Palibenso zonyengelela amuna onse a chimasomaso chaka chino. Akapezeka akagwila ukaidi wa kalavula gaga.
Mkulu wina wa zaka makumi awiri ndi mphambu zisanu (25) wa mu boma la Machinga walamulidwa kukagwila ukaidi wa kalavula gaga kwa miyezi makumi anayi (40) ati kamba koti anagwila bele la msungwana wina.
Bwalo la Milandu la Majisitireti mu boma la Machinga linamva kuti pa 10 January chaka chomwe chino, a Gilbert John anapita pa sukulu ina ya sekondale mu bomalo.
Iwo atafika kumeneko anapeza mwana wa sukulu wa Fomu 4 wa zaka 19 akugwila chibalo.
Ati a John atafika anamugwila mtsikana uja bele kenako ndi kumugwilanso Mbina mochita chomukakamiza.
Iwo sanasiyile pamenepo komanso ati anaononga ndowa ziwiri pa sukulupo ati chifukwa a sukuluwo anali ndi ngongole yawo yokwana 3 sauzande Kwacha.
Izi zinapangitsa kuti a chitetezo aitanidwe pa sukulupo ndipo anagwila Bambo John.
Iwo atafika pa bwalo la Milandu anapezeka olakwa pa mlandu oononga katundu ndi mlandu ogwila munthu malo osayenela mwachipongwe.
Bambo John analira pa bwalo kupempha kuti asawapatse chilango chokhwima kamba koti aka kanali koyamba iwo kulakwila lamulo.
Koma oweruza Milandu anawagamula kuti akagwile ukaidi wa kalavula gaga kwa miyezi isanu ndi inayi (9) pa mlandu oononga katundu. Pa mlandu ogwila munthu malo osayenela, mwachipongwe anawagamula miyezi makumi anayi (40).
Ngat ulamuliro ukuvuta uauzen atulepasi udindo Mr Peter chifukwa munthu sanagwile bere koma wagwila chovala chomwe chinali pa fupi nd bere zopusa et osamanga obachimanga bwanj February ikubwera njala mkat ndie mkumalimbana nd zogwilana mabere ulamuliro opoila
Kuuma ntima
milandu ngati imeneyi sivuta kugamula koma yoba chimanga ndindalama ayi.
Wogwira amagidwe,nanga wowonesa?
Mabere ake akumapsa ndi Dzuwawa?
sometimes I am vry surprised to our leaders always encouraging things which can not developing our nation
Malawi wamabvuto. The one who stole government money are kept for less year but just to touch a woman breast costed someone that much in prison thats a nonsense judgement.
NDNDAN WACHTA ZMENEZ
Ogwira bele 40minths Ku nde nde nanga odya milomo? Kkkk
Nanga president mbavayo zaka zingati kuba ndalama za boma?
Ndiye njala itha ukagamula choncho?
Ogwira bele miyezi 40,oba ndalama zaboma akuyenda Montang’wa.
bola anakagwira Ndata koma bere kkkkk
Koma malawi akupita kuti uyu munthu kuba ndalama zankhaninkhani osamangidwa kapena kuti kuba ndalama za chimanga osamangidwa mpaka pano uyu wangogwiri bele sanalichosepo lili ndi mwini wake yemweyo koma mukumumanga kodi inu majaji umbuli kapena kusaganiza.
Kodi belero anakaoda kut? Kodi iyeyo mamuna wake wagwila kangati? Kodi iyeyo sadzayamwitsa? Nanga mwana wake azakamumangitsa? Amalawi tizikhala ndi chisoni ndi azathu ukaidi ndiwowawa. Nanu akhothi kumaona ndi nkhani zake. Koma mumangoti ma section kodi munayamba mwawadziwitsa anthu asanalakwe. Koma malamulo timawadziwa ife Amalawi tikalakwa basi ma judge nonse wakumoto kwamulungu kulibe chanu anthu opondeleza inu. Mmalo molimbana ndi maizegate mukukalimbana ndi belegate Ngat munthuyo wachita kudula belero.
kkkkkkkk is too mch chaponda akukuberani chimanga mukuchitapo chian
Ogwila mabele kundende okuba ma bilion ay tiafufuze kaye mukuonjedza ma validwe give them punshiment
Boma ilooooooooo.ppppppppppppp.
Nanga wachimanga amgamula bwanji.
Mukumatha kupatsa chilango chokhwima kwa anthu okhawo amene ali osauka, pamene a Cashgate mukuwalephela apa. Bunch of failures!!!! Fooooools
Nice amuna anyanya kumatenga zamkabudula kuika poyera mkazi modzi osawakwana mau odyera amati akazi ngambiri yet mulungu analenga modzi kwa modzi nde masiku ano bwalo likugomera azimai adatipondereza kudakwana tipna tiina akutha osaugwira mtima
Wachimanga asapasidwe chilango chilichonse,adzaweluze ndi mwini wake Mulungu.
Yah do it mr BoMa
Kkkkkkk kungogwira bele kokhako?
Fucken chit ndi malamulo anuwo mwamva ndipo ndikanakhala ndi mfuti bwezi nditakuombelani chifukwa zikundiwawa mmasuleni munthuyo inu ma satanic
Kumkwinya kwanu wat about kutaya mimba
Bu shirt anthu akuba ma billion osawamanga or mwezi nde uyu mpaka mezi 40 why malawi full of shirt
Ah basi mulandu tazenga
Ena akumamukoka nyini koma osawasumira,koma mphawi kungogwila kabele kalekale 40 months with hard labour mmmmmmmm!!!!! malawi
Chilikuti chilungamu chija
bele ladura
Mungopanga zausilu ku Malawiku eti,mmalo mokamba nkhani ya kubedwa kwa Chimanga kugwira bere ndi chani anamugwilira
Ndiye kut azimayi tikamakwera nao magalimoto asikwera mbali yawo kuopela tingawagunde bele.
Had it been it were a minister who did that no arrest would be done due to the fact the minister could not even go t appear before court due to his superiority, the ruling is illegal and biased, demolished all the courts and prisons if they are there for ordinary people
Xa ziiii
Komatu ife akaz ena amatikoka ndevu
Pamalamulo alipo?
Kaya amwene
Akagwire ukaidi basi.
akuluakuli tiyeni tizikhala ngati ndife mzika tiziziwa malamulo aziko lathu ndipo chigamulo chimenecho zili mmalamulo ndithu and ambiri timapalamula koma chifukwa amene timalakwilawo saikoka mkhaniyo timaona ngati ndizosalakwika chonde tiyeni tizigulako buku lija silodula kumawerengako pliz tizazizimuka wina titamugwira muchunu ulendo mpka kukasekeredwa zanga ziwiri mdithu
Iyaaaaaaaaaa
palibe nkhan apa kabele nkachan,ena akumamkoka nyini osakasumira bwanji? dziko lapansi lamulaka mphawi
aisja
Bullshit
Komenta comment yopusa uone ukaseve 46yrs imprison ment with hardlabour and breaking tree shrubs
Komenta comment yopusa uone ukaseve 46yrs imprison ment with hardlabour and breaking tree shrubs
AAAAAAAAAAAAAAAAAA azikazi WO NDE akumachita kutigunda dala malisani ndeife tiziopa kubwezera iwe wozamanga zakowe uzayelekeze kundi gunda ndizakuonesa zakuda ndukuza mukujaila malo mopanga zazelu kumalawiko mukumakhalakhala ndikumataya nthawi ndizaku nyelo tisiileni tokha tinaziyamba tokha timalizitsaso tokha zachamba ife ay
vuto ndimamvalidwe atsikanawo
Ambiri amagidwa chifuKwa salivala bo mafanawa azifufuza Kaye azamanga chibwenzi chake. Azibisanso maberewo. KungowayaniKa,mwana mamuna akadatani?? Koposa Kugwira. Flash ndi Kutchurch Komw?? Amangansotu Abusa!!!!!
okuba chimanga mu Kumusiya. nde kabele komweko ukaidi onsewo.zanyemba basi!
Anawa akumaonjeza kuvala mabere pamtunda zoona?akut ufulu umenewo wa azmy
40 months for touching awoman’s breast.
Kunoso nsikana wa zaka 14 anari std 5 ari ndimimba ya achimwene ake koma ariyese akukana kumuthandiza mwanayu.
Ok any way. Akagwire ukaidiwo but y taking minor issues so serious though anthu ofunika ukaidi akungolambasha mwa mtendere? Such as. ……………..nda.
Loading. …..
Alephela muthu okupha alobino kumumanga 40 years ndiye muthu ongogwila bele pakachoncho inu mukunama ine ndyesakugwila bele ndiwonechichitike.
Alephela muthu okupha alobino kumumanga 40 years ndiye muthu ongogwila bele pakachoncho inu mukunama ine ndyesakugwila bele ndiwonechichitike.
Its Too Much
Go back to court for the right sentence passed on him.
baaaaaaaaaaad this is nonsense
Zopusa bas
.ndasiya kuwerenga nkhani za amenewa zimakhala zaboza mpaka kunamizira imfa munthu ife kuononga airtyme yathu kumalemba ma RIP
Mulowelerepo ambuye…ndibere lomwelidi koma?????
Zitsiru inu kongongwila bere basi nanga oba ndalama za maize cash gate aja za manyi basi?
ife nde tikugwira dairy
Amuchita bwino osakagwila lambuyake bwanji atsikanaso ndi anthu osati chiseweletsa
Yachepa miyeziyo
Kodi bele linaphwanyika po ligwirapo?
Nanga chaponda wagamulidwa bwanji.
Mmm its too much musamawa khomelere atsikanawa zimawa sangalasaso zime ezi
KKKKKKKKKK KOMA OKUBA CASH NO CHILANGO
No way, just touching no harm, kkkkkkkkk okey, what about these who store maize money the serious of fence, is he surviving.?
full of shit mzuzu county ok any coz am not malawian but ds not matter xem
Koma ogwilira gogo ndiye timiyezi tochepa,koma ma judge akwathunso ndiye kayaaaaaaa!!!!!!!!kaya ma xul a za malamulo ake ndiye ati kaya
Kuba ma blions osamangwidwa
kuyenda mbulanda ndi ufulu
ukamugwila ndende ulamulilo
wa satana uwu
Koma oba ndalama za m’boma nde kwasiya adziyenda mwa ufulu ku makwera Ndege ..kapolo nde 4 yrs shaaa dziko kukomera opata ili
Aaaaaaaaaaa
mtuluseni muthu athu otembeleledwa inu mwapangana kuti muzuze athu ovutika onse kusiya olemela
3 years yoh
zoopusa basi ,bwanji osapeleka death sentence kwa okupha albino
40 months (miyezi) & not 40 years (zaka). Check pls.
Wangochita tsoka ameneyo kwathu kuno kugwirana mabele nde macheza athu..
Akuti miyezi 40 not 40yrs. Amalawi phuma.
Kupupulumatu ngati mabi akufuna kutuluka malawi ndiye ameneyo kkkkkkk
Mutimanga ambiri sinati
Zofuna ine zisandikhudze isaaaa
Since you guys, Malawi24, have mistakes infused in your blood, do you really mean 40 years or 4 years. Murderers and housebreakers are given soft ones, why this man who only touched a body part? The judge involved is surely sarcastic.
thats true my brother
It’s 40 months which is 3 years 3 months
Akutitu miyezi makumi 40 not years
Za chamba basi bwanji simukumanga okuba ndalama za chimanga?
Eeeeeeh but this topic has atracted a lot of attention just like the woman herself atracted the guy.Anyway whatever everybody is saying here is making plenty of sense and I’m just speachless.Pena pake azimayiwa akumationjezadi kwabasi ndi mavalidwe awo amakonowa.Wuzaona mu American wapanga timalegeni ndicholinga choti atsikana adzivala akamalowa mu netball pitch kapena akamakaimba pa stage, iwo akumatigula timene tija nkumativala mtown ali pheeeee! Zosawakhuza iyayi.Nde kuli timadress tinatake akumati tima see through, akumakhala ngati kuti avala zadzitali bwinobwino koma wukawayang’ana amangokhala ngati kuti sanavalepo chinachilichonse.Zovala zoyenera kumavala mudzipinda mwaomo kuti amupange arouse mwamuna wawoyo iwo akumavala mtown nkumakakopa nazo wina aliyense.Nde pena mavenda tu amapangira dala, yimakhala ngati mbali yimodzi ya punishment.Akumationjeza anthuwaaaaa.They feel very much better when they are exposing their private parts.Expose them to your hasbands! Or if you are not yet married then expose them to your boyfriends if you think it is right to be doing these before getting married! But don’t just expose it anyhow to the public.Mukumationjeza kwabasi.
ma court ali bizzy kulimbana ndizogwirana ma bere m’malo moti alimbane ndizama billion.achina chaponda akukuderelani kupita kunja pamene ali pa mirandu akudziwa kuti ma court akumalawi ndi opusa auchitsiru.ma court akumalawi lamulo siligwira tchito pa munthu wa dolla koma pa kafunyanya malawi sadzatheka.
Everything we read here are lies,even comments are all lies,there’s nothing real here. Even my comment is a lie.
Waphwanya lamulo ayenera kumangidwa , koma muzipanga chimozimozi ndi anthu amene akuwononga chuma cha Boma.
Ndiye nkhanza tsopano
No comment coz I dnt know wat happened kuti amugwile bele
Nkhoti zogamula zake za ziiiiii!!! Mmalo mokhazikisa mamvalidwe abwino kwa azimayiwa akuchita kuwatokosa dala ndi zovala zowonesa tsonga zamatakowa koma kumalawiii! Eish!!
Kkkkkkkkk koma…..
eeee, nayetu nde waona zakuda
Chaponda nde akusiyidwa pati lol #zausilu basi mxieewwww
Akuti ndinthawi yolimbikitsa azimayiwa kuyenda maliphyata, malichaje ,kapena kuti aziyenda maliseche kaya sakudziwa amakhotiwa azimayiwa akumapanga dala zimenezi kuti azitikopa ,muyambe mwazimitsa moto asanapyse osadikila katundu kupysa nkumazimitsa moto simukuthayi amakhothi pamenepa
Fucken
Koma mtsikana ameyo uxangokhululuka ngati amudura, bolaxo iye asazalakwire munthu
Koma yah ok chimenecho nde chitukuko cha a Dpp kapena chitetezo?
Lavuta ndibele apa
Nanga ona ndalama zachimanga?
Bele lomela lokhali ndithu mpaka kumangana miyeze 40
ati miyezi 40 osati zaka 40 muziwerenga mofatsa osati mwaphuma kuti mumvetse pepanitu
ndiye miyezi 40 ukuichepetsa
Miyezi 40 kaya?
Zaukape
Kulakwa
Kugwira bere ndikukhuta, ife tili ndi njala tikufuna chimanga chathu chabedwachi basi
ka malawi satana wakapolamila ndithuuuu abale miyezi 40 alaaaa mwinanso mukuti anagwilacho Ndi silipasi yachabechabe
Osadabwa ayi Amalawi sitikondwera ndi munthu wopalamula mulandu waung’ono koma wakuba cashgate (Joice banda) kapena wakuba ndalama ya chimanga (George Chaponda) ndithu ndithu mukhale maso ndi mbava zimenezi sizidzamangidwa olo pang’ono. mmmm kodi kukhala tizitero?
Fufuzani ndi lamulo lanji agwiritsa ntchito ganizirani ogwilirira amampatsa zaka zingati? Angofuna tiwerenge nkhani zawo awa.
Akumugwilira ukayidi chaponda ameneyo.
Fufuzani a Malawi ndi bodza ili.
Palibe kunyengerera kumene, agwira bwanji bere lamwini? Walakwa
Lamwini ndiye labwino. Ogwira ndi ambiri. Ogwidwa, ochepa.
nanga chapondayo bwanji 24 bilion iiiii wina wagwila bele ha ha malawi laws kuba ndikugwila bele bola tizingoba okuba samangidwa
Hahaha
so sorry .call Him to help him
Indecent assault is a felony and this dude deserved much more years than this
Only kwa amene sanyenga can say this
Eeeeeeeeeh uyo nde ampweteka.Dats too much.Sitikukana ndinjira yimodzi yotetezera atsikana komanso kuthetsa mtchitidwe wogwilira ana komabe 40 years is just too much for just touching a woman’s breast.Peaple are stealing billions of kwachas but they are just moving scort free koma mwamunayo kungomugwira bele mkazi basi 40 years? Ummmm, its too much.What about real raping? How many years do they give to a rapist?
40 months not years dude
not 40 yrz bt 40 months.
3years n 4 months
Kkkk
Bro fix your calculator keypad.
Kkkkkkkk
Kkkkkkkkkkkk Ok ok ok, sorry, I didn’t see it properly.I thought its years.But that story could’ve ended even by just discusiön.
its 40 days kkkkkkkk
Akut muchite fix calculator keypad Ken Malekwa kk
No problem its just a mistake boss
Ndiye anakakhala kuti wagwiriratu, basi unali moyo wake onse pa 40years-po. Umawerenga, ukuganiza chiyani? Kanundutu uyu, koma zachabe zilipano.
Kkkkkkkkkkkkkkk zimatha zimatha.
AKULU AKULU KUMAVETSETSA AKUTI MIYEZI 40 OSATI DZAKA
Kkkkkkk osafooka pali anthu paziveka mphokoso iweyo yadya 1
Kumabweletsako tima arguments pang’ono.
Kkkkkkkkkkkkkkkkk koma eeeeeeee amalawi sitizatheka ndi zaka zitatu(3) ndi miyezi inayi(4) osati zaka 40 eeeeee kucita kumupotsa odya misokho ya amphawife.
aaaa amuna ndi ochepa kale nde mukufuna muzingo wachepesabe!!!
This is a fucken rule oky
ndili mturo!!!
Bele lenilenili? Ofunika commission of inquiry!
anandigwira bele!!!!
anandigwira bele!!!!
anandigwira bele!!!!
Ma court aku Malawi too corrupt plus kukondera zachamba basi.. Kungogwira bele ngati kuti anamuvula zachamba chosecho okuba ndalama ndi aja mumawapatsa 3 yrs fodya….
Bele lokhalo mpaka munthu mumuzunze kundende miyezi 40?, bele lake lotani limenelo? tagwilatu mabele ife mwamva inu kukhothi uko, that’s a FUCKING judgement.
Kkkkk. Breast is important than Maize
Tsoka likalimba amakuotcha ndi ice cream .
Nanga bele leni lenili ndi chianinso !
What’s wrong with our Courts?. 3 years & 4 months in jail for only touching one’s breasts when another gets 4 or 5 years for raping an under aged & 7 years for rape & infecting with HIV.
Zazii nayeso mtsikanayo ndi nkhani yokanena ku police imeneyo
KKKKKKKK eti malo momamanga mbavazo koma boma lakwathu
Pena akaziwa akumaonjeza akumayenda ali kale mbulanda ndiye ma swazi atani?kumangomangana zopusa basi january mwanya naye mwayamba kumangomang zilizonse
kugwira bele mpaka munthu kumangidwa?mnyamatayu akufuna kukwatila tsono chomungila ndi chiyani?
Kkkk ine mkazi kundiseweresa ndevu kamozi ndimachita kuchonderera kachikenanso.
Koma wakuba ma billion miyezi itatu kuwafusa kuti mwachitlanji izi akuti tikufuna kuti ndalama zomwe adabazi zidzikagwira ntchito
Fool why u not tell them that they must stop moving naked kukaniza chilengedwe osamanga Chaponda bwanji wapha mtundu wa amalawi ndinjala
Nanga okuba chimanga?
munthuyu mwantani kodi?mesa anthuwo anafunana? mukumumangilanji?akhoti mumakondela. opalamula osauka simuchedwa kuwamanga.anthu akuba olemera mumangowasiya adziyenda momasuka osawamanga. uyuyu mumutulutse kundende mwamsanga kuti adzakwatilane ndi bwezi lakelo.
treu, kugwila bere latsikan its process of sex akuyenela kumangidwa
i think am gonner report this fucking page to the ceo mark zacherberg ur giving fake and useless news,
its tru story war happened in machinga a man who touch a breast of secondary sxul student has been sentenced to 40 months in prison wth hard labour
Iconic be like ???
wakuba chimanga is just the same as killing nde mumutani ameneyu poti wogwira bele mwati 40 months. Umphawi umalowetsa anthu kundende koma olemera amangovakacha ali phee kuno mpaka ku Germany and back osamukwizinga. That’s justice pa Malawi.
#belegate
Bola kuba chimanga ngati Chaponda boma likhoza kukukhukulukira
Kodi Inu Amene Wagwiridwa #BELE yo anapanganaye kapena amamudyelera maso
Mamvalidwewanso eh mwina ndigweroso
Kugwila bele basi mpaka zaka 40? mwina mukunana. Nanga ogwilila zaka zingat?
40 months ..3years n 4 months
Ine singayelekeze zimenezo bola ndibe chimanga basi
its Not Fair Okuba chimanga ali pheee wa cash gatso chimodzimpodzi #uchitsilu basi Bele ndi chaniso aaaaah
Wina adaba chimanga moti agogo anga akuvutika ndinjala kamba kaiye koma muli phe osapanga kathu mukugwira munthu woti wagwira bere ,osati
mzinyengerera okupha ma albino ,mxiiiii kupu…….. .kupepe….. zauts…..
Admn you must be joking! Nanga okuba chimanga ndiye zaka zingati?
Waiphula.njala wasemphana nayo ameneyo!
kodi bele ndi zija amakozera nkazi? tell me pliz
Eyaaaa paja amako amakuyamwisila kokozela kwawo
Yoh koma cc mwayankhatu
NOSENSE
Wa Cashgate faiv years wogwira ka bele 40 yrs wat a fuck M-Dapts
Paja ndende mudamangira anthu osauka et ?chaponda akuyenda mwaufulu uko mungomuyang’ana
inenso kuno ku Mzimba ndikugwira mwana wa nchewa wina wake akapita kumunda ndiye mundithandiza bwaaaa? hehehehe
Bere? Lakugwanso Ngati Ilo Aahh Chilungamo Chaima Apa
Wa Cashgate faiv years wogwira ka bele 40 yrs wat a fuck M-Dapts
bodzatu ili
Kkkkkk akulephela kuwamanga amene akuba chimangawa bwanji
Zopusa basi osakamanga anaba chimanga aja
Poti wagwira bele miyezi 40, wina anadya ndalama caahgate akuyenda mwaufulu
Zalowa business!! Bele nde zichani azimayi akumaziyamba dala kuvala mwa uhule