Conjoined twins that were born over a week ago at Nkhotakota District Hospital have died in the course of a surgery to separate them, Malawi24 can report.
The twins died few hours before surgery to separate them at the Kamuzu Central Hospital (KCH) in Lilongwe.
Spokesperson for KCH, Mable Chinkhata confirmed the death.
According to Chinkhata,kids were supposed to undergo surgery on Wednesday but the process was delayed due to shortage of blood suiting their blood group.
“The twin needed about 200ml of all negative blood group but due to the fact that the hospital did not them,we failed to carry on the surgery”,querried the PRO.
It is reported that the twins died as they were struggling to breathe and efforts to resuscitate them failed.
So sad rest in peace bonana
Tikukhala Dziko La Tsoka,atsogoleri A Tsoka,umoyo Wa Tsoka,chakudya Cha tsoka Ndiye Ife Titani? Tingoti Amene Adalenga Anawa Alandireni Ambuye Poti Sadziwa Kanthu Ndipo Muwalandire Monga Mwakufuna Kwanu Amen!!
Zimenezo Ndiye Zopusazo. Munthu Amapangidwa Operation Mukudziwa Kuti Pali Magazi Ochepa? Ngati Sakadatha Akadapempha A Mabungwe Apite Naye Kunja Osati Manyaka Akunowa Ayi.Poti Mavutowa Akuyambira Kumtunda Mpaka Kothera Kwa Dziko La Malawi Ife Tilibe Chonena Chifukwa Umoyo Anawo Akadakhala Ndi Atsogoleri A Maiko Ena Sibwenzi Tikumva Zopusazi Ayi. Ndiye Zatero Ayi Tikukhala Dziko La Tsoka,chakudya,utsogoleri,umoyo,kuyenda Tikukhalanso Mwa Tsoka. Zaoneselatu 371 Ikugwira Ntchito.
Zimenezo Ndiye Zopusazo. Munthu Amapangidwa Operation Mukudziwa Kuti Pali Magazi Ochepa? Ngati Sakadatha Akadapempha A Mabungwe Apite Naye Kunja Osati Manyaka Akunowa Ayi.Poti Mavutowa Akuyambira Kumtunda Mpaka Kothera Kwa Dziko La Malawi Ife Tilibe Chonena Chifukwa Umoyo Anawo Akadakhala Ndi Atsogoleri A Maiko Ena Sibwenzi Tikumva Zopusazi Ayi. Ndiye Zatero Ayi Tikukhala Dziko La Tsoka,chakudya,utsogoleri,umoyo,kuyenda Tikukhalanso Mwa Tsoka. Zaoneselatu 371 Ikugwira Ntchito.
Sad news
May ur innocent soul rest in peace
The procedure was not successful. Not some stupid comments.. U don’t even knw a damn about surgery and ur busy insulting doctors.. The government..
The pain so unbearable for babies
they were just complitely unlucky to born in malawi very unlucky!!!!!
It’s so sad,may there saul rest in perfect peace
Abale Mwa Ambuye,tiyen Tiphunzire Kuvomereza Zinthu Zikachika,rmemba De Bible Syd,pachilichonse Yamikani Ambuye,end yense amene anabadwa akuyembekezeranso kumwalira,imfa siimathawika abale coz nthawi yamulungu ikakwana palibe angaibweze.Mulungu Akukhululukireni Nonse Amene Mwayankhula Udyo Kamba Kopsa Mtima.Tisaweluzane Coz Kuweruza Ndikwa Mulungu.Mizimu Ya Anawa Iuse Mumtendere.Amen!
Hmmmm! Si sad anali okongola
Aaaah zamabodza bas
Very sad koma god knows akanakhala kuti anali ana amunthu oziwika pano mutaitanisa ndege kupita ku maiko aluya koma poti ndi osaziwika mwapanga zofuna zanu ok nthawi ikubwela
zovesa Chisoni kwambiri.
Ooo pepani, kunonso Ku SA Boma ndi akubanja Ali pamadiscution kuti apange bwanji coz vuto ndilomwero chaku western cape uko kwabadwa Ana olumikizana pachidale koma vuto ndiloti kuti aalekanise m’modzi ayenera kumwalira chifukwa akugwilitsa ncito chiwindi chimodzi ndiye madotolo akudikila yanko kuchoka kuboma ndi akubanja kwa Ana, kuti atani.
So sad…
So sad.RIP.
R I P,God he knws
Bolani mudakawasiya chonchija akadakhalabe moyo…..
Let’s do something.Let’s donate blood.
Why not gov helped to send them to other countries for good service through the minister of healthy???? It means muntu akakhala osauka mulibe nayo ncito eti? I’m sorry may God Wellcome their souls in heaven.
So u mean they started operation while they dont know where to get blood?
very sad story may their souls rest in piece
I knew it will come to this,poor services always in Malawi may their innocent souls rest in peace
I think it was God’s will for them not to survive. Rest in peace beautiful and innocent kids
Amen
Mmmmm,RIP
Rest in peace innocent souls
May they rest in peace .Whatever God has planned has planned we all come from him and to him we retain.
Amen
MTSRIP
Rest in peace kids
so sad,,only God shall punish the reckless doctor,,sangapnge oparation while there’s insulficient blood.
vry bd
Anawo anali ndi magazi ochepa kale ndipo analinso asanayambe kuwathandiza anthu mumachulusa zokamba mukadwala madotolo ake amakuthandizani ndi omwewa nde mukuwanyozeranji
May their innocent souls rest in peace. Too bad
so sorry indeed , may their souls rest in peace.
Bcz of lack of professionalism!RIP
Eish vry sad
I blame malawi
Rip….innocent souls
Shame, unqualified doctor, shame, try to do your recomendable job so that we can be proud of you.
So Sad,May Their Soul Rest In Eternal Peace
Oooo…so sad
We love them but God loved them so much we have to pray for them amen
the twins have died due to the inavailability of blood(group O rhesus negative which is scarce) before surgery NOT during the operation! it seems anthu ambri mukungo commenter osawelenga nkhaniyi bwinobwino…
ndipo inu…ndiye macommentwonso eishhhh
Thats Asad Storry Eeesh Zikuchitikilanji Zimenezi Eee May Their Saul Rest In Peace
vuto z de type ov blood group imene anawa anali nayo otherwise we gat experts dat might manage to save de lives ov these two……..anywey maytheir soulz rest in peace
inna lillah wa inna ilayh rajouin ;
Amayi pepani ámálawi enafe tinabwadwa oģwirá ntchito anaĺi omwewa mpaka pano tiĺi nďimoyo añakamwalira ķu uķ simukanatokota chonchi shame palibe munthu amapanga moyo only god emweyo atothoze banja loferedwa i proud to be malawian
+17million people, where does the blood which we donate GO? #donate blood to save 1 life
Need clearance indeed.this is something very painful.ha.gwaragwara
Shame
Pepani kwambiri
Too bad
When Mpho And Mphonyana In R S A G6j Vqt
So sad,,may their soul rest in peace
oooh God..so sad
R.I.P
Am So Sorry.
Mesa chamma 10am lero amat analephera kuwapanga oparation dzulo ndiye amat akamaliza ku KCN lero masana, so which iz which??? Penapake2 mukutionjeza aNews24
Ok boh
R I p. Ambuye Khalani Ndi Banja Lokhudzidwalo, Ngati Ali Satana,kuweluza Ndi Kwainu.Afungatileni Ana Anu,Zonse Tizisiya Mmanja Mwanu AMEN.
Shaa shaa shaa. Oooooh no…… Am saddened to hear this. What a loss
Really sad mtsrip
ich ndiye chamba magz aja mumakattenga k xool? ndn Zitsru’..afh
We shall meet these children in heaven if do better here in the world of sins
Amen
Everthing is atime, or you can go anywhere, but time, its only God knows R.I.P.
So pathetic hmmm rip
Eish,,we don’t have enough equipment in malawi for serious operation,on top of that the doctors are not often dealing with kind of operation that need well trained doctors
its nt the doctors’ fault. the operation did not take place sir & this was because of blood (group O rhesus ,negative which is scarce)..the babies died of cardiac failure due to severe anaemia (don’t trust this site
Sorry. RIP our twins.
So sad R I P
NDIFE ALENDO PADZIKO LAPANSI PANO : ANAWA KWAO KWATHA, MOTO UMAYAKA KOMWE KWASALA TCHILE. NO JESUS NO LIFE. >>>>> 2016
Very sad ,I pass my conferences to the family
Tipaone bwino bwino pamenepa amafuna ayesele kwa anthu timayesela kwa zinyama. Izi zimayenela kunja izi akanakhala mwana wa munthu wa m,boma bwezi ataba za misonkho yathu kupita kunja koma popeza ndi osauka mwapha osalakwa musamale
makolo awo anali kuti osawapititsa kunjako? mun2 wa boma nde ogwiritsa ntchito misonkhoyo ka
Tilibe madokotala kuno. Onsewa ndi ma clinical officers
nt the doctors fault cause anawo amwalira cfukwa cha severe anaemia before the operation…and the blood that was required is O- which is scarce…so maybe MBTS fault
Guyz!! the operation did not take place,mudzimva kamodzi
Bwanji osatumiza kunja? Inayamba itakhalapo successful operation yoteleyi kumalawi? Mmafuna muyeselepo chifukwa ndi wosauka.koma the gvt spends millions on nkhalamba zofa kale
mmmmm nkhalamba zofa kale? God iz watching dont tok like that nicca
Lack of blood or lack of professionalism? Their soul rest in peace.
Very sad R.I.P
Amalawi musamangonyozesa dziko lanu muzilizonse, anakunamizani kuti kunja kulibe imfa ndindani?, these twinz deserved to die than leave a miserable life, period
Nobody ever deserve to die,I know of one pair who are alive and growing but not in Malawi.
I don’t understand wen u say “nobody ever deserve to die” bra, death is there, wheather we like it or not, the pair u ar talking about was just lucky, just like here in Malawi, there’s also another pair somewhere that survived the same operation, wat if the operation of that pair u ar talking about was a failure, do u think pipo of that country would stand on top of the mountain and accuse the doctors of incompetency?, its a complicated operation we ar talking about here, its life or death
these twinz deserved to die than leave a miserable life, Im against this part coz once you are born,you deserve to live regardless of your physical ability.Its only in our country where everything is awkward.I dont mean we wont die but circumstances sorrounding your death is what we are talking about here.Sorry my grammar is not ok…english is not my language.
Olivian u ar very wrong nobody has death as an entitlement am a zambian mayb there in malawi but i doubt ankolo
Thinking like a witch why? What if they were your twins? God have mercy on you friend! May their souls rest in peace
yu cnt say thy deserve to die why? if yu say others survived wat about these ones?? think like a human pliz
Nyapapi iwe bakha tokhwetokhwe kaligondwe gokhwiro iwe wandikiya kwambiri,,They deserve to die.what if those innocent children you were the father and someone saying those how would you feel ? instead of feeling sorry for those innocent soul because of poor management in the hospitals of Malawi and what you to know is that when the doctors want to take a serious operation that they always make sure that every thing is set ,not as what they are saying blood shortage…Poor malawian we will always be killed as cockcroaches ,,these greedy politicias are out there enjoying with their families our on money not donating for this operation to done by experts who know their work not these trainees…Am really ANGRY with you for your heartless words *#-+ Mtumbo wako matongo ako uli ndi ana koma iwe ?mwina umadya maliro eti?? Gojo iwe umakudziwa kubala ?? Mutu ndi machende ongodzadza ndi MAMINAwo moreover Machende amako galu iwe kuzolowera kumwa magazi eti nde upite ukatenge matupi a anawo ungochita ka Braai ukhwasule munthu opanda chisoni Phwala lako mboli yako Olivian Oliva Twist Pagone …
kkkkkk, #Alex, nkhani yake ndiyomweyi koma!?, don’t take it personally bra
Ndimayembekeza kuva good news not sad lyk this? What happen had happened May their soul rest in peace
Stupidity is writing your comment based on recent comments or based on a story of some headless chicken of a journalist, who said the kids died cuz of an operation cuz they were not operated… I repeat, the operation did not take place.
So sad may their Saul rest in peace.Rip
asatinamize its organized deal in a case dat they share never ever separated organ why doin surgery in absence of blood
So sad RIP
Nde wamva mochedwatu
May God rest their souls in peace
Onatulukabwanji mwayimo aliomatana
Am sure that doctors is making operation he surposse to punish. Can’t do operation if there is no blood how come.
Please dont trust this site. The kids went it cardiac failure cuz of anaemia, nobody operated on them.
May be you know the truth, tell us nicely u know people talking too much but he don’t no the truth is.
the kids were not operated,coz they were still waiting for mire blood to supply the kids before the operation & the kids were aready anemic.Im sure it was God time to make them die.
Ok may be we just prayer to them becoz if God says yes no one say no R.l.p
So sad Rip
Why carrying a serious case when you know you don’t have blood?
they died before the operation due to severe anemia..and the blood group reqiured O- is scarce (don’t trust this site
Beautiful babies, so sad . May their soul rest in peace
Sorry
Maybe its Gods plan,this is the first case in our country.if God says tdy is ur tym to die ,no matter hw many qualified doctors are infront of u,but u wil surely die bcoz its ur tym
The same operation was done in 2013 and was successful at kamuzu central hospital
zowawa kwambili. oroso kunu ku SA ziliko ana anabadwa mwezi wathawu koma ophatikizana chest nde akuti ngati kuli kotheka makolo avomele kuwapatula koma yimozi mwa anawo amwalila after operation nde akudikila makolo kuti ngat amvomeleza kutero ma doctor apanga mwatchito yao. but zimakhala zowawa kwaife monga munthu wamayi kusunga mimba mpaka miyezi 9 koma kungovutika pachabe so sad. Rip
May his soul,R.I.P
that kind of operation was once successful in Zimbabwe.
Zandikhudza kwambiri ndikaganizira mayi nzanga kungotsala ndi bala la operation lopanda nalo malipiro umalimba mtima ukamaona chiphyera nkumamuonanso mwanayo…zandikhudzaa kwambiri ana aja sanaenera kuwapangira operation kuno…anaenera anakanwatumiza kumaiko anzanthu amene amakwanitsa ntchito imeneyi….Autse Mumtendere…komanso tiyeni timupemphere nzathuyu amene waluza anawa…amene muli naye kufupi mpatsen mau a CHILIMBIKITSO…
Sure, mm zovuta komaso zopweteka,this is grivous story.
Mkanawatumiza kunja for advanced operation not zanuzo that shows luck of experience
Stupid Malawians osangowatumiza kunja anawa bwanji, mmafuna muphunzire ntchito pamoyo waanthu chifukwa chani, mizimu yao ikuvutitseni
mwapha ndinu zitsilu agalu amene mumaziona nokha oziwa
KCH inali kale,pano anthu ake samakhala serious pa ntchito, ndilibe nako mawu ine! RIP
R i p
Mwandikhumudwitsa.
Akadakhala kt adali ana amunthu wandale wotchuka kalekale sizidakafika potelepa. Amalawi timalimbana kufunira zabwino anthu omwe alindikuthekera kale oti zoterezi zidakawagwera adakatha kupita kunja ndi ndalama zaboma kusiya zawo zili phwiiii… Malawi nyasii kwambiri!!!
sibodza ife tikumwalira mkumati zikuyenda
inu mukumwalira??shiya
ifetu tikumwalira kkkk!!
kuno anthu akufunsa akuti kapena anawa mwapha kuti muchotsele ziwalo zikagwile ntchito kwa a president athu aja akudwala?
Kkkkkkkkk that great matikileta angayendele ziwalo za mwana,koma america!
anthu kuno kumudzi akutipanikiza ndi mafuso?
Ine ndikamva kuti awawa ndi a Dr kapena Professor so-and-so, sindimanjenjemera. Ena ndi awa adakwanitsa kungotchola nthiti ya Daniel Phiri wa. Ena ndamene akulephera kuyendetsa dziko wa.
Kkkkkkkkkk
was the operation done while there was no blood ????? MHSRIP
Wat i know munthu sapangidwa operation palibe magazi okwanira how come that the doctors operates the babies while there was insufficient blood? its lie you have killed ana thanzi ngati amenewo. God will punish.
The operation didn’t take place.
Sanapangidwe operation tu..dnt rush into judging musanamve bhobho
Ine I think anapangidwa angobisa,nthawi yonse akhala bwanji akanwalire 2 hours before operation?
Akubitsa anawapanga Operation koma chifukwa choti awapha. Ana athanzi akamwalire lero? Samamwalira dzulo bwanji? Mukaphunzilire pawanawa zoona inu anyamata aku COM
They were not operated on.
Someone was on radio yesterday day she said they were operated on
Do some research on survival of conjoined twins.. There is no way they can hide issues like these.
Its just that our media can’t be trusted
God will not punish anyone here coz if they made a decision of operating them, it was for there own gud coz the survival rate of conjoined twins is slim becuz of their physiology. So stop blaming doctors and do urself some research
RIP
Ndiye zachamba zimenezo osangoti mwalephela kuchita opaleshoni bwanji,madokotala akumalawi osaziwa ntchito yawo koma kukadakhala kupeleka asipline ndi panado basi,kulatila adwala.
Mmachitapo chani pa zaumoyo wanu mukapita kuchipatala?
Zomwe iweyo umachita.
U r stupid
when I hear about twins death ndimanva kuwawa coz I lost one of my boy was twins too, RIP parents just believe in living God
Concerned
may their soul rest in peace
Vuto ndi la magetsi kuzimazima musatinamize ife
My God ,RIP
zauchitsilu magazi mumatenga ma xul aja mumadya…anyani agalu mangova oparation et..u hv killed
Rlp
Sad RIp
I heard they died before..operation
Bodza limenero
May they r.i.p
Govt take note
Eeeeeee u Doctors is this true blood shortage?how many litres would these kids use in 4hours?may their soul rest in peace
Musaname kuti anasowa magazi pakuti ukadaulo wavuta apa, mumapanga ntchito yoti mulibe nayo zipangizo bwanji?cilungamo ndichoti afa kamba kotaya magazi pochokela ku opaleshoni inapangidwayo, osati kusowa magazi, iyah muuza ana? Fotseki.
Operation was never done bro
lnnali mllah waina illah rajiun
RIP l blame the surgeon, was not prepared enough
they died before the operation..and blood group O- is very scarce
Ok
Opération yogwiritsa ntchito nkhwangwa,fosholo,chikwanje muti zingatheke pa Malawi? RIP❌2
Pepani
Mhmmm Innocent Souls!…
mmmm 2 Bad
My Fear came to Pass, so sad MTSRIP
So sad, poor babies, may there souls rest in peace
so sad
So sad RIP.
Its so sad may their saul rest in peace, this was serious operation that it really not be done in malawi it was surpossed the goevernment to help to donate money so that it could b done out of malawi
Very true iwas even telling my self the same….
Its painful my friend
This Malawi is tired
And any time erectricity gone why they can manage to do the great job like this ooo rest in peace
The same operation was done in 2013 and was successful at kamuzu central hospital
well spoken bro
Kodi mwawelenga o mungopanga post ma comments?kanakakhala kachinai,ndd zakhala zikutheka katatu konse ndi Dotolo wake yemweyo.nd amwalila b4
Amwalira asanapangidwe coz blood group yawo magazi ake amasowa it was 0+
Zonse ndi a Escom, anazimitsa magesi, kodi company yopanda solution ngati iyi ikukhaliranji paka lero? igulisidwe sikutipindulira, ma bwana awo anakachosedwa ntchito coz samatha kupite ena, pano mukuti madzi achepa mvula ikagwa muzizati zinyalala zavuta, wake up Escom mxuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuu
They wanted to learn from them nothing else… Rip
Poor Malawi ndimadokotala omwe poor asogoleli poor anthu akeso poor kungokhala very poor,poor,poor,poor
Hahahahahaha????!!! Ndasekaaaa ngati zabwino tu koma ayi ndithu, moti pena ndimati Malawi ndi dziko lotembereredwa, ngati ndimalakwitsa, Yahovah andikhululukire, coz zimachitika kuno ndizomvetsa chisoni komanso zoseketsa… everything poor indeed. Pena kumaona ma citizens ena ngati amisala coz momwe akuonekera;osasamba komanso kusowa zovala zabwino. Malawi ndi dziko lomvetsa chisoni, literally, to an extent that you could cry. Koma poti amati Mulungu salakwitsa, we still give thanks for our land Malawi.
Hahahaha kulila sikuzatha m’bale kudziko lathu
poor doctors!? what role did they play in the death of the babies. the operation was not done, so do u blame the doctors for blood inavailabilty?
Very pathetic
Magetsi ake ati mmapangira operation wo ?
This is lack of expertism I am sorry for the death of these babies and am sure suppose the were born from a family of prominent politician the government could use government money to take them to an expert outside Malawi. May their Souls RIP
Shortage of materials in hospitals of our that’s leads to lost our familys and friends.government take note on that issue pliz Rip
very bad
Sometyms zipatala zakwathuk zipangizo ndizochepa coz vuto ngati ili likadadziwika before anawa asanabadwe n akanapenza njira yoti anawa athe kukhala pake-pake, so sad.
Angoamalizitsa kamba kosowa zipangizo.
So bad indeed…. koma yatha bwanji nkhaniyi kumapetoku..?… Chizungutu chinavuta ku conclusion ku… wake up malawi24!
I second you Chanza!pre op care
Nanga Kwathu Kuno Ma Surgeon Ake Ati Ndi Zida Zomwe Zero Mwina Akhodza Kukhala Kuti Aduwa Chifukwa Magesi Anathima
R.I.p
Due to blood shortage or because it was a complicated case?am sure they had to make blood available b4 surgery. Dont misreport these things
I heard the twins had. rhesus factor “O” negative, of which it’s really difficult for the blood bank to supply more blood for the procedure…….
Why did they start the operation in the first place?
Q
Amafuna kupanga mbiri kuti anthu awatame ndiye tiwatama ndi tsoka
Our friends azungu amatenga even years to prepare koma kuno ma short cut basi
ooooh what a tragedy
mmmmhh so sad
mmmm !!! so bad!
aaaa! this is sad news M.T.S.R.I.P
RIp
mesa amati magazi apezeka okwanira angoti ntchito inawakulira
Zoonadi ntchito inakura anaenera kukawapangangira kunja kwa dziko lino anawa…
Mmm 2 bad
REST IN PEACE
RIP