Gospel musician Patience Namadingo has fired warning shots at Electricity Supply Corporation of Malawi (ESCOM) over persistent blackouts.
In a video clip that was posted on his personal Facebook account on Monday, the singer insinuate consequences that may befall ESCOM staff should the situation remain static.
He hopefully concludes a day is coming when consumers shall know the one responsible for hitting the switch-off button.
“Akazangomuziwa dzina amene amazimitsa magetsi, kungomuziwa nkhope kuzavuta, kungomuziwa yemwe amadina, yemwe amadina, yemwe amadina batani lozimitsira magetsi, kudzavuta (when people will find out the identity of a person responsible for switching off electricity, there will be trouble),” sings Namadingo
The end part of the clip exposes real feelings from the artist as he addresses the situation. He violently plucks the guitar then exclaims, Ndakwiya kwambiri ndi zamagetsizi!
The video is currently enjoying downloads with many people sharing through social media platforms. Feedback has been overwhelming as evidenced by large numbers of people applauding Namadingo for his creative mind.
Malawi is currently experiencing never ending blackouts due to drop in water levels in Lake Malawi. The situation has gone from bad to worse with some areas going for more than 18 hours without power. This has had ugly effects in a number of areas.
Will tht make any difference??….anthu anayakhula kut asagulise malawi savings bank,alipo anamva,there’s plenty example of kusalabada in our govt
Mukati asalowelele fukwa ndi muthu wamulungu sono ife ndi athu asatana iyeyo samagona mmagesi
namandingo is also amalawian who z facing same problem of blackouts ndiye wangoyenera kuchitapo kathu kosatengera kuti iyeyo he z gospel artist ndi munthuso naye oti achitepo kanthu iweo #hastings #singini ukamufusa namandingo bwaj za climate change ngt akuphuxira ku luanar kwakoko usadxive mzeru kuliso anthu ophunzira kwambiri kuposa iweo nyani galu wachabechabe
zavuta kumalawi tangoganizani fridge zenizenizi anthu ayamba kusungiramo zovala ena kumasungiramo makope amafana akachoka ku xul eeeeee malawi ndima bad news.
In my poor understanding a man of God has a huge role in the society as well. So to me Patience singing this song is no crime at all. Don’t be holier than He guys. Atumiki a Mulungu ndiye ofunika kulankhula pa zinthu ngati izi. If I may ask ndi Umbuli wangawu did Jesus not send His disciple to fetch for a peny to pay tax? Was that not part of social responsibility?
Munthu wa mulungu wakwiya amwene
I like the song keep it up patience.azajaira
You can’t solve the problem
0888626587
Titumizilen ka Clipko pa 0994574040
Soka Limakhala Kwa Amene Amaziwa Chinthu Koma Sachipanga,,amaziwa Kuti Ichi Ndi Choyipa Koma Zazuzula,, Apapa Namadingo Wachita Bwino Chifukwa Iyeyo Ngati Munthu Wa Mulungu Aziwa Kuti Escom Yikuzunza Anthu Kulibwino Ndiyizuzulee Ngakhale Ndikampani Koma Yimve Ndithu,, P.Namadingo Wachitabwino Kwambiri.
Akunama patie waitha afikapoagaluamenewa
mmalo molimbana ndi dollar kumangolibana ndimangesi
Big up Patience…. “Ndakwiya nazo”
Big up Patience…. “Ndakwiya nazo”
Big up Patience…. “Ndakwiya nazo”
Malawi needs reform i wish… we should hv a crank-down of all old leaders who previously served a 10yrs term no matter to which political party governing @ that time should exit the open door for youngsters- 4 this modern world needs modern leaders not iron age leadership it doesn’t balance the generations need.
Wait i told you some MWians are gallon headed
Wait i told you some MWians are gallon headed
I don’t see why some of u r too emotional .. I think he was trying to entertain us and here u go calling him all sorts of names I don’t know about u but I think the human brain functions in different ways and your brain’s functioning is jus pathetic .. Aliyense akumakhala wa satanic kwa amalawi ambiri .. Who r u to judge tamakulani anthu … Ndipo its true if some of u knew adina kuti magetsi athimeyo munakamupha kumene why do u have unknown hate for nothing .. Votsek
People are fond of making names out of nothing. To me the clip has nothing wrong. Honest speaking what he’s done had to be by all Malawians. Kwathu kuno zinthu sizikuyenda. Both Escom & Water Board akutionjeza kwambiri. On the hand the guy has just proved how rich he is with talent. Zamunyasa ndi zake zimenezo. Palibe akachite sacrifice nyumba ya kwao kuti magetsi asayake. Big up Patience
amaitha
Sopano video-yi povinira pa nkhokwe bwanji?
kodi anthunu munakhala bwanji?uyunso wasanduka wa satanic?kodi mumadziwa bwanji inunso mumakhala konko ku satanic ko?chifukwa amene amdziwa mfiti nayenso amakhala kuti ndimfiti amatambira limodzi
Mawu!
ukunama ase actions speak loud than words
Namadingo know nothing about Climate Change….you have just destroyed your reputation as the gospel artist……shame on you…..ESCOM imagwesa Mvula?….Umbuli wanuwo khalani nawo choncho…..ndakwiya naweee
Naweso nd umbuli wakowo ndno bwanj ESCOM imango onjezelbe electricity consumers yet magets nd ochepa wy!!!!! Iwes usandkwiise ok.
iweo usamadzive mzeru kape wachabechabe iyeyo namandingo ndi malawiso akuyenera kuchitapo kanthu xa escom iweo galu sukudziwa kanthu
Ndipo anthu onsewa akusandaula zamagetsiwa iwe waona namadingo ekhayo ndiweso mbuzi eti
Nonsenu ndinu nkhuku….simukuziwa zomwe mukunena…..muzingodya za achamanu apaaa
Who is he? Kkkkkkkk koma tiana toyimba nyimboti
Auze ngamo
Escom si company yopikisana nayo wanyika ase kkk malo mogwada mkupephera kwachauta apa ukukaimba nyimbo yoweruza wat 4 kapenatu ndinu a illuminati masiku omalizadi
Electricity Supply Commission of Malawi amatero ku zionetsa kuchenjera mwapala nazo apa kkkkkkkkkkk lol abbreviation inavuta apa kkkk
Tigawireni +27837465498
halla me on 0881420707
I have done that
Still waiting
Nothing will change
Keep it up old friend that’s the sign of patriotism. Your true son of Malawi. Since you spoke these for the first time in Lilongwe being in electricity for 24 hour. Am blessed, we need such brave and courageous people like Namadingo not always Yes Bwana. We are tied
Wat are those phone numbers 4?
Ineyo anga ndimasowa
Ineyo anga ndimasowa
Mukulimbana ndi uthenga wa Magetsi malo mofalitsa za thenda ya Edzi yavutayi wat is magetsi after all
Mukulimbana ndi uthenga wa Magetsi malo mofalitsa za thenda ya Edzi yavutayi wat is magetsi after all
Nde mwaziwa mochedwatu.
So what ??? Why can’t you lead us into prayers ??
Kukhudzidwa kulibe zoti uyu ndiwa gospel mind u newz 24…
Ndye magesi angasiye kuzima bcz of mr bombocrat kaya mumamuti nadingo zazi m’malo mot uzikamwa magaz kumidima kwanuko iya
Udamuona wakumwa magazi baba samalani mpagulu yapa
sibhoo kumunena munthu umboni mulibe mulungu akhale nawe pansi!
Ngat mulimadolo panganipo kanthu ndipeze mavuto chabwino pakut panu agalu inu chonsecho mumagona mu nyumba zopanda magesi ndye mungandiuze chan inu
Amene alibe ayike watsapp number yake ndigaile..
0740916867
Ok fine
Dia l don’t find your number please add this number and just say hie +265888333814
0888494710 share me
Zatheka eti?
This blackout their bringing our economy down.Malawi the stupid dead state
q
Sorry we hv changed the name from ESCOM to BOSCOM(Black Out Supply Cooperation Of Malawi) if we change the name again, we will xplain to the public….soon after America
0881969658
kekekek #akazangopezekawothimisamagesi
Porah!!!
my dad once sent me to pay electricity bill and i used the money to play airtel car competition. When i got home i explain what i did with the to my dad hoping he will understand but he beaten me. Next day when we woke up my dad opened the door and there was a brandnew car standing outside.We were so excited and in tears. Until we realised that is the electricians with their tools to cut our electricity off. and my dad beat the crap out of me eish #zovutazedi
kkkkkkkk
Nafwaaa
mukanalemba chichewa ndife ochewa ife iiii chavuta chingerezitu apa ,nafwAaaa yemweyonso nane
Akafuna kupanga show amawauza kuti apangeso hire generator nde zikumalowa zambiri ndizowawadi tiye nao namadingo
THANKX 4 DC IDEA KOMA AS NOW MALAWI 4 SELL
If u dont hv dat video jst drop ur whatsap ill send it
0027780157435 plz send it to me
0999926719
0992181543
0740916867
0888402188
0991167647
0882833272.tadalila man bho kma.
0991235076
0888606239
Kkkkk…ndie magets asiya kuxima?kapena water level ikwera? Zaziiii..
Sure
siunalakwitse… nanga ma session angayende bwanji?
Thats gud i dea
Wasatanic ameneyo shoupt
Muli ndi umboni onse kut ndiwasatanic, naphapo ndani modz mwa inu kwanuko , ok abwana tamva, zomwe mwanenazi , komaso saletsana ai . Nde sibwino kumaipitsana mbiri zonyasa pa gulu la anthu, pamawa mzalakwa nazo
Baba mudamuona wakuchita zausatanic samalani yapa mpagulu
kufuna kuntchuka kwambili anamadingo limbikilan
Next time my fellow brothers don’t let things go to point where it can’t be solved #organizeabigmuch n shut down Malawi in so doing thy will respond so quick plz all workers starting from the government labour n thevself employed pipo plz do it n u will blv me thy will take attention on that do it for 3 days no one must go plz plz i beg
Blackout Will Never End Till Our President Dies.
Zazii! instead of composing gospel songs
Well done Namadingo!!! Bt to de other side ‘t wrong kulowelera nkhani ngati idzi as a man of God..
hhahaha wrong interpretation of things. So, man of God has to remain quite mkumaonerera zinthu zikulakwika? Malawi sadzathekadi
Kkkkkkkkk nzeru zachepapo apa
man of God does not need electricity.??
Pangan zomwezo man 0999531845
Zikulakwikadi koma nyimboyo is it a part of Gospel?? Ok mwatengamo uthenga wanji wamulungu?? Nothing
don’t bac ur self mr #chavula he is a concerned citisen too he has the right to criticise where ever things r not ryt so u expect that a gospel artist must just concentrate on Gospel music wherby he sees that his fellow Malawians r in limbo I guess a big No to #Teamblackouts
Ok big man Mr Mike” point taken l hv nothing to say… Let it be lyk it is.
TIKANAKHALA KUT TONSE NDIWOYELA MTIMA YESU SAKANABWERA AND MUNTHU WA MULUNGU AMADZUDZULA CHOLAKWIKA AKHUNGU OKHAOKHA SANGALONDOLERANE NJIRA NDIYE NGAT ANTHU A MULUNGU AKHALA CHETE ANGAYANKHULE NDAN POKHALASO MFULU WA DZIKO MAVUTOWA AKUKUMANA NAWO
Zamveka #Tawonga palibe nkhani apa
kkkkk,lol,idakalipo nkhani apa #chavula
kkkkk,lol,idakalipo nkhani apa #chavula
Angamuope ameneyu? Kkkk
Wayintha mfana
Tell us alternatives
He is min! Escom is a victim of climate and political change! Until you and me including the Namadingo realize that we have a role to play. (i.e on next polling day or our behavior: environmental management)
What if the environment still stand the way it is now, should we still tolerate this? Think big mr Phiri, Escom has to go for other power generating alternatives we f….cd tired of ………
Bertino Sir! That’s why I am saying “change” hence there is need for escom to adapt this change too!
Kali bho ndili nako….lililili
Ndili nako ndipo kali nyatwa
A Escom aojezadi
Mzimu oyera alikuti,,,,?
ok
tigaileni ka clipko guys
Hala m on 0885774949
i lyk the clip ndipo wachita bwino. wait soon il realise myn #escom_watchout
real artist.umatiyimirira Namadingo.
Wakhwana mwanayu ..tikazangomugwira ameneyu tiżamupanga za Bin ladeen
correctly done.
inu mukuziwa lero???
Zitanthauzanji kwaife?
Gospel music?
Gospel is Body and soul
Zazi!!
sanalakwise tilipambuyo pake
Chabwino