Asilikali awiri omwe anasowa dzulo apezeka
Asilikali omwe anasowa dzulo ku Mulanje pamene boti lomwe anakwera linakokoloka ndi madzi apezeka. Nduna yowona za Chitetezo a Harry Mkandawire ati awiriwa agona mu mtengo ndipo anthu omwe ali kumeneko atsimikiza kuti ayankhulana nao.… ...