Kafukufuku watentha ku Mzuzu University pa nkhani ya Malikisi ndi chisembwere
Itaphulika nkhani yokhudza mchitidwe wa aphunzitsi a sukulu ya ukachenjede ya Mzuzu University kugonana ndi ophunzira pofuna kusinthana ndi malikisi kuti akhonze, sukuluyi tsopano yayamba kufufuza kuti apeze yemwedi akuchiti izi. Sukuluyi yatsindika izi mu… ...