Mtsogoleri wa chipani cha United Democratic Front (UDF), a Atupele Muluzi ati iwo sanapinyolitse chipanichi kwa a Mutharika.
A Muluzi amene ndi nduna mu boma la a Mutharika anauza anthu ku Ndirande kuti iwo ndi anyamata a ndale zamakono zofuna kumanga dziko.
“Zikatha zisankho, timayenera kuyamba kumanga dziko. Ine ndikugwila ntchito ndi a Mutharika kuti tithandizane kumanga dziko,” anatelo a Muluzi.
A Muluzi anati ndi ndale zachikale zomakokanakokana chifukwa choti munalikhilana mumchenga pa chisankho.
“Dziko likutsogola ndiye machitidwe athu a ndale nawo atsogole, tizigwilila ntchito limodzi,” anatelo iwo.
Pa msonkhano omwewo, a Muluzi analandila a Clement Chiwaya amene anali nduna nthawi ya a tcheya koma anapita kwa amayi.
Kkkkkkkkkkkkkk pinyoli
kkkkkkkkk
CONGRATS ATUPERE YOU KNOW WHAT DON’T AGUE WITH FOOLISH POLITICIAN THEY JUST WANT TO DISCOURAGE YOU
This man is dreaming, in his dream he can see UDF that one bar left. The end of ambitious. Be smart don’t make deal with croocks.
munthu ofuna kukhala President sayenera kukhala munthu osintha mawanga a mayenera kukhala munthu wa nganga muchipanicho,ngati Lucius banda.
Mesa apapa bwanawa ali kuntchto
Kkkkk koma unatani unangobweleketsa eti ai akubwezela bola antcheya awasiye kkkkkk
Mudzakhala otsutsa mpaka liti? With or without Atupere Dpp will be a strongest party. I just lyk Atupere’s political style
MUNTHU OTSATILA ATUPELE NDI WAMISALA ODYA MASANZI
this guys is greedy and doesnt respect his dads party
Yamukulila Mwana uja
Baby wadzuka kutulo kutopa ndikuyamwa mkaka wa DPP wayamba kulira akuyesa a Malawi ndiopusa eti
Amangwetus son
Wakuba ngati bambo wake uyu
Koma aHdha
Kunama wapinyolisa iwe iya nanga tiname kkkkkkkkk
Kodi UDF iripobe?? kkkkkkkkkk
Atupele bakhalani mudzaimabe 20chakuti ok
Palibe chosatha chipaninso mkachani?mxiiiiii
PANGA ZOMWEZO ATUPELE
The Youth have lost trust in you. Come 2019 we will go for Chakwera as he is the only hope for us.
Leave Atupele alone, waponda mwala.
kkkkkkk koma ziliko koma chomwe ndimaziwa abwino sakhalisa
Chipanichi dzuro ndimadalira inu koma apa nwandiwonjeza kungoti phwiiiii osatakataka
Ndimachikonda chipanichi
UDF ndiye yovoterayo,sindingamakhale bizy kuvotera DDP kapena MCP,zachambazo ine ayi
Nanga siwe m jinga nchifukwa chake kape iwe
Mwachita bwino ngati mwatero Mr Ndale zimafunika anthu okhwima mudzeru osangoti ndadzuka lero basi mkuyambapo ndale mmmmmm! Sichoncho ai ndipo takunyadilani. Ingoyambani bizines. Asi kaya kaunjika kaya ya msomba kaya ziwala basi
Chipani #chaku mmawa timadalila inu mwatikhumudwitsa kkkkkkkkkk
NDIYE ATCHEYAWO KUCHITEKETE ACHALUMI ANYAMATA APA TOWN ANAONONGA CHIPANI OKHA
CHIPANI NDI CHA L BANDA CHIMWANA CHA MULUZI DYERA BASI KODI TINDALAMA ADA ATATE ANU TIDATHA KALE.KAPHE NSOMBA KU KIA KAMUZU ADAKUMBA DAMU UPUSA DYERA BASI LUCIOUS BANDA WOYEEE .LUCIOUS
UDF ilipo guys osamakhala ndinkhwidzi kaduka ugogodi ndimnyamata uyu ngati walowa m boma sanalakwise iwalani Neale zamakezama
Komano atupele ndi wa mzeru conz a akuwabela mzeru mwa paspasi
Nde pano ngat uli ndi samba la 4m 4 pita uka join ndale conz deal ndiyomweyo bas
Sazapezekanso anali emwe uja wany wadyera koma ndalama amayisiya mmanja mwa ma vendor, choncho ndalama simasowa.
Unapinyolitsa
Timalimba mtima kuti tidzakhala ndi president wachinyamata koma aaah ndikaona nako kalibe kulimba mtima. Komanso ntakayang’anitsitsa ndapezanso kuti nkadyera kamunthuka. Bola Lazalo kapena Petulo kkkkk
Kape wachabe chabe uyu #nyapapi
You are killing UDF Atupele. It’s a party with history. If you don’t take my advice, it shall be late.
Atupele i no longer trust you, you let us down
Wakaphunzira mabedwe a chimanga Ku Dpp
Kkkkkkk koma kugwira ntchito limodzi thats great idea Atupere keep it up. Za chipani ziyike nthawi yikakwana nyamka kumakapen baxtu man ulibho enawo asakulakwisepo pano.
Atupele the gold digger dont fool us u sold ur power to DPP
Akunjika kae thumba
osamamvela anthu amisala gwilani my choti
Atupele my best politician is playing politics of civilised and knows when to develop or campaign
Atupele moto kuti BUUUUUU ine ndeweniweni wa atupeleyo,nkhani yakuba ndiyina sizikugwilizana ndi atupele ayiiii kambani nkhaniyina ngati mwakhuta khobwe pitani kuchimbizi mukazithandize.ATUPELE NDI DILUUU ana mwachepa.
Niye kt chani nanu. …ogona inu
Atupele ndiwanzeru adaionela patali pano bambo ake akunzunzika ndiye musaiwale kuti zofanana nthenga zimaulukila limodzi kuti mufufuze Atupele sakukhudzidwa ndi zosolola koma akuteteza bambo ake MCP ikalowa m’boma adzapiso komweko koma at the end chipani kutha ngati makatani.
Atupele tinakuonani kuti munagulisa chipani chathu so chimozi mozi ifeso ungatigulise chipanicho apitilize kuchisogolela Lucius banda munthu osatekeseka ayi osasintha sintha mbali.
Lucius ndiotchuka ndikulimba mtima komwe, koma sapanga qualify kukhala president. Pali malamulo okhuzanso maphunzilo amunthu. Ndiyesa Soldier MSCE certificate ya fake ija anamulanda nde mpomuvutilako pang’ono mpando wa upulezidentiwu kuimilila.
Wadyera uyu
2024 Atupele adzakhala mtsogoleri wa dziko. Boma la lero lidacoka mu UDF. Chomwe akugwirizana anthuwa tonse sitikuzizindikira. Palibe munthu amene amafuna kukhala otsutsa ayi!! Atupele sanalakwitse kugwira nchito ndi prof ApM
#udf_inatha_ngati makatani
Ine atati ayima bambo ache Dr Bakili Bakili mluzi, atchair nditha kuzaponya voti yanga,vuto Atupere tidamkonda kwambiri poyamba koma mphamvu zautsogoleri zikuchepa, salankhula, sasusa,ayi komabe Ali booo
Ndiye mwanayo ameneyo sadziwa chomwe akuchita kkkk Tcheya Junior nduna ya Yoswaa
Game hot now for Atupele thus why he’s coming out of cocoon to explain some issues that have left people speculating. Too late to save Jerusalem. It could have been pachiyambi pompaja osati lero ai. Waona chani kamchacha. Hon. Atupele, let me tell you the truth here in case Ken Ndanga gives you false hopes. You may see people flocking to your rallies but they have so many questions that need your answers. UDF will never be a national party again. Some people assume leadership positions in UDF NEC they think you have money or they’ll have contracts they’ll benefit from. Agenda for change was a good approach but has since been scorched by yourself. People out here are very furious. To convince an illiterate villager is not as simple as you may think. The language out here is that Atupele adagulitsa chipani and even if you deny that today, it’ll not convince them. You could have explained UDF plans pachiyambi pompaja osati lero. In 2004, Chakwamba of Mgwirizano coalition after seeing that he has lost elections, he quickly had a press conference in which he informed the nation on a working relationship with UDF under Bingu. With Atupele, it was contrary. Quiet! Now people are about to teach UDF a lesson. Believe me, they’ll.
lesson 4 what udf will vote for Atupere ,& u will vote 4 chakwera anthu a mcp inu you go against for Udf mwauponda
Muthu wazelu amagwila ntchito limozi ndi boma.moti 2024 U D F boma basi.
Anagulitsiratu,,,,relo wawulura
achinyamata amasikuano alibe nzelu bola akale aja atupele muluzi dyela basi
Like father like son
Akuziwana anthu awa pt amadyera limozi ndale zapamalawi umapita komwe ukuona kt kuli kudya
Atupele sanalakwe inunso ngati mukufuna gwilani limozi ndi boma.Pano nanunso pangani chitukuko zotukwanizana ayi.
Achair adachira mankhwala ansana ndi mgwirizano wa udf ndi dpp kkkkk
Timve nao
Mungonena kwachema mgwilizano unali wa awili eni chipani sanakufune ndimaplani mumapanga ndi mpanda mano, waona kuti palibe chake ,kuthandiza chitukuko boma siungachite kulowa mkati Mpanda mano adanenetsa msonkhano waku Mangochi uja kuti kwatsala kukhazika Mbendera imodzi , Blue Yellow kwavutako mongotero kwavuta kukupasilani boma
pumbwa uyu sangadzatsogolere dziko ayi Kusamva komwe ankapanga bambo ake ndinkona anawalanda dziko anzao omwe poyamba ankaoneka ngati ogotomala aka
Komati malume pamenepo wanena mau muludzi analandudwa dziko dzuwa lisuswa mtengo
ukungolankhula iwe supita Ku convention iwe oimbayo sangaime pa ATUPERE
Ife tipitiriza kumukonda ATUPERE sitingavere inu a MCP mwanya nawo powona kuti ATUPERE akugwira ntchito ndi boma mwauoponda ATUPERE sangagwire ntchito ndi mcp
Nkhani ya M CP yachoka pati, galu iwe anakuuza kuti MCP ikufuna Atupele ndani
kkkkk Atupele akukupwetekani kumene inu a kongelesi munya akugwira ntchito ndiboma kuphunzira kayendetsedwe ka boma mawa tikamutsankha kukhala president sadzavutika
Kkkkkkkk!! Ndikukaika ngati a MCP angafune Atupele,coz sangakwanitse kusintha zinthu.Its shameful to see Atupele working with a failing gvt of Proffesor,Kkkkkkkk!! Atupele is not a brave politician to say no wherever it is needed
Wakhungu akuphunzitsidwa ndi wakhungu mzake.
robert ndiwe wamisala woyenda mbulanda stupid pa Atupere sudzafikapo udzingolira ndi umphawi
DPP woye UDF woye
Mudzakhala otsutsa mpaka liti??
Ndi bomalo akupanga chani cholomela udf supporters mmmm udf is down I just lost ma tym to vote the nonses party udf
KKKKKKKK OKAY BAMBO ATUPELE MULUZI, KOMABE musaiwale KUTI simukulankhula ndi Ana & nsonkhanowo mumapanga masana sikuti unali usiku, Nde musakhale ngati mukuuza ana anu
Boza ili mukugwira nchito zokubazo?
ZILIKO NKULINGA UTATOSA
Za ana safula njuchi uyu uyu uyu aaa
Koma tikumbuka kuti ma sapota a UDF ndi DPP adayamba kukangana ku Mangochi zotsatira za chisankho zisadathe kuulutsa? Kodi UDF ikadakana kugwira ntchito ndi boma, dzikoli tikanakhala pa mtendere chonchi? Izi ndiye ndale zoti tiphunzitse aMalawi. Ndale zokhobolana zija ndiye zidatichedwetsa chitukuko.
Yaaaaa apa nde ndamunvesesa sopano adawa amathadi awa alamule basi
Agama Mumatiyimila Kwambiri Tiri Pambuyo Panu Agama Ine Bare Wanu 0882889061
Poti alepherera limodzi kuyendetsa Dziko
Anthu Opusa Munapanga Bwanji Ndinanena Kuti Nkansa Ndimupasa Galimoto Ineeee!! NDINANENA KUTI Nyimbo Za Mkansa Zimakoma Kumvela Mugalimotooooo!!! Amufoilisa. Ndimadolo Yawa Samalani
Muluzi songolo palibe apa zipangani za Dpp zo
Ndale zaku Malawi zadyela basi ngati akaphathikana ndi chipani cholamula iye pamene ali otsutsa akaona cholakwika akwanitsa bwanji kutsutsa? Ndale Atupele wachepa nazo sangakwanitse kutilamulila ameneyi.
Mwa inu mulibe utsogoleri.
UDF 2030 Boma
THAWI ZINA NDIKAKUMBUKA ANACHITA BAKILI MULUZI kuchitila chipani anthu amakonda UDF khaza
We are not 2years Old
Bwanji Zaka Zonsezi Sanayankhule Akuyankhulapano Cholinga Atigodomalise
Atupele what you are doing in my view may be construed to be politics of selfishness. Where kugwira ntchito nfi boma only mean you and indee you alone must be a cabinet minister. How would you let the contribution of others in UDF count too?
Mwayamba Kubwela Poyela Sopanotu Mwayamba Kutifuna , Sir Lucius Banda Moto Kuti BUUUUUUU
Amayankhula mchichewamoo
You learn through mistakes….. Zanus izo baipisani mbili yadziko lanthu labwinoli mbuzi za anthu inu muuzane mitu kukula ng@ nyumba yopanda plan…
NDALE za ku Malawi, dziko la anthu osamvetsetseka. 2014 kunali ukulu ukulu ndi ungono ungono. Anthu anavotera ukulu ukulu. Lero Atupele akuthandiza ukulu ukulu, ndi izi mukuti akulakwitsa ,kodi iyeyu kuti akhale okhoza atani? Manyasa tell him. Atani?
NDIZOWONA SANAPINYOLITSE CHIPANI AI, MAU AMENEWA AMATULUKA KUKAMWA KONUNKHA KOSACHAPA NDI MSWACHI. AKUTI IWOWO NGATI ANADANA NDI CHIPANI CHOLAMULA NDIYE NAYE MTSOGOLELI WA UDF NAYE ADANE NACHO MAGANIZO OPUSA KWAMBILI. NGATI MWAGONJA PA CHISANKHO KUMAVOMELEZA KUGONJA NDIKULITHANDIZA BOMA LAWINALO PODIKILA ZAKA ZINA 5, MULIKIILE DZIKO NGATI MUNACHITA LOBWELEKA BWANJI?? A CHEIR ANANENAPO MAU AKUTI AMALAWI TAKWELA BOAT LIMODZI TIKACHITA MA VUVU TOSE TIMILA NDIYE ANDALE AKUMALAWI AMACHITA NGATI DZIKO LA MALAWI NDILOBWELEKA.
Koma nkamakaninsotu osangovomela kuti zinachitika asaaaa kkkk
ONYOZA NYOZANI KOMA INE NDALE ZA ATUPELE ZIMANDIGWIRA MTIMA NDIPO ENANU MUTAPHUDZIRA NDALE ZA ATUPELE MALAWI AKHODZA KUKHALA PABWINO
Ndalama idakukomera ngat bambo ako atupele, chipani kugulitsidwa ngat malonda a chamba pa malawi.
Ngati mumamukonda bwanji nsimunamuvotele 2014 musiyeni apange zake
Palibe chanzeru apa.akuononga chipani cha UDF mmalo mokonza
Chipani cha UDF sichayinu nokha baba mwasata ndalama kuwasiya okusatilani pa mbalambanda dyela bansi tangosiyani udindowo ife tisankha wina sitinakusankhileni kuti timakuwopani ayi kapena ndalama ayinso komatimaganiza kuti mutinthandiza koma ayi
Thandizolake umafuna akupangileni chani bambo???
Tionane 2019 kkk
If you cant beat them join them and see their weaknesses so that you know how to deal with them later.
None ov my busness bola I’m alive GOD is my President
Atupele is smart. He is a nationalist! Osati pakuti ali ndi chipani ndiye kuti asagwire ntchito ndi boma ayi.
PASAVUTE, pinyoro sikugulisa ayi, kumakhala kuti iwe mwiniwache uli busy ndi zina zake, nde timati anzanga bagwirani apa ine ndipange izo
anapangisa pinyoro chipani kuteteza bambo ake kuti asamangidwe murandu ujau oro pano vuto ra msana uja rinantha kkkkkklkkkkkk u!!!!!!!!!
ine ndekha ndimakukonda kwambiri kuri kose ungapite vote yanga ndiyako basi
Kkkkkkk
Vomelezani a Muluzi, you weakened the party single handedly, it is no longer the same UDF we used to know, it was sold to the highest bidder (DPP) long time ago no wonder it’s not even an official opposition in parly.
nde akumunamiza ndan
wayambapo2 akhale komko bx ife sikuzavotaxo ku cipani ciliconse
Akamaz
tapanganiza nzeru zioneke maasewela basi ife tatopa ndi zpusa bamboo ako sanapange zimene iwe ukuchitaazi ganizaa bwino
Mesa bambo wake ndamene anapinyolisa UDF mwana atani?
Aaaa Uyu Nde Wamisala
Bambowa ife tinawakonda ndi mtima wonse koma mmmmm ayi ndithu nzeru alibe
Palibe nkhani apa
Atsogoleri ofuna kumanga dziko adzitero adzilekanitsa nthawi yopanga ndale ndi yomanga dziko 2024 Atupele muluzi ndi boma basi udekhe after moya ndj iwe basi zikumunyasa adzilume kunsana
Hahaha dreaming ..
chipani chinatha kale ichi kkkkkk musandisekese
Inu mumafuna aime paokha cholinga choti mcp w
Iwine mwauwuuponda udf/ddp same tress
Hahahaha Hahahaha kulota likupsa mtengo ndithu.
mumafuna Atupele adzipanga zombwambwana nga chakwera?ufumu umapita kwa anthu okhawo odekha ndi odzichepetsa Atupele 2024 bomaaaaaaaaaaaaaaaa! !!!!!!!!
u d f idapita ndi mwiniwake bakili political engineer madala madala.paja amati galu wa mfumu ndi mfumu ya a galu
Mwana Boma ilo
Pasadi Katole umaganiza wava? ndale zanji zosavomeleza mukaluza makatumba wali-wali ngati mukulamula ndinu bwanji? what kind of people are you? first mcp fulishes.
Mbewa iyo yokonda mtedza ( money ). Adzavoteredwa ndi. Mbewa zinzake . wanzeru sangavotere munthu wosakha zikika bola Lucias Banda
Bulutu, ngati ukumanga dziko bwanji unangokhala chete Chaponda atatibera chimanga. CHAKWERA NDI DEAL
Ngati chakwera adanyoza mulungu pothawa ntchito yake( yona) kuli bwanji anthu ife,ng’ona zija sizibwerara? Yemwe anaona ntchito za MCP pamene imkalanga anthu sangabwererenso asinthe chipanicho dzina mwina tizavola ichocho.Koma MCP mmmmm
Musaiwale Anthu Aja Anafa Pazioneselo 2011 Aja,pamalaw Palibe Chipan Chabwino.Tien Tingosankha Yesu Samakhumudwisaamapasa Mtendele Wamumtima
Kodi atupele ndi pitala mukunena apawa amasewera timu yanji
Atupele anagulitsa chipani ku dpp phindu lake amalipeza ndi iyeyo ndi bambo ake
Akuteteza bambo ake kuti asakwidzingidwe paja nawonso ndi tsizinantole
Phindu lenileni kwa munthu waku mudzi palibepo
amalaw chot mudziwe chakwela sangawine upresident adathawa ntchto yamulungu kutsata za dziko kumalankhula zosemphana ndi mau amulungu ameneyu mulungu anakwiya naye thats y sizikumuyendela
Kkkkk paka kupinyolinsa
Timawaona ngati ali ndi mzeru monga wachinyamata koma mmmm alibe mzeru ndi adyera, ozikonda apereka chipani chikulukulu ndithu
Kuteteza mbala ija idaba ndalama za boma zokwana K1.7 billion. He has disappointed 900000 people who voted for him, 2019 adzamuvotere ndi makolo ndi abale ake basi, munthu wadyera, ine abweze voti yanga bakha ameneyu.
Atupere ndikatundu omanga ndi mawaya _Adakalhala kuti ndiwawamba aaaaa sibwezi anthu akulimbana naye ndiyetu simunati chifukwa ayamba kutikita iweyo amene ukudzinamizawe kuti ungakaime ndi Hon Atupere ku convetion we ndipo ukagwa mochititsa manyazi chifukwa mavoti ako ndi 34 kenaka tikamalizirakulu wako amene akumakupatsa ma tshirt ankhuku pasanayo ndi pamene mudzamudziwe Atupere mumangomuona kufatsa etiiii
Nawenso umbulu ukuchulikira oba ndalama za boma sukuwadziwa amatthawa dziko lawo ukufuna kunamiza ndani amene simalawiyo
Mbuli ndiimene sikudziwa kapena kuvomeleza kuti Bakili Muluzi adaba ndalama za boma, ngakhale mwana wa ku primary akhoza kukupambanani kuzitsata zinthu. Koma umbulidi ndi matenda ndithu.
Uuuh Pinyolo Imeneyo
achawa a dyela awa dyela la ku mntundu tatewake ndiye engine ya dyela
nanunso nde out of comment..the issue is amatter of political not mitundu…kungozolowela moyo watsango basi…shame on baba
Kumanena nkhani mmene ili osati zamitundu.NDIWAKUTI KODI IWE?
Choka what is wrong with achawa it’s this topic about chawa people muli ndi bvuto bambo inu why do you hate chawa so much?
UDF yatha ngati makatani, a chair woyeeeeeeeeeeeee!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!