Ndi kutheka onyoza amawanena a Chakwera kuti ndi Yona othawa ulaliki koma mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika ati a Chakwera ndi Yudasi basi okonda ndalama.
A Mutharika dzulo ananyogodola a Chakwera kuti apinyolitsa chipani cha Kongeresi kwa a Sidik Mia. Ati pa mtengo wa K200 miliyoni.
“Pofika 2019, patsala DPP yokha basi,” anatelo a Mutharika pa msonkhano omwe anachititsa pa Biwi mu mzinda wa Lilongwe.
“PP ndi ija mwini wake anathawa ija, ikakhala Kongeresi ayigulitsa dzana lomweli ili ku Chikhwawa kwa mkulu wina wa malonda,” anatero a Mutharika uku owatsatila akuomba m’manja.
Ngakhale sanatchule a Mia, a Mutharika amaoneka kuti akunena kuti Kongeresi yagulidwa ndi a Mia amene alowa chipanichi loweruka kwa Ngabu.
“Ikafika 2019, tikunyenyaninyenyaninso,” anatelo mozitamandila a Mutharika.
Dzulo kanali koyamba kuti a Mutharika athililepo ndemanga pa kupita kwa a Mia ku chipani chotsutsa.
Pa msonkhano omwewo a Mutharika adanenetsa kuti Boma lawo lipita chitsogolo ndi ndondomeko yopatutsa madzi mu nyanja ya Malawi kuti azipita ku Lilongwe.
Ndondomeko imeneyi yakhala ikukaikilidwa ndi a mabungwe komanso anthu ena ati kamba ikuoneka ya katangale.
Aziti tizabelaso forsek ngati anawina anthu anawavotela
more fire chakwera
Tikamawerenga Buku Lomwe Agwitsa ntchitolo, Timamva kuti Davite Mwa Wa Banja la jese Anasankhidwa Kukhala Mfumu Munthu amene Anali koweta Nkhosa,mzotheka Achakwera 2019.
Nobody knows tomorrow and God’s plan is not man’s plan..lets wait and see who will win
Onyenyedwa saziwika aliyense akupalasila kudoko kuti akawoleke osatha mau
DPP ndi boma ilo
Chakwera akutenga boma 2019 akunama ameneyo.
mukazaona munthu akukamba zaneba wake ingoziwani kt amamuopa kwambiri,,,afro barometre unapangilanji zimenezi ona nkhalamba zikusowa mtendere pano
Linda madzi apite ndipo udziti ndadara!!
Onsewa Nd Akuluku Osawanikha Vot.
Hehehehe
Zazjiii
Mukungonenadi mwanayu Yemwe adapinyoletsa Kwa inu chipani chake.
Koma anthu ena, mukunamizana kuti yona alimba, ali m’mimba yansombatu akukamutayila ku chuch kwake, ndichifukwa mcp muli mabvuto adzaoneni chifukwa mtsogoleli kulibe anamezedwa ndi chinsomba, zandale sazitha kwatsala kuti akafika ku nenevi akapepese mudzaona pofika 2019
Ife Tangoyambapo Iwo Kuyamba Kunjenjemera Paka Malungo Nanga Tikalowera Ku Ophedwa Ndi Mwala Wabible Uja Zitha Bwa
koma gaez mwakhutakhuta numakamba za DPP siboma koma manyaka
4 v first time mcp izakhala pa namba 3 in 2019..ndanenera2 et mukazamavotera chgawenga chakwera muzazwa kut panamba 3 bas am not jokng am serious
God is not Mutharika nor DPP, come 2019 only God knows. Those who are pro dpp are devils agents, corrupt figures, evil cannisters. A normal thinking and God fearing human being cannot go for dpp. Zachulukaso paforum iyi kukhalira kumbuyo dpp ndi mbuli, a gong’oli and boot leakers, useless cowards who cannot talk sense
Only God knows who ll sit in 2019
sangawinetso ameneyo waononga dziko ngati mugambe kape
Dpp could win if msowoya joins them.The coming of mia means alot to the political landscape of the country.Peter will get msowoya then North malawi will b blue kkkkkkk
Kkkkk koma yah 2019 kuvuta
Malawi si south africa sir
Koma Inu Achakwera Ndiye Boma 2o19 Mwaiwalanso Banja Lonyonzana Limakhala Nthawi Yayitali Dpp Yatithopetsa Ndikhalidwe Lake, Education , For Secondary Xool Mkuganiza Kuti Mwana Kuchokera Form 1 Up To Form4 To Write Maneb.
more fire
I love money.zinanzo zinatipita Ku mazereeeeeeeeee fuck u all u love it
Chakera ndi big just wait alittle
Mcp Samala Ife A Dpp Ndilipo Ndipo Ma Cardet Ena Mwiwo Ndife Tikuswan 2019 Tinatopa Ife Ndiulamulilo Wanu Mumatiika Mu Drum Ya Chitez+gonji+phulusa Nkhani Yake Yongotchula Bakha Wanu Uja Kamuzu Iyaaa Ufulu Kwaufulu Pano Iyaaaa
Pangani zanu ku DPP tisiyeni ife MCP tikudziwa chomwe tikupanga
USSD code running……
What is wrong Mr President?
Mmmm ayudasi ndi ambiri apa musiyeni chakwerayo agwape inu mwatitopesa
KOMA NKUNYENYEKA DALA, LINALI KALE LOMWELO!
People Should Have To This:
The National Registration That You Are Doing Is What It Gives More Powers To The Dpp Members.
Anthu They Never Know Kuti Kalembera Yemwe Mukuchitayo You Are Voting That Time There4 Palibe Chowalepheretsa Awa Akubawa(dpp Theafs/robbers)kumayankhula Molimba Mtima Like That Saying #coming 2019 Mcp Inyenyedwanso.Enanso Ma Page Ngati Awawa Malawi24 They’re Involved In That Foolish Encouragement Kwa Anthu Instead Of Talking About Crisis Ya Frames Mwina Ambiri They Can Take Reaction On That.
#Synet ukafunse Zuma ampangila zionetselo katatu kuti atule udindo amulephela mpando waprezident Chakwela ndi Yonadi 2019 DPP ndi Boma basi kumalawiko sindikuona chipani chomwe chikhoza kupikisana ndi DPP
AAAAA! kaya koma tikungotaya nthawi ndi kumanyozana tokha-tokha anzathuwa ndiolemela kale.Tikati tiwone pa mitu yakayendesedwe kaboma achakwera nawonso alikale m,boma pano.
Kodi kachimutuyu alive manyazi folena uyu kakaka ukazaluza uzathawa iwe hehehe sindinaone munthu wamkulu buzy ndi ana osamayankhula zachitukuko bwanji buzy kunyoza tikayamba kubweza moto muli tikunyoza boma zachamba bax simutitha apa
MBAVA YA DZIKO,NOTHING HAPPEN IN UR RULING SORRY
Galu wamunthu angazakuvotele ndi agalu amzako bwampini iwe
Bwana sionse omwe akukondwela ndi ulamulilo wanu ngati mwatopa asiyileni azanu coz cholinga cha inu mukufuna mungoona dziko la malawi basi
Nonse Ndinu Makanda Pandale,munena Zaena mupange zanu,mukunyoza mtunda wina,madolo anuwo 2014 anali kut?kuyendesa,nkhonde,mtumbuka,mshona,yao,mchewa,ngoni,mang’anja,bathwa,nsena,musayese chophweka,mukapambana nanuso muzadedwa aliyense afuna tribe yawo ilamulire zomwe ndi null set,dziko si mbumba yakwanu muzingolima fodyayo nchikulire
ayi sitikumufunaso muthalikayo apapa akuyenera kupitaso ku opposition basi watikwana akubowaso
wamwa midoli uyu!
Its rediculous to tell people that u will win the election despite all blunders u r making while u r in the same government.Mr President u r a professor through education but look at what is happenin in education sector.For instance how on earth can a primary school teacher stay at college for five yrs in the name of producing quality teachers?a secondary student sitting for examz after 3yrs are you expecting that kid to pass it?This current syllabus is full of challenges.Malawians have eyes and ears.
Dats fact iiiiiih dis government mmmmh
vto ndlakt amalawi tmakhulupirir kt munthu akaphuzra kwmbir bdy ali nd zeru zautsogoleri.Ati anal kw america tmuvotere mchfkw chke adabwer kzaba basi.Amalwi munth akphuzr ndalam zmwe amalandl patchto ymwe akgwr zmakhl zake osat zadzko ndy pot peter anaphuzr mmaona ngt ndalam zake azayndetser dzko kkkk.wethr u lyk it or not bt chakwera is leading this country in from 2019 aft elections.
Vote 4 DPP Again!
kkkkkk those who are suporting chakwera their names are Identical kkkkkk of the same r from kkkkkk zodo
Dziko Kuyaluka Khan Mmisonkhano Ingokhala ya Chakwela. Abc Radio Zokhazokhazo Tingat Abc Ndiza Dpp? Msowoya Sangakujoinen Ndimunthu Ozindikila
munthu ukamakula zoyankhula pena zimakhala zopanda sense, ngskhakebena aombere mmanja, amaombera uchitsiruwo
Vaccancy announcement tenable at state house,vacant post HEAD OF STATE (PRESIDENT)anyone can apply male or female of malawi origin closing date of receiving applications is 19 may 2o19, method of application by hand to your nearest district comissioner .
n’dala wabodza iwe ukuona ngati udzafikako 2019 et
Kkkk Mungokangana Owina Tili Pheee #UDF 2019 ukutengansoo believe me!
madala omweo 2019 Dpp woyeeeeee!!!!!!!!!
Kwako kwatha kulu
palibe munthu amene azapange zosangalasa aliyense m’dziko muno.
Malawi wadzudzika nikale chonde Ambuye tichotsereni mnthuyu asadzawinenso chonde Ambuye Mulungu pitala Bwampini Chikutumbwe Matchona nzika yakunjayi ngakhale mwana wake sakudziwa dziko lawo achoke mnthuyu 2019
Khalidwe laanthu ochimwa ndikunyoza azawo basi,komanso munthu amene alibe cholowa ndizinthu za mulungu nthawi zonse amangodziwona iye okhonza pamene anthu ena onse amakhala olakwa.ntchito kuloza anzao olakwa tsiku lina mudzaona kuti Mulungu samapangana ndi munthu poika munthu pampando.inu amene mudawina sinzeru zanu koma kuti Mulungu adalola kuti mutsogolele mwanthawi yanu,chinamuvute ndichani kukuchotsani ndikuika munthu amene simukumuyembekezera,popeza mau amati Mulungu amapha komanso kupereka moyo,iye amatsitsa ndikukweza munthu pampando!1samuel 2:6.
MCP can not win elections bcoz they dont hv structers at grassroot
Kumuopa Mia kumeneko,kambani za reshuffle yopanda phindu liri lonse ku ntundu wa malawi.
Ndipo Anyani Amenewa A Mcp Wa Tikwanyenyadi 2019 Tilimodzi Ine Olo Atandithila Acid Mkamwa Sindingavotele Mcp
Akatele Pitara Aku Njenjemela Aziwona Tingot Pheeee! Tiwone
Not dis time peter!!! Are you saying dis as a loser?
INE VOTE YANGA MUZATENGE YA 2012 cos ndatalikila
Za utsilu Ku votela DPP
Tadzuzidwa mokwana akapume basi
MCP❌ DPP❌
Siza vota 2019
1994
1:UDF
2:MCP
1999
1:UDF
2:MCP
2004
1:UDF
2:MCP (Mosogozedwa Malemu Bingu Muthalika ndye Chfkwa Chot #BAKILI_MULUZ Amkachuluka Mzeru Nd Anamuthamangitsa Ndpo Nthawi Yomwe #MUNTHALIKA Anayambitsa Chipani Cha #DPP
2009
1:DPP
2:MCP
2014
1:DPP
2:MCP
Inu A MCP Muzngonyadra Kamba Kot Mumakhala Pa #Number2 Pa Chisankho Chnachilichonse…
#DPP_2019_BOMAAAAAAAAAA!!!!!!!!!!!!!!!!!
The truth is being told in our own eyes, the Ngabu rally has shaken them up!! The table turns , lets wait n see. Cant fool them all the time remember.They are looking for change .
kodi malawi akumutenga ngat kamuzu stadium popangira mpikisano eti?
Kkkkkkkkkk tamusiyani Petulo uyu mutu wake sukugwira chifukwa wakhala akamunyengerera Sidiki koma adamukana kwamtuwagalu kuwonjezera apo ati kusankha Atupele kukhala nduna yaza health chosecho sanaphuzireko college yokhudzana ndi health,ndithu wasokonekera apite ku Zomba akachire kuja kwa amisalah
Ukat ndikunyenyani iwe ukuona ngat azakupase mavote ndindan? Tapanga zimenezo uone. Yemwe ukufuna umunyenye lero mmawa ndiyemwe adzatsitse makatan mnyumba mwako, adzatulutse mpando, adzakoleze moto panja panyumba yako iwe utatsinzina. Teyenazo!
Zoonad nkhalamba ikamakula imachepa nzeru zaziiiiii 2019 uzawinila kutiko? Mxiilll
Koma zinazi abare
Na Gulu ili lonse ndiloduka mitu kuyambira mtsogoler wawoyo amunyenya ndan popeza anthu mavote tidaponya kale mmitima mwathu 2019MCPboma!!!!! Nkhalamba ku state house ife ay1 takana
Na Gulu ili lonse ndiloduka mitu kuyambira mtsogoler wawoyo amunyenya ndan popeza anthu mavote tidaponya kale mmitima mwathu 2019MCPboma!!!!! Nkhalamba ku state house ife ay1 takana
kkkkkkk mantha abwana mukudziwilatu kuti 2019 palibe chanu.
Na Gulu ili lonse ndiloduka mitu kuyambira mtsogoler wawoyo amunyenya ndan popeza anthu mavote tidaponya kale mmitima mwathu 2019MCPboma!!!!! Nkhalamba ku state house ife ay1 takana
Na Gulu ili lonse ndiloduka mitu kuyambira mtsogoler wawoyo amunyenya ndan popeza anthu mavote tidaponya kale mmitima mwathu 2019MCPboma!!!!! Nkhalamba ku state house ife ay1 takana
Na Gulu ili lonse ndiloduka mitu kuyambira mtsogoler wawoyo amunyenya ndan popeza anthu mavote tidaponya kale mmitima mwathu 2019MCPboma!!!!! Nkhalamba ku state house ife ay1 takana
Gulu ilili lonse ndiloduka mutu kuyambira mtsogoler wawoyo amunyenya ndan popeza anthu mavote tidaponya kale mmitima mwathu 2019MCPboma!!!!!
Gulu ilili lonse ndiloduka mutu kuyambira mtsogoler wawoyo amunyenya ndan popeza anthu mavote tidaponya kale mmitima mwathu 2019MCPboma!!!!!
Ndi nkhosa yotayika ija ibwezeleni ku khola paja ikasowa zizake imakhala kuti yayamba misala mkhululukileni nkuluy nd misala ndthu agwade pasi asale kudya ziwanda zichoke DPP woyeeeeeee!!
DPP BOMA MPAKA 2024 woooooo
kkkkkkkkkk , ndale zapa Malawi
que sera sera in 2019, let us wait for 2019
Kkkkkkkk Pitalayu mutu wake sukugwira…. Ndaonera zomwe ewyankhula dzulo….. I think Ngabu rally is shaking these guys and it’s clear
You are just talking as children bros and sistaz.Can mcp make it, realy? with tambala wakuda and kwacha slogan? am afraid.Is Mia more powerful than Chakuamba who failed to kwachalise southern region? Let us give professional political statistics to the masses.
defeated and disgruntled DPP
Big up APM…..BOMAAAAAAAAAAAAAAAAAAA
Aliyense ali ndi ufulu olowa chipani chomwe akufuna palibe za pinyolo apa. Akamati democracy ndi chani abale.
Adpp Tatopa Nanu Mwatikwana
Big man kuthoka ngamo Sam Pochettino Mpindamalata
mwakura baba pumani mamo mwina akamere kuholidy ret chakwera be chakwera
hahahaha
We will see as 2019 is nearer
pa kholo pako iwee wasaukisa ziko
Kkkkkkkkkkkkkk
DPP inali kale ma striker olamulila ndinzimayi
Kololiliko!!! Kwachaaa!!!
Guyz mantha ayambila patali munthu akakhwima nzeru zimachepa apa DPP idakalamba 77years mtsogoleli atsogolela bwanj? vote yanga ngat akuifuna andipatse 88800000 chifukwa wakalamba uyu.
bwinotu bwino Mulungu akumva zonsezi….
Ine comment yanga ndi yoti…God chooses leaders but his ways are not our ways.Lets wait until 2019
Ukunama mphwanga
Z Only God Who Choose Leaders Not On Mouth And When Jesus Says Yes Who Can Yes No
Asiyeni bwana kusosoka kwa MCP kumeneko satana amutikita chakwera dyera
Hahaha pitala adapanga xpire
Nanga Apulesidenti akunama kuti othawa ulaliki?,kodi mungakhulupilire bwanji munthu osiya zaCHAUTA kuyamba za ndale kuti angakhaledi mtsogoleri wabwino?.Ziwani izi:maonekedwe anthu ndiomwe amaonetsa makhalidwe komanso makhalidwe athu ndiomwe amaonetsa tsogolo lathu.
It’s only God who is the best judge.
Utumiki si ku church kokha kapena ulaliki
Fredo anthu sadziwa kk
you mean chakwera sapita kuchurch? umbuli siwabwinodi km
Religion & Politics R The 2 Sides Of The Same Coin.U May Wish 2 Ask Why?Coz Pple Who save God In Different Religions Are The Same Pple Who Found, Form,join,participate In Different Political Parties Depending On Difrent Degrees Of Doing Things.
Nkhalamba Yawoyo Sitidzayivotelanso Ife, Siyiyankhulanso Zomveka Kukhala Mkamwa Muli Miyala………2019 Ulendo Wakumudzi Kwawo Ameneyo
Akunena atupele ndi udf
No more DPP…come 2019…mark my word…!
Chakwera ndiudasi mpata alibe ameneyu mulungu amulange.go back were you were that’s it to you Dr chakwera
Ine m’modzi mwa anthu akumudzi koma sindi kuwona phindu mwabwanawa asathe mau
Bola yudasi anapulumutsa akhristu ku machimo
m.c.p 2019.boma amalawi muzakhala chocho mpaka liti anthu ozaganiza inu mumakhala ngati munabadwa ka mbuzi bwanji mwanyela pososa aDPP .muonaso mwanya nazoni ..just look another countrys in Africa alipheee kandalama kao kamphanvu osati panyasaland mmmmmm.munabadwa ku anthu or bwanji ..aaaaaaa oho nazoni .2019MCP bomaaaaaa
MCP moto kuti buuuuuuuuuuu,wina alira,Lucius chokangoyimba pa nsonkhano wa MCP anthu m’mimba kutsekuka kuyesa kuti mwana wa dziko walowa chipani choyenera, lets wait and see 2019
Plz Mr Presdent first you must check the facts in your statement before you open up your mouth…that’s not apoint.
Kusonyeza kuti iyeyu akuziika mgulu lowina? Kkkkkkkkkk moti sakuona komwe ma voti akupita ndiye kuti? Bp ikaza shooter tizakaika kundata farm osadanda mwene
Kicks of adying horse. Instead of minding your own business of hw you cn transform yr corrupt party, you’re busy talking abt chakwera. Hmmmm!!!! Inu mwagwa kale, jst wait and see!!!!!
This is his business my brother and that’s what politics is all about, do you expect him to applause the opposition? The fact is, it’s none of your business neither mine. Let them insult each other!!!!!!
Fact!!!! You are right, Leyton.
Kuchita Matha Kumeneku, Wayamba Kuyataya Mtsogoleli Pagulu Ngat Apa, Liliratuni A Dpp Boma Lakukanikani Ife Mcp Boma Wina Ufune, Usafune Unyenyedwa Ndiwe Wa Dpp .2019 Subelanso , Mcp Moto Kut Buuuuu !!!, Voicing Out Views Freedom Of Expressions.
Peter, nzelu zatha ,,,,,,,,,,,akulila
Awatu kunyenya amakudziwa osaiwala pajaso Bingu anadzinyenya ekha kkkkkkk ife tilipheeee kudikira 2019.DPP chipani chobela a Malawi
Then we have too many Yudases mr Apm. One of them being Atupele who is 100% in your armpit.
Kkkkk
Amanenadi zoona kuti munthu ukakalamba umabweleladi ku mwana nanga siizi tikuzionazi basi tingowakhululukira angtichimwise only Jehova knows
Ngati votiyo tikaponyera kunyumba kwake , nkhalambayo iza wina koma ngati ndimomwe zimakhalira nthawi zonse.mmmmmmm , nkhalambayo yizakumbukaso komwe iyachokera.
Apita Asiyeni Atilamulire Chaka Choponya Voti Chafika Kale
palibe muzanyenya ndani muzanyenyeka nokha mukutenga ziko ngati lambuyanu .kusogolo kuno azatha anthu nmalawi kumangopita kwa eni ..2019 alukamwaso phala pitara .kkkkkkll
Kkkkkkkkk
Building the Castle in the air…..wat will happen in 2019 none of DPP supporter will believe it mudzavinidwa chindimba
I feel good exile
Shuwaditu Bwana Peter tinyenya nyenya ife tambala wa black Lazarus wawuphawi abwelele ku nyumba ya Mulungu, kulira ndikosayamba ku MCP atibela atibela mudzingolira ndipo mudzaliranso 2019.
Lets wait and SEE our beloved God cannot let us cry everyday MR CHAKWERA THE ONLY HOPE FOR MALAWIANS
Zoonadi Achakwera Ndi Yona Basi Komabe Nthawi Iliyonse Akapezeka Ku Ninevi Mulungu Sathawika Ayi
Kkkkkkkk
PETULOYI ASAGANIZE ZOTI 2019 AZAWINA AMENEYI ,AKUNAMATU,SIMANTHA AMENE AKUMPANGISA.AKUONA NGATI AMNZAKE ANGATUTUMUKE?
Nde mwati anavala jakete ngati kanda Bongo Man?
Hahaha ngakhale ndabwera mochedwa , ngati simukuopa chakwera bwanji mwayamba kale campaign? Ino sinthawi ya campaign, khala pansi nkhalamba iwe wachabechabe..tidzavota ndife anthu osati iweyo..M.C.P ndi boma Kale win afune or asafune.
umakwana
hahahahaha ndaseka ine Muuze azwletu si ufumu uwu asiyre ena ndpo amandkwana aaaaaah
PETULOYI ASAGANIZE ZOTI 2019 AZAWINA AMENEYI ,AKUNAMATU,SIMANTHA AMENE AKUMPANGISA.AKUONA NGATI AMNZAKE ANGATUTUMUKE?
DPP will die come 2019 believe me or not. I was a strong member of DPP but with what it has done it has disgraced me.Education yawonongekelatu boladi a Chair analinso bho
fact
Kwavuta Kuma Polititians!
#DPP_IS_AFRAID_OF_CHAKWERA_AND_MIA’S_INCLUSIVENESS_AMID_2019_POLLS_DPP_IS_COMPLETELY_SHAKEN_KKKKKK
wanena bwino ase ngat mulungu ndi wa DPP adzawinadi a nyapapiwa
Malawi yakwera chakwera DPP ikwera MCP wina afune asafuna 2019 Boma!!!!! kwacha! kwachaaaaaa
Kodi mukanena kuti boma silimaluza amavota ndi anthu okha omwe ali bomamo mesaso akunja kwa boma nafenso timavota ku Zambia bwanji chipani chosusa boma chinapambana tatopa ife ndi ulamuliro wa dpp tikufuna tione dzina ife 2019 dpp yikugwa chagada basi!!!!
,asiyeniamenewo kwawondi kususa
Kudakati kusakhale Bakili Chakwera ukanamunyenyera kuti idiot
kodi amia akadalowa Dpp akadane chani osachulu
ngati mulungu ndiwachipani cha dpp ndiye muzawina koma ngatindiwaaliyetse dikilani madzi apite ndipamene muzinena tadala.
Koma munthu wabwino bwino angamadza votere dpp?
Tawina kale man kaya simudza vota koma ife tili olamulira basi tatini pheeee pamenepo muzazionere nekha
DPP IN MY VEINS
ngati ndinumulungu mwawina koma ngatindinumunthu basi mudikile kumbukirani mumene tinadandawulira ndi bingu ndiye alikuti choti muziwemulungu si james ndimulungu basi.
Dpp singawine or
ngati dpp sikukhulupirira izaziwona 2019 ndipamene izaziwe kuti kumwamba kuliyawe.
Koma vuto lilipo amw ndithu kumavota ngati osapenya mpaka kuvotela anthu abanja limodzi kupepela chani?
ndizona kt yudasi anagulisa yesu ndipo akhristu osatila yesu adataya chiembekezo kt kwatha koma patangopita nyengo zipaso zochokela mkugulidwa kwayesu lunayamba kuoneka ndife pano lero tikudyerela ufulu kuchokela pakugulisidwa kwa yesu…….so ngat mcp yagulisidwa ndekut tasala pang’ono kudyerela ufulu wakukhala mmalawi onse osowa nthito ibiliv in the name of God through chekwela tizapeza nchito…….aphunzisi azayambaso kumva kukoma pogwila ntchito zao……..amen
ndizona kt yudasi anagulisa yesu ndipo akhristu osatila yesu adataya chiembekezo kt kwatha koma patangopita nyengo zipaso zochokela mkugulidwa kwayesu lunayamba kuoneka ndife pano lero tikudyerela ufulu kuchokela pakugulisidwa kwa yesu…….so ngat mcp yagulisidwa ndekut tasala pang’ono kudyerela ufulu wakukhala mmalawi onse osowa nthito ibiliv in the name of God through chekwela tizapeza nchito…….aphunzisi azayambaso kumva kukoma pogwila ntchito zao……..amen
Amen
When did a teacher enjoyed his work in malawi? Ask those who are still around and were teachers during mcp era, I have one as uncle here, he will opennly tell you kuti during mcp uphunzitsi was complete slavery, not only it, police, nurses, prison officers etc were receiving peanuts bolako pano they can fight for their rights in as far as renumeration is concerned but during mcp umatengedwa ngati oukila. Apolisi kukakamizidwa kuvala makabudula ati uniform. It seems you do not know what you are saying by insinenuating that aphunzitsi azasangalala ngati kale yet were sleeping on empty stomach, mbuzi iwe.
Amuthaka mukamati achakwela añasiya kusogolele ñkhosa zamulungu iñu mukusogolela agalu amuluñgu?.tazilañkhulañi bwiño
Zotsatila zamavoti pa fb ndi MCP 60% DPP 30% anthu ammizinso I hope azavota pa fb pomwepa alinso ndi ma Android phones I gues kkkkkkk
Zaziiiii
Amuthalika akuopanji, why targeting MCP each n every tm? musiye chakwera adzawina ndi2 or umudetserere.
Kulira kwa namfedwa kumeneko……ayambilatu kulira 2019 isanafike hehehehehehe
write in English please haha
Akunena zoona peter. Congress yagulisidwa iyi zikuoneka zokha
Mwantha Mawu Koma Amene Adaziona Sadabwa Tidikire Madzi Apite
Wapenga ameyu kudabwa anthu kuthawira Ku opposition azapenga zenizeni 2019 MCP yomweyo kuli wawawa
Wachamba iwe mutharika akuvotera ambwiyako
YUDASI NDI ATUPERE MUKUZI
Owooo
ndiye kut atupele wagulisa chipani 4 dat matter ndi president wa udf akutani ku dpp ndipo mia sanali president kambani zina
Kulowa kwa Mia Ku MCP it’s normal koma akangowasakha kuti adzakhale running mate that’s destruction. Msowoya ndi amene ali bwino kunena zoona comparing to Mia.
I agree with, Msowoya can be good for Vice president administratively than Mia. But Mia is good politically; he has far much votes than Msowoya. Msowoya adavutika kuwina ngakhale dera la kwawo
Chakwela!! Chakwela!! Chakwelapam’pando2019 boma,peter akupitakumudzi 2019.
Mmmmmh Grandpa!m’mesa anapinyolitsa chipani ndi ATUPELE??mwatani kodi mbuyache
Malota achumba kukhala ndi mwana.cadet ndipati pomwe sukumvesa???
Tieni Tizingo Kudyasima Ndikukhuta Bola Chakudya Chizipezeka Coz M’tsogoleli Mwini Wake Yehova Akumudziwa Tsono Tieni Tikondane Pamenepa Ndioneke Mbuli
Copy & paste – But forget,this time it won’t work.
Mkuluyu fundo mulibe.
Tidikire Kaye, 2019’yo ndamva kt mai Joyce Banda akubweranso ndiye mudzanyenyanadi
I wonder anthu kumanena kuti chakwera wathawa ntchito ya mulungu kusankha u president, are you telling me kuti utsogoleri wa dziko ndiwa satana?bwanji inu nomwe mumanena kuti utsogoleri amapereka ndi mulungu?its possible mulungu yemweyo akufuna kukonza zinthu.
No part in politics,dirt games!
Abale tiyeni tiasiye chifukwa chimene akuchita akuchiziwa ife samatipasa kalikonse lolo atatozana bwanji muzawaona limozi samadana koma ife timavutika nazo
Zoona aaaa
Good day my friends I am so happy to share my great testimony to my friends on Facebook and Twitter all over the world I was a HIV patients for 6 year my friend introduce me to DR ABUMEN who cure me from the deadly virus I am now negative now I am a living testimony if you are affected with this virus because when u keep silent the virus will eat you up, You can also email him for any kind of help via email ([email protected]) or whatsapp him on +2347085071418.
Ahahahaha Kondwani Magombo akukushoshanitu pitala mutharika ahahahaha
Kodi akutuma iwe eti?
Kkkkkkkk adhaa I smell war kukubweraku sure
Dpp Mafuta Atha Mu Tank Ndiye Ikuenda Koma Mokakamiza Pokana Ukhumudwitsa Oitsatira 2019 Ifika Koma Movutikira Ndipo Ulendo Uluthera Pomwep
hhhhhh chakwera ndiwachunga et
DPP(Demons Putting-foward Personal-needs)
Kuvotera chakwera ndchimodzimodzi kudzangokhara osakavota chimunthu chankhaza ngati chimene chija DPP 2019 boma!!!
Muli mmadzi bambo .I think u r not in Malawi
Don’t judge for you will also be judged. Let God be the judge. If you have never sinned throw the first stone
Or zauzika ndaDInditsaso madoro nde mudzit sindr ku malawi kuno koma chakwera zot nkulamulra dziko kkk ay ndithu ngat ul ndi nkungu kavote koma yanga sindingabetse chifukwa udas ngat amene uja.
Akugwa 2019 Pitala M C P Boma!!!!
politicians are dangerous criminals on earth…..
Mantha chabe awa mr president, coz southern region is up for grabs now with Mia in contest.
ndilibe nthawi yovota amavota nd ma computer not inu olo munene chotan kukhumudwa simuzaleka
Zopinyolitsa chipani akuzembera Atupele koma sibwino choncho, azanu mukugwira nao ntchito limoz kumawa nenaso?
Kkkkkkkkk umakwana ase sibwinod choncho
Ine sindiyankhulapo kanthu kuwopa ma member anzanga a mcp.Komabe tiyeni tivomeleze munthu(peter)abusa athu aja sangamukwanise.
Kkkkk mybe it can happen but eeeeèe nuthng tks about dc
POTI ADAZOLOWELA KU BELA MAVOTI ADZAWINASO KOMA PACHILUNGAMO MALAWI AKUMVUTIKA
Are you looking for a way to get rid of hiv/aids and everything seems not to be working, you have been criticized because you are positive or you can’t live to the fullest because of your status, sometimes your happiness turns into sadness when you remember that you are positive and you start thinking what will happen to your children or family, my brothers and sisters cry no more and be sad no more God is not asleep there are no problems without a solution, Dr Abuu made me believe that all problems has a solution contact Dr Abuu anytime anyday for your HIV problem to be over, he has cured a lot of people and i was cured too by his medicine, please beware of those people claiming they were cured by some doctors i have lost money through them until God showed me the light by meeting Dr Abuu, i can’t keep this to myself i have to share to save lives just as mine was saved, whatsapp or call his number +2348066454364 or send him a message on his email address [[email protected]] contact him and thank me later God bless you all.
Anyenya ndani?Wopusa wogwa nkumina wovotera Mtharika munthu opanda ndondomeko pautsogoleri ndani?
Ngati atazadzivotele ekha zizatheka koma ngati akudikila mavoti athu Ng’oooo!!!!Mwina Rigging.
Muchedwa nazo boma timasitha pakatha 10 years basi don’t waste your time aa inu ndi munthu wabwino wanzeru I know u bwana wanga
MIGHTY DPP WOYEEEEEESSSS!!! LONG LIVE APM..LONG LIVE CHILIMA!
Cholinga chake ndikufuna kupulumutsa anthu ake kumbava ngati inu
Feel the heat. 2019 I am voting MCP. We gave you a chance but you misuse it with a ou cadets. Now we want a change.
Ine ndi wa DPP koma apa pokha vote yanga Mia watenge.
Ine ndilibe pulobulemu Bwana mulamulira moyo onse asafune ayanike ufa pachingwe #WAYAWAYA
Yudasi kkkkk
Koma Nkhalamba Iwe Ukuganiza Kuti Timakukonda?Shame On You Mr Mugabe.2019 Is Not Yours,77yrs Koma Kuganiza Ngati Mwana.Za Mcp Zukukhudzani Bwanji?Mthira Kuwiri Iwe
Akuwopa chani iyeyu? Amagenda mu mtengo womwe muli zipatso. Iyeyu azingowonesa zitukuko agogo sananame kuti matchona nzeru zimatha
Juda chaiyee akapfeka nhembe dze church
Pitala akunama kwabwera game changer sidick mia mfana wa Ku shire valley,mfana wachikoka. Pitala game IYI samakanso
Guyz guyz , Ndikurangizeni Azanga nonse otsatira za Dziko anthu awa ndima Guy zawo ndizimozi sayambana ayi amagwirizanaso zed koma amafuna azipusisa opusa ndiye tikumayambana ndife amphawi iwowo mkumaseka Ali phee akudya ma supergt pizza ndi pk akakakumana Dziko la azathu lija ngat Ku RSA. aa KFC sinkhani ife kuno titadurirana malire kutemana, kuphana kumene wawa ati wina wanyoza Pitala sunamuone sukuziwa
Mu MCP mwalowa anthu ambiri pakatipa koma mukumangokweza dzina la Mia lokha kumuopa eti? u President ochokera banja limodzi tatopanawo kani ndi umfumu?
Mau omwe anayakhula bingu iweso ukubweleza iwe pitala u will never win in 2019, bingu anachita bwino term yoyamba koma iwe failed
Iyeyu adzaimanso?
Anthu akhumudwa. Aone zina
Manyazii bwanji Pitala?. Maloto a chumba amenewo. Ukuganiza kuti ndani akusangalala ndi ulamuliro wako?. Unyenyedwa ndiwe 2O19
Muthalikayo adziwe izi Vote ili mu mtima asaone kuti enafe tikumuonela kukondwa pa zomwe akucitazi
Boma ngati munaliona likuluza. MCP muziwafunsa aja anatisiya aja a chakwamba anadya one koma zinathera kuti
Lupia adaluza bwanji ku Zambia? Mudzienda osangofuchilira pamodzi modzi mudzakula nazo musakudziwa chilichonse
Iam with you brother #Danweck,tell them..
Enatu samaziwa so let’s open their eyes
Nanga Joyce Banda adaluza bwanji?
Akumuopadi Lazaro!!
Kkkkkkk mpaka ku pinyolisa chipani koma Chammwamba nde wationjezasotu kkkkkkkkkkk
Koma Akunama?Waigula Basi Mia Mcp Kkkk
Kulira kwa biggie biggie kkkkk amamunyengelera Sidik Mia kuti ajoine DPP, koma Mia waona kuti DPP ndi yokuphwa kkkkk
Olo atati kuvota amavotera pa fb ndi ma comment, MCP yawina kale
makape nonse khalan chete mukundinyas,tizimvela inuo?komwe akudyela ndalama zaozo simukudyanao.tien tidkile 2019 bas.
Mwana olowelera alandilidwa ndi Yona mfana othawa ulaliki kkkkk
Khalamba iyi mutu wayima ndi anamandwa omwe akulowa mcp
kodi galu ameneyu iye siwamulungu.nanga msonda DPP adagula pa bwa kkkkkkkkk APA zaoneka kuti DPP yapita motchipa kwamsonda pamenepo MCP yapita mokwera.
Tikumanganitu,,,,kkk
kkkkkkkkk ok koma mukozeke kudzalipira .
Pacibwampini nje nje njeeeeeee
Chitukuko chake chilikuti choti angazawinileso Mbamva zimenezi tikungofa ndiwumphawi
In a free & fair elections Nyapapi will neva win.A Malawi anachangamuka pano,anatopa nd chitukuko cha pakamwa.Tione kuti october by election iyenda bwanji mostly ku lowershire ku
iwe ndi wa mcp ndani sakukuziwa ma coment ako amakhaka otukwana ngati siye mamuna man nanga mcp angawine dziko pa central poka muziganiza bro
Hahaha hahahahahaha mpaka yudasi hahaha
DPP mpaka kale kale eishiii boma iloooo
Ayamba kale kunjenjemela ndi MCP kkkkkk..
Ayambapo manjenje
Ma cadets thukuta mkamwa mwayamba kale kunjenjemera……..MCP yanyamuka .
Mmmm Yoswa, vote ili mu mtima
Zinazi muzisyilako anawa aziyankhula bwererazo, nanga munthu wa nkulukulu zaka 77 nkumachita zinthu ngati mwana. komaaa!! a president and a proffessor for that matter, ndimaona kuti on his 77th birthday he will demonstrate maturity koma ashiiiii ngati kamwana ndithu, munthu wankulukulu believing in lies and fallacies.
Hahaha eti munthu akuti ndi professor kuyankhula ngati mwana wa zaka ten.ndi chifukwa Malawi yasaukitsitsa ndithu ndi nkhalamba ngati imenei.
I thought simumanveratu ma speech ake monga inu ana a zimbano , munvadi kuwawa. Kkkkkkk kumsuzumira neighbor kumeneko?
mmalo moti angochilimika kuchipinda,tikufuna mwanatu ife,,kkkkkkkk
No more nkhalamba ku state house, akanakhala wina akanangoti sindiima 2019 to avoid embarrasment. Malawi is not zimbabwe nkhalambayi ikapume.
Unfortunately he does not have a strong competetor. Is somebody failed to manage a church with about less than 1mil followers, then he us failing to manage his party with about 4-5 million followers. Can he manage 17 million people? I daubt. Let’s wait and see how it goes.
Iwe ndiamene ukuona ngati alibe competitor, mwiniwake akudziwa kuti he will face stiff competition in 2019. Ndi chifukwa chake competitor wake amamutchula pafupipafupi. Chakwera never failed to run the church, he was not fired. He made a choice kuti ayeseko ndale. Ena anapangaposo nhati achina dumbo leman, wilson ndomondo, mzomera ngwira kungoti enawa ndima mp zaupresident sanapangepo.
Chakwera is a small boy pa ndale, sangamake
@Olivia, don’t fabricated your self
Kumaka ndani, peter mutharika ndale waphunzira liti. Munthu oti amakanika kuyankhula zomveka.
Kaya Amakanika Kuyankhula He Z Stil Ur President And He Will Also Win In 2019 trust me on that one chakwera wil never be a president on this planet
iweyo Victor ndi munthu omvesa chisoni heavy ukuyakhula ngati uzavota wekha bwanji?
Muzakhumudwa bcoz chakwera will form the next govt. Chakwera will pay this old man his retiment package.
Prestent wazmawu ngt wavumata nthuli ya nyama ife ai, chakwera moreeeeeeeeeee fireeeeeeeeeeeee
Chakwera ana akhonzeka kumugubuduza ku convention..Jessie Kabwira moto kuti buuu!! DPP WOOOYEEEESSS!!!!!
Jessie kabwira sangawine ku convestion ya mcp or atapikisana ndi ine. Nde angagwetse chakwera, impossible.
ka kabwiranso ndi ka chani?? za ziiii
Kaya bola nzanu ali kale Ku state house, ndipo akupitilizaso 2019.winawe uzingobwebweta basii olo atani palibe chake chakwela trust me DPP,will carry the day!!!!!
Azatulukako kumenekuja dzuwa likuswa mtengo. Ukaluza ngati pamakhalaso xcuse yokhalira ku state house, umangotuluka mwakachetechete.
kkkkkkk awuze aixe ukalunza ku state house sumakhalaso ndi mitre
Rod Ine Ndi Wa Chelsea Iwe Wa Asernal Always On The Loosing Side Bwanji.If U Follow Politics Dpp Has A Big Following. Kodi Anthu Okalamba Ndiamene Amasamala Mudzi Amene Timafunsako Nzelu
Ndi chifukwa chake tikuti azikasamala azukulu ake ku mudzi osati ku state house.
Ndi chifukwa chake tikuti azikasamala azukulu ake ku mudzi osati ku state house.
Sitikufunaso Anthu Otopa Kale Ife Nchifukwa Chake Akumaba Ndalama Za Boma Chifukwa Amadziwa Kut Ine Ndakalamba Kale,,,,,,, Usayimenso Jst Pack And Go Ku Thyolo
Mukufuna azawine amene inu mumakonda?
Koma kuvotela MCP , kulikbwino kuvotela chipani China chimene
Dpp 2019 Boma again !!!!! wina afube asafune remember 2014 chakwela analikuti nanga uyu Peter anali yani that time
Dpp 2019 ku opposition, there is no reason yokakamila nkhalamba anyamata alipo.
Mutha -rika,osusa Mutha Mau,mesa Big Late Man Alipo Mukati Siufumu Kut Alowe M’bale?Nkaona Ngat Muli Nd Bale Wanu Kt Alowe Mmalo Mwake Mungonena Mulibe Vision Vuto Ukamafuna Utsogoleri Umakukana,koma Umakana Umakusata,nonse Osusa Mukhale Macandidate 2019 Mukakhale Ku State House Tione Ngat Mungakambe Zanzeru Mwamva
Coppy and paste mr blessings moja. Ndinayankha kale comment yanui anaiposta dixey mwale.
koma yaaa lets wait and c 2019
aaa zoonad a chewa mukavotere kamnyamata kanu ka chakwera kkkkkk angoni vp wathuwathu chilima…alomwe adad adadadadadad mcp probably nganganga ku oppostion no doubt about that,
Kaya Zawo Izo Ife Za Political Tilbe Nazo Busy
i think unali usanabadwe m,mene kamuzu Banda amaluza eti.? Vuto mkusayenda, Lupiya Banda analuza bwanji? Ngati iwe ukavotele dpp it doesnt mean kuti idzawina ayi. . Kamuzu anali muthu muthu osati izi aaaa awa…! koma analuza, ndeye munene izi? Aaaaaa. Ukamufuse Dr bakili Muluzi or Dausi about kamuzu. Aaaa ati petulo ehe!!! Kaya.
Wise words
True
100% true
Bola uwulutsa zisamkho asadzalirenso.
Nose a dpp ndinu zisiru agalu akhakhakha kuphatikiza ndi kapre…… kanuko mbanva inu, mcp 2019 boma.
DPP iwinaso 2019. Many of their project are set to be completed before 2019 just before the election. I greatly believe it will be a campaign weapon
DPP iwinaso 2019. Many of their project are set to be completed before 2019 just before the election. I greatly believe it will be a campaign weapon
kkkk ma project osalimba ngati Karonga-Chitipa road. Anthu akuona ndipo DPP ikulandira Red Card. PP inaluza bwanji? So shall DPP lose too.
Lupia adalitu president ku Zambia koma adaluza kuli bwanji Nyapapi wapakamwa pobwafukayu?
Sakuziwa mafanawa ….ife boma talamula
Ine I stay in Mangochi. Ndipo I have seen ka improvement. Mangochi – Liwonde road under construction. Then Mangochi Stadium, Mangochi Town hall, Water Tank, Mangochi Technical College . Of course some projects in progress. That’s why I say these will act as Campaign weapons during the Election. Ofcurse pali transformation atleast
Which projects?
Duncan Zulu Waona Mafana Akuphweketsa Boma Eti Dpp Ingaluze Pali Iweo Ndi Ineo
Zonsezo ndakambazo anamaliza only that Road is under construction.
Zonsezo ndakambazo anamaliza only that Road is under construction.
Ine ndilibe pulobulemu DPP wayawaya Kkkkkkkkkkkkk Peter Mutharika woyeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee
A Manlord Kumafunsa Dala Which Projects Umakhala Ku ASIA iweo as if u r blind jst look around u wil get the answers
Which roads
Boma silimaluza
hahahahahah muziona 2019 peter wanuyu chitukuko chake chiticho chitukuko anapanga ndi nkulu wake osat iyeyooo chakwela 2019 bomaaaaaa
A chikoko muli ndi maso inu come ku nzuzu kuno ,,odl cumpus ķu mzuni ikutheka;rumphi ttc ikutheka,saļima wàter project ikutheka,nkhatabay road strabag ikumenya,chitipa water project sawa group ikugaya!!ķođi inu muneña chani inu asayenda inu chaķweŕa wañuyo adzapangachani??adzambila pàti kkkķkk ķoma mulimbetuu??cancer ceñter nañga???àka tumbu onyela n’dàmbo munya 2019 dpp ikunyenyanidiii!!!
Maloto omqngolota usanadye siabwino mudzamuthawa malawi nonse A Dpp
chakwera ndi more 2019 boma
Malawi the warm what???????? I disagree to agree with anyone of you
chakwera 2019 bomaaaaaaa asakufuna akakolope nyanjaa yomwe mufuna kulanditsayi agalu inuuu
Zake izo Chakwelayo!!!!!ife bola tikudya mgaiwa wautaka basiii!!!
kodi chitukuko sakupanga kumpoto kwanuko ife kwanthu kuno sadabwele mkomwe tikanena zachitukukocho nde ndi zero nde tikavotere dpp yatani kufuna kuti tisaukilebe mmene watinkhaulitsila nkulu ameneyumu
Emanuel auze agalu amenewa ndipo kulibe ulamuliro wandivetsa kuwawa ngat umenewu shaaaa
nthawi yochita chitukuko yatha kale musazinamize, yatsalayi ndi ya kampeni
komaso ku mpotoko olo mutaphatikizana nonse kuvotera ka dpp kanuka sikut mungawine nonse kumeneko ka population kanu ndi haif ya Dowa kkkkk
Hahaha odzavota ndife anthu, kazipusitsanani nokhanokha.koma chilungamo ndichakuti M.C.P ikudzatenga boma..ngati simukuopa chakwera bwanji mwayamba kale campaign? Kodi ino ndinthawi ya campaign? Chi president chafundo ngati mwana hahaha professor oyankhula fundo ngati mwana wazaka ten.M.C.P ikutenga boma 2019 Lekani kulota anyapapi inu..
Mukati Mcp Ikudzatenga Boma 2019 Boma Lake La Nchinjitu Likakhala La Malawi Iwalani
mukawauze anawo,osatengeke njoka ndi njoka ingasinthe manga
A Stain Chikoko Mpaka Ife Agalu Kutukwana Anthu A Kongeresi Simuzatheka.Mwatukwana What Difference Does It Make Then Have You Become The Ruling Party Now. You Dont Knw Politics Wait Til 2019 Mpamene Uzaziwe Kuti Dpp Ndi System Ina Iweo Ndi Ka Mcp Kakoko Ka Tukwana Ukhala Choncho Ife Tikulamulira
Auze asamaderere boma
KKKKKK chakwera sangawine or patavuta bwanji
Kodi MCP kuwinako izadusa potani? Kkkkkkkkkkkkk muwafunse a chair ananena kale kuti palibe amafuna kubwelera m’mbuyo, pano ndi nthawi yopita chisogolo za MCP iwalani ndi maloto chabe amenewo. Mbiri ya MCP inaipa kale-kale panopa ngakhale atachapila boom singaele kapena kusukika ngakhale pang’ono
Azabera mavoti
My blood is blue.Can any mcp member convince me why I should vote for chakwera come 2019.osamangobwebweta apa
God loves malawi pliz every leader akhoza kulamulira dzikoli
But If He Is Not A Leader Sangalamulire Olo Mulungu Akutikonda. God Loving Us All Does Not Mean We Can Rule Mw Whenever U Feel Like Becoming A Leader.
Ofunikadi azanyenyedwe amenewa achulusa zoyankhula kkkk
Tanthauzo lapinyolo lavuta apa,Sidik Mia waphwanyitsa ena mitu apa,inu tadzingoamwetsani anthu bibi mu LL mo
Kkkkkkkkkk mau
Hahahahaha kkkkiest
Sime of these comments are not worthy of a whole Head of State. Leave some of these things to loud mouthed Regional Governors or whatever they are called. Honestly such utterings zinayamba witj the likes of Charles Kamphulusa Davies Kapito Morris Kachimbwinda and now the new kid on the block Jeffrey….come on give us a break and start talking about policy.issues!
Akatero wakwiya Yoswa
Akatero wakwiya Yoswa
mcp nd bm 2019
mcp nd bm
ndipo osatinso kunyenya mwake kongoyelekeza aaaa iiii, kunyenyelatu aganize bwino analowa zolakwika kuthawa kusamala nkhosa za mulungu, mulungunso akumuyang’anila kumbali bwana peter tinyenye basi osawasekelela
Udziwe ichi Lupia ku zambia adali president koma adaluza movetsa chisoni ndiye kuli bwanji Nyapapi wapakamwa pobwafukayu?
how much did they pay you….
Zandalezi sikweni kweni,koma iyiyi yandifika,achakwelatu akusakaniza zithu akapanda kutengazithu bwino ziwasokonekela mulengi akakwiya nazo,mbusa akhala bwanji mmsongoleli wa dziko,ndimmene ayakhulila a lucias mu?
Brother #charles,kkkkkk!!!!!kukhala kutekedza 2019,akamufuse Tembo zomwe anaona mmbuyomu
DPP woyeeee
Mcp woyee
hahaha zaka zino munthu kumalimba mtima kumat ine wa mcp,kkk olo atatenga doom kundiyika kamwa na mcp yokha sindigakavotere and mcp sizalowaxo boma believe me
Boma silimaluza inu ndi JB yekha analuzapo ali m’boma
Musaiwale kuti PP sinasakhidwe kuti ilamulile BOSS AM AGREE WITH YOU
Boma limaluza mudziwe zimenezo kuyambila lero 08:28 nthawi imeneyi
Lupia waku zambia adaluza bwanji? Mudzienda osamangofuchilira pamodzi modzi mudzapusa nazo
Anzanu amkateroso mudzadwala just wait 2019 is just around the corner
tonse tili apa ndakapolo oti sitikudziwa kut zimakhara bwanj kwathu mkutenga ma ziphaso zovotera mkukayima pa line kuvutika ntchito yot ena agwira kale kutereku vote ya winawe nd ya peter kma sungadziwey
Vote ndinu ntima gyz tiyeni tizaona
Now ur talking koma boma ndi boma
If you trying to say dat boma silimaluza what do you mean? Ask kughana ngati sukudziwa kumayenda amwene osamangokhala malo amodzi in Ghana opposition is the one who is rulling now
Ndiye tigwire ziti mukuti boma LA pp lidaluza Kaganizani ngati amalawi , with this president this nation won’t develop any more
Boma limaluza ,chipani cholamula chaku America chimene amayendetsa brack Obama chinaluza,Ku Zambia chipani cholamula chinaluza,Ku Ghana chipani cholamula chinaluza Ku Brazil chipani cholamula chinaluza ndiye bwampini iwe ukuti chiani?
KKKKKK Ya
Trump anawina Ali kutsutsa zukan mani
kumbali yanga ndale za ku malawi kuno ndimaona ngat zimasiyilanako ndi za mayiko ena,fanz kuno ndimaona ngat imakonda chipani chifukwa cha mtumdu wawo komaxo chigawo chomwe akuchokera kona dpp ili ya mphamvu kumwera mcp pakati pomwe nowdays kumpoto pp ikumaoneka ngat ndi ya mphamvu kumeneko,another thing ndichakut chiyengo chimachuluka kwambiri so pa chisakho chipani chili boma zimaone kut chimakhala ndi upper advantage than anzawo JB uja anagofoyira yekha kuyiwerenga kona akadandaula kut chisakho chaberedwa,believe me dpp izawinaxo
Manyi mu llz plz bwanpini zooona? Iii anthu amwa manyi
Anyenyeni kwinaku mukunyenya dziko lathu lokongola ,nanunso mamilion adzapezekanso kunyumba kwanu mukadzayamba ulendo wotseka maso,tinyenyeni tinazolowela kudyeledwa ndi anthu opanda history.
achakwela siyan za ndale si mbali yanu
Ndale za pa malawi kkkk
KKKKK, KOMA ABALE PENA PAKE TIDZILANKHULA ZA MZELU MUNTHU UKANJENJEMELA BWANJI ULI M’BOMAKALE. TAMAKUMBUKILANI INU 2014, APITALA ANALI AOPOSITION OLAMULA ANALI A PP KOMA ANATEMBENUZA APP KUKAPEZEKA KUNJA MKULUYU M’BOMA ZINACHITIKA PAMENE PAJA AMAI MPAKA KUSOKELA. ACHAKWELATU ALISO POMPO.
mwalo ma Mia kulowa kongeresi zapanga opposite Congress yalowa mwa Mia lol
SANGAWINE PITALAYO MCP BC
pali zitsiru zina zawanthu unzimva DPP 2019 m’boma… kaya kumakhala kusavala chovala chamkati. inu DPP nchonyadila? mumanyadila coz ndi mbuzi xa anthu. nde pali asasamba ena a MCP. awa nde dziko sazalamulira mpang’ono pomwe kumangozivuta Chaka chilichonse. mukuona ngti anthu angapange xoti mutenge boma? nyau zingalamulire dziko? zosatheka. achewa pezani china chochita. ati MCP. mumawina pa Facebook basi akanganya inu
Sakunama dpp woyeee
mmm muthalika chikumukhudza ndichani pa khani za chipani cha mcp? Ndi member wa mcp iyeyo? Mmmm wakalambadi uyu eti? Useless. Man. Akuwopa chani ?
Peter yemweyo. Kuli wawawa kaya ufune usafune vote ndi peter basi
Musathe mau bwana sionse omwe akukondwela ndiusogoleri wanu ziko muliephela kulamula mukathila phula nsewu kwa 1kiromitre mukumadziguguda pantima kkkk ine olo atandithila doom kamwa yaine yokhayi vote simuzainukha
Ukuonangat Vote Yako Imozi Ingalepherese Peter Kuwina?
Ineso sazainunkha
Ovota ali ku mudzi, apa anyamata a Youth nthawi yanu inapita ndi kamuzu
timavota ndife tili kumalawife mesa iwe uli ku jon
Kkkkk
Ine olo atavula nkupolama kundionenesa nthangala zake mbambadi ine nditha kungoona nkukavotera uyu ndikumudziwayu
kkkkkkk ati ovota ali kumudzi anyamata a youth tym yanu inapita ndi kamuzu apa kkkkkkkkk
Nobody knows about tomorrow so watch ur mouth
Words of wisdom. Very true.
All are shit
True words,brother #kamwendo
Asieni bwana azalilanso kachikena paja amanama ndi silogani yawoija yoti atibela anthu olephela away DPP bomaaaaa 2019bomaaaa
Pambuyo pa mbava munthu wabwino bwino ngati iwe kkkk zachisoni kwabasi
mbava ndi ndani? ife nde tikusangalala ndi Dpp
Ngati ali mbava osakawasiya Ku police bwanji?muziona ndikuzigwila komwe simunati!!!!
Chita manyazi zoona iwe kumati uli pambuyo pa DPP a president opanda pindu ngati awa
Are u Malawian or who??
Palibe olungama woweluza woona ndi mulungu yakhe basi don’t judge me or APM fear God
Kodi akayange mmafuna anthu onse akonde chakwera?mulira simunati dpp 2019 bomaaaaaa
tiona mesa tili limodzi
man mulibe manyaz wachinyamata wozndikira sangakambe zmenezo ugwera limodz ndi nkhalamba yakoyo.
Iweyo ndi amene ulibe nzeru becoz ndale suzidziwa ukazadziwa udzandivomereza
Munthu wanzeru sangasapote DPP chimodzimodzi kutungira madzi mudengu lasungwi
Chisankho chako ndi MCP ine DPP chifukwa chake tili anthu awiri osiyana
Bola ukuziwa
Iwenso ukudziwa kuti DPP ndi boma kale
yeah ndikuziwa kuti ndiyakuba
Inu khalani kuja ndikusaba kwanu
umufunse chaponda akuyamkha
ine oro atandithira doom mkamwa oro kufuna kundiviika mmadzi ozizira koma ndikunenesa sindidzaloraso kut ndalama yanga ya msokho chaponda kut apondeso,sindidzalora kukhara ku chanco for 8 years for a degree,munthuyu ukamakura umabweleradi ku chimwana ,u make decisions ngat mwana ndaziona ine ndili ndi umboni mu dziko la malawi..pepani a Lovemore bwana anuwo sitimawafiraso
DPP woyeeee!! Peter muthalika woyeeee 2019 Boma, chakwela kuilaso.kachikena 2019 Kkkkkkkkk
MCP ili m’madzi 2019 no chance
Chakula apa ndikunjenjemera 2019 sinafike asathe mau
Prezdent Wanuyu Ndimbuli Alibe Fundo Munthu Wamzeru Sanganene Izi
mukanva ndale ndi zimenezo
Judas,Jonah koma munthu wa mulungu sakuyenera kulowelera ndale chifukwa a ndale akasowa nzeru amathangira ku mpingo kukafunsa koma apa wakumpingo alowa ndale tikafunsa ndani?
Kkkkkkk!!!!brother #Allan,akafusa kwa satana nanga sathawa kale kwa Mulungu?
Kuteloku kuchoka kwa chakwera mipingo kumalawi kuno yatha? Thats not true the foundation of a church is God
Ndale zimafunika anthu andani?
nde kuti andale ndi asatana eti? kkkkkkk I see ndaziwa nawo kkk
Koma ndizoona kodi Mia akukalowa muchipani kodi pakati pa Mia ndi Mcp amene akanapanga hire Lucius akanakhala ndani? Chopani chapita basiiii
MCP Can’t rule this nation hihihi
Mukugwilitsa phone yanji yovuta network’yo kut ma comment adzadze anu nokha?!
If God says Yes! Who can say No??????? Don’t cheat yourself. We are all Malawians and equal in the eyes of God.
Are you God?
MCP Can’t rule this nation hihihi
Mumuuze manja adziyimika onse mmwamba
MCP Can’t rule this nation hihihi
IWE CADET SUNGAWONE MA COMMENT KUTI 99% IKUDANA NDI NYAPAPI WAKOYO??UZAMVA NKHWANGWA ILI MMUTU IWE.
Pitala Saakunama! Chakwera Wagulitsa Chipani Kwa Bwana Mia! Kkkkkk Ndidzakumbukikira Mawu A John Tembo Oti Chakwera Ndi Nkholokolo
Comment reserve
mumuuze kuti akunama pitalayo amudzadza iye ndimantha……kuvuta kumpandako
mantha ndi lazalo kkkkkkk
Sakudziwa muthu kukanika kulakhula kkk ati tibwelesa khuku zamkaka muziweta ndi ng’ombe za mazira kkkkk
kkkkkkkk Tiona
Lazalo abwelera kwa nkhosa za Mulungu basi kupanda kutero athera mwamia omwewo
Sidik Mia sanalowe congress koma Congress yakamulowa Sidik mia.
Mukulemba zotsamveka mmawa ngat uno kid mukumva kudzidzira
President Wanuyo Mutu Siukugwira! Ngat Wasowawa Fundo angonena
chilungamo chimawawa
nde misalayo imeyi! nanga palinxo fundo zoti munthu wanzeru zake angamat ndchilungamo apa? what can Malawi benefit from your lunatic’s President’s saying? you both deserve to be nincompoops, morale rotten guys!
Usakugwira ndiwakowoooo
iwenso nde mbuli yeni yeni