
Tikamazimitsa moto sitisankha madzi – Kabwira
Mneneri wa chipani cha MCP, Jessie Kabwira, wati ndizotheka kuti zinthu zina zomwe wayankhula mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera Lachisanu potsekulira Nyumba ya Malamulo ndi zonama, koma wati boma lawo lachita chitukuko chomwe sichinachitikeponso… ...