Mlingo wa madzi mnyanja ya Malawi ukutsika
Patapita nthawi ma bizinezi ambiri atasokonekera mmbali mwa Nyanja ya Malawi kamba kakusefukila kwa madzi, a National Water Resources Authority (NWRA) ati tsopano mlingo wa madzi mu mnyanjayi ukuphwera. Malingana ndi mneneri wa bungweli, a… ...