Wapha mamuna wake atamukoka maliseche
Apolisi ku Chitipi m'boma la Lilongwe amanga mayi wina wa zaka 24 kamba komuganizira kuti wapha mamuna wake a Misheck Byson powakoka maliseche. M'neneli wa apolisi m’bomali a Sub Inspector Hastings Chigalu, atsimikizira za nkhaniyi… ...