Machinga second grade Magistrate court on Wednesday sentenced a teenager and an old woman for trespassing and tampering with a grave at a village in Machinga district.
The two have been identified as Faison Walusa, 18, and Sime Daimani. State prosecutor MacRhino Lungu said Walusa was also answering charges of being found with human bones.
The woman however was only answering charges of trespassing since she directed Walusa and three others to the grave Chiuja Kenneth who died after committing suicide.
According to Lungu, Walusa and the other three thugs who are at large exhumed the body of Kenneth and took ten pieces bones.
Passing his judgement, second grade magistrate Maxwell Boasi said what the convicts did was inhuman.
He then sentenced them to two years imprisonment with hard labour.
Walusa comes from Mozambique whereas Sime Daimani is from Chigomile village in Traditional authority Ngokwe of Machinga district.
Ufiti
Amafuna akadye kapena akangulitse, sor this is a very bad behaviour.
Zodabwitsa izi,.malawi wangotsala ndi ma court okha basi ma judge adatha. Ine nde kungopeza anthu amenewo.. Bazuka agwire ntchito,.
Ufiti
komatu ku machinga satana nde apondako ndi mapazi ndithuuu
Atleast they will have something to eat at jail let’s hope jails have enough food aswell. Kusavuka ndiufiti nanga ncha?
koma kumwera nde awonjeza chaka chino,,,,,kaya nchifukwa chanjala kaya mpeto ake azayamba kutisaka ngati nyama za mutchire nanga tinene chifukwa chaumphawi????? ngat ndiumphawi bac uli dziko lonse la Malawi…
only 2yrs,akanangokonzatu zimenezo
Its not like the guy took the bones ayi anzake anamunamiza kuti akawedze nsomba kma atafika kumanda anafuna kuthawa kma anamuopseza kuti amupha amukwilira komko and they will cum back kudzatenganso mafupa ake coz amafuna mafupa angozi….after kukumba mandao the guy anakaulula yekha kwa amfumu
Bones of dead person. …
Yoh yoh we will go to punishing with god
Yoh yoh we will go to punishing with god
mmmm ths district why bt?
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
2yrs only? eshhhh God will judge himself anthu otembeleledwa inu mukayankhanji pamaso pa Mulungu ??? shameeeee! !!!!!
2yrs only? eshhhh God will judge himself anthu otembeleledwa inu mukayankhanji pamaso pa Mulungu ??? shameeeee! !!!!!
Aaahhhh so with 2yrs only u think dis act will end?anthu amalizatu ma albino onse,,what a shame on malawis judicial system aahhhh tanzania amangophatu zimenezo
Munthu oteleyo akapezeka Nayenso
Mpaka kuba mafupa?
the root of this? – the belief in witchcraft. its disgusting
kma kumachinga ayayaya
give 30yrz
its too much now what are yu malawian police doing
milandu amaweruza ndi a court not police
owk. bro
My district eish so bad
2 years is too small, what kind of a judge are u? Be serious when giving a sentence please.
Sugestion ” Any human found in connection or posetion of fellow human body parts should face mob justice”
munthu amaba kubzala kotaya zinthu zopanda ntchito
Umbuli basi ziphani ma albino zisatikhuze
Iiii Izinso Ndiye Ndi Zinazinatu,,,
Koma ku machnga zanyanya
I’m not convinced with the 2yrs IHL sentence.
I prefer mob justice
Anthu amenewa tikapexa otchani.ma judge nawo amadya nawo ndalama zamafupa bwa
Koma yaaa
Arrest them fools…
Machinga,Mangochi,Kasungu,Phalombe ndi Dowa.Maboma awanthu okhwima mopanda Chisoni ndithu
Mwakula ada Amanda
Any crime=2yrs sentence??
Amenewo nde kuwapasa 2 kwa iyayi chifukwa choti ndi achi zimayi akanakhara njonda pamenepo bwezi mukuti 21 kwa iyayi
Mmmmmmmmm hhhhhhu
Zigamulo zanuzo ndizimene mupangitsa anthu kuti azingolanga okha, komano kuba nkhuku ndiye mpaka zaka 5 that is stupid
Zimakomera anthu okuba okupha amene sumapanga izi umamva kuwawa dziko lathuli mavuto ndiosayamba guyz tinangozolowera coz alpolices lyk money withought money nothing can’t be better
2 yrs only???Apolisi akuyesesa kugwila zinyama zimenezi koma inu a court mukumaphweketsa zinthu..mob is gud.
Kkkk tere afera kufifintha? Koma kufera dzawenidi ndithu.
Agwileni
two years!!! what it were bones of their relation you people giving sentences. why not slapping them with 15 years. these days 2 years is two weeks. wachamba 2 years albino attackers 2 years sizilibwinotu apa. abale let’s unite for change to some of these sentences.
Zaka ziwiri zokha? Za chamba basi. I think any crime involving human body parts should be fetching stiffer penalties.
Koma anthu akulimba mtimba eti,koma ndi zoona kusiya kugona kukafukula manda? Aaa apa mwandiopysa aMalawi
akukuuza iweyo ukapeze mafupa a abale athu achi albino kuti ulemere….iyeyo ndie osauka kotheratu buanj osamufunsa kuti iyeyo kulemerako samakufuna???anthu opusa mwana wahule.
Tizakato tikucepa conde kodi bwanji
Why a two yr sentence with such an inhuman offence… Anthuwo ndi Mfiti