Dzukani Kwacha! Lekani kulota tsopano chifukwa DPP ikhala m’boma kudutsa 2019.
Mlembi wa mkulu wa chipani cholamula cha DPP Mayi Greselder wa Jeffrey wanenetsa kuti mu zisankho za 2019 DPP ibubuda zipani zotsutsa.
“Zoti DPP ituluka m’boma, maloto a chumba bwanji?” anafunsa choncho Mayi wa Jeffrey.
Iwo anapitiliza ndi kuulula kuti chipani cha DPP chikumanga maziko a chitukuko tsopano ndipo pochoka 2019 iwo akhala akupitiliza kuchita chitukuko chimenecho.
Chipani cha DPP chikuyenela kusankha owatsogolela polowela ku chisankho cha 2019 ndipo a Peter Mutharika akukhala ngati adutsa opanda opikisana naye pa mpando wa utsogoleri.
Anthu musakhale ogona zitsiru zandale zisamatisokose,,, tyeni tizingojamayathu,zkakhalazaozi tiauze kt apange force aminister of labor kt aziona mmene anthu akuvutikira mma campany mesa anati aonjezere ndlama zowalipira anthu akulandilabe 750,800 zkakhala zambirit ndpin bas kma ndlama ikusikabe mphavu pano iyi 2000 amafunaso 5000 ndye mmalawi akhale bwnji, ndye mulibzy kulimbana ndzaziii zaozo ndpo tye amalawi tose tisaza vote kkkkkkk azazivotere okhaokha makape amenewa
I lost trust in DPP but it will win.
Hahahahaha you must be joking dpp inatha kalekale or wat attracts people to vote for dpp????? The answer is nothing mwagwa nayo! !!!!
Akudziwa za mawa ndi mulungu….simunthu ayi
Anthu inu chifukwa chani simuona inu muzalira ndithu ndithu paka kumakamba za MCP inu inu simuziwa bwanji chakwera sanalote chipani choti alowe simuziwa KT ndisatana anamulozere kumeneko .chifukwa chothawa baibulo
This is very true amene sakhulupilira anazolowera nyakula ndikugwililira azimai aka mbumba
Maloto salesana asiyeni adzilota
Ndindan Angafuneso D P P Ipitlile Kulamulila Boma Kapena Mwana Obadwa Lelo Amene Sadaoneko Zanyasi Zanu Zomwe Mukucita Mubomamu
This DPP is making development for their own POCKETS not for the COUNTRY!
And the plans DPP is preparing for 2019 is about finishing the Country by enriching themselves forever more!!!!
DPP ILI SHIT ADS
mmene adululila magetsimu kkkkk muzivuta ndintima
Kodi kamuzu anali wakumwela ngat……tired of recycled polititians & its e reason we r stuck…..chichichonse tikusalira,this means we need change….ts about time now
Mwavota Kale A dpp Mpaka Mwawina Kale 2019 kkkk ndiye crossing the b4 reach it osachita phuma inu a dpp shiiii!2019 akuvelani shiii!quiet mbava mbava za dpp akuti zikubaso kkkkk amalawi mulola eti ine ndi Mcp Basi Imandikwana
Mwavota Kale A dpp Mpaka Mwawina Kale 2019 kkkk ndiye crossing the b4 reach it osachita phuma inu a dpp shiiii!2019 akuvelani shiii!quiet mbava mbava za dpp akuti zikubaso kkkkk amalawi mulola eti ine ndi Mcp Basi Imandikwana
DPP ikawina ine wakujoni basi. Enough of their garbage.
Akulesa Izi Ndani? You Can Now See Many Are Flocking To Dpp Again.
Akulesa Izi Ndani? You Can Now See Many Are Flocking To Dpp Again.
DPP sikuchoka mboma musavutike inu osusa
bt according 2 reality w as pipo from southen w can’t allow any 1 from central 2b president of malawi. Whether some 1 need or nt bt president is suppose 2 b 4rm south das o. U gonna make any plan which u need 2 do bt i ansure u dat u can’t defeat us mwera’s pipo w love our side n also w love our president das o. Whether u want or nt 2019 DPP wil still going 2b a government of mw with professor peter muthalika amene zamuwawa ayanike ufa pachingwe.
what we kno about dpp is nepotism tribalism and regionalism thats all makape
w don’t care abt wht u r talking bt w r still 4llow DPP as national party n professor PETER MUTHALIKA as our president of mw in short muthalika is father malawi whether u want or nt das de truth.
Tionana konko
Ndizoona! Jeffrey Wapamkhate Sapheka.
kwa ine olo atandmanga kwa zaka 30/ ndikaseweza kupewa kuvotera chipani chaukape ngat #DPP foool ov shits
Udzabera kapena udzavota wekha
Ine nde sndizakuvotelanitu vot yanga smuzaiwona
Sizingachitike zimenezo dpp yingowinatso ulendu uwu.tizapanga za ku Zimbabwe bus.
Zoonadi zunenedwazi…..Mcp leka kulota zot utenga boma 2019
paja ndinu andale
Eya ndi kazisata nkoz
No one knows ma plan a Mulungu let’s just wait
Ntchito zamanja anu zizakuchitilani umboni koma chonde chosankoni quater system.
Achewa adati,
Ovala Sanza sadumpha moto
Ukapanda mano usamaswe mphale
Mukudzinyenga ndinu mai kuti dpp ikhalamobe m’boma awa ndi maloto a Chumba
The Story Of Pharaoh in the Bible…
ALENDO KHALAPHETIKUWUZENI.UKANAKHALA M,MALAWI SUKANANENA ZIMENEZO NDINALI KU BT MAVUTO ANTHU AKUTAYA ZAKUDZA CZ FRIGE SIKUGWILA NTCHITO BLACK OUT IS OVER MAVENDA SAKUGULIDWA ANTHU NDALAMA ALIBE ALIMI AKULILA MITENGO YAMBE VERY LOW CHIMANGA 4500/BAG MUGULISA MATUMBA ANGATI KUTI MUGULE FETELEZA 21000.00 1BAG ,NANDOLO 30.00/KG MUKANATI DPP YASISA 1 FETELEZA 2 MITENGO YAMBEWU YAKWELA, 3 BLACK OUT YATHA 4 KATANGALE WATHA 5 MITENGO YAZINTHU ZAMUSHOP ZASIKA MWINA TIKANA OPUSA ATENGEKA NDIZIMENZO KOIFE AYI
Adzavota ndiyeyo mavuto onsewa akutadzikolino ngati palibe otsogolera usatiyankhulitse pambali mkazi iwe ngat watopa ndi ……!
Even wamisala sangavotere dpp… to hell Jef
wamsala thawi zonse akavula naweso mkula nose amati ndinu wansala nonse amene mukuti dpp idzaluza kukamba mowona sindidziwa kuti kaya mumadya msima ? mwachidule dpp singaluze olo zitavuta zitani 2019 dpp mboma basi
Zipani ZANU zatha ngat makatani DPP 2019 boma ilooo
or 5-1 ija Munkati muwinatu paja
Mulungu amalawi tatopa ndi awa ife
mukati D.P.P. singawine izo zitha kukhala zoona pamaso panu.mukufuna usogoleri uti? MCP nkhanza two much ndipo inalamulira 31 years. kwake kunatha komatso kulibe Munthu yemwe ndikumuona kuti angaime pa u PRESIDENT. chifukwa ndale ndi za church ndizosiyana. U.D.F. nokha mukuziwa kale anatilondolera ndi ku D.P.P. ndi Bakili muluzi, ikakhala P.P. ndie ndi Big mistek ndalama zoika ma mini bus.komatso PRESIDENT oyamba kugwa kwambiri ma voti ngati Amene aja. ndie agulukunyindu inu chomwe ndingakuuzeni zidalireni panokha.osati ife pano tilibe ndalama .chikhalirenicho manja alilendee.
that. was old MCP baba dzukani mudakali mtulo! wake up! Dpp and its thugs will neva win! 2019 MCP ndi Boma
anayambira 1994 zimezo mpaka pano samatenga boma.ndiye iwe ukuti chani apa.ndiwe wa kumalingunde? kapena kwasathe?
kkkkkkkk , mtumbuka sazatheka guyz mutsiyeni , koma zot president azachokela ku mpoto iwalani , inu zaka 30 chitukuko chomwe chimaoneka ku gulu nd kuvina nyau basi kkkkkkkk shame SIBWENI
kkkkkkkkk asatikwane ndi gulewamkulu wawoyu. tikakhala chete mukamabwebweta za M.C.P zanuzo mumaona ngati Ife osizina? zambiri akafutse agogo awo Che Tembo.
Abwera mmalo mwa kaliati ameneyu
Pokhapokha tonse titakhala ana a Jeffrey mwina zikhanza kutheka poopa kugona ndi njala monga ana ake chosangalasa mtundu wa amalawi sunabadwe kwa munthu obwetukayu.
Ife ndiye sitikudabwa oil wachepamo mmutumo mmatitenga ngati ana anu woti mukawuza zinthu mkumakumverani shame mwatikwana nazo zanuzo tiye uko
ukamuziwa Yesu uzasiya kusapota ndale,panga zasogololako
Moto kuti buuuuu DPPP Woyeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee
An empty buckle makes the loudest noise,only the clock knows the answer,you cheated us about generators, frequent blackouts,what next…..!! 2019 is around the corner.
Dpp ndi boma
zitokotani,, m’Malawi paja ndi tsiku lovotatu musaiwale..unuyo a DPP khalani choncho mubazinyenga nokha…tidzawona nthawi yovota
Mukunena zoona mama,amene akudziwa Mulhako sangakusutseni
Ovota ndiife mutulukabe basi come rain or sunshine
But how can one be so sure yet akudziwa kuti iwowo chitengereni boma there’s been nothing but chaos in this country. Makes no sense . We can’t let this country go down.. it will be an insult to those fore fathers who fought hard for our freedom and betterment of all.
Amai awa during mza by-elections aja amalankhulanso choncho and what was the verdict! Kufuna kusunga mpando wawo popusitsa abwana ake that’s all!
Ukavota Ndiweyo Geofrey…? Sukudziwa Amalawi Ndiokwiya Ndi Chipani Chakocho…Tikumana 2019 Ndikuyankhula Kwakoko Zobela Uyiwale Amalawi Sakufuna Dpp Yakoyo Usatikwiyitse Wamva!!
Ukavota Ndiweyo Geofrey…? Sukudziwa Amalawi Ndiokwiya Ndi Chipani Chakocho…Tikumana 2019 Ndikuyankhula Kwakoko Zobela Uyiwale Amalawi Sakufuna Dpp Yakoyo Usatikwiyitse Wamva!!
Ngakhale chakwera nd mboni ya zimenezi,
Ndamva mmene wayakhulira pa zbs.. Zaonetseratu kut anthu awa zizikuwakhuza mmene amalawi akuvutikira pakhani zina monga kuzima zima kwama getsi
poti mumaziwa kuba thus why mukukamba zimenezo koma ndinu mbuli za athu yaaah
ndye ovota ndi iyeyo2 ….
kkkkkk only God knows
sikudzakhala kufuna kwanu.. so don’t bother yourself
Atikwanaso awa tione zina apa chaka n chaka DPP ayi tionana bolani time ikwane
Ifetilinganga ndi DPP
saying so means u dont love malawians give chance to others to try real development sikuti awa nde anzelu taziona kale TIME UP
Adawinapo akuganiza amalawi ndi opusa avomeranso zomaberedwa ma voti aziona
Amaika chipani mboma Ndili uyp akuyankhula kapena kumvetsela?
sakunama dpp have 100% chance to win 2019 polls.inatenga boma 2014 from pp ndiye panopa ili kale m’boma momwemo ndiye mukuona ngati chani.
Muzabelatu ?
Truth
amenewo ndi maloto achumba..
Ngati angaza vote. Yekha ndi ana ake
MCP yawina Komano pa fb kkkkkkk
Adza voter okha
Is she married? Tell her to go to bed and dream more and fall pregnant… by may next year a baby boy will born into her and she shall name the boy mcp
Dpp imaba kwambiri a Malawi chenjerani dziko likuwonongeka
Kodi simumkanena zomwezomwezo pa by elections aja
Ndakulapa nkulinga utayenda naye,takhala nanu kwa dzaka ndipo takuonani ndipo mmm ai mwina tiyese ena koma,tikudziwa kuti mukudziwa kuti chisamkho chayandikira ndipo muyesetsa kuti mwina mukhale abwino komabe eeee tamva nanu kuwawa
Muzabere muzanya muzawona
Kumakhala ntima voice capture kumbaliku pano bdikuphunzila zachilima yemweyo name
Simuzaberaxo agalu kma musaiwale kunja kuno kuli mulungu akuona zonse
Musazabere ndi ma network anuwo
Zoona izi .sindingavotere Lilongwe congress patry
patry….kkkkk…ndiye kuti chiyani? zoonadi inu ofunikadi kuvotera Thieves party…nanga kulephela simple spelling…
Patry? Sindinamveko Mr bombastic kkkkkk
awo anali a sakamula.. kuyakhula mopusa haha
Xul siinakupindulire ndithu, wake up Mr… Lilongwe mwati?
Am happy kut I have communicated to you.
Amene Mwanena Kuti Dpp Idzapambana Ndi Bodza Imeneyo Mungowona Nokha Momwe Zinthu Zavutira Dziko Lino. Magetsi Akuvuta,chuma Sichili bwino Kuphatikiza Apo Chaponda Adaba Ndalama Zambirimbiri Sakumangidwa Mpaka Pano
Davis Zimba za ziii ukudandaulazo chuma chavuta kuti
2014 anthu ankafuna kut amayi achoke ndipo mwamuna alamulile koma 2019 ndi nkhan zina dpp pakilan amenewo ndi maganizo anu odzavota ndife koma ngat mwavota kale ai mwina zikuendelan koma ngat mukudalila kut tivote ndife mwalemba mmadz
Izi ndiye zoona izi
Same to you madam musazinyenge come 2019 you are out
iyi ndi ng’oma yolilitasa……. and empty bucket……!!
Pakuti woponya vote ndi amene akunena zimenezi
Kulibe kubera this time… Mukhaula…
kkkkkkkkkkkk atikwana
please you stupid woman think before you speak why to compare barren women to your politics kodi anafuna kuti akhale osabereka
KKKKKKKK Nafwa kuwinanso kkkkkkkkk
dpp imanena zoti cholinga cha chipani chawo ndi kuwonetsetsa kuti anthu ali ndi chakudya.chitetezo .chitukuko.pophatikiza apo kulumikiza a Malawi posankha atsogoleri mbali zonse za muno mu dziko ochokera kumpoto pakati ndi kumwera.the president is from thyolo.the vice is from ntcheu.minister of finance from mzimba.the secretary general is from nkhotakota.Can somebody tell me here zolinga zomwe amafuna a mcp atapanga akawina chisankho.mcp has only one tribe in its politbro.who is a senior tumbuka in its executive in mcp? who is a senior mlomwe in mcp executive? who is a yao in mcp executive? kulibe and you expect to win.Dr chakwera make mcp a national party not Lilongwe congress party
Zose mwalembazi zilibe ntchito, ife tikufuna prezdnt who can develop MW and not just who can know how 2 mix tribes but then embezu public funds and ruine the country instead.
Banda …chilungamo chokhachoka wanenecho. Uyo ndumudziwa ndi cadet
@innocy. iwe uli ku south Africa dzithawa a home affairs.leave us who knows whats happening in our country to comment. keep the hate which you kept on parties. .
a phozongo chiwadziwiren sanayakhulepo za zenru.. looks like ndi cadet
Proud to be one from Central Region… only party that can save the Malawians from the Villians is MCP … if you fear God you know how nepotic is DPP …
@ phozongo, am a Malawian regardless of my whereabout,. DPP has failed and has nothing 2 offer Malawians. They are thea to take little funds Malawians have,. If the worst has already happened in the first term what wld happen in the second? U r here talking about inflation rate yet the cost of living is higher than expected,.
kodi abale kukhala cadet wa dpp ndi tchimo? that a question to you mcp lovers. its only in your party forum where you will agree on one thing but here there are some of us in dpp.others in aford and I wonder with you mcp people. kunyoza kutukwana.thats why ndimayankha mwano sometimes.mudzasinda liti kodi inu a crocodile party. start rebranding mwina anthu akulondolenu.
@innocy. a question for you.what did you expect dpp government to do in three years? you expected Malawi to be like cape town in three years? dpp has done alot both long term and short term.do you think winning donor confidence is a joke? simasewera achimwene.kukhala ndi chimanga ndi chakudya si nthano.international maize vendors were on our boarders to mop our maize but the president tried even though chakwera was against that idea of keeping maize in this country. inflation goes with cost of living.pamenepo pitani ku school kawiri mukavetsetse .infrastructure development ili paliponse.ma district stadiums.community colleges. do you think chakwera wanuyo bwezi atagwetsa manna wachitukuko zaka zitatu.impossible. again dpp is a team full of international connected people.mukuphweketsa aphwanga.anthu ambiri amakinda dpp if you dont know and thats why it won from opposition benches.
inu M.C.P. ndiyopoira anthu osatira aketso ndiopoira.chipani cha mtundu wanji chongokhala chigawo cha pakati? kulemera ndi kudya. D.P.P.siigonetsa anthu ndinjala.komatso siifuna mbuli za anthu.alesi ozolowera kupasidwa ndalama.amanja lende .Chakwera wanuyo akagwere uko.ndipo mukamabwera mawa mubwere ndi background yake ya sukulu.osati ndimuve wina akundibweretsera back ground ya u busa.
VIVI OKONDA KUDYA AKUMANA MAPIKO
chipani cha mcp nd chipani cha dziko laku mpoto osati la Malawi kkkkkkkk
kkkkkkkkk auzeni ndithu avetsetse.
Good Analysis.
Kundendeso ndi m’bomatu !
Ee kma DPP gys nd 1, ndmkafna ndzavote UDF kma ndizomwe apanga zofna kupanga kasakanizazo nd zomwe zandpangtsa kut ndtembenuke bas, nde apa nd DPP basit ndiyomwe ili 1
Those are like kicks of a dying horse
Kulira kwa anamfedwa 5 – 1 in my mind
2019 GET OUT! Tione zina.
DPP ukayivotera wekha, sitikuonako mtsogilri ku dpp
anthu akwera lekani ku mfera fungo povota, onani momwe mwavutikira.
inuso nde kayatu,,dpp ife tinaiponya mchimbuzi,,akakuvotereni ndiokhao amene sanatsuke maso,,stupid dpp
zmai uyu amayakhul mwausilu ngat kt akavota yekha
Iyeyu ndi amene akudzinyenga ndi chala chake
Kkkkkkkkkkkk akulota ameneyo ndithu or wamisala sangavotere dpp taluza hope
kkkkkkkkkkkkk vote yigwire ntchito amalawi tatopa nawo ufumu umenewwo
Watopa nawo osati tatopa nawo ine ayi my vote Dpp
DPP isayembekezele mavoti ambili kuchokela kwa amalawi come 2019
Amene Angavotere Dpp Ndi Wamisala…
Am not a fool that mch to vote for dpp enough z enough
ife tinapita kusukulu tili pambuyo ndi D.P.P. agule wamkulu inu kagwereni ukooooooo! shupid!
Ine ndlibe chipani but i vote nde vote yaine dpp siyiona kkkkkkkkk chisankho changa
Hastings…kulipotu kupita ku sukulu ko koma mmutu muli mamina okha okha nde ndizomwe mupanga inuzi apa
Tichita mokukakamizani by vote
kkkkkkkkkkkkkkkkk by vot i agree with u bro kkkkk
Its Not You Who Are Going To Vote Bt Is People So Dont Trouble With Your News To Support Dpp
Dpp ikhala m’boma chifukwa anthu akumwela sakufuna kupeleka ulamulilo kwa anthu amzigawo zina,koma utsogoleri wabwino kulibe ndipo pachifukwa chimenechi dziko la Malawi lipitilira kuvutika kamba ka utsigoleri oyipa WA Dpp.
Nanu, kunja kuno kuli Mulungu. Ndipo Mulungu salola zoputsazo. DPP ikuturuka basi.
kkkkkkkkkm, iwalani guyz , Lilongwe congress yadzuza anthu osalakwa ndipo anthu sakuiwala nkhaza zimenezo mpaka lelo , ife aku mmwela tilibe problem
Usadande kumwela mia wagwedeza kale MCP moto kut buuu
Kkkkkkk okay ayi pakamwa Ali napo sangalesedwe kulankhula. Ndipo zainu zokuti mumatha kutokota palibe amene sakudziwa kuti mumalankhula zopanda pake, ndikukumbukila kuti ndinu nomwe mudanena kuti anthu akumpoto aiwale za utsogoleli ndiye apapa palibe Amene angatsutse zomwe mukunenazo, kuba mumatha ziphuphu mumatha kunyoza mumatha, Koma kuwina pachilungamo ndi zomwe simukutha, ndiye dziganizileni Kaye.
Likadakhala Pemphelo Ndikadangot
Amen!!!! Awa Ndie Mau Congrats Mr
hahahaha
KKKKKK ndukuuzani Abroz & zina zimakhala zodabwitsa kuti amenewa kulankhula kumeneko mmutumo zimaenda ndithu kapena Pena pake padavuta. Ngati Ali madolo azasiye zobelaxo azaone bland slide yomwe azakumane nayo.
Kkkk man mwandimaliza
Otsusa nawoso apeze njira zot azabere kod akaswir obera amapezeka Ku DPP kokha
KHOKHOKHO
yea true
This woman’s speeches are always irritating. There was madam Patricia Kaliati……. One day you will be silent madam.
Tizaona yemwe azakuvoteleniyo
DPP can stay in 2019 only if they hv plan be to use not from vote from people