Malawian artist and Times Television presenter Annie Matumbi who is popularly known for mocking fellow artists, has been at again as he has openly ashamed afro-pop icon Maskal.
During a live broadcast of “Urban trend” programme yesterday, Matumbi whose real name is Chiyanjano Muhezuwa, uttered words which may be hardly accommodated in Maskal’s ears.
His ill language followed from the “Udalire” video by Maskal, when it came to an end, Matumbi could not help but go off-track to mock the Udalire star concerning his live perfomance.
“Ameneyo ndi Maskal akuti udalire. Nthawi imeneyi anatchuka Maskal aliyese kumangoti Maska! Maskal! koma pa stage kulepheleratu, samatha ata, (that is Maskal. He was man of the people when he released this video but when it came to live performance, he was as good as nothing), ” said Matumbi
Matumbi is considered to be an artist who uses sarcasm against fellow artists.
However the audience is meant to understand that he does not mean it.
A few years ago, he released a song which exposed mistakes by other artists on the claim that they are all his friends hence the liberty to make fun of them.
Hehehehe koma guys!
Ng’weeee!! ng’weeeee!!! ng’weeeee!!!
Success attract alot of enemy
Aaa zoona man2mbi waitha
Ummmh Man 2mbi! Reality talking z wat we bliv in. Ndimakufila man. Ngati ukunama ntchentche indizomphe pa msanapa!
so what?
Malawi woyeeeeeeee
Tamva kt maskol mwathana naye ndiye wasala wina ndan auzin amalawi24 Amtumbi kt ave
kkkkkk sydo mix happy hour
kkkkkk sydo mix happy hour
guys 2mbi sakunama and u knw it,kma an2 omwe mumamkonda maskal smukufuna kuvomereza ngamo,,,! maskal amatha kuimba kma pa stage zmamukanika,tinenepo ngamo apa..! amene mukumunena 2mbi kt walakwitsa mongozitaisa nthaw,coz iwowo nzot amachezerana,inu mul bzy ku bwebwetuka apa…! osangozisia bwanji,ainakewo akuziwana..!
Mnkhwidzi za anthu ena kufuna ma2mbi zimudere…
chilungamo.
ku inbox kwanga kuli malo, ma babies nonse ndipezeni ticheze wezi,o salimbana nawo ma artist amadyera mbale imodzi,
PHD syndrome
#Maskal is the biggest part of my playlist. I wl never stop buying n listening t his musik, even goin t his shows……. #Maskalslingjay
za rudo eeeee!! ma nip akewo
kaya ???
dzulo nde ndinayaka guys…..
Man mulipo mwasowat
aaaahh!! basi..
I thought being a broad caster is about being a man for the people, not a selfie… He aught to have out grown the practice… Big up Maskal ndinu ma pioneers a modern music m`Malawi.
zakumachende et!! Pali nkhan pamenepa..
Yoo!!
Music is a mission not comption memba that
Zikalakwika nenani osamango buulira mkati #Masko zimakuvuta pa stage sakunamizira
2mbi amanena ngamo masiye uja saatha ndi panja penipeni lol kkkkkkkkkkkk
Zikadalipobe??????????????????????????????????
nsanje
za ziiiiiiiii
hahahaha
A2mbi Aghenano Eti Mpaka Kumuheta Maskal?? Maskal Ndi Doro Kaya Samatha Pa Stage I Dont Care Ndimamu3ra Mfana Uja!!
maskal yemweyo
Athumbi tatontholani mose mwayambira kulira muja. Munatha inu tangovomerezani basi. I know kunyoza anzanuku mukufuna attention ya anthu basi APA mwayipeza are u happy now???????
Iwe ndye umatha?
Non of my business
Kod Flames ndi team yaku Malawi konkuno?
u r like ma bra
Tamva ndiye inuyo a Malawi 24 mufuna ife titani?
Ukhalira yomweyo anzako akupanga makobidi.Iwe ndinyumba yomwe yosalongosoka mpanda wa tsekera kuvalanso kukuvute ntchito mowa basi,panga zoti udzasiyire ana ako.Zapa stage chikukukhudza ndichiani?Nyumba yomwe umakhala ingafanane ndi ya Maskal?Kuli Taygrin,Blasto,Theo Thomson ndi ena ambiri amayenda mma overseas ndikumakamenyanso bwino pa stage koma akabwira kuno samaloza chala artist aliyense kuti samadziwa kuimba pa stage.Iwe ngakhale ndi Makawa siungafanane kumbali yandalama but ur no.1 kunyoza anzako.Mowa weniweniwu umamwa kachasu mtengo wa black label siukuwudziwa.Udzafa ulindi mache…..okhaokha
ngamo wayiwala uja anapala ku lake of starz
In as far as music is concerned …Maskal satha kuimba” ma off code.. plus pena ikwere zosakhala bwino”‘ i like his music thou'” koma satha kuimba & i dnt hate hm.. koma chilungamo
Basi??? Iweyo ndiye umatha??? Malawians u will never change
Mzoona Maskal pa stage samatha kuimba….mufunse anthu ku show yake ku Jonzi aaaaaa
kkkkkkkkkkkk chonchi tisamabene? kumangopanga zin2 ngati mugula nokha bwanji ? pangani zoti an2 akamva akodwe osati kuyambanitsa an2 omwe amakukondani!!
macheeeeezanu achabe a thumbie
let,s try 2 accept the reality.
iiiiiiiii zimene amakamba zija nzomuchititsa munthu manyazi,,,?smungayesele klemba nkhan yoona,,?
amene ali ndi charger cha cmo head andibweleke pliz
Hahahaha ine ndili nacho
ine ndichifukwa chake ndili Nganganga pansana pa #PIKSY…iwe Matumbi ndiye CHIDZUKULU cha #DZITSILU….bwanji osapanga zako??? kuimbaso siumatha kuyambila kalekale matama okhaokha,,,chimbale chilichonse utatuluse amakupanga feat anzako,,taona sopato ukuyamba zandale,ulimbikile kuti uzafanane ndi PIKSY N MASKO,,,,kaya amakumenya ndani panyimbo zako CHULE iwi,,kulira kokhakokha munthu ngati CHIMwana
chi page nchopasula anthu, guys zifuseni kuti ndiliti lomwe chi page chonyasachi chinapangapo post nkhani zoyamikila munthu or za nzeru ? ndipanga unlike basi, bye bye
Koma Malawi sathekaponso ayi kaya ndindani anasintha zina lot nyasaland bolani nyasalandi kusiyana ndi Malawi. ….
Iwe nde….wa breza ngamo.₹₹₹Up! Up!! My man.
Kikkkkkk
kodi kamunthu kopanda minofu aka kadakalipo?
Nthawi zonse chilungamo kunyukunya
Thyolo again Eeeeeeesh!
Matumbi. sadzathekanso
Zoonad maskal live perfomance imamuta
Is this news? Malawi24 at it kkkkk
Ntchito Zina Za Kape!
U r all our artists & we luv all,nobdy behind nor ahead of other.
maskal ndi dilhu zili ndi iwe kuti umukonde ngati ine kkkkkkkkk dedicated ,to my wedding day zili ndi iwe
Amatumbi mukuphukilabe kod ?
Truth always hurt mkanakhala maskal ndikanavomereza past weakness coz 2mbi amakamba zanthawi yakale not now! kmaxo oyimbanu mumaziwana bwanji Lulu ndi 2mbi ?
Matumbi anatha kale kale .ndani amavera nyimbo zake
mukunena za ku luso kodi lusoyo ndiyake munthu susintha company? ngati anaona kuti ku times kudyeka bho enanu zisakuboweni….mulekeni aufire basi mo fire 2mbi
Amanama ngati?
Nyakwawa amatha amwene …. mukufuna muziti chani apa inu zoti maskal amalowa ma off code nyimbo yokhala yake simunaziziwe…..samathadi pa stage Maskal ndi studio artist basi
ma off eni eni…ine it was lyk i was joking nyimbo ya zilindiwe” was telling my frend kut koma ndie walowa ma off ..kkkk koma mzoona” dzimamuvuta
kupusa……
NDE maskal kaya alikuti,anathad
Kukula konseko kuzipasa zina la chikazi….Kufuna kutchukira zina la nzanu.muthu wankulu koma kumalira munyimbo..hahahaha….zakoyo ndi wina winner…malo mozenga milandu uko kulimbana ndi madolo…ndalama zojambulira nyimbo zinachokera nthumba mwako?eee?…..prat…panga zako zikuthandize mwina uzafika pa Maskal….koma i doubt if u will….amatumbo….sorry amatumbi…
hahahaha zani izo ife tili phee
nc pic
Ngati Matumbi anayankhula choncho ndiye kuti iyenso nthito saiziwa. Matumbi nyimbo zake zonse amajambula Video ataledzera komanso amakonda kugwira pa lisani ngati akufuna akodze. Mwachidule tinene kuti akumana osatha okhaokha koma powayelekeza Maskal ndi dhilu.
Hahahaha kma amakwere
Si anzathu awawa ndi ma haters nooooooooooono , ndipatsire machine gun ratatatataaa, ndipatsire bazuka kweeeeeee phu, ndashuta. I like Atoht manje Majerasi.
kkkkk dats stars ov Malawi kumaphwesana choncho dat hw world goes
KuNyasand ngati kuli zoba ya oyimba ndiye ndiMatumbi,Nyakwawa yamakape…!
Iwenso zoba
hapy with ma two cousn in capetown
Oooooooooh
Piwah Nkhoma
Matumbi akunena zoona Maskal sathadi kuyimba Live vuto lamalawife timadana ndichilungamo
nothing wrong here nde thumbiyo amalawi munazolowera kuyamikila mbora basi here we go with leadership hardships…. munthu akazuzula mwapeza nkhani kupusa eti munya criticism is there forever
ma guyz a 24 u suck n’ honestly i dont knw kti amakutuman nd ndan bt u jst confuse ppo,cant work on me though.ingoxekan ma studio anu bax agalu opanda michira inu.
Reality talking z wat wi bliv in
That’s the theory of jelousy,allways tryn to pull down who’s doing bettr than you
Nsanje, kaduka,nkwidzi, uchisilu uli thoooo mumtima why mkumapitaso mma nite xool kukaphunzila kenaka muzapangeko post mapositive stories kutero Malawi azatukuka osati izii even kuvaya kujoni vep ndizambiri kuno mumatinyasa zomadanisa anthuzi inuyo alesi osakonda ziko lanu lomwe
Chace VanderWolk
Bo Clayton
ife ndi 2mbi basi
0
Kodi mdalai mose muja adayamba ulendo wazoimbaimba sadafikebe
zawo zmenezo,,,,kma iyi nd nyakwawa nde yaweruza motero
SITICHEDWA KUYIWALA – By Melifa yao
Padzana Mabanja anali kutha ati chifukwa wina anachezera panzere wogula mafuta a galimoto,
Makono Mabanja akutha ati chifukwa wina akumachezera kotunga Madzi a pakhomo,
Kafufuku naululula kuti Chipala chinatulutsa Amalume ankatiyang’anira nthawi yovuta mafuta,
Mchipala chomwecho chinatulutsanso Amalume akutiyang’anira panthawi yovuta Madzi inoyi
Tilimbe Amalawi, Mabvuto akadali, ntheradi anthuwa ndamodzi, angosiyana Silang’i (Slang).
Onena nkumanena, Amalawi sachedwa kuyiwala!
Tsano yatentha nkhani ya UNGA, mosasiyana ndi kutentha kwaku Jahena,
Koma yayi, Mapulezidenti athu, ku UNGA ndiye kokaziziritsira kummero,
Enawa kuwadzudzula kuti ku UNGA mwatenga khola la Mbuzi latunthu
Iwo akubweza mokumbutsa, amvekere enanu padzana mmatengera makola a Nkhuku ku UNGA komweko,
Nkhuku zake nazonso, Misoti yokhayokha, a Tambala makamaka akuda ali phee kulera wana pa Nyasaland,
Nkumapitiriza amvekere, Amalawi sachedwa kuyiwala!
Tichilimike posunga bwino nkhani zochitika Masiku ano,
Zidzukulu zathu zisazawaphonye za a katswiri a amasiku ano,
Palitu akatswiri oyenda mmalere,
Palinsotu madolo ena akafuna kutsuka nkamwa ndiye kuti apanga kapinyolo,
Pakuti iwo wawo, ndi ukadaulo wopanga ‘Chenji Golo’ ndalama za boma nkukhala zawo
Nkhawa ili bii kuti angakhale mmodzimodzi manja awo ayamba kuvala maloko,
Akuwerengera kuti posakhalitsa sikisi julaye izawatulutsa,
Pakuti Amalawi sachedwa kuyiwala!
Wati Zii Mpira wa Ntchemberembaye, pamene wina akunyadira kuti waja ankati ndichoke aja pano andiyiwala.
Zisankho zayandikira za woyang’anira mpira wa miyendo, inde matchona akumati mpira wamapazi,
Achulukirenji wofuna kuyang’anira, a Samvamgugu nkati okakamira mopanda Manyazi
Tawafunsani za ndondomeko za makobidi mmene akhala akuyendera, amayankha thima lili zii,
Ali ngati wafunsayo ndimmalawi, osandaula, sachedwakuyawala.
Malawi 24 please learn to unite malawians
Who cares
Kkkkkk
Maskal mukumunenao zake znaela ndpo anaphula pamene a2mbi kuymba smudayambe lero koma mulibe ngakhale njinga.
sanamunyoze man,,,,amat wapanga improve hevy,,,,oz d@ kunyoza,,,?nde muli buzy kumunena mun2 ot sanalakwe nkomwe,,,,amakupusitsan awa amatembenuza nkhan nkumalemba zabodza,,,
Munthu wandakatulo akamba bwanj za oimba.nsanje c umuna
matumbi should apologize if its true……
but if it is true of what is written above,then he was wrong he need to apologize for sure
searching other peoples mistacks is atiresome job,you only waist your good time while others are developing
Hmmm!
Birds of same feathers
no comment zachamba.
Kodi2 the dude was telling the truth & apreaciating maskal kti wasintha
Ineso that wat my consious tells me….. this dude amayamikira not kumunena maskal….. i watched the show osat zimene akunena makapewa!!!!
Ndimazoba satha nkomwe utola nkhani
Ine wanga ndi Lawrence Mbenjere
atumbi kuziva sugar kodi Ku luso TV anawachosa amuvurunganya
Kuyimba kochita kulankhula, samanthanso kuyimba
mukunena zoona anyakwawa, zonena inu timadziwa kuti ndi zooona, maskal mwathana naye, tiyeni winanso anyakwawa, chitsuloooo ndi mwala mwala………
Eeeehe
Bwanji ben
24 bushhht muziyamba mwavexexa zithu b4 u put ur article here!!!
if u say bulshit ur also bastard .have u ever go for journalism professional
mmh malawi 24 ur somehow bringing confusion it was of yesterday of coz but matumbi was nt trying to bring shame kwa #maskal he was tryin to appriciate that there is a big change kwa maskal
Guys nkhani zinazi musamangotithera nazo data iyaa!
Pali nkhani yapa?
Osamalemba zokhuza ulimi wa m’thilira ndi njala yavutayi bwanji…
Moti u dont know kuti oyimba ndi pachibwanawe and amakhala akudziwana nde mpaka buzy ndi chi article ngati zenizeni??
Tilembereni zogwira mtima osati udzu mukudzula apawu…
vuto m’bale wanga anthu anzeru tilipo ocepa m’dziko koma iwe ndi m;modzi mwa ochepawo
Kkkkk thanks
Amangokuwad zopanda pake?
koma mumasowa nkhani eti??? asaaaah ndamvera sizoti ndamva kwa munthu he said poyamba maskal pa stage zimamuvuta but now anajayira amamenya bho bho amasangalasaso anthu…..muzitipasa nkhani zoti tidzitolapo kanthu osati za ziiiiii ngati iziiii asaaaah
don’t say like that dear!!! news iyi imayesetsa Ku tipanga update nkhani za booh independently that’s core of peoffesional journalism
but this news is out of truck…cnt u get it????? amapanga update nkhani za bhooo eya then why this instead of za bhoo wo zo???
kkkkkkk else Lungu choka seka pajamwapakopo
Asiyen akambilana
Kikiki
Dont Forget
2-0
Matumbi????
This article doesn’t make any sense. Try next time to learn how to balance a story,,,you are using ‘dresses down’ language and yet you fail to hear from Mascal’s reaction? Its like you are being in Mascal’s shoes..Poor reporter
Kikkkkkkkkkk Zafika Pamenepa
I understand he doesn’t perform so goon during live shows,but #Maskal is the best.. Annie Matumbi has to be taught how to respect other artists works as an artist ?.. Osati kuyakhula pa TV ? show kuti Maskal Samatha,iwe ndiye umatha????? Poti nyimbo zako timaxikonda coz we like ? you not your music… Instead of encouraging your friends ukumawanyoza….. #Zooooooooobbbbbbbbaaaa!!!!!
So why du u lyk a person nat music? Mwanama amwene mumafila zonse
Nope.. Think of it,pali anthu Ena sanamuoneko #Annie_Matumbi koma they still say akufuna nyimbo xake..
ndwe gay
Hahahahaha. .. My God..!!!!! U think you are not getting my point ?…… Mpaka #Gay……kkkkkkkk
senseless
he said maskal wachita improve oz d@ kumunyoza man,,,?mukngotha zankamwa chonsecho smunamvetsetse zomwe amanena,,,,komabe maskal nd zoba wakulila muja kmapala pastage,,
sakunama siuja anabalalika ku bba kuja ameneyi?
Sakunama bt he was jst joking
wen u got paper n u pai 4 toz xpensv studioz doznt min u gwd!………ts not anly him hu hu forcd music in hiz o he path!..includin matumbi yoxo!…. oxamangogwra mu officmo bwnj!
Ndie mwat Annie Matuviii?
Eyaa,, Anne Matuvii,,kk
Page ya anthu openga iyi!
ahem
I lyk Maskal
Thats true Maskal aint Musician I got Dissapointed when i listened to his song Called “Ndiwe Wanga” the Lyrics are wack he goes like “Chikondi Chathu akuziwa ndimboni nkona sinalakelake zopita ku Joni/chikondi changa sichapa phone mkona sinapite ku Bank kotenga Loan/” whats that?? There Is no connection Of Words there at Kaya Rymming eni akewo Mxiew it sucks
wanena #fact
you always write trash
2mbi tsopano ndi yake ija
Kachikenanso
anthu osatha kuimba ndi choncho ka amalimbana ndi anzawo..nyimbo ya kape ameneyu kuyamba mpaka kutha kumangolilamo..wat a phoney
Are you bringing unity among Malawians or divisions among people. Media is there to bring good report to the listeners and readers. Have you called Matumbi and ask him why if he real true that he commented so? The first thing before you write, you need to ask from both parties and have a concrete truth and then you write your article. Thereafter your Chief Editor if you have, must check and sign that the public should read. What you are giving to people are lies and nonsense! Stop this before you are put to the Book of Law!
thas true!thse r irresponsble mediahouse described by the presedent….giving people incoplete&uninvestgativ stories…nice co.
Yes! I dont know what Macra is doing there in Malawi. It should start looking into these Media pages!
Levelz 2 dhiss maskal
Kkkkkkkkkkkkkk
osapanga zako bwnji
kkkk Sandimina
bullets 1_0 ebola wandaZi