The UK Aid and Irish Aid have donated £6.8m (K6.6 Billion) to the Malawi government– funds meant to meet the food needs of over 500,000 vulnerable locals.
Malawi Vice President, Saulos Chilima together with UN and NGO implementing partners, will launch this support in Nsanje today, Wednesday 20th December.
This new package of development assistance from the UK and Ireland will help hundreds of thousands of Malawians with cash transfers to buy food and other essentials during the difficult pre-harvest lean season, and is in support of the Government of Malawi’s forthcoming National Resilience Strategy.
In line with Government data and plans, DFID and Irish Aid are targeting the most vulnerable districts: Nsanje, Balaka, Chikwawa and Mwanza (the worst affected four Districts) plus Machinga, Blantyre, Mulanje, Phalombe and Neno. This
According to Jen Marshall, Head of the UK’s Department for International Development (DFID) in Malawi, this year is a better year for food availability in Malawi, providing the chance for Government and Development Partners to do things differently.
Marshall said this cash-only safety net programme provides cost efficient, flexible, immediate assistance and says now is the time to plan how Malawi’s long term social protection programmes can better respond to high levels of vulnerability.
“Importantly, these cash transfers are being provided alongside a further scale up of UK Aid funded resilience-building interventions that aim to reduce communities’ and the country’s dependence on short-term responses.
We all agree that Malawi urgently needs to break the cycle of annual emergency response and find long term solutions, including expanded long term safety nets, more resilient livelihoods, and more predictable markets for maize and other crops.” said Marshall.
Ah apangira ka Compghain a DPP zina banso Chaponda bola tonse titsegulitse ma account ma Donor aliense adzimupatsa ekha! cox Mbuzi izi za DPP they are doing nothing kaya 2019 ifika liti tilowetse MCP?
But we don’t see any improvement
Izi nde zisalowe Cash gate
hehehedeeee ndi Andale ake awa kkkkk kaya
nthawi zina ndalama muzizigwilitsa ntchito yake osamangoba a very times
Only 1 billion wil go to the beneficiaries … the 5.6 billion its for allowances and benefits for top officials… ma meeting/ ma training osatha ku sun n sand, nkopola every week…thats an african way of helping the poor…
that’s great kma muwona ndalama zimenezo apingira kampeni yowagulira anthu mafoni mafoni ngat adya mafoniwo
Wasting of money it has been already shared among dpp officials anthu atikwana awa
Di system na full of liars
Sizioneka ndalama zimenezo
Donors please just start bringing food stuffs rather than money because you can not trust malawi government with money….they fail to control 2 billion so what about 6
Osauka saonapo kanthu zalowakale muthumba lamunthu wankulu ,mmalawi mwini kumavutika kumangomva kuti mulandi thandizo mpakana mawa wina athawanazo ngati chaponda.
Achaponda Akudziwa kma kuti ndalama zafika?
yayaya
Kukongola ndalama kumaiko akunja , zikuthela mmatumba, ana ndi zidzukulu ifeyo titapita , iwokumadzabweza kkkkkk what about free donated money ?
The amount of money donated is no longer the same since agawana kale ma share while eniake ofunika thandizolo ukungotuwa uko! demet!!!!!!!
The money donated is no longer the same since agawana kale ma share while eniake ofunika thandizolo ukungotuwa uko! demet!!!!!!!
Only MK0.6billion Will Reach The Locals While MK6billion Will Be In Pockets Of The Big 6 In Cabinet.
Azidyeso anthu opanda chisoniwa
Kunoko kumafunika kumatipasa cooked beans,and cooked poridge otherwise cash imapindulira anthu 10 dziko lonseli……
Pk !
Ndalamazo siziwoneka komwe zapita mumangoponya mmatumba mwanu agalu inu mxiiii!!!!
But i thought kut abwana ananena kut palibe munthu olo m’modzi yemwe alibe chakudya, nde chakudya chinenedwa apa nde chitchit? K
6 million kwathu 6 billion iiiii sheme
y nt to donate for this blackouts,stupid
Wina pamenepo dovu likungochucha wasala pang’ono kuzibwira
Better just buy the food & give it where its needed otherwise Malawians cant be trusted with cash nomore…akaba kusungira campaign zimenezo
Kkkkkkkkk pisher wasowa ndufuna nyimbo
Take a careful look at the so called vulnerable districts.?????????
This money will be eaten by Peter and his friend while poor are dying in rural areas. God will act one day
This money will be eaten by Peter and his friend while poor str
This money will be eaten by Peter and his friend while poor str
In dollars is how much the kwacha is like the zim dollar
Mwachitola madala
Kulibe njala kuno..
Aaaaa sizioneka zimenezo..government will only buy 50 bags of maize at K40/kg.i am a pure Malawian, i kno Malawi better
Ok
The donors have always been here…what they stopped is giving funds direct to acc # 1.. musachitepo matukutuku apa…
The donors have always been here…what they stopped is giving funds direct to acc # 1.. musachitepo matukutuku apa…
Injecting money into Mw…..are satisfied with good governance.
Good governance from which people ?
TIKHALE NDIMALOTO AKUTI NTHAWI ZINA TIDZAKHALE IFE AMALAWI TIKUTHANDIZA ENA
Tizawawunikira ma donors mbali zoyonera chithandizo, lero ndinthaw yomathandizana chakudya mmalawi muno? 5000 people from where ? Plenty of maize even Government can assist on that,
Akatere pitala ndi agalu ake agawane chithandizo cha anthu obvutikacho eeish God ingophani anthuwa once
Imeneyo moti muthandizire magetsi akuvutawa. Paja mukuti chakudya chilipo chokwaniratu mpaka zaka zitatu.
Dolla yake sioneka bhobo, ena ayamba kuipangila kale ma plan… Mxieeeew. Ku malawi nkwausilu, my foot.
yah, apa magamoto adula aja agulidweno, ndalama za manner si zabwera zokha
Thats a x-mas package for those in govt seats.
Muzavutike ndikulemba izi ndalama tadya kale!!!!
Donor aid is back again….a opposition mukutipo bwanj kkkkk muphulikatu
Vuto Ndikusolora I Think These Donors Should Come And Do The Development Themselves Not Giving Us Cash, We Are Good At Misusing Cash!
Eeeeeee basi kulemela anthu amenya kale masamu
im happy to because god bless rain contauly of malawi ndi 34% seachs
Mukutichani????
lol! Kkk
za enidi izi???
Kkkkkkkkkkiest
vout mzafune at kmze tkygern aaaa
izi nde zoononga boma izi!!!!! kodi simukuwauza anthuwo kut ndalama amapanga donate mumabaso inunomwe??? we dont want donations, we r grown ups
Jst knw we r in xmas n newyear celebration vis donations will be used for the palace parties ie blue night and mulhako wa alhomwe via ndata..shame on
Wapatsa mbava zilemere tsopano
Bava Ndizolemela Kale Kma Zanu Munakwatla Paka Mamitala Zanu Izo
aufiletso aphawi akatsangalala ku mwamba akadya nyama zabwela zokha
We are running without donor support.
Why don’t u say ‘UK donates K6.bIllion to Dpp’?
Not to DPP, koma kwa pitala coz ineso ndi DPP yomweyo koma sandigayilako akanganya amenewa nzonse kundata kwakeko kusakuthatako mmmh God bless Malawi
Ziko u r right kkk
Some government officials shall soon become fats
Zindalama phwiiii koma vuto la magetsi osatha eish!!!
But they said is for Agriculture….muzitenge bwinotu man
All these billions for Agriculture? Ulimi Wake utiwo apa taulozeni akulu inu? Kuzitenga bwino? What do you mean by that? Do you think i give shit with your government?
mudyeso zimenezo osaukawo azisauka azigona ndi njala othandandiza ndiye akuyesesa koma A Tsogoleri A Malawi dyera 4 much not 2 much.
mukatelo muthyolele mmatumba mwanu… chikwapu chamulungu chikujimula… muzanya muzawona
For free or with some profite?
Malawi anali kale timati tikagona osadya afiti amatidyetsa usiku pozuka tili ndi power koma pano afitinso adaimika manja sungalote ukudya nsima uphawi wafikapo hvy.
kkkkkkk
hahaha ndithileni juwis ndakomoka
Hahahahaja
KKKKKKK koma
Pajatu Chimanga Tilinacho Chokwanira Sinanga Sitinagulitse Potengera Mitengo Yake,mapeto Ake Ndalamazo Zithera M’matumba Akuluakuluwa.
Guys Ku Bomako Chitani Party Aid Ndimeneyo,,, Awa Amaba Mwanzeru.
mukulemba pa internet waperekeredwa ndalamayo sakuziwa
anyapapi azithyolela mthumba zimenezp
gawanani
Tigawana Kumene
Tigawana Kumene
eya mwasandusa Malawi kukhala Mlakho ndi Ndata vinchewe iwe
Ndalama zipita matumba zimenezo…kapena zapitaso kale….zili ku Ndata…Zina kuMwaza kwa mwanaa!!
ma donors nde ndi amenewo,bravo APMs govt
Bravo indeed ….share it accordingly and keep it in your mansions….
Bravooo!!
Kkkkkkkkkkk… Failire *1000000000
Mubeso ndalamazo anyapapi.
Actually its not because of your apm…
Akuti zithandize anthu anthu osati zozapangila campain timvetsesane pamenepe inu ma kadeti a pitala
Zikupweteka Akasume Ayeee!!!, Anthawa A M Y P Awaa, Viva A P M
mukuti chani kd,,,,,chili chose ndale basi kma ndinu a Malawidi inu?
Ayidya okha amenewo ..
Mumva kuti boma lilbe ndalama,, chonsecho we’ve been given
kkkkkkkkkk koditu ndalamazi akamapereka amapereka akudziwa kuti zigwira ntchito yoti ngati wina wakupatsa K2000 kuti ugulire nsapato ndie iwe ukasinthe kukagulira malaya ndie kutsokonedzako kumeneko ngati ndalama izi apereka kuti zigwire ntchito kumbali ya ulimi ndi ulimi basi osati chifukwa choti dera lakuti kulibe mseu ndie titengeko half ya ndalama za kuulimi zija tikamangire nseu uko ndie kutsokonedzako
Kkkkkkkk is that what I mean??? Are you just okay upstairs??? Kufulumira kutsutsa wasuya eti?? ? what i mean is chimene ma donors aperekera ndalamacho,, ndalama zimenezo sizipita ku department imeyo thats what i was trying to say,, are you a Pitala fun?? ? ? ? ?
Mmamvela kaye pa zodiak radio?