Tiloleni titsilike nkhalango kuti odula azikanika kuziona – ng’anga zapempha
… Asilamu atsutsana nazo Ng’anga mu dziko muno zati zikufuna chilolezo cha boma kuti zithe kutsilika nkhalango za mu dziko muno kuti anthu odula mitengo akhaule. Malinga ndi malipoti a olembankhani, madolo a zitsambawa anena… ...