President Peter Mutharika was not happy with Paramount Chief Ngolongoliwa of the Lhomwe following a downpour at the Mulhako wa Alhomwe Festival.
The Lhomwes were holding their big feast this afternoon in Mulanje but many people at the cultural festival got drenched by the rain while the space left for dancers was a muddy field.
This did not please the Malawi leader. When he rose to speak, Mutharika said he was disappointed with the chief for not preventing the downpour using traditional medicine.
“Chief Ngongoliwa, you mean you failed to prevent the rains from falling?” said Mutharika jokingly.
He went on with his speech in which he among others attacked Vincent Wandale, advised Malawians to stop being jealous and mentioned what his government is doing to end reports of bloodsucking and resolve power challenges.
Tiziwona when political temperature rises in 2019
Akudziwa atha kulanda ngengeo chifukwa ngolongoliwa ndi guye kwabas
AKUYENELANA AKWATILANE BAS
A bad joke
Bodza
Thanks to Dr.momoh who saved and cured me from hepatitis B.. virus.with his herb medicine you can also reached him for similar issue on +2349068579672
A news 24 mapwala anu
Kusowa zolemba eti , osamangozikanda kumpheto ko bwanji !!!!!!!!!
Pita he mst fire we’re tired and that rubbish wat his doing stupid
This story has nothing to do with elections
Mmmmmmmm do not judge
Zowona mvula imayenera kugwadi
Ethupo ophwile mathapa.. Kkkkk
amene timadziwa bwino za ahlomwe timati malo omwe pavinidwa gule wa tchopa mvula imayenera kugwa basi,thats a sign of how strong is the traditional dance to God and timati Mulungu walandira mapemphero athu osati za chamba zomwe akunena mtolankhani opusayi,mwana wa njoka,osayamba wafunsa bwanji za ahlomwe ngati ukufuna kudziwa,u think Ngolongoliwa angadane ndi President?ukuchedwa aise sungawasiyanise anthu amene aja,achokera kutali ma guy amene aja!!!!
Wakwiya ndi nkhaniyi ndi mfiti
Koma page iyiyi imadziwa kupeka nkhani
Atolankhani akuti amacheza koma malawi
Stupit journalist!!
u thought we ar so fOOlish to follow ur suggestion siyanitsani btw ur job nd timalingalilo tanu
Tsono zugwilizana ndi chithuzi mwayikacho?
Kkkkkkkkkkkkk usova
Iwe Amene Wa Lemba Nkhan Imeneyi Ndwe Chtsiru Plz Malawians Lets Lov Our Country,chili Kwa Mzako Usamat Chigwire Nyanga.
Hahahaha! Koma maboza enawa muzikhalako ndi manyazi. Amanena zocheza za mvulazo guys tiziti simumamva ndinu agonthi?
xah ndie xake its kt zili chonco
Zadziwika kuti akulu aja alibe ufiti koma amangowopseza basi. Zawakanika kumanga mvula kuti isasokoneze mwambo wawo omwe.
I personally followed HE’s speech he was just joking and couldnt know that it would be blown out of proportion like this. Shame should cover on of the owner of article
Did the rain fall kwa Chonde kokha?It has been all over Malawi.Pull your socks amatuer reporter they are near your ankles
Ine bola ndizingokhala konkuno nkhani yake yoika pa net koma imeneyi? ?
Kkkkkkkkkkkkk chatsitsa dzaye kuti njobvu ithyoke munyanga ndi chani?.
He was just joking abaleeeee!
The reporter of this story is very stupid. Why do you deliberately misquote our President. So you want to create enmity between the President and Chief Ngolongoliwa? Once again I repeat “Go back to your journalism school and learn on how to come up with a good story heading” This is un called for, nonsense and aimed at bringing confusion among the Lomwe people koma wachepa ndipo sukuyambapo. Uwauzenso anzako omwe anamva speech ya Bwana koma akulankhula za misala pano kuti achepa.
Zaboxa izi guys kkkkk
He was just joking guyz eish
Kkkkkk koma abale
Come again, can’t get you
Kaya Nokha Akumalawi Inu Ife Akumupoto Sizikutikhuza…
Ifollowed All The Function Too On Mbc Tv To Say The Fact Mutharika Said, Angolongoliwa Bwanji Simunamange Mvura? But He Was Just Joking, Nde Inu Amalawi 24 Kufuna Makomenti Bwanji?
It was Just a joke guys nde mpaka pa news kusowa zolemba et
Kkkkkkkk
Mwayambapo kudanatu munasakhana nokha kkkkkk
Kkkkkkkkkkkkk
Whatever
…..malawi is malawi
usakwiye nesa udamukweza wekha
#politics
Nde poti ndi nfumu sangaichose udindo koma akanakhala wa ddp atamukwangwanula kale apa tizingonva zomwezi basi
Zosatheka zimenezo.
Go To Helo With Ur Poor Reporting!!U Mean Out Of All Good Things He Said U Only Chose Jokes As Ur Headline?
Is ngolongoliwa God to stop the rains ??? That means the president believes in charms. ..shameful
A reason not to follow Malawi24.
What type of journalism is this? The president was jocking
Mmm
He was joking not an issue
Biased and misleading reporting.
Ndikudabwa kuti ambiri apa sakumvetsa tanthawuzo la comnent ya a Muthalika. Umbuli ndi matenda ndithu.
He was making it a joke but deep down he knew what he meant!!
Kkkkkk Martha! Martha!!! Kkkkkkkk
Kkkkkkkklkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk.
Zaziii lembani nkhani osati zimenezi
Mboli zanu anthu opusa inu
Wizard Ngolongoliwa
Zomwe amatha amalawi ndizimenezi, maboza too much
Akazitape akumalawi kununkha nkamwa kuona mapazi mmene aswekera !umangodziwiraru kuti si zazanchironso koma kupempha chiphuphu.
Malawian journalist ovala sandals tie pakhosi mij imeneyo kunamiza anthu
Anyapapi mwatsowa zolemba???….Chi Banzi chimenechooo muyalukatu
I told u already guys kut this page was created with idiots, so don’t b surprised with u see stupid posts like dis
This is stupid and unprofessional reporting! It was a joke but u misinterpreted it. #amnotprodppthough
I think so too,, ,,
Mwagulidwa eeti? Kusaphunzira kapena mbali imodzi ya ntchito yanu yofuna kukopa makasitomala ndinu andale eti Aaa aaaaa mwachitika bwanj? Kodi peteryu azingokhalabe ngati ka chisilu kanu taonani anthu akukuposanitu kudziwa kapena nanunso mwangomvanso kwa ena koma tizikukhulupilirani inu Mmmmm
APM alibe problem!
Nyasatimes same as zammaboma….. Kupeka nkhani cholinga anthu awerenge mxiuuu
kupusa
aaaaaa, asamatikwane nthawi ina iliyonse kumangomunena basi kusowa zokamba chani
Guyz zapamtundu izi akudziwana ife salomwe ok shame on u,, also peter stupid guy .!!!!!!
Malawi news I will sue you for giving me half baked news. Tereza Ndanga must probe this because last time she refused to accept that journalists in Malawi are corrupt. We know Malawi news and MCP are two faces on the opposite sides of the coin. Shame!
zikugwilizana bwanji ndi mcp? wasowa zot ukambe osangokamba za yemwe wapanga postyo bwanji?
kkkkkkkkk,wasowa zokamba kumene,osakasumira chi mbctv uko bwanji??? osakasumira dpp voice,dpp independent,dpp eye uki bwanji??? kulani amwene please,kkkkkkk
Ngati Wapsya Mitima, Upsye Mtima Zinizeni.
Ngat umadana ndi mcp ukozekere kuzasamuka kumalaw kuno 2019 tkamazalamulra.chlchose mcp mcp mcp mumasowa chokamba?,kumasiiranj mbava znal kumulakho wamlomwe
Ukunama Maloto A Chumba Ndiwe Fana Palibe Ukudzwah
ngat sumabeleka ndie ife zitikhudze ngat umalota uli ndi mwana chonseche ulibe ngakhale okunamizira, leave MCP a lone kod simungakambeko za mafunde, NDA, PP ndi tizipani tangot mbweeti? kuli zipani 56 koma mcp, mcp, mcp, mcp mcp, mcp. kulephela kumagona ndithu.
Almighty Ngolongoliwa kudzagwetsa mvula pamenepa paja! Ha ha ha ha kkkkk Malawi is indeed a comedy.
When cabinet meets tomorrow just tell Peter Mutharika that so too Malawians are not happy with him,and we are we are planning to aust him any time soon.
What to stop ra
ngongoliwa watani apa iyaah
zopusa bac
Poor malawi24.com. .. are the admins of this page really Malawians. . Ndale zokokerana pansi zitifikisa kuti? Munthu asakambe zocheza eeh… kulepheratu uku..
DPP I really like you like My Life…
Malawi24 is this the way how this joke can be reported?
kunamizana tisamatere. Say exactly what the president said at the function.
the more you hate someone the more you bless him Peter will winwir
Adakunamiza Nyozani agogo ako
Kkkkkkk adamunamiza et
Pwipwipwi dziko lake LA mulanje ndi thyolo akapikisana ndi wandale
Nyozani insult sin
Atolankhani aziphuphu amatero,osamadabwanawo.osa
Kkkk u people olemba zimenezi pachakuti chanu don’t u think kut Vula amabwelesa ndimulungu….shame
Comment loading……..plz wait
aaaah ndilibe nazo ntchito….a malawi tikufa magetsi all day apa isaaa
Iwe machend…ako wamva usamasochelese amalawi,mbuzi iwe eti
Akulu akulu i followed the event. Pliz he jokingly said kuti sanamange mvula bwanji? Komabe achita bwino coz anthu akanavutika! Eeeeeee koma Malawian journalists, please grow up!!!!!
Eti eti? AKuti headline imeneyo kuti iwakomere. Ha ha ha ha
I also followed,,,it was a mare joke,,,a MW24 b serious Pliz,,,mwasowa headline
Mw24 ndi mtedza.
ofoira awa…kaya u journalist wawo adakautengera kuti aaaah
Amalawi 24 Mwayambapo Bozatu Apa, Manyazi Bwanji? Ifollowed All The Function And To Say The Truth Mutharika Said Angolongoliwa Bwanji Simunamange Mvura, But He Was Just Joking Nde Inu Kufuna Makoment Kumeneko?
My lungs please. He is not God.
he he he NgongoliwaGate….alomwe alomwe….viva Mapwiya.Nkhani yabwino imeneyi…big up Malawi24.
he he he NgongoliwaGate….alomwe alomwe….viva Mapwiya.
Mwayambapo nkhani yake ndiye itiyo anakuuzani kuti sanakondwe ndi ngolongoliwayo? eeeeeee, ananena kumuuza ndani mmmmmm koma amalawi ai sitizathekanso chauta azitikhululukila, asatilange tisanaziwe kuipa kwathu azingotikhululukila poti ndife anthu obadwa ndi mnkadzi masiku anthu ngowelengeka tifota ngati duwaa
Munthu ndi ovuta aise ndipo sayamika
ndipo osati masewela iiiiiii mmhuu
Aaaaa!
Ine pheee Kumangomwa Midoli Ena Mukukwiilana!
Kkkkkkkk zikwanje za yehova zasokoneza mwambo.Ukakhala namwali funsila,ukakhala ntchembere umadziwapo kathu.
poor reporting bad reportingyou are mis leading malawians ine siwa dpp koma president sanadane ndi munthu lero.
It was a joke, mabodza bwanji?
Negative Reporting….. It was joke. Kodi a president asachite thabwala???
Napepe Nkholonkholiwa Ndi Katundu
Napepe Nkholonkholiwa Ndi Katundu
Koma ndale za pa Malawi!!? Joke yomweyi inu kupeza nkhani???
Koma atolankhani ena? iiiiii mmmmhhhh
President opepera,dnt mess with Ngolongoliwa he don’t give shit about politics
if u want pipo to remain in this group, stop this madness
Who forced you to comment
And who forced you to comment too???
If you are not happy here log out
log out chan nawe iwe””chamba ett
Just logout and turn off your data you will never see them again talking those nonsense,kkkkkkkkkkkk
Us we are happy u just go out with your ppl
lol, I’m I in the land of Idiots or what?
Lets hope you are just adding some syrup to sweeten your column.
You people are very foolish.Everybody heard his speech and can be able to differenciate between a joke and a rude remark.Was the president angry that time? If its politics ,then its kindergatten type of politics or its rubbish type of it.
Awa nzitsiru bcoz that was a joke koma ma admn a page iyi akulowa ndale zopepera
Kkkkkkk
Joking and not happy, poor headlining
Paja Ngolongoliwa amazotama ndiufiti
Alekeni ndi Alomwe okhaokha awo akudziwana
nosense
It was a joke haters
Kumavetsetsa abale panali zokwiya pamene paja?
APM wagomezga vyawufwiti ndimo wakwiyira amfumu Ngolongoliwa.Mxx
So what? Im also not happy today.
mwasowa cholemba?????
HEs right becoz if it was mulakho wa ayao ,,it cudnt rain coz kapoloma knows how to handle it !!!!kkk
Kkkkkkkkk
Mwanyi adzuru sanunkha kapoloma linasala ndi dzina lokha
Mwayamba kunyoza a yao fe
afana mukusewera ndi dziko kadyani ganjayo.
Kkkk dikilani kwasala mulakho wa atonga ndi atumbuka ndi ma date tikuwuzani?
AYAO NDI DEAL AZIMBOBA !!! kunyoza ayi amatha kuisunga ndithu
hahaha dats my grand pa i know him very wel
anthu amutopera uyu uyu kaya mumati ndani kukhalanl ngati dzina lake limayamba ndi ( P ) komaoizirako ndaiwala kkkkk
Eya uyu… uyu….. ujeni
Bodza ili.How can Mr President be angry with chief Ngolongoliwa ad if he is the one who made the rains to fall?Is it possible for the chief to allow rainfall or not?
Ndibodzadi! anthuwa amafuna kuti wina azioneka wabwino mzawo azikhala oipa!
Kaya muthana konko poti ndinu ANYAPAPI NOKHA NOKHA
muzimvesa nkhani penapake a MALAWI 24,
Aaaaaaa kkkkkk no no no no
Since DPP lost bye-election on 17 oct ,Mr president is not happy.
wakwiya ndinfiti
Mutu Wake Wabalalika Uyu
Did you follow his speech anakwiyayo?
Malawi and its people
Sanati
Atangodzimangilira bolani kkkkkk chipongwe
kkkk
Palibe nkhani apa yoti anthu azionongera nthaw nkumawerenga
You Have Said Yourself That He Said, “Jokingly!” Malawi24, You Are A Joke Too! Please Be Serious!!!!!!
Kkkkkk but these bush journalist.
Kkkkkkk! Mavuto Pa Nyasaland Ambwiye
This nonsense posting must stop.The president crack a joke ,u take it as your headline confusing people.shame on u
asolva
This nonsense posting must stop.The president crack a joke ,u take it as your headline confusing people.shame on u
This is poor Journalism..
Next time it will be rich journalism.kkkkkkkkkkkkkkkkkk
Yea
Zilibe pindu nkhani dzimenedzi
asolva
This nonsense posting must stop.The president crack a joke ,u take it as your headline confusing people.shame on u
dont say the president was joking, definetly he was not happy with the rains. what we all know is that he could not emphasise on the remarks he made bcz its about superstitions ndiye sakananena mokwiya. if u remember it was the same chief who a week ago told the president that the blood sucking issue shud be left in their hands because its about witchcraft,so shud we say he was joking? with all that emphasis?
President was not joking he was indeed unhappy with ngolongoliwa this president like witchcraft too much that’s y he spoke on public n shout to the cheif on y he let the rain to come,if you are offended with this post pluck your eyes .
every word from the mouth of the PRESIDENT need to be officially fruitful not jokes,if he likes jocking then he does nt much in that position and does nt deserve to so called President of Malawi
People without sense of humour eish. Obama used to crack jokes that would leave one in stitches of laughs. APM is only human and not a robot. Not easy being Mnyasa eish
Exaggerating, he was just cracking a joke
(-_- )ndangowelengako
false,
chakwela aķangosankha MIA kukhala running mate waķe kumpoto sitidzamuvotera
Asankha Abraham Banda chabwino
Enafe tidzavota iwe udzakhale bas
Kotakota wopenga iwe go to hell
TIVOTABE kkkkkk
Chakwera basi
Osamuwuza Peter Zimenezi Bwanji?Chakwera Mumamuonelera Bwanji?
kkkk musiyeni inu mzanu wadya chamba
Mbuzi imeneyi yatopa nutukwana Chakwera lero yayamba kumupangira chochita.
Ine ndizamvotera …koma ndine wakumpoto..ife tikufuna ku wina osati kusangalasa munthu
Kaya adah. Ubwino wake Wa Ku mpoto siiwe wekha
Ku Mporo kuli anthu angati go to hello
achewa mumatitukwana kwambiri ife atumbuka pa fb
Kodi ku mpoto Kuli a Bandanso kapena ndiwe mtengwa kumeneko. Uleke kumalimbana ndi Chakwera si size yako uzilimbana ndi mtchona nzakoyo wamva
Iwe ndiye chidempete cha munthu.nkhope ngati chotsekera pa nkhunda. Abraham abraham ndiye chani.
kulibe zoti chakwera angamvotere kuno ngat angamsiye richard msowoya’msamaiwale ndale zapamalawi makape inu
Ine ndi wakumpoto,ndi zavotera chakwera.tikufuna president osati vice
2014 Richard Msowoya was there but u pple voted for DPP and pp so mufuna mutiuze chani apa.
Kodi umangobwebweta za chakwera bwanji? Kkkkkk chambachi
Ife tizavotera chakwera sitiyendera ndale zapa mtundu koma ameme atha kulamula dziko
Wapulika Abraham mundele?
Kungoti anthu andalewa amabakilana taganizani Mia is another crooked polician. Chipani chiti sanachilowe, kuthawa maliro ali mnyumba kukalowa pp lili dyera. Lero MCP akusangala ati apeza munthu wabwino. Eya! Wa bwino kapena crook?
kkkkkk eti asiyeni 2019 awathawa MIA
@chindiwo ngati ndi u cadet ulibe nawo nzelu, kodi Atupele Muluzi ndi wachipani chiti? Nanga Dausi ndi azizake osewa ali mchipani chake chiti kale lija? Ukufuna kundiuza kuti aliyese amene ali mu Dpp sadayambe atakhalapo mchipani china? Munyatu inu kwabasi Mia alindikuthekela kosintha zinthu mdziko muno monga momwe zayambilamu owona udzinjatilira watsala pang’ono
kkkkk mudawinapo liti inu from 1993 until now mpaka Pp chipani choyamba kumene kulowako m’boma
DPP woyeeeeee….!!!
ine ndidzavotela chikwela with or without mia being vp
ine ndidzavotela chikwela with or without mia being vp
Cadet koma abale ine.
Ngakhale 2014 inuyo simudamuvotere ,anthu osintha mawanga inu
Iweyo ndiye amend suzavotera chakwera ndipo nzokaikitsa ngati ndiwe wa Ku mpoto chifukwa ifeyo a kumpotofe tinagwirizana kuti 2019 tidzavotera chakwera.
Abraham Banda Ku nkhotakota nkumpoto eti,?
Atanani kuti akwiyitsanenso apa
aaaaaaa!!,gyz apa nde mwatinamizatu
Mmm miss interpretation
by de way z ds true….???
HE’S ABOUT TO GET ANGRY WITH GOOD TOO KKKKKKK
Useless reporting
Kkkkk ooo
Is this journalism? Kkkkkkk!!!
Ife zisatikhudze
ayee ayee
ANGRY WITH EVERYBODY
TILL HE GETS ANGRY with his own life and die
jkkkkkkkk
and then you STAY forever
AND FOREVER MORE. No anger with any body no credit no one to blame
You will die by the end of November, i prophecies
Then heart attack kkkk
It was better to say no comment rather than to judge him
OK I should die. Iam tired with this world . I know heaven is very very nice.
kkkkkkkkkkkk koma guys
Philimon Brown Kadeluka Mike Yakimu Joseph Chisi Wiseman LG Mphale Jimmy Baxy Avica Bin Bandah Brave Mankhaka Billiat Kunje Tonny J Kalupsa Chikondi Jason Antony Ant-kay Kaundama Chawezi Tembo Austin Mvula Rodwell Wa Fanuel Kapinya Velli Nyirongo
NDIYE?
Chaka chake ndichino baba
WHY?
Ukooooo
kkkk..but how? i thought ngongoliwa was his side chik??Zayambapo..
Akuti y he let the rain falling during his msonkhano which hindered some party gurus to attend. He said Ngolongoliwa should have stopped the rain magically. …kkkk iyeyo ndi Mulunguu?
He was just cracking jokes
Everyone has a right to crack a joke but fools will take it as a story
Tilibe nazo ntchito aaaa zausiru etiii
Kkkkkk
Asatisewerese siife ana …. Tatopatu ife
Kkkkkkk,ziliko koma kumeneko
Kuteleku?? Chabwino