can’t play or even wish to watch it being played

 64. This former president of Malawi is very ugly … Indeed cant compare her with Zambian ladies .. Ayenda chabe Ku Jere! Malawi police will with bicycles to arrest you … Poor a country with no police vehicle

  1. Aaaaah wat z de connection btwn her uglyness en de story?? Wat about police vehicles??? Were z de connection?? Can u elaborate more mr zambia boy

  2. Comrade no one is ugly in the prences of God, we are the same coz God created us in hiz image and for ur on imformation Malawi is not a poor countly sorry but i think ur mind is very poor,may the Lord have a mercy on u budy.

  3. You very wrong … Kumalawi u are still using black berry 9630 you think its latest… When you see Madonna you think america is in your country ! # shame!

  4. Iwe Ka rain season kupusa , think before you talk .. You are just disappointed with your country were police men are using a bicycle!!! Kkkkk but anthu aku Nyasaland?? ¿ unga dabwe

  5. point of mr zulu, malawi police z not using bycircles, they hav land cruisers which r very expensive cars, kmanso zakumalawi zakukhudza bwanji? Ngat uli wanzeru osamangopanga zothandiza dziko lako kumeneko bwanj? U r a fool

  6. Precious ndiwe opusa … Your face resembles big problems your country is facing now … ?? You think bushiri is your God kkkkkk false !!!!! Us we don’t tore late false prophecy we are cleaver !!!#via technology..

  7. Malawian people are nice.am Zambian and love that country. Please stop insulting them.any beautiful Malawian lady inbox me…kikikikiki

  8. Rheo am not worried about my engleshi .. As long as you got my point you fool ! I thought you a genuine a guy… Kupusa ! Check your profile picture ! Decent but your re a stupit Malawian! # shame

  9. Don’t waste ur time insulting people Mr Zulu what are you gaining from that? Ur saying we are poor are you the one who is taking care of us? We have seen rich countries and rich people but they are cool, so watch ur mouth, kazambianso mkachani?

  10. mistone mind your business even kabwe is very poor also ndola the road are poor go around to kithwe you will se that zambia is another impoverishi country

  11. I know zambia any coner and zambia its not rich country rich country wit somany potholes all over the country from chipata ndola kabwe kitwe what shame place to be hhhhhhh kkkkkk fill sory to you boy

  12. Black China you are u dreaming .. I will look for your relative who are illegal immigrants in zambia and report them … Soon they will be deported..

  13. #zulu you are nothing but a piece of shit,..lemme not hide this from you, you are a shameless creature with nothing but rotten brains inside your oversized head. I don’t remember if I have ever seen Zambia among the top 15 richest countries in Africa. You are a day dreamer, probably a fool, holding a Rubber band tied phone, pretending to be rich and talking shit after a long masturbation. Poor black Asshole….*****Try fucking with me and regret it*****

  14. We don’t no? How we discrable Him, sorry God forgive us small zulu nzeru ulibe sukuziwa za ku Malawi nkhala phee panga zaku Zambia bushit

  15. Bertha , emma and prince … You are idiots .. Why do u kill albinos to get rich? Ndimwe opusa … Poor boys and girls of mala .. Bushiri is your god because you like free things … Us we have copper

  16. Wasiyah ? Even your means ” you have left your brain in the toilet and that toilet is a pitta trine not flashable cause Malawi is poor

  17. Yah chilungamo chimawawa chikamalakhulidwa.mistone anthu akubakila mbamva zomwe zidaba chuna chadziko sorry to them koma zomanyoza malawi ndithana nawe pokuuzaza kuti kuno mahule onse anachoka kwanuko ku zambia koma bushiri unenayo ife timangomva ukamupatsa chuma dzina la upolofeti kuti akudalitse ife timangoti ndi mwana wathu wamudzi tikhonza kumutuma uthenga wamaliro

  18. Sizikugwirizana nd nnkhan …..when u said she is ugly. What d u mean ….d u min God didnt know how to create. If is that why dont u create ur own human being which will looks beautifull the way u want
   Shame on u brother

 65. to be arrested doesnt mean ure guilty bt rhe court of law does so u can say alot here bt we hv never head her side ov story so keep ur accusation at bay as u knw we still hv to wait 566 billion under dpp whn zat madala was incharge so we cant say he is guilty at all

 66. vuto la munthu chala sichidziroza. ukapondo ose wachita peter pa 577 bilion nde aziwauza apolice kt agwira BANDA Y? William Tebulo Woyipa Sasamala John Chakwera Mia Mzika Ya Malawi Eisenhower Mkaka Vincent Wandale Zinaumasiyaa Wa Chanza Wofatsa Koma Wolowelera

 67. Koma muthu ukakhala sogoleli chithu chikasowa umapedza mavuto nyanji anali zimai hahahaha inali thawi yazibambo uchuluka mzelu kusolola makwacha amai akungogona avekele zilibwino koma ziko lapasi losawusa zedi kuyu dzodya ana zopota wakulu pepani mai

 68. Anthu ena mumamva mukuthamanga, Kodi anaulura kuti kunja kuno kuli cashgate ndi ndani? Ndalama anaba ndi bingu ndi agalu Ali panowa. Koma chifukwa chosadzitsata zinthu, munaona ngati anaba ndi Joyce banda…. 572 billion inayenda bwanji? Bwanji osayamba kukufuza Kaye zimenezo?/ chilungamo mudzachidziwa patsogolo….

  1. Amalawi sitizitsatado zinthudi chifukwa cashgate eni ake no a UDF and DPP. We have an organisation called INTERPOL yomwe imagwira ntchito pofufuza ndi kumanga munthu oti ali mziko lina. Bwanji nthawi yonseyi sanagwiritse ntchito organisation imeneyi kuti mayi Banda amangidwe?.wake up Malawi!! We are busy chasing the wind and that’s exactly what DPP wants us to do. They are very selfish people but unfortunately you can’t see that. Pompano wina Nyumba mwake mwapezeka ndrama zankhaninkhani koma still sanamumange munthu uja pa mulandu osunga ndrama zambiri Nyumba zomwe it’s a crime. Ngati dziko lathu lipitirire kuvutika it’s not the politicians fault ayi but it’s our own fault .chifukwa tikudziona tokha zomwe zikuchitika koma we chose to make noise only among ourselves kotero kuti these politicians amadziwa kuti olo abe amalaeife sitipangapo kathu.so we need to be united posatengera kuti inu ndi a chipani chiti.ngati tisekerera nkumaikira kumboyo makhalidwe a umbava ndi umbanda zimanhoonetseratu poyera umunthu wathu and it also shows kuti mmakomo mwathumo mabanja athu samayenda chilungamo so let’s unite Malawians and fight against corruption for it start within you.

  2. the law always arrest the one caught stealing or mentioned in connection with it not basing on speculations that’s how i see it

  3. Phuma,poyankhula guys ena kutukwana,kunyoza zija zosakhala bwino,kodi zili ndi phindu lanji kunyoza munthu kaya kutukwana munthu? (chilungamo ndiye chidzamasule zonse,pewani kunyoza atsogoleri.) pewani kunyozana sibwino choncho ayi.

  4. Gift if u don’t mind why u are talking about Bingu? She hav to be arrested this is what happened in Africa if u are out of power and this clue their day is coming

 69. It’s not easy for an ocean to dry if rivers still flows to the ocean unless all rivers are diverted to the sky.arrest not arrest but the truth is life is good for the rich.as for us poor people let’s just drop our comments here and make them famous to the world.

 70. Bwerani mayi ma dora wo akufunika kuno ngati ndizitukuko zapangeni konkuno zimene mukupangazo mukusaukitsa dziko , zimatha ndikukambila osati kuthawa thawa .

 71. She should have been ready for the arrest even at the time when the buses were brought to the country but she was the president. Abwere adzachite clear dzina kuno

 72. Bwanji apolisi mukupanga za ndale? Mumangotumidwa zilizonse simumadziwa malamulo paja mudziyamba mwapeza umboni kuti zomwe tikuchitadzi nzolondola mudzitsatira ndondomeko chifukwa ngati zili zimenezo muyambe kumanga onse ndatchulawa

 73. JB you have yourself to blame. Why didn’t you arrest and imprison Mr. Ibu on treason charges that he wanted to assume the presidency on the death of his brother? That was crear treason. But you left him scort free. See now dziko lakutembenukirani mai. Apa ndiye ndiye mbava zokhazokha kumangana.

 74. Anthu okuba onse awa,mai Jb akafika kumalawi kuno awaulure amzawo ena onse omwe amaba nawo ndalama, chifukwa ena omwe adari mu PP mai Banda ali mtsogoleri wamalawi adalowa pano chipani cholamura akufuna azidziwonetsa ngat abwino pamene sizili choncho, Iwo ndiamene akupereka information ina yokhudza mai Banda momwe adasakadzira ndalama, ndicholinga choti awoneke ngat Iwo abwino,ndili ndichikhulupiliro kt mai Banda akamangidwa achaponda nawoso amangidwa ndi maize gate yawo ija,ngat sizitero ndiye kut bwana Muntharika akudziwapo kanthu paza bwana chaponda.

 75. Areested for what? Firstly arrest Bakili secondly Bingu or impound some properties belong to Bingu owed by his gashfate then arrest amayi cant we proud of the first woman president in Malawi

  1. musaiwale kuti PP and JB sadawinepo chisankho dziko muno adangopitiriza mpando wa masiye uja.malemu dzimkakhala kkkkkk

 76. Dzana lomweli mwatiuza mmaso muli ngweeee kuti a Joyce Banda abwere ku Malawi athandize pa chitukuko. Lero mukuti mufuna muwamange.
  Anthu oipa inu. Mundisamale

 77. You m’mayi you are most wan’ted here so do fast coz ukamavuta we can just kill you ngati mmene unachitira ndi #AMALAWI ife tatopa kunotu isaaa!!!!

 78. Please guys don’t support politics. That’s squandering of time. Let politicians collaborate themselves because it is really a very big secret among them that we citizens aren’t know. We mainly differ in supporting two parts of politics ( ruling and opposition). Do not worst your time supporting profitabless things in your family life by letting others gain via your power. Instead, go with time, find means and ways on how make your family live a happy life that gratify our Lord. Stay away from danger!

 79. You m’mayi you are most wan’ted here so do fast coz ukamavuta we can just kill you ngati mmene unachitira ndi #AMALAWI ife tatopa kunotu isaaa!!!!

 80. All talks will end when Jb come back to her motherland some pipo are just commenting badly but when she come back they will not even go near her and say what they saying now no one is perfect even bwampini himself after all i cant even see development during his leadership

 81. She is innocent until proven guilty by competent court of law. Cases shall never be examined in media for fear of prejudice and perjury from public opinion. Indeed it is important to bring to book all those people involved in plunder of Malawi economy through abuse of office, embezzlement, corruption, dishonesty, looting, mischanneling, mishandling, theft, crooking, hooking, booking, misappropriation, extravagance and mismanagement. Malawi will be blessed if all suspects are traced, found and punished.

 82. Bakha..bwera unya uwona…Cashgate master minder wache nde iweyo..ndipo akanangoti tikakugende pa kamuzu stadium..

  1. Anachita bwino kuthawa amaliwongo ake amenewa akanangomumanga asanafufuze ndipo amayi ndi dolo akamadzabwera nthawi ya campaign munayitha amayi wina akhaula

  2. ndamuona sunday mu shop ya spar ku 4ways shopping mall.4rm there to jozi its 16rands joburg to malawi 1400rands kkkkkk

 83. Its almost three years now since JB came out of government.. And the reason why the government stayed phwi without making any arrest is because alibe umboni…and now akuti akummanga koz of what people are saying buhahahaha….anyway let’s see how it ends

  1. i believe that it is the wish of peoples saying to arrest JB and not the wish of government because those in government will follow suit @ the end of their term of office,do not forget that “khoswe wapatsindwi anaulula wapadzala~.

 84. We can say alot of things but we should know that all these leader we were choosing plus the one on the sit (mbava zokhazokha) go to cashgate,maizegate and the time of yellow party

 85. Muzingokhalira yomweyo yomanganayo mayiko oyandikana nanu akupanga chitukuko. Kodi doko la Nsanje pano linayamba kugwira ntchito?

 86. very brave woman she is the one who ask for auditing in government,,,,,she is still innocent until proven ,,, ,,,,,,lecture me guys kodi involvement can seek arrest or the could only ask her to clarify what happened,,,,,,,, what about the 566billion watching u from a far

  1. amangidwe basi.akanakhala kuti sanathawire kuno bwenzi atamangidwa kalekale.tili nawo kuno akupanga share pa space ndi mrs ……. usovenge kkkkk

  2. hahaha koma guys ,,,,we have never hear that his company or charity organizations is directly involved right koma tagowakumba ndie tione ngati atakwanitse

  3. That’s nonsense, samangidwa yekha ngati iwe ukukhunzidwa ziwa kuti mbava yathaziyi ikangolowa muchitokosi iwenso akakutchula nonse mulowa,kulankhula ngati wanzeru pamene kasambala ananena kuti amayi abwere,

  1. Hahaha Inu Simumadziwa Kut Citizen Aliyense Amakhoma Msonkho?? Mukakagula Bread,kaya,soap,sugar,mumakhara Mukukhoma Misonkho,and Zangosonyeza Kuti Ndiwe Kapolo Wachabe Chabe Sugwira Ntchito.Wubwele Wuzawone Pay Slip Yanga Msonkho Womwe Amandidula

  1. Amai Ndithawi Yozatenga Boma,coz Boma ili Nde Mmm, Mmosemuja Amadikila Kut Chisakho Chiwandikire,koma Tikalande Kaye Nyanja Kenako Tizakumangeni Bwino!

  2. Ndale zimapanga anthu blind ndithu chifukwa cha tinsalu tomwe mumalandila tija basi mitu zweeee osaonanso kuti dziko likuonongedwa kapena ayi tidzafa ovutika ndithu.

  3. koma inu anthu how blind r u ….do you call that this dpp government is doing batter than jb ??? koma people are really blind ndithu

 87. Munthu oipa ameneyi kuba ndalama kuno kumakadyera ku America moti bwenzi akudyera komkuno….abwere kumene adzalandiliretu chilango cha pansi pano chitsale chakumwamba

  1. Mukhululukilen mkuluyo ,ziwanda zamupeza , coz nkhani iyi siyotukwanizana ayi, mzimu wake ndiofooka akufunika alandile Yesu

  2. Eeeeesh! koma anthu ena kunvetsa chisoni, ine sindikuona chifukwa chotukwanira apa, zikuchita kuwonetsera2 kuti mutha kutukwana kholo lanu zamunsalu khalidwe mulibe man

  3. akuti ready to be arrested ndi omuyika mawu mkamwa…okha mayiwa sanganene ali ndi mantha aliko.the arm of law must work on her as well.jail her and throw the keys to the nearest lake

  4. people should understand if the government does not have money always they start blaming the former President about money

  1. It never matters whether she’s my relative or not…enanu kusauka munasauka 1990 koma pano mukut she contributed to your poverty hahaha JB being your escape goat? mxiew

  1. Zamalamulo mumaziwa ndi inuyo big man. But if she is innocent then let her come and be here. Her party misses her. Kkkkkkkkk you idiot

Comments are closed.