Zonse zija zoti a Malawi ochuluka akunyema pamseu, zoti akunyema pofuna ziphaso zoyendela (passport) ngakhale za u dalayiva, Boma la Malawi likukayika zoti kuli katangale.
Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika amene nduna yawo ya za malimidwe yakale a George Chaponda anachotsedwa pa udindo powaganizila kuti amafuna kuchita za katangale, lero akhala akutsegulila msonkhano wofuna kudziwa ngati zili zoona zoti mu dziko muno muli katangale.
Msonkhanowu ukuchitikila mu mzinda wa Lilongwe. Bungwe lothetsa mchitidwe wa katangale mu dziko muno la ACB mogwilizana ndi unduna wa za Chilungamo ndiwo akonza msonkhano umenewu.
Malinga ndi uthenga ochoka ku boma, ati msonkhano umenewu ukufuna kutsimikiza ngati katangale akuchitikadi mu dziko muno kapena anthu angokokomeza.
Pa msonkhano umenewu umene anthu ena audzudzula kuti ndi chibwana chabe, aitana namandwa wa mu dziko la Kenya kuti azayankhulepo.
Kumangoti dziko layipa, tikuliyipitsa tili ife tomwe. Tasiyani katangaleyi titukure malawi, mulibe manyazi kodi?
Zilekele ciani ukhalako
Ok ilo silikukhulupirirA?
Kuli katangale osati masela
ndigone kaye ndikubwell
Kudziwa amadziwa koma mumati angatiuze chiani?poti iwonso ndiye amene akutsogolera katangaleyo!
yes xibwino agalu inu mmati ndiopuxbwin tienaxo kkkkkkkk
Corruption is everyday life in Malawi every department in Malawi is corrupted.
ndiye waku kenyayo athandiza chani kwawoko ndite nyanyi koma mukungu akukuonani muzaona polekera
kungoyambila mbuli ya chiyawo ija mkubwela jb akuluwa osanena nakuba akachita chbwibwi
The corrupt free government: Daniel 2:44
iiiiiiiiiii Apulezdent Maine nde Salimumalawitu kikkkkkkk Atumize Ma Cid Akaona Xoopsya muma department ambiri Aboma ……ndipo Azakhumudwa………………..vuto Ma cid akalandilaponso ka chiphuphugate koma kaya tilowela kuti kikkkkkkkk…
No comment am afraid of daggers
Katangale sazatha aliopobe zaka zikubwerazi ndiye mavuto osaneneka. Tangopitani ku e migration kuli mavuto osaneneka
mbava zokhazokha moni achaponda mbava yayikulu
Ali ku Mars amenewo not Malawi.AkaDzafika ku Malawi adzaDziwa
Kuipa koika anthu obwera mmaudindo ndkumeneko,,zoona kt katangale kulibe..? Zitsiru…
Ilili Boma Ndilanyasi Ndiboma Losaganizira Anthu Akumudzi Zaka Ziwiri Zathutsa Koma Palibepo Mlimi Yemwe Akusasangalala,boma Ili Lilipo Ndidyera Basi Katangale Thoo!Bolaso Boma La Bingu Komaso Joice Alimi Timakhala Ndi Ndalama Anthu Amagulaso Galimoto Koma Pano Tsopano Chino Chaka Ndichachitatu Koma Opanda Chochitika.Ulimi Sukuyenda Ndibwinoso Programme Ya Subside Athetse Yalowa Ndale Akupindula Sialimi Koma Andale Makoponi Awiri Pafumu Sichipongwe Chimenechi?Ndiye Mkumati Boma Langa Lili Bwino.Chipongwe Basi Especially Kasungu Santhe Sitimudziwa Nkhope Yake Pulesident Ongowina Sayerekeza Kudzawona Mavuto Awanthu Kuno Tsankho Lokhalokha.Ndiye Mkumakana Kulibe Tsankho Ayi Ndithu Ili Siboma Lokomera Anthu Akumudzi Komwa Mwina Amtown.Mlimi Kwake Ndikulira Basi Ngati Sasitha Ngati 2019 Adzawine Adzandifuse Sangawine Olo Mwana Sangakambe Zabwino.Subside Athe Mkwabwino Angochepetsa Mulingo Wogulira Fertilizer Komaso Makalabu Basi.
Afuna atibere
Kodi KATANGALE ndi chiyani?. Katangale ndi kupeza ndalama kapena zinthu kwa antchito kuchokera kwa anthu adyera kapena opanda zodziyenereza kupeza chomwe akuchifuna mosayenera. Kodi katangaleyu amachitikira kuti?. Katangale akuchitikira m’maofesi onse a Boma, M’mabungwe onse amene saali a boma, M’mpingo ndi monse moyendetsedwa ndi anthu olembedwa antchito. Kodi kuthana ndi katangale nkotheka?. Ine ndikuti AYI, chifukwa ofuna zinthu m’njira zoyenerazi alipo miyanda miyanda ndipo a m’maudindo ngakhale atalandira malipiro ochuluka bwanji, sadzatheka chifukwa katangale wa chaka chimodzi akutha kupanga zomwe sadakatha m’zaka makumi awiri. Mutapita kwa ma MP anthu onse chiyambire 1994 mukapange kafukufuku mukapeza kuti chuma, ziphaso zoyendetsera Galimoto, zilolezo za mabizinesi anazipeza kudzera m’katangale kapena kuba kumene ndalama zoyambitsira bizinesi zao. A ACB, M’mabungwe omwe siaboma, M’mipingo ndimwina monse muli anthu pafupi onse amenenso angayankhepo milandu ya katangale kapena kuba ndalama kumene.
Mmmm atolaķhani opanda zelu ńgati awa añgalembe zabwino,,,,?
ndy chani! akamakaikira aah naye ndi muthu sikut ndi ngelo! Naye amadya
ndy chani! akamakaikira aah naye ndi muthu sikut ndi ngelo! Naye amadya
Yap its hapeng frm hdadcoach even to choöse cabnet thy corupt him.kupanda chson ndi osauka
Zaucilu basi
Kuba kwanu nose
Nyoooo!!!!
Nxt
mkukuyu lero walankhula mbeelela
Stupidest federation
amasenda.achoke.basi.moti.tikubwela.kofot.achoke.amasenda.pita
Kkkkkkkk koma mkuluyu mutu wakwe ukugwira ntchito? Si yekha pompano amanena zoti akudziwa kuti boma lake katangale alimo koma achita chotheka kuti athane ndi aliyense okhuzidwa nde pano akufunsaso?
ofunika tionane naye mu 2019! Vote ikayankhule..
Kkkkkkk madala atha xeru
Katangale alipodi panyasalande pano!
Kkkkkkkkkkkk ok akanaziwa mavuto a passport kuti ituluke sakanatelo
They are blinded by our tax money, they will see it when the commander will command for the about turn
ironiboza mwapoka ndalama zawanthu boma lakuba ili kuyambira bakili mupaka Peter mupaka ndiye sono sokupusika tawanthu yayi katangale walipo ndipo ngwambula kumala
Il
Umeneo ndio timautcha uchisilu a Malawi, ndani asakudziwa zoti Ku Malawi kuli Katangale, ACB nao linangokhala dzina pano, Kuba kuli nkati…..
zopusaa, mkaitane munthu Ku Kenya kamba ka Nkhani yakatangalee?
Malawi dziko langa likumvetsa chisoni…….
izingodyani Ndalama zoo mlemele ndinuuu
Thats y ifeyo sitizasiya kutukwana pa fb cz boma ili ndi lankhutukumve zokhazokha ndichifukwa chan mukulesa zinthu zoti ife tikuvutikanazo abakha inu mbuzi za an2.
Zazii! Mxiewww koma this failed govt… The problem with Malawians is that we elect thieves to lead us which is totally shit,,,
They know each n every corner do u think that they should say yes there is corruption in our gov even u, u can’t say yes while u know the truth go to traffic or immigration
Uthenga opita kwa ma cadet nonse @DPP kuikira kumbuyo zinthu zoti pansi pamtima mukudziwa kuti zolakwika komanso zikuzunza fuko lamalawi ndi tsoka!!
Pali nkhani zoikira kumbuyo Boma apa?
mmmmm Malawi Malawi my country,what kind of leadership is this? u think we dont know what is happening eshie nanga ndalama zija boma linalipira magalimoto kuchoka ku SA zinayenda bwanji mumalo mwamagalimoto 8 kubwera atatu five missing eshie
If someone doesn’t know that there is corruption, then he is not a Malawian and does not live in the country
Amayambisa ndi akuluakuluwo nde ana nkutani tawonani aja a maize gate
Corruption is everywhere in the world, only in heaven you won’t find this nonsense.
So you are comparing Malawi & some countries? Maiko ambiri omwe kuli katangale anatukuka kale ndipo amakhala moyo otsogola.kkkkkk ukukamba ngati chifukwa chakuti Ku Russia Ku li katangale ndiye ife tizipanga katangale. Waiwala kuti maiko amaneo anatukuka kalekale ndipo anthu sakhala mu umphawi ngati Ku Malawi.
J kay Luciano, my friend, forget kuti malawi idzatukuka, tili masiku otsiliza .
U mean tizingoba popeza tili mmasiku otsiliza? Tiyen ngakhale tili mmasiku otsiliza tikonde dziko lathu coz palibe yemwe akudziwa tsiku lenilen mwina kwasala zaka 100 kutsogoloku
Malawi is worst corrupt country in the world as well as poorest country. Don’t compare it with other developed nation in the world
Ok watelo nanga … What f ur brother hv a head chopped-off and u catches a guy who did it…and the guy got alot of cash and he agreed not put in jail coz he bribed wil u say its gud………. B’ generous….. Corruption its not political only my friend……… Some of us we hv faced unlawful judgments due to corruption” this should come to an endnow am in USA this month its not like Wat z there at home
Tony phiri, U.S.A and malawi is different, there’s corruption in U.S but u don’t know coz is developed country, and even here in Britain, people r singing the same song, but we poor we don’t know, so don’t expect malawi to change, kamuzu never develop malawi and no one will develop malawi.
Aziwa bwanji? poti akupanga ndiomwewo.
Aziwa bwanji? poti akupanga ndiomwewo.
Mesa iwo ndie anuwake akatangaleyo ndie akuyenera kukayikiradi
A Peoples Party Anatuluka Ndi Cashgate! Adpp Maizegate! Ndiye Bola App Bcz Anthu Ntchito Ankalembedwa Ndalamaso Zimalowa Kuchoka Kunja Ambiri Anthu Anapeza Nchito Muma Department Osiyanasiyana Pano Kuba Kokha Opandanso Manyani! . Sindine Wachipani Koma Zabwino Zoyipa Timaona!
Ndani Angavomeleze Zochititsa Manyazizo?Palibe But The Truth Z Mw Z On #1 Corruption.Mukanena Zapamseu Apolisi Ndiye Siyani,tifunseni Ife Timauser Public Transportfe.Eeesh!Nyaaansi Pamseu
Zaziih
Vuto Ndilakuti Atsogoleli Ndi Omwewa Koma Amangosintha Zipani Ndiye Katangale Atha Bwanji Poti Amakhala Kuti Njila Akuidziwa Kale
Idiots
katangale ndiwa bwino ndipo apitilire.
kkkk fuso lachodziwadziw ili
Zamanyi basi mxewx
Katangale amayendetsa zithu fast changu pa malo.
Ngati siunamenye nawo deal pasport yako yikhala 4years isanatule
Sangavomele ayiwala kale kuti nduna yawo (Chaponda)adayichotsa poyiganizila zakatangale? Timapenya maso tilinawo komaso timava makutu tilinawo simungatinamize sindife ana.
Boma ngati silikuziwa za ma department ake zomwe zikuchika nde kuti ali ndi chidwi ndi anthu ake??? Ulamulilo wa DPP ndiplephela.
Vuto katangare sadayambe ndi boma lake lilipoli ayi adamba ulamulira wa Bakili komaso ngat ukuchifuna mwachangu chinthu uyenera kunyema basi.
True true. ..same like ofuna thandizo lapamwamba they go kuma private hospitals
Meaning DPP/UDF Collision it’s major agenda if to promote tactics of Corruption backed by Corrupt leaders with their savages the so called Cadets/Young Democrats? Manyaka a BOMA awa!!!!
Akakhala pamkhate sapheka.
Maka maka ku IMMIGRATION ngakhale PASSPORT yatuluka sangakupase ngati sunanyeme eti kukufunsa kuti akukuthandiza ndani
atumize ma cid ku ma department amenewo akaziwonera okha
Komanso ma CID ale asakhale asakhale akuno ku Malawi (they are so corrupt to the core themselves).
kkkk ndipo inu ine ndakhala 1 week pa mzuzu traffic department
Aluza 2019 chifukwa chainu koma ine nditamvotera osatha zamkamwa sindiona president wina mmalawi muno mwina povota kapena pa campaign pano iye bas nde tiyeni tidikile 2019 mukukhala ngat osazindikila bwanj president nde angatule udindo chifukwa chomunena remember president sachosedwa ngat zino koma inu ayi mukundi………ZAMKUTU
Mmmmm koma zoonad boma ili ndiye lanyanya
Boma lopanda katangale ndi lakumwamba basi
Oooooo Ndakuyamikilani kwambiri chifukwa cha ndemanga yanu mwene ndipo ndiyogwira ntima kothelatu zimenezi amene amazidziwa ndi ochepa kunena zowona
Chilungamo ndithu
Zowonadi
The leaders are corrupt and you expect the citizens to be innocent? Mikoko yogona inati, Like Father Like Son.
kkkkkkkk zoonaa bro
Sangavomereze cz katangale wakula mchipani chawo cha DPP
They must go to Road traffic and immigration offices and see for themselves
They knw the truth but they can’t agree coz they also inside it! Corruption is all over our nation!
lilipo boma lomwe tingati kulibe corruption koma mw ndiye ndi #1 moti ndikuganiza zoipangira award yapamwamba hahsha my mw
Ndye ng@ sakudziwa inu m’mati atani?.Mwasoweka zolemba eti?
cadet
No am not polotically oriented
Katangale. Corruption