Bambo wanjatwa kamba kobera amayi omwe amawafunsira pa fesibuku
La fote lakwana! Bambo wina walilime lakuthwa yemwe ndi wa zaka 39 ali m'manja mwa apolisi ku Lilongwe pomuganizira kuti wakhala akufusira amayi pa tsamba la nchezo la fesibuku ndikuwalonjeza kuti awakwatira koma akakumana nawo… ...