Ufiti ulipo, ine ndimkulu wafiti – watelo bambo wina
Ngakhale boma limamenyetsa nkhwangwa pamwala kuti m'dziko muno mulibe ufiti, mkulu wina m'boma la Zomba wabwera poyera kutsimikiza kuti ufiti ulipo padziko lapansi pano ndipo wati iyeyo ndi wankulu wa afiti. Mkuluyu yemwe dzina lake… ...