Musazinyenge, DPP sikutuluka m’boma mu 2019 – wa Jeffrey

Advertisement

Dzukani Kwacha! Lekani kulota tsopano chifukwa DPP ikhala m’boma kudutsa 2019.

Wa Jeffrey: Zoti DPP ituluka m’boma, maloto a chumba bwanji?

Mlembi wa mkulu wa chipani cholamula cha DPP Mayi Greselder wa Jeffrey wanenetsa kuti mu zisankho za 2019 DPP ibubuda zipani zotsutsa.

“Zoti DPP ituluka m’boma, maloto a chumba bwanji?” anafunsa choncho Mayi wa Jeffrey.

Iwo anapitiliza ndi kuulula kuti chipani cha DPP chikumanga maziko a chitukuko tsopano ndipo pochoka 2019 iwo akhala akupitiliza kuchita chitukuko chimenecho.

Chipani cha DPP chikuyenela kusankha owatsogolela polowela ku chisankho cha 2019 ndipo a Peter Mutharika akukhala ngati adutsa opanda opikisana naye pa mpando wa utsogoleri.

 

Advertisement

153 Comments

 1. Anthu musakhale ogona zitsiru zandale zisamatisokose,,, tyeni tizingojamayathu,zkakhalazaozi tiauze kt apange force aminister of labor kt aziona mmene anthu akuvutikira mma campany mesa anati aonjezere ndlama zowalipira anthu akulandilabe 750,800 zkakhala zambirit ndpin bas kma ndlama ikusikabe mphavu pano iyi 2000 amafunaso 5000 ndye mmalawi akhale bwnji, ndye mulibzy kulimbana ndzaziii zaozo ndpo tye amalawi tose tisaza vote kkkkkkk azazivotere okhaokha makape amenewa

 2. Anthu inu chifukwa chani simuona inu muzalira ndithu ndithu paka kumakamba za MCP inu inu simuziwa bwanji chakwera sanalote chipani choti alowe simuziwa KT ndisatana anamulozere kumeneko .chifukwa chothawa baibulo

 3. Ndindan Angafuneso D P P Ipitlile Kulamulila Boma Kapena Mwana Obadwa Lelo Amene Sadaoneko Zanyasi Zanu Zomwe Mukucita Mubomamu

 4. This DPP is making development for their own POCKETS not for the COUNTRY!
  And the plans DPP is preparing for 2019 is about finishing the Country by enriching themselves forever more!!!!

 5. Kodi kamuzu anali wakumwela ngat……tired of recycled polititians & its e reason we r stuck…..chichichonse tikusalira,this means we need change….ts about time now

 6. Mwavota Kale A dpp Mpaka Mwawina Kale 2019 kkkk ndiye crossing the b4 reach it osachita phuma inu a dpp shiiii!2019 akuvelani shiii!quiet mbava mbava za dpp akuti zikubaso kkkkk amalawi mulola eti ine ndi Mcp Basi Imandikwana

 7. Mwavota Kale A dpp Mpaka Mwawina Kale 2019 kkkk ndiye crossing the b4 reach it osachita phuma inu a dpp shiiii!2019 akuvelani shiii!quiet mbava mbava za dpp akuti zikubaso kkkkk amalawi mulola eti ine ndi Mcp Basi Imandikwana

 8. bt according 2 reality w as pipo from southen w can’t allow any 1 from central 2b president of malawi. Whether some 1 need or nt bt president is suppose 2 b 4rm south das o. U gonna make any plan which u need 2 do bt i ansure u dat u can’t defeat us mwera’s pipo w love our side n also w love our president das o. Whether u want or nt 2019 DPP wil still going 2b a government of mw with professor peter muthalika amene zamuwawa ayanike ufa pachingwe.

  1. w don’t care abt wht u r talking bt w r still 4llow DPP as national party n professor PETER MUTHALIKA as our president of mw in short muthalika is father malawi whether u want or nt das de truth.

 9. ALENDO KHALAPHETIKUWUZENI.UKANAKHALA M,MALAWI SUKANANENA ZIMENEZO NDINALI KU BT MAVUTO ANTHU AKUTAYA ZAKUDZA CZ FRIGE SIKUGWILA NTCHITO BLACK OUT IS OVER MAVENDA SAKUGULIDWA ANTHU NDALAMA ALIBE ALIMI AKULILA MITENGO YAMBE VERY LOW CHIMANGA 4500/BAG MUGULISA MATUMBA ANGATI KUTI MUGULE FETELEZA 21000.00 1BAG ,NANDOLO 30.00/KG MUKANATI DPP YASISA 1 FETELEZA 2 MITENGO YAMBEWU YAKWELA, 3 BLACK OUT YATHA 4 KATANGALE WATHA 5 MITENGO YAZINTHU ZAMUSHOP ZASIKA MWINA TIKANA OPUSA ATENGEKA NDIZIMENZO KOIFE AYI

 10. wamsala thawi zonse akavula naweso mkula nose amati ndinu wansala nonse amene mukuti dpp idzaluza kukamba mowona sindidziwa kuti kaya mumadya msima ? mwachidule dpp singaluze olo zitavuta zitani 2019 dpp mboma basi

 11. mukati D.P.P. singawine izo zitha kukhala zoona pamaso panu.mukufuna usogoleri uti? MCP nkhanza two much ndipo inalamulira 31 years. kwake kunatha komatso kulibe Munthu yemwe ndikumuona kuti angaime pa u PRESIDENT. chifukwa ndale ndi za church ndizosiyana. U.D.F. nokha mukuziwa kale anatilondolera ndi ku D.P.P. ndi Bakili muluzi, ikakhala P.P. ndie ndi Big mistek ndalama zoika ma mini bus.komatso PRESIDENT oyamba kugwa kwambiri ma voti ngati Amene aja. ndie agulukunyindu inu chomwe ndingakuuzeni zidalireni panokha.osati ife pano tilibe ndalama .chikhalirenicho manja alilendee.

  1. kkkkkkkk , mtumbuka sazatheka guyz mutsiyeni , koma zot president azachokela ku mpoto iwalani , inu zaka 30 chitukuko chomwe chimaoneka ku gulu nd kuvina nyau basi kkkkkkkk shame SIBWENI

  2. kkkkkkkkk asatikwane ndi gulewamkulu wawoyu. tikakhala chete mukamabwebweta za M.C.P zanuzo mumaona ngati Ife osizina? zambiri akafutse agogo awo Che Tembo.

 12. Pokhapokha tonse titakhala ana a Jeffrey mwina zikhanza kutheka poopa kugona ndi njala monga ana ake chosangalasa mtundu wa amalawi sunabadwe kwa munthu obwetukayu.

 13. Ife ndiye sitikudabwa oil wachepamo mmutumo mmatitenga ngati ana anu woti mukawuza zinthu mkumakumverani shame mwatikwana nazo zanuzo tiye uko

 14. An empty buckle makes the loudest noise,only the clock knows the answer,you cheated us about generators, frequent blackouts,what next…..!! 2019 is around the corner.

 15. But how can one be so sure yet akudziwa kuti iwowo chitengereni boma there’s been nothing but chaos in this country. Makes no sense . We can’t let this country go down.. it will be an insult to those fore fathers who fought hard for our freedom and betterment of all.

 16. Amai awa during mza by-elections aja amalankhulanso choncho and what was the verdict! Kufuna kusunga mpando wawo popusitsa abwana ake that’s all!

 17. Ukavota Ndiweyo Geofrey…? Sukudziwa Amalawi Ndiokwiya Ndi Chipani Chakocho…Tikumana 2019 Ndikuyankhula Kwakoko Zobela Uyiwale Amalawi Sakufuna Dpp Yakoyo Usatikwiyitse Wamva!!

 18. Ukavota Ndiweyo Geofrey…? Sukudziwa Amalawi Ndiokwiya Ndi Chipani Chakocho…Tikumana 2019 Ndikuyankhula Kwakoko Zobela Uyiwale Amalawi Sakufuna Dpp Yakoyo Usatikwiyitse Wamva!!

 19. Ndamva mmene wayakhulira pa zbs.. Zaonetseratu kut anthu awa zizikuwakhuza mmene amalawi akuvutikira pakhani zina monga kuzima zima kwama getsi

 20. saying so means u dont love malawians give chance to others to try real development sikuti awa nde anzelu taziona kale TIME UP

 21. sakunama dpp have 100% chance to win 2019 polls.inatenga boma 2014 from pp ndiye panopa ili kale m’boma momwemo ndiye mukuona ngati chani.

 22. Is she married? Tell her to go to bed and dream more and fall pregnant… by may next year a baby boy will born into her and she shall name the boy mcp

 23. Ndakulapa nkulinga utayenda naye,takhala nanu kwa dzaka ndipo takuonani ndipo mmm ai mwina tiyese ena koma,tikudziwa kuti mukudziwa kuti chisamkho chayandikira ndipo muyesetsa kuti mwina mukhale abwino komabe eeee tamva nanu kuwawa

  1. patry….kkkkk…ndiye kuti chiyani? zoonadi inu ofunikadi kuvotera Thieves party…nanga kulephela simple spelling…

  2. Amene Mwanena Kuti Dpp Idzapambana Ndi Bodza Imeneyo Mungowona Nokha Momwe Zinthu Zavutira Dziko Lino. Magetsi Akuvuta,chuma Sichili bwino Kuphatikiza Apo Chaponda Adaba Ndalama Zambirimbiri Sakumangidwa Mpaka Pano

 24. 2014 anthu ankafuna kut amayi achoke ndipo mwamuna alamulile koma 2019 ndi nkhan zina dpp pakilan amenewo ndi maganizo anu odzavota ndife koma ngat mwavota kale ai mwina zikuendelan koma ngat mukudalila kut tivote ndife mwalemba mmadz

 25. please you stupid woman think before you speak why to compare barren women to your politics kodi anafuna kuti akhale osabereka

 26. dpp imanena zoti cholinga cha chipani chawo ndi kuwonetsetsa kuti anthu ali ndi chakudya.chitetezo .chitukuko.pophatikiza apo kulumikiza a Malawi posankha atsogoleri mbali zonse za muno mu dziko ochokera kumpoto pakati ndi kumwera.the president is from thyolo.the vice is from ntcheu.minister of finance from mzimba.the secretary general is from nkhotakota.Can somebody tell me here zolinga zomwe amafuna a mcp atapanga akawina chisankho.mcp has only one tribe in its politbro.who is a senior tumbuka in its executive in mcp? who is a senior mlomwe in mcp executive? who is a yao in mcp executive? kulibe and you expect to win.Dr chakwera make mcp a national party not Lilongwe congress party

  1. Zose mwalembazi zilibe ntchito, ife tikufuna prezdnt who can develop MW and not just who can know how 2 mix tribes but then embezu public funds and ruine the country instead.

  2. @innocy. iwe uli ku south Africa dzithawa a home affairs.leave us who knows whats happening in our country to comment. keep the hate which you kept on parties. .

  3. Proud to be one from Central Region… only party that can save the Malawians from the Villians is MCP … if you fear God you know how nepotic is DPP …

  4. @ phozongo, am a Malawian regardless of my whereabout,. DPP has failed and has nothing 2 offer Malawians. They are thea to take little funds Malawians have,. If the worst has already happened in the first term what wld happen in the second? U r here talking about inflation rate yet the cost of living is higher than expected,.

  5. kodi abale kukhala cadet wa dpp ndi tchimo? that a question to you mcp lovers. its only in your party forum where you will agree on one thing but here there are some of us in dpp.others in aford and I wonder with you mcp people. kunyoza kutukwana.thats why ndimayankha mwano sometimes.mudzasinda liti kodi inu a crocodile party. start rebranding mwina anthu akulondolenu.

  6. @innocy. a question for you.what did you expect dpp government to do in three years? you expected Malawi to be like cape town in three years? dpp has done alot both long term and short term.do you think winning donor confidence is a joke? simasewera achimwene.kukhala ndi chimanga ndi chakudya si nthano.international maize vendors were on our boarders to mop our maize but the president tried even though chakwera was against that idea of keeping maize in this country. inflation goes with cost of living.pamenepo pitani ku school kawiri mukavetsetse .infrastructure development ili paliponse.ma district stadiums.community colleges. do you think chakwera wanuyo bwezi atagwetsa manna wachitukuko zaka zitatu.impossible. again dpp is a team full of international connected people.mukuphweketsa aphwanga.anthu ambiri amakinda dpp if you dont know and thats why it won from opposition benches.

  7. inu M.C.P. ndiyopoira anthu osatira aketso ndiopoira.chipani cha mtundu wanji chongokhala chigawo cha pakati? kulemera ndi kudya. D.P.P.siigonetsa anthu ndinjala.komatso siifuna mbuli za anthu.alesi ozolowera kupasidwa ndalama.amanja lende .Chakwera wanuyo akagwere uko.ndipo mukamabwera mawa mubwere ndi background yake ya sukulu.osati ndimuve wina akundibweretsera back ground ya u busa.

 27. Dpp ikhala m’boma chifukwa anthu akumwela sakufuna kupeleka ulamulilo kwa anthu amzigawo zina,koma utsogoleri wabwino kulibe ndipo pachifukwa chimenechi dziko la Malawi lipitilira kuvutika kamba ka utsigoleri oyipa WA Dpp.

  1. kkkkkkkkkm, iwalani guyz , Lilongwe congress yadzuza anthu osalakwa ndipo anthu sakuiwala nkhaza zimenezo mpaka lelo , ife aku mmwela tilibe problem

 28. Kkkkkkk okay ayi pakamwa Ali napo sangalesedwe kulankhula. Ndipo zainu zokuti mumatha kutokota palibe amene sakudziwa kuti mumalankhula zopanda pake, ndikukumbukila kuti ndinu nomwe mudanena kuti anthu akumpoto aiwale za utsogoleli ndiye apapa palibe Amene angatsutse zomwe mukunenazo, kuba mumatha ziphuphu mumatha kunyoza mumatha, Koma kuwina pachilungamo ndi zomwe simukutha, ndiye dziganizileni Kaye.

  1. KKKKKK ndukuuzani Abroz & zina zimakhala zodabwitsa kuti amenewa kulankhula kumeneko mmutumo zimaenda ndithu kapena Pena pake padavuta. Ngati Ali madolo azasiye zobelaxo azaone bland slide yomwe azakumane nayo.

 29. This woman’s speeches are always irritating. There was madam Patricia Kaliati……. One day you will be silent madam.

Comments are closed.