The ruling party wind has once again swayed Joseph Nkasa to employ panegyric tactics, in favour of the governing political body.
The veteran musician who is popular for political songs, speaks highly of the ruling Democratic Progressive Party (DPP) while dressing down Malawi Congress Party (MCP) in his latest song.
The song which has gone viral on social media, portrays DPP as a peaceful party which makes it more deserving to be ruling Malawi.
Nkasa strengthens his position through exposing the dark history attached to MCP.
The opening verse begins with a Biblical allusion; he narrates people’s choice of Barnabas over Jesus when they were asked as to who should be granted freedom.
“Lero kunabwera DPP chipani cha mtendere, la chitukuko boma ndi Arthur Peter Mutharika, Anthu ali pa ufulu DPP chipani cha mtendere, misewu ya phula ndi Arthur Peter Mutharika, Chimanga kutapa kutaya DPP chipani cha mtendere, sukulu za luso ndi Arthur Peter Mutharika, olemba nkhani akulemba DPP chipani chamtendere, opanda omangidwa ndi Arthur Peter Mutharika pazifukwa za ndale, DPP chipani cha mtendere,” he sings on chorus.
The song gets ugly for the main opposition party when Nkasa mentions the atrocities that were committed during its rule.
“Pomwe panadulidwa mitengo yaminga, pozaphuka sipazaphuka wa papaya, minga yomweyo ndiyo izaphuke, Fisi akasamuka kupita Phiri lina sikuti kumeneko akasanduka nkhosa, mtima waupandu amayenda nawo, kumbukani chifundo cha nsema mitondo, chinadyesa matumbo ake onse mmimba, Malawi Congress Party ndi ma vampire.
“Zikanatheka kuifusa mizimu, kuti tambala wakuda abwereso, inakakanisisa kwa mtuwagalu.”
This is the third song Nkasa has done in the political realm this year. He started with a public relations song for former Minister of Agriculture Dr George Chaponda in the wake of maizegate, then he produced Yoswa for President Peter Mutharika.
He got into the limelight with political songs during the late Bingu Wa Mutharika’s rule in 2007 with Mose Walero. In 2014 he engineered another political propaganda tune for Joyce Banda.
Against all my belief and convictions;
I think Nkasa have just proved me wrong, … This is one great Malawian artists!
Just one single product has attracted all these comments, proves that he is a great artist whose products really go to the core of his audience.
Love him ore hate him his song tickles almost all of his audience.
Kutetedzana? Kkkk anayimba za wakuba mmela uja pano total trash muziona Malawi wake si wadzana uja tikuona zomwe mu kuchita afisi
Mbalame ya munthu iyi
Munthu wa khwinthi uyu..
Mbuzi ya Mbuzi yongotengeka bola ndalama.
Very true
Tikufuna mechanic odziwa ntchito abwele adzatikonzeleko mutu wa mkasa wafoila (mental mechanic Mm) call me soon after
Nkasa Amapembedza Mafano Musiyeni Akaziona.Nkasa Ndi Munthu wadyera. Nyimbo Zake Sindingagule Bola Ndidzimvera Sir Paul Banda”dzatamanda Ambuye Ondipatsa Moyo”
A nkasa ndi kusapita ku sukulu kwawoko alibe nzeru.
peter munthalika he is like joe gwaladi or josephy nkasa .musicias who sing song without knowing what they are singing .no wonder gwaladi calls himself a proffesor and mind you muntharika is also a proffesor
What the problem here coz ndiufulu wake mkasa kukamba zomwe akuona kuti ndizabwino kwaiye inuso ingoimbani ngati mukuona kuti paliwina akuchita mofanana ndi momwe mumalingalira
Stupid nkasa wadya mayi eti
Running out of ideas baba
Nkasa kuimba nde waimba ,amene zamunyasa awona kuti apanga bwanji,makutu ndianu
Chimutu chachikulu koma kabongo ngati full stop (.).
mkasa komwe uliliko undimvere ukumaimba nyimbo kumanyoza anthu mudzina la ndale ukulakwitsa,udzayenda mmanja mwa anthu.anthu omwe ukuwanenewo zimawapweteka akadzakwiya sudzawafuna.
Mkasa ndiopepela
That’s stupid people do,they don’t think of tomorrow
Wina wamisala oposa vincent Wandake ndi Nkasa.
When those vampires come into power you will praise them in your songs just to gain favours because that is what you do with every government, what sort of person are you without direction?
Mbuzi ya mbuzi zonse ndi imeneyi
Nkasa galu wamunthu umphawi wamuvuta wangofuna ndalama alibe kalikose pano ndicifukwa adakungenda kunambuma iwe nthwi ya amai
awa anayamba ndi Bakili kenako Bingu lero ndi izi follo 4 leader chifukwa chake anthuwa samasiya zatumbwazi chifukwa cha anthu ngati okomedwa osayankhura zolakwika za munthu kumangokhalira
awa dyera lidzaphetsa ndithu
Nyirenda, Nkasa is talking the truth, Mcp started long time under Kamuzu to be Vampires in Malawi ( Blood Suckers).
Donton Tchale, can you tell us one muscian in Malawi who has vision. What vision re you talking about?
Wakumtsetse Nkasa……
Shame
Bulutu la oyimba
time talks mkasa & be careful with it
This ball less guy must be very mentally disturbed
Anaku menya pang’ono
umphawi sizinthu kuyamikira zaziiii kut upeze cholowa. utha kugulitsa nazo mkaz wako nkumauza anthu kt ndi ccta wako izi
Kkkkkkkkkkk nkhondo ya mawu yayambika ku Malawi
Mkasa ndi mbuzi yenieni sadziwa chochita amangosapota boma lina lilirons lomwe lingabwere just looking for money.
mbatama ina iyi
Mbuzi ya munthu iwe
Dzulo anali kwa mai lero akut wabweranso ku DPP peter anali poison l as nw ndimunthu waphindu hahaha mkasa xool ndi yabwino koma poti umadziwa kut zabwino kudyera akapusa ndie adyereni
Ngati ilipo nyimboyi tigzyireni +27 618 606 007
Yu mean zombie’s ,heh!!!
Ma sunglasses avalana. Kkkkkkkkkk!
Koma ngati uli umphawi !!!!!!
kwa oyimba athu onse mdziko muno,mkasa ndi wadyera komanso wodanisa,tangokhala phee ndi umbuli wakowo
Imwe mwanyithu Mukususka MCP kumbukirani vinthu vyose vikawa mitengo yiwemi nyengo ya MCP muboma mulikunjira vakuba vekha tawina malawi tikusuzgika ivo vikwenda mumiti yawo nkhuba. MCP niboma lakuvwira tawina malawi 2019 MCP
Nkasa alibe nzeru amayamikira chilichonse kwa iyeyu nsima ndi yokoma, chiphwisi nchokoma komanso ndowe nzokoma.
mhuu mwatokotatu braz
Inu uyu kapena osapota mbava Ndani angasangalale munthu waba chimanga cha amphawi akumudzi kenako mkumayimba Zomuchemelera that’s very stupid
Koma anakuphwanya mutu muja iwe nkasa sunachilapebe eti
A Nkasa ndalama timapeza pogwira ntchito osati kumabera andale powanamiza.kumachitamanyazi nthawi zina ..
NKASA NDI WAMISALA NDALE ZIZAMUPHA
Nkasa akanakhala mkazi bwenzi Ali ndi ana ochuluka APA tchire uyu
koma adha kkkkk.mwatumidwa inu
Vuto laumphawi umangochitapo ndizosayenera zomwe… Sorry Mr. Mkasa… Madyera too much. Mumudziwe Yesu ndiakuphunzira ake..
Suja unkati chaponda this chaponda that iwe?
Awanso nawo aaaaa
Zipatso za std 2 yakale,kumvetsa chisoni a Nkasa
Kape uyuso udzaziona 2019
Umbuli basi
Mkasa ndi akatundu amangothibula mmimba samanyengelera we are behind you more fireeeeeeeeeeee Ana achepa
Ife tikumaveeranyimbo ngat kayiuzeni nkhandwe ,,,yakwiya ndimizimu zinazo zake
Nksaa anadwala kwambiri ndipo sanachirebe, once mad always mad, forget about him
Aman
Zoti Nkasa mutu wake sugwira sadziwa ndi ndani kodi nanu,kazingomuonani uyu mwezi uli ku mdima ukatuluka akhala bohbo josey
Mitu ya anamapopatu imaoneka chonchi?
Nkasa is fortune seeker. He will find us here
Nkasa ndi more, osamumvetsetsa onse ndiye ma fools amenewo, anati iye ndi woimba si wandale ndipo amamvera boma lolamura. Kaya atatenge a Mcp azamvera iwo muzingomuyangana basi ndi woimba, mumafuna oimba otukwana boma mpaka boma liziganiza zowapha chonchija eti?
amavera boma lolamula ngakhale likulakwitsa?
Ndiye nkasa ameneyo, likazagwa azaliimba za mwanonso likumva. Palibe boma lingaganize zokupha oimba ngati nkasa amene amanyadira boma lolamula. Tiyeni timvere boma chisankho chikazafika tizasankhe amene tizawafune.
Mmmmm ulesi awa!!! Akosowa podyela
KkKkkkk, koma nkasa ngat ali ma ARV omwe ukumwawo akuzunguza mutu ukaikaso minga pa mjigo.
Nkasa supports government of the day,so do i.bravo Nkasa!
Tell those who listen to your sht kati
Shameful dog nkasa
MKASA WAMISALAYU?
Munthu osadziwa chimene ukufuna,,iwe usandiyankhulitse pambali pakati ndupaona,shupit wandikwitsa*1000
Ngati pali munthu winaso ovuta maganizo pa dziko lonse la pansi nde ndiwe Mkasa
Kkkkkkkkkk
Nkasa oro ineyo sindifuna kuveraso Nyimbo zake adandinyasa adakakhara wina sadakayimba Nyimbo ya mose warero ayiiii Nyimbo yabwino ngati imeneyija koma zose ndi 2019 muva kuti nkasa mwakataya atamugenda zenizeni osati mujamu adamuyerekeza muja ayiiiii komatu sakuremeraso ayi zaziiiiii
Kkkkkk galimoto kagwire ntchito komaso iwe tiyeko mkasa tivote panopa uwerenge makomets ngati pali a darkness Democratic paty
AAAAA CHOKA IWE USATNYASE WAMVA TNATOPA KUMVA ZAKOZO
kaye kunyasa mau
Plz share ti this number …: +27613220095
Nkasa sazamva….. waiwala….??
Nkas analikaleso awa
Fisi wa chabe chabe iwe
Kodi tintedi imeneyi akuluwa amagwila ntchito yoochelala chani chifukwatu ndye samaisiya
Alimbe kalikose Mr Nkasayo ayambe umbutsa please
mukulimbana ndi munthu a samuziwa?
Don’t waste time discussing about useless musician he was there with Muluzi, JB, Bingu and now Peter let’s assume leadership is changing tomorrow he may change as well
Ndinachipeza xhikudya mbatata pa std bank city centre Kaya samadikila lobowoka
Kodi nintundu wanji Wa munthu nkasatu? Amanya ndalama ngati akufa lero? Musiyeni aone ngati magetsi amuyakile kwaoko.
Nkasa is just a stupid musician, put your whatsapp numbers ndikutumizileni nyimbo imene inamunena pitala, not ija ya Analila ija
Anthu anyau ndiokhwima kwambiri amatha kusanduka galu, fisi, kazizi, mkasa guyz akunena zooona
Nkasa ..mbuli ..geri mulibe musalimbane naye
Umbuli wamuchulukira mkuluyu
asamalowelele adzamukunthanso waiwala ku dowa eti
Uyu ngakhale Manyi atha kudya bola apasidwe ndalama basi
Iye amati
Sindinyoza Boma lolamura
I like his point
Nenani zakuvutani a Nkasa bwanawo akutandizeni munazolowela
Nkhasa doesn’t know zat there is tomorrow.
He shud be careful when criticising political parties for he does not know which party will b monitoring our flag after 2019.
Kkkkkkkkkkkk comment yanu Andrew Kamwana mukuti bwanji mkasa afuna galimoto uyu savage
Okupandani inu
Awa anatha mapulani kalekale ntchito kupempha basi .
knkkkk m
Inu ankasa nde simuzasiya kulila anthu akumenyani mpaka kutope kma mungopemphela kt azingokumenyan asaganize zokubayani ma jekeseni mwamva ankasa? mbuz ya oimba
Mbuzi yamunthu iyi
MCP ndi dhilu asafuna akhale 2019 chongu✔ tione zina tavutika ife ndi misika ya mbewu.
anapha #gadama #gadama anachita kuphedwa poyelayela whitewhite
anapha #gadama #gadama anachita kuphedwa poyelayela whitewhite
Is mkasa a musician?
Woyimba wamisala ameneyu. …Masikini..
kkkkkk Nkasa is just one illiterate musician. …kubakila each and every govt Cholinga awone podyela. ….visionless freak yuck!!!!
Mcp ndi Anthu oipa kwambiri akupha asazaloweso boma amenewo tizakhala pamamvuto owospa kwambiri akulu akulu tiganize mofatsa chonde chonde ndagwila mwendo wanu Anthu akhaza awa alibe achisoni azingokhala osusa boma paka paka koma simuzawinaso ndikulumbila mulungu modzi yekha
Mkasa akunena zoona,even Bakili ananena kale kuti JZU.m’manja mwake muli magazi okhaokha.
nkasa network idaduka
Write a comment…lol
Woza bwana mkasa imbani Basi kuti awo azipsa mtima kkkkkk
Xhilungamo akuchiziwa iwe ngati ufuna kutengapo gawo tenga sizo tukwana munthuzo vuto la pampanje ndilimenero uyu akhale Ndani ndichifukwa ndina thawako akuziwana awa (kunxqono kuthula)
This is why education is important, m’baleyu umphawi, umbuli, u chitsilu ndi zimene zimamuvuta
Kamaso kanundu
MUSIYENI MKASA NANU ZIIMBANI NDIUFULU WAKE
koma nkasa please uusatiyankhulitse pali
mwachidule tingoti mkasa ndi hule chifukwa amakwela imene ikulamula pamenepo even MCP ikaxawina muxamuona mkasa akuimba zochomelela mcp yot anainyoxa .koma opanda mxeru ndi andalewa chifukwa ndikakumbukila mene adainyoxela DPP sibwex ali nayexo
Utsi umadyawo nkasa. Udzakupweteka one day.
Mbuli ya oyimba ngat imeneyi sindinaione pano ndiye chafika popeperatu thats y ndinasiya kumvera nyimbo zake
Kkkkk
uyu ndiwamisara uyu …saziwa zomwe amapanga
anthu aku dowa !!!!!!! anamumenya nkasa
Mkasa
Mkasa Ndi Mende.
Muona safunsidwa olo
Nkasa ofunika naweso ku mental .
Udali kale iwe Bakha wachabechabe
Nsanje ndi ufitinso…
DPP killed Chasowa,Njaunju, and 20 others on July 20,if these are not vampires what are they ? Mind you Nkasa is not a musician, he is a story teller.He started with Bingu kanenere a Police,then a mayi ,Zonse NDA mayi JB,it was all praises with a Mayi,now with President Peter as Joshua,4m contract with Katsonga went sour,Does he know what he is doing ? His stories are for money,that’s all. With MCP 2019_he ll change tune. This is the man we need not to waste energy with,it’s a matter of time.
Tidye nawo uyu
Makape inu mumafuna anene kt mcp ndiye yabwino ng’oo mwauponda,anammenyako a myp ndiye sangaiwale ayi enanu kunalibeko
Ammenyetsenso pansi sanalape
Saona wakuyeriko uyu
wokuswa myala lero watola chikwama mmati anganeneso chani abale . Konseko kuopa kubwelera kokaswa myala kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk nde akufuna chintuwisa
Anali phungu uyu , lero chakhala choseweletsa andale. Very sad. Umphawi sizinthu.
Liar
Paja anapengapo akuluwa
Izi zichepe dont mask others
Akufuna kt apondedweso mutu ameneyu,Nkasa sadzava gys ndie akadutseso mu Dowamu akhaula
how hot Malawi is? our pockets are dry we don’t see any hope, what we see is darkness ndiye wena azikamba za nkutu tikimva kuwawa?
Nkasa is an expired musician
Phungu is one of the nonsense people ever… Even chipereni wind has direction but him no where to go. What he wants is to milk funds of poor malawians
F**k Nkasa…In your p
Phungu ndi Phungu sangakwele zakupwa game ndi DPP wina afune olo asafune
anakwela ya amayi sanakwele ya kupwa
Thanks to Dr.momoh who saved and cured me from hepatitis B.. virus. with his herb medicine you can also reached him for similar
*Or any other….virus…like.. Hepatitis…..C… Virus….
You can reach him through this number…you can add him on WhatsApp believe me you will never regret it
+2349068579672
Your cure is here for you !!!
Ankasa mutu wawo sukuyenda bwino
awa ndie kayatu,its better to choose a dog…..it can help you
komatu munthuyu akunena zoona guy’s, mcp ndi chipani chankhaza chimadyetsa anthu ku ng’ona kugwilila azimayi ndikuba ziweto zamphawi komanso idapha achina gadama mwankhaza powakhoma ndi misomali m’mumu
That was those days bro wake up ! Thats y we wil neva c change if we carry that mentality!
Umbuli siwabwino
Ndiwe kape wamva
Chasowa adamupha ndindani?
Kape ndiiweyo@kaphetsa,mbuli ndiiweyenso Zione wabadwa pompano iwe mentallity yachani inuyo kuzindikira kwambiri shupit
Nanga Chasowa Inamudyaso Ndi Ng’ona?
Iwe ngati nkotheka Mulungu angokutenga pompano ndithu…you’re very useless citizen.
Mukakhala ndi mtima umenewo sitingapite patsogolo MCP yakale idathera ku chipani cha DPP chifukwa mambala akuphawo anathawira kumeneko. Pano chipani cha MCP chilindi anthu owopa mulungu
Kuopa Mulungu kwake kwa pakamwatu osati mumtima….mudzawona ndiomwewa omwe adzatitafune akadzawina….abible says: no man can please another man except God himself..
Umbuli basi tima China phone tanuto ma cadet plus data free basi
Pakopako wamva iwe
Mbuzi yamwana
Tikupeza konko mpakana ukalowe ndende mphwanga kkkkkkk
NDINU ANA ZA MCP SIMUKUDZIWA. ALMOST 18000 PPLW LOST THEIR LIVES IN MCP ERA. ZONGOMVA ETI?
mukulimbana ndi mcp panene akupha aliku dpp expeciouly dausi
Mkasa sanayambe lero kunyoza mcp, he is a coward and a fool who stands to eat evil money, to hell with your cowardice
Mvula ikagwa kumachuluka zoliralira, owinayo 2019 aliphee satekesekasoi chakwera kale
Mkulu uyu ndi was government of the day….alibe pabwino
sadziwa nkuwerenga awa ndipo wamuuzira mau oti vampire Ndani? Umphawi wamukantha pompano timva ayimba nyimbo praising Bushiri kuti apeze kanganyase kkkkk
I’m in need of that song, can someone share to me
Kodi madala amenewa nanga si amati asiya kuyimba zandale. Ayamba utumiki wa mulungu
Awanso awa!!
Are they? can you prove, I never vote for them and I will never vote for them in the future but I can not call them vampires but rather good friends and my bosses.
Hahaha awa NDE ayi amalawi mphepo imangowombapo basi
Kudana ndichilungamo mukufuna achite zomwe mukufuna inu mwagwa nayo tiye M
Nkasa DPP ikufuna anthu ngati iwe MCP yaboowoka yaphofomokanso DPP more fireeee
MM MM
MCP should sue Nkasa for deformation Coz boma linati opopa magazi kulibe so why Nkasa is coming up with these claims ….let him alongosore bwino
ofunika kupitanso nawo kudowa kuja akang’wing’wi apangeso beat sense mmutu mwa ankasa
tikuziwa bwinolomwe ma vampire ndi a D P P nde akuti muzavotele ngozi zapensewu komanso akuti ali bwino kuposa akulu
mmmmm nanunso inu.. magetsi omwewa eti??? tazingoyimbani magitala anuwo kumeneko
chitsiru ichi changotopa ndi maluzi,chamisala osachitengela zake DPP Ikutuluka m’boma 2019 akazabela tizapanga ma demo opanda malire mpaka tizavotaxo anyapapi inu tatopa nanu MCP boma tione zina
Ukunama mkasa ine ndingodikira 2019 kt ndidzavotere Chakwera.izo ndizake mkasayo ine mavampire ndikuwadziwa
umakwana phungu tauze ana abadwa nthawiya democracywa
Mkasa sunalape muja anakukomoramu kamba ka mbwelera zakozi eti kkkkkkk
guys , possibly admin wa news page iyi akunama.we can just expose our stupidity pomamunyonza munthu yemwe.sanalakwe. ndiyankhabe ndikaimvera nyimbo yo my self. i have smelt a rat in this issue
Judas Iscariot. Betraying his fellow countrymen for money.
Koditu Nkasa si munthu oti ndi ali ndi nzeru. Adati si wandale, then ati Mose wa Lero, then adanyoza DPP saying amene akulamulira ndi amayi, then adanyoza boma lilipoli saying a police malipiro sakukondwa nawo, then akuti Joshua wa Lero. Itati ilowe MCP muzamumva akujama ya MCP. Uyu amangofuna ndalama ndi chitsiru munthuyu amasowa zochita. Ine sindikuona chodabwitsa. MCP 2019 boma koma Nkasa ukagwere oyimba athu tili nawo kale.
Chitsiru chimenechi koma.
Mbuzi yeniyeni.
Chofoira
People are cowards busy accusing Nkasa opusa mbuli inu ainkinu osayimba yanu yasukulu bwanji. We’re commenting coz tamva. Kaduka pa Malawi
Language ya minth wa nzeru you. Assess your language before you write. God loves everybody
tangodyani ndalamazo mwakachetechete
Umphwi sizinthu sure ….ukhoza kudya nazo zoyipa kuti upeze cholowa basi
Kkkk simukunama mpakadi utaphuzila ufiti kuti upeze ponona
Koma ali ndi tsoka ameneyu
eeee……..eeeeeee……eeeeee……eeeeee kma mphuno yake inakalota anakakamba zamzeru bt he need 2 irumminate hs idear,,
Mkasa u r useless clueless and just a wasted talent… You are a shame in the music industry and Malawi at large… You just a boot licker youre greed for money will kill you… You are calling MCP vampires yes they suck ignorance poverty and corruption your thinking has drained like you are a 2015 baby….
We are not kids axe, that time is long gone and we all know it. That’s why you were beaten 5-1 by the so called vampires. You see vampires but we see redemption, meanwhile the clock it ticking.
useless artist
More fire Nkasa kuimba salesana! wina wakubalaka waimba zakenso ndani wadandaula?
A nkasa simudachimine a chair adakunamizan galimoto pano mulilaso kachikena
To answer a foolish person you can become a foolish too
nde nchiro zawo a MCP palibe saziwa zimenezi!
mkasa uzivere uziganiza mwa umunthu pochita znthu; ndiwe mbuzi
Kma Mulumana sure
Chamba chamupweteka musiyeni! Oyimba muja adayambilamu Osawoneka kusamba?
Akufunika ku mental uyu ndi wamisala nde bola mbenjele tu
kkkkkk akufuna cash uyu
This guy is obsolete we don’t give a hoot about what he says or thinks
Kodi iyeyu wayiwala kuti adatibulidwa kale ku Dowa atanyoza MCP
Uneducated savage who don’t care about his reputation as long as there is money
Kodi awa sukulu adalekeza kalasi chani?
munthu wadyera uyu opanda manyzi…Panja anthu akut dowa adamuchita kanthu
Mose waleo
Pumbwa
Komadi Pumbwa zoti zinthu zimasintha osadziwa ai
Kkkkkkk
Chitete ameneyi
Mutu sugwira ameneyu akuchedwetsani guys…..
Kapolo wa dziko uyu
mwatokotatu
nkasa anafika pawuchitsilutu kkkk ndalamadi ndisatana basi
Mkasa;waiwala zomwe anakupanga achewa ku Dowa?Panopa ndiye akupha
I hav never seen a stupid Musician lyk this Idiot called Nkasa.
Paja mkasa akasowa mafalanga amatero kupempha kwake musamuiware.
DJ nyimbo ija anaimba Nkasa amati poison
A nkasa ndichisiru ndipo akuganiza kut a2 angawcthe maganiz ndi dyera lakero? amalawi pan anachangamuka uchisir wakew asapak naw a2 ena
mmm koma ndiye mwayakhulatu
There is no substance in that, he has just shown how greedy and untrustworth he is
Ithink it useless kumamuyankha nkasa wanuyo ndi oyimba amene saziwa wt he want
Ankasa ndaninso,garu wa chabechabe. President aliyense amuyimbire nyimbo ndicholinga chopempha ndalama. Bulshit, kang’wing’wi iwe.
Kumachita mention dzina lake kuti aziwerengele yekha ma commentwa,,si choncho bwana Phungu Joseph Nkasa?
Uyu akanakhala nsikana bwez ndi hule…bambo awa amakonda ndalama ngati ndi amapasa nazo
Kkkkkkkkkkk,, akulu play him well.
A man without vision
Umbuli ndi matenda heavy
Idiomatic opportunist…
Ndinali mmodzi okonda kunbvera nyimbo zankuluyu,koma pano ndimanyasidwa naye heavy.
Ndimunthu oyimba amene sakudziwa za tsogolo lake.
Idiot
I have never see the stupid musician like this ugly man called himself Nkasa.
Mkasa ndi wandale bola wandale
Chisilu ichi
Oyimba amene ali mphawi kwambiri nyimbo zakenso za chamba ngat mukufuna kupempha amuthalika akuguliren galimoto just go direct
Mkasa maso ake amayang’ana kuwiri, ma vampire ndi a DPP coz anachallanger kut ngolongoliwa amaziwa bwino kutamba
Achitsiru a nkasa mumadziwa chan zandale inu mbuzi
Awa school idawadutsa kumanzere ndachitsiru amangipita kulikose komwe akuona ngati kuti akhoza kupezako kanthu mboli yankhuku iyaaaaa
I wish Mkasa can come and read all these comments, it’s his time to learn
Ali ndi nyimboyo atipange share apa pliz nafe timvere +27842531486 thanks
Mmmmm no comment.
Vampire ali iye amene
Koma Gome zathu ndizimozi aise…. Kuyambira timu… Chipani MCP 2019 bommmmmaaaaaaa basi
Mcp has to sue him as of now a certain senior chief in the south did say him knows who are begind it and that he can deal with them! So for Nkasa to claim otherwise then he has to prove in the court of law I suppose!
Kungoti school mulibe man wa ndiye samaona mmene dziko likuyendera.Ndikape uyu
He is unfortunate person amadzigulitsa pamtengo wotchipa he’ll die like a coward
MCP 2019 boma, Chakwera boma, dpp kwao paulendo akapitilize kupopa magazi.
ankasa mwamwa kale? Umangidwe anzako akuseweza ongotchula kut vampire
Nkasa sazamva
This Person is now useless how can he involved himself in these dirty politics and he is no longer Joseph Nkasa we know
Nkansayo ndionse a DPP ndiamene mavimpire nkasa kupemphapempha ngat mwana oyimba anzako amalimbikira ntchito.
The #1,greedy musician in MW ,
MULEKELENI AZIONA UYU THAWI IKWANA
akufuna adye nowo mbunzi iyo,botolo lomwe lilibe madzi limapanga pokoso kwambiri ndiye mkasayo.Kapolo sakwiya
Kungoti Anthu Osephana Maso amakhala opepela
I don’t see the reason of betraying one another while truth is uncovered. Stop to dig over our ear drums with your speechless accusations
It doesnt matter spellings capture his content of words. Amalawi tidatani kodi? aati ifeyo ndiye odziziwisitsa vizungu, bwanji ngati tafikapo why
Nkasa munthu opusa iwe
Nkasa palibe chanzeru chomwe anganene ndi tidye nawo uyu.
milomo imeneyo idzapitilira kukula, udzienda komko.
Achitsilu a nkasa
unaimba kale mkasa nyimbo ina yake yoti wanunkha malawi tilowera kt under the same leadership of peter ukumukwezay ndie tidakadikirab kt mutiuze kumene tilowele
wsh nditayandikana nawe wa masaya akuluwe, tisazakuone uli khwekhwerekhwekhwere ndi ma vampire ukutinenafe titatenga boma 2019 with clean sheet, kaya akutuma, akupweteketsa ameneyo, n dziwa kut zopepera zakozo zikungoonjezera molalo ku MCP, koma a DPP ngat iri pressure ndiye muzakomokatu 2019, tambala wakuda more fire
Zoona bambo nkasa
Ngati kuli mbuzi ya oimba ndiye ndi Mkaaaaa______________ kwinako pitilizani guyz
Nkasa afela za eni awa iiii makobidi basi anakukanikani
This Guy is a whole for a penny..if he was a woman he could be selling Kutchie pa Mboya or 47
Nkasa is one of the visionless musicians who do not have actual direction. And I believe he even do not know what he does.
He focuses where there is green pasture
Apita nazo kuti ?
Akuimba chilungamo Dr Nkasa kusiyana ndi gogo yopusa Lucius Banda
chilungamo chimawawa chikamalankhulidwa musakwiye AYUFI
There’s no reason here to talk about Lucius Bandà while you know that issue not concern him
Ñdakwiya kwebes
Opanda vusion ndiiweyo,aliyense amayang’ana chakudya chapakhomo lake ndiye mkasayo ngati podyera pake mpamenepo musiyeni mkomwemkomwe a mcp mukuilimbikirayo anthu sanaiwale mwina ma born 4 nu ndiamene mungamaombe mmanja poti mumangova kma kadxina kameneka koti m……c…….p kanationetsa zoipa kuposanso mautsogoleri mukunenawa,mwina chakwera adakasintha dxina lachipani koma ichi cha 31years anthu tikumangidwa nyakula fukwa ulibe ndalama yamsonkho kapena card lau membership very sad
Chiluzi Iweyo uganiza muthu akhoza kuyira zimene zikuchitika nukumbukira zochituka 20 years ago Ndiye chamba
ANkasa? Chosadziwa anayimbira mfiti mmanja! Zili uku anabwerako ndimwendo wathabwa.
Kkkkk ine bolani ndiyovinika
a Chiluzi koma mwamva kut kukubwera k5000 yogwirana? under the dynamic leadership of pitala kkkkkkk
Nkasa paja anakuswaso kumpoto
Usiru kkkkkkk sanakulakwire
King of the Nosense-nkasa
Avule magalasi tione ngati ana sathawa
amkasa ndimwi achilekwa,ndimwi achitchiru
Focus on singing your local trash songs don’t involve yourself into dirty politics just for money
He should be arrested
Kodi nkasayu waiwala zomwe tinamupanga ku Dowa? Pa nsomkhano wa Amai Funso langa kwa nkasa ukufuna kuphwanyidwanso MUTU
Phwanyeni basi
Ali ndi mwayi pano ndili ku theba
Eishii nkasayo awona polekera iya
Stupid mkasa
Kkkkk characters of pple in dpp and its acosiates : KULI ANTHU OPHUNZIRA KWAMBIRI,KOMA NDI OPEPELA OKHA OKHA…chisanzo aliyense akuchidziwa KULINSO MBURI ZAMBIRI ZOMWE SIDZIZIWA CHOMWE ZIKUPANGA…the likes of nkasa ndi chisanzo…
UMPHAWI NDI UCHIMO LERO NDAMVOMELEZA NDITHU Kodi mkasa osamutengela ku mental hospital ngati muja mukumuchitira wandale Vincent uja bwanji???? Uyuso ndi openga kaya ngati simukudziwa mumutengele pa chiyambi myimbo zake zinali ndi matanthawuzo omveka bwino koma chama 2010 myimbo zake mukabvera bwino bwino mundibvomeleza kuti mkasa akudwala misala ndi openga akufunika thandizo la chipatala mwansanga asayambe kugenda anthu ndithu
Nkasa ndikape kuimba kunakuvuta basi.manyaka!
DPP ndiye ya ma vimpire.kupopa magaz.kupha achi albino.kuvulaza otsutsa boma.then ma vampire mndan.umbuli ankasa unakuphan.ku mcp suzalandilidwa ase ngat umakwera boma ku mcp malo suzapeza
For wat reasons simunasinthebe dziko la demokalase
phwete
A Nkasa mudzafera za weni inu ndi umbuli wanuwo. Advice is free don’t say i didn’t warn you
M’KASA NDINANZIKAMBE ALIBE BALI PANO NDIWA DPP 2019 ANZAKHALA WA MCP AMENEYO NDIYE M’KASA YO.
uyuu ofunika kumenya kobasi wa usilu sure
Kkkkkkkkkkkkkkkkk
A failed musician
Vuto lozorowera kupephapepha mapeto ake umayakhula nazo zinthu zopanda nzeru ngati izi aaaah!!
Utenati wolima bale unamupha galuyu mtayeni atitaitsa tym fisi weni weni,kapena akufuna aone zoposera za ku dowa zija
Munthuyo adzafela zaeni ake pajatu adayimba nyimbo yonyoza Peter Mutharika pamene amakodzekera iye za kapeni m’chaka cha 2014.
Amenewa timati Amimba tiye kudyakuli konko/atidye nawo
Mcp
2019
bomaaaa
Foolish nkasa iwe, chifukwa choti adakuteketa anthu ku dowauku wayenekutero mtidyenawo iwe wayesa ulandiraso galimoto kape iwe.
Ndipo timuteketaso ayese kudutsira cha kuno
Kusakasakano pofela kkkk
Akuluwa mutuwawo sugwira ntchito wamisala nkuluyu
Alipo awa, but akanakupha nthawi ya Joyce a DPP.
Eeeh mkasa ndalama zzamupha uyu aaah kaya nd umbuli kaya,
Opempha can do anything to please the giver……….. pitilizani kulidyera boma. Otherwise the truth mukuchidziwa
Awa akula mozunzika tikuwadziwa Asiyeni….A Nkasa mwayamba zimenezi eti…Zizaululika..tiye nazoni…Mwaiwala ku Manja kuja eti…
Sunalape za ku Dowa zija oky pitiriza .
Mmene Akuonekera Nkhope Nkasa,Anthu Sangachite Kufunsa Kuti Ndi Vampire Weniweni Wa Dpp
If you ate tired if singing Nkasa just go kwanu ku Machinga ukapumule. What you are singing is tosh and absurd, what you are praising in your song was done by a line of presidents from Kamuzu, Muluzi, Bingu and partly Joice, what have Peter done so far to be recognised as a good leader rather than shielding corrupt government officials? Stupid Nkasa.
Nkasa,chilipo,chikumusata
Amkasa ndinu achitsiru munthu wanji wamthira kuwiri kungoti kumene kwapita mphepo mkomweko
munatha inu ankasa munali kale simuthaso kuimba nyimbo zanu ine ndikuntha zaka pafupifupi 10 osavela amene umawatamandawo sakutenga mkomwe kukankhala zochitika kusonyeza kuti ulibe luso lamaimbidwe uziona 2019 inu ma vampireyo akulowa m’boma
Mkasa woyeeeee
kusowa chochita ankasa kkk
Failure
Vis man need to be sued
mlomwe opanda mzeru.
kodi iyeyo tanthauzo la vampire amalidziwa kapena wangoneneramo??,,,,anamapopa dpp,,kupha ma alubino dpp so who are the vampires here??,,,,the opposite is really true
sanamphuzire inu uyu akufunika kumutanthauzira kuti akati vampire ndi chani
kkkkkkkkkk akufunika sukulu yapadera dera yakwaaachaaaa kkkkkkkkkk nkasa mbuzi ya muthu
He is an empty headed dude, an opportunist
Hahahahahaha don’t u know vampires u also? Ndiye wakuposanitu wosaphunzirayu eti??
Sakunama
Kkkkkk Nkasa akuti chani?
I think this guy is box2 is mentally disturbed
kkkkkk mkasa is my raw model keep it looked mr mkasa your one who represent us
raw indeed
Raw model wabwino
Say by to ur brainwashed dude so called nkasa
Fooled entertainers aways entertain fools i
Raw model yemweyo hahahaha! English didn’t love us
Raw model yemweyo watsapp grp
Raw model keep it looked??? wangoyeneradi kukhala friend wa Nkasa ada!!
Keep It Looked Mr Nkasa Kma Yaaa Zaunkasadi Izi
Eeeeh boss kuchipha chizungu cha Queen Elizabeth kkkkkkkk mpaka raw model kkkkkkk koma sukulu za naiti eeish sizinthu. Tabagulisami ma memory card anyimbo kale za malume bokosizo mwakacheremu kkkk
nkasa is a vampire too….and his ruling party so called dpp
Kkkkkkkk amkasa mulipo mundibwerekeko ma tintediwo kkkkkkkk
Get behind me eee ujeni
KKKKK UMAKWANA MKASA!
Koma nkasa udzafera za eni mphwanga
Zanu izo
kkkkkk umphawi sizinthu!!!
Mmmmm
I used to respect Nkasa but he has turned out to be a stupid political musician. As Malawians, we should learn to give creidit where it’s due; those who tarnished the image of MCP are in DPP now. Who killed Njauju, is it MCP? How about Chasowa, Mbendera and the 20 striking civilians in Mzu and this is happening during multiparty time. KUBA in all ministries, the blackouts, drug shortages, water scarcity and Nkasa wants Malawians to keep on clapping hands for DPP no!!! that’s madness…………….