Daring thugs on Monday stole a gun from a police officer as she was guarding World Vision International office premises in Thyolo district, Malawi police officials say.
The thugs injured the officer during the robbery and she is receiving treatment at the district’s hospital.
Police identified the officer as Elida Kusakala who was guarding World Vision International offices in the district.
Reports show that the thugs attacked the police officer as she was doing rounds in front of the building with two other officers.
It is said that these criminals tied up the guard who was watching over the premises but it is not known whether the thugs had planned to steal at the institution.
Kadadzera said that it has also been established that the thugs went away with the officer’s gun. He said they had not yet arrested anyone on the matter saying investigations are still underway.
Iwe sumaba?
Iwe sumaba?
Boma lachitetezo Dpp wo eeeee! Ine niribe polobulemu kikkkkkkkkkk koma ku Malawiiii
umangoziwilatu.
umangoziwilatu.
achita bwino
Zolembana kudziwana!!, zimenezo ife zitsatikhudze thananazoni nokha, coz ife munakanika kutilemba ntchito poti si abale anu!!
Zolembana kudziwana!!, zimenezo ife zitsatikhudze thananazoni nokha, coz ife munakanika kutilemba ntchito poti si abale anu!!
People in thyolo are living in fear there is no security, anthu angophedwa every weekend
People in thyolo are living in fear there is no security, anthu angophedwa every weekend
Sitimanewani tija tija timeniti? Upolice omalemba tiyana ta 17 year poti ndimwana wachemwali anaphiri basi ena ali ndi paper labwino anamaliza geri 2010 mpaka pano no job koma awa kuwatenga mayeso a 2014 asanatuluke eeee dziko ili kaya
Sitimanewani tija tija timeniti? Upolice omalemba tiyana ta 17 year poti ndimwana wachemwali anaphiri basi ena ali ndi paper labwino anamaliza geri 2010 mpaka pano no job koma awa kuwatenga mayeso a 2014 asanatuluke eeee dziko ili kaya
Amagona ameneyo
Kkkkkk…..my mother land
kkkkkk
kkkkkk
Bvuto si iye,kma omphunzisa ndi omulemba.zolembana kuziwana, mwati mkazi,zithera komko.
Bvuto si iye,kma omphunzisa ndi omulemba.zolembana kuziwana, mwati mkazi,zithera komko.
Iyenso amaba
zolembana sunday we hav strong citizens here koma tilibe yo disha abalenso tili kuti tingapeze vep zimene then we have to train them how to be a police officer …kkk its part of training
Ntchito za ana amunna ndi amuna basi zimawonekelatu nthawi yowumba madongo mkazi samaumbapo mfuti koma wa muna
Ntchito za ana amunna ndi amuna basi zimawonekelatu nthawi yowumba madongo mkazi samaumbapo mfuti koma wa muna
Komabe nzoona zenizeni zomwe ukunenazo.ntundu wakuba ndi wakuba ndithu.
Hahahahaha malawi yanga
Inu a #Malawi24 u re coming pano while this happened 4days ago,it was the same day u posted this is when then #Gun was found in a tea estate ku Thyolo komweko,pliz try 2break the News as soon as it happens,
arrest all her boy freands mfuti imeneyo ipezeka basi otherwise it’s zero pa ten
Ine kumvera mkasa song ANALIRA on repeat, mkango kulandidwa nyama mu territory chimodzimozi wakuba walanda mfuti wapolice kkkkkkkkkkk shame
Moyo sagula Sister, Wachita bwino kumusila mfutiyo wakumbayo, bwenzi atakupweteka ulele, kunja kwavuta uku . Usafele ntchito .
Anthu aku thyolo ndi mbavadi ,ndaonera olamulira ochokera kwa che Moto (Ndata)
Ndipang’ono pamenepo aunt tiyamba kukugwilira kenako ndikukulanda mwado ndi mfutiyo wanvaaaaaa
Iye amalondela ndimfuti ife tatenga tipangile chuma asa abwereso wina tizatenganso gulu lathu equip ikusowa
Wapolice pamene wakhala nfuti imakhalapomwepo,pepani, munthu sungayiwalile mwendo wako poyenda,
Wapolice pamene wakhala nfuti imakhalapomwepo,pepani, munthu sungayiwalile mwendo wako poyenda,
tha’ts a problem of not well trained ,am always left after interviews 4 having a triangular shaped head
tha’ts a problem of not well trained ,am always left after interviews 4 having a triangular shaped head
Its her boyfriend that stole the gun because real thugs would stole the gun and kill her
Its fine as long as she is alive.
Pamakamulo a asilikali akunena kuti asilikali azikhala awiri kapena kuposela apa. Here u talk of only a woman police, was she alone?? If others were there what did they do in order to overcome robbers?? Apolisi timadalira inutu ndie msazionese ngati ngati ndinu ofooka. Mayi osakhumudwa, zimachitika pa moyo wa munthu. Limbikilani ntchito. Mukazagwira wakuba aliyense bwezerani chiwembucho. Koma osapha. TAPULIKANA??? Tilichete pa RUMPHI. MONILE MOSE.
Kkkkkkkkkk koma ndi wa police amene? Awachita bwino adzichenjera.
Kkk this is my riffle,it is my best friend,without my riffle i am useless kkk.
kkkkkkkkkkkkk.bullshit
koma chonsecho anaphunzitsidwa self defence mmmhhh changa ndi chisoni
Hahaha women are weak ase though amawapanga recruit in the army and police..if that incident pakanakhala panali wa police wa mmuna tikanamva kuti waphedwa
Kudelera magarden boy kamachoka kuno Ku jon
Imadya pomwe yamangililidwa
ntchito ZA PACHIBALE akanakunyenga koma.
mmmm,mwina athana naye.
mmmm,mwina athana naye.
hahahaha
kkkkkkkkkkkkk koma apolice akumalawi kaya kufoila kaya
Pepani kwabasiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii
Tight security imeneyo?
So you characterise a thug as darling?
akuti daring osati darling man. bwanj phuma. kumawerenga chimodzichimodzi ngati vimakuvutani vizunguvi.
Zokambilana ku mowa izi
ndiye?
ndiye?
How
How
pepani “#collection ,,wapolisi wapasa wakuba mfut wake kut akabele anthu ena…#malawi24.com
pepani “#collection ,,wapolisi wapasa wakuba mfut wake kut akabele anthu ena…#malawi24.com
Praise God kuti sanamuphe, here in South Africa a police with a gun is not safe akuba amamupha ndikuba futiyo. In this case i can’t blame the officer.
Praise God kuti sanamuphe, here in South Africa a police with a gun is not safe akuba amamupha ndikuba futiyo. In this case i can’t blame the officer.
chilichose chalowa tchayina,apolisi nawonso alowa tchayina,boma nalo lalowanso tchayina
chilichose chalowa tchayina,apolisi nawonso alowa tchayina,boma nalo lalowanso tchayina
Wakuba anamubela
Wakuba anamubela
Wa polisiyo amatani kuti mfuti ibedwe? Anene bwino mayiyo!
Wa polisiyo amatani kuti mfuti ibedwe? Anene bwino mayiyo!
Please english
Please english
True lies
True lies
Koma ndıye tızıtı chıtetezo chılıpo nanga ızı bwanjı kkkkkkk mpaka wa polısı kubeledwa mfutı
Koma ndıye tızıtı chıtetezo chılıpo nanga ızı bwanjı kkkkkkk mpaka wa polısı kubeledwa mfutı
kupusa kumeneko zoona wa police weniweni mkubeledwa mfuti ndiye kuti amagona thank god anangomubela osamuombera nayo
kupusa kumeneko zoona wa police weniweni mkubeledwa mfuti ndiye kuti amagona thank god anangomubela osamuombera nayo
nde yake!!
nde yake!!
nde ife titani ??
nde ife titani ??
Yagwira ntchito apa ndi mbava, bwanji admin sunayike logo ya mbava?
Yagwira ntchito apa ndi mbava, bwanji admin sunayike logo ya mbava?
ntchito zapacibale azibetsa choncho mfutizo,sanamugone kma ameneo?
Hahahaha ibu,thawi:Dbetsu mfuti kkkkkk aa wakuba ndioopsad et mpak wa polisa betsu ap nd bolas wa G4 ap nd zfikap tidalile ndan????
Kumeneko ku Chimake cha mbava according to statistics,Kodi simmadabwabwa kuti ngakhale president ndi mbava, si ena aja imfa idapeza akuthawisa matumba andalama? Mtundu wachabe uwu pilizi
Kkkkkkk
Kkkkkkk
Samala m’bale
przdent yu Umbavawo ndiye Angapose Amai anu!!???mukuwaziwa Ulemu ndiumene wandipha ndikanawatchula.
Asamalepo chani ndimbale wako ameneyu??
Asamalepo chani ndimbale wako ameneyu??
Kunena pagulu kumakoma and sikumavuta,koma gulu likabalalika umasala wekha its when umadziwika,utsamale lilime lako nzanga ndi dziko kapansi ili ukatha moyo uno tikakomananso.
Do I live on your farm that you can threaten me? Look at yourself,idiots that think they r the best than everybody. You are fools with no life. No wonder your old half dead president climbs on top of the mountain and announce to the world that he has no proplem while ppl he leads are dying of hunger,diseases due to lack of drugs not to mention unemployment and high cost of leaving. You r senior fools, shamelessly praising a failure who is only good at thieving with his group of thugs in the name of ministers
Tell them man
Tell them man
pepani kuzolowela ntchito, anawona kuti sali ready mu zimai ameneyo kkkk sorry
kodi ndi mfuti kapena gologodela?
hahaha azichenjera naye buahahahaha akuifuna ilipo plzz kindly inbx m
[READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS.
Kkkkkk wagulisa asaname ameneo anamenya deal ndizosatheka kuberedwa mfuti,
Kkkkkkkk Kekekekeke Apolice Athu Amenewo Heedee Uluuuu!! Tiye Naoni Apolice Wa Amanyanya Akamathamangitsa Mavenda
Wa police akabetsa Unyolo kapena Mfuti Nyota imasika n’ithink it was a Mission how come people without any weapon managed to rescue aGun She could Fire awarning Shot n’they cn be dispersed!Remember those guns will be used 4robery
Women are weak though govmnt recruit em in the army and police..that incident happen in blantyre also wen thugs attacked a male officer mkazi anakanika kuombera and ankangolira mpaka kukodzedwa ma cases ngati awa amaphedwa kwambiri ndi ma male officers
Absolutely true
kupusa
Kma Ndietu Mpaka Kubeledwa Mfut nthaw zna amakhala atagwrizanatu cifukwa nowadays police officers are fond of corruption
Akanagwilizana wa Police sakanavulazidwa ndi chitsulo mpaka kukhala admit ku chipatala
Akanagwilizana wa Police sakanavulazidwa ndi chitsulo mpaka kukhala admit ku chipatala
Ndikhal8iwe lawo, IMAKHALA NTCHITO YATOPESA. Manyamulidwe ake ndi amenewa akumalanditsa mfuti
apolisi aku shambani amenewo sakhala a juck up,amakhala atulo kugona ndi masana omwe
mwina ndi chibwezi chake ameneyo kkkk
mmm pangani
mmm pangani
polis inali kale ya azibambo athu ija
polis inali kale ya azibambo athu ija
Kkkk, Waziziwa
Kkkk, Waziziwa
Mmmmh Ndiye Akapezeka Tisiye Kuwaotcha. Kkkk Poti Mukuphweketsa Chitetezo Nokha Ife Tikawagwira Tizingowamba Basi!
kodi chimanga bag ku admarc lili pabwanji
akuziwana
kkkkkkkkkkkkk are we safe ??????if a full trained police officer akumupanga zimenezi nanga enafe
Kkkkkk bola aG4s police kubesa mfuti aaaa
How?