Bungwe loyang’anila ufulu wa Atolankhani mu chigawo cha Kum’mwera kwa Africa, koma la mbali ya ku Malawi kuno, la MISA Malawi lati ndi lokhumudwa.
Bungweli lati ndi lokhumudwa kuti ogwira ntchito awiri a nyumba youlutsila mawu ya MBC anamenyedwa pamene amakatola nkhani ya zionetselo za oyang’anira akaidi.
Malinga ndi chikalata chomwe watulutsa nkhalapampando wa bungweli, a Teresa Ndanga, a MISA ndi okhudzidwa kuti Atolankhani anachitidwa chipongwe akugwira ntchito.
Iwo ati izi ndi zoika pa chiopsezo ufulu wa Atolankhani ndipo sizikuyenela kumakhala choncho.
Mtolankhani wa ku MBC, a Patrick Dambula anamenyedwa limodzi ndi ojambula zithunzi wa ku MBC ku Maula komwe amakagwila ntchito.
Iwo amakajambula za kunyanyala ntchito kwa oyang’anira akaidi.
Why only MBC reporter?
It serves them right! MBC reporters are just too partisan
ibooke basi ndende,akakhala awo mwachita bwino amafuna akutapeni mkamwa.
Kkkkk kumaonako plz kokalemba nkhaniko, muziyamba mwaona adzikutibulanitu ohoooo kkk
KKKKK
Or anakaphedwa
awamenya pang’ono basi?Akabweranso muwadule mitu
Kkkkkk kugundika
Atolankhan A Mbc Amaonjeza, Ndinu Aboma Inde Koma Muzikhala Ndi Malire
kodi inu mmangolemba khni zopusa bwanji??
kodi inu mmangolemba khni zopusa bwanji??
Sorry guyz ndiye magombo amenewoo
achita bwino
Plophes Asa Pita Wamu Khalika Wanene Tsa Kuti Mtedza Wusatuluke Pakadali Pano Apezeke Ndimulandu
Eya Apa Ndekuva Bho Awachta Bwino
Awachita bwino,amakatola mabodza. Anawatuma ndi Dausi.
kkkkkkkkkkkk achita bwino kuwaswa amafusa zopoira ameneo
Kodi Wa Zodiak Anatani Osamenyedwa? Mesa Anali Komweko, MBC ask yourself why?
amaonjeza amenewa saphunzitsidwa kuti intervie sipangidwa ndi munthu wokwiya.
Musasiyile Pompo,,,,, Mumenyeso Prezdent Wawoyo!! Amene M,mati Pitalayo. Zintax AchebeMan Wa Zintambira Fätsäñï Fäxýbwõï Rüssïæn Birdman Lpsgc MW TinTin Vynteen Chifu Stevie Di Biest Nkhata Zintax AchebeMan Wa Zintambira Man Fedzy Wa Undiscovery Kholowa Ç Ger Mashini Misslinah Mzumara Mathews Troopad Nkhata
For MBC journalists, the warders did a very recommendable job. No need for complaint. We hear nothing but lies on MBC, but we pay for it.
This officers they need respect coz one point u will be there
Awachepesa tikati tamvela zabwino pa mbc zizikhala zanyengo basi ikakhala mbctv ndiye ali busy ndi program ya malata ndi cement ati osika mtengo,,, thanks for MACRA popeleka ma certificates kwa ma mbc ozindikila,,
Nzili bwino kwabasi pa chiyao amati. idyesile chenene. Kujijilika amenewa iya…
Out of order
Thats being savage…violence isnt a solution…its not a part of self help remedies kaa….now the grieved p/warders myt be facing battery charges
Bolaniko awalawa makofi akundende,kkkkkk
A times sanamenyedwe
kkkkkkkk aliyense akungoti anakamenyedwa Philip business
Apanga boh amalemba khan zabwino zokha za ku state bas
Kkkkk….nokha mukuti oyang’anira akayidi…that is redline ,,,those people anatopa kale …lol
We love our job bwana.Dnt understand wt your kutopa statement.
Xorry….bt.wz..jst..refering…to..ur..work..is..as.the..sem..as….sodiers
Iguess should b #phillip_business
Amapusa amenewa
Nanga bwanji sodapite kuunduna woyang’anira mapilizoni ukawapanga interview? Wanjala nkumafunsafunsanso?
Kkk
zilibwino KT nonse muli boma
Amaonjeza kulemba zokondera boma answedwe makofi basi
kodi ku mbc kuli atolankhani
Akufunika Aphuzitsidwe Kuti Asiye Kugwila Nchito Mokondela
God knows our problems just kneeldown and pray to Him,and He will answer our matters
Kkkkkkkk
Kkkk
Phillip business ofunika ena oonjezera
They are partial awachita bwino
mvuto la atolakhani akuno sadziwa karate koma uhule ndi umfiti basi
Awachta Bwno Pakuwamenyapo Amajaira Hvy Agalu Amenewa
akunthidweeeee
Kkk,anzao akumapita konko bwanji osamenyedwa,MBC wake up,don’t be a puppet
ZBS,Times,BBC,Power 101,Timveni jst to mention but a few.
Sure
next time azachapidwa zenizeni.
Azichotsa okha ntchito amenewo akhala akaidi zonse zikatha alowa mkati kwambiri nkhaza zimenezo
Dada Chirwa u are missing the topic.We are condeming zomenya ma reporters osati zomwe mukunenazo.Hope u are not drunk.
Nanga kumenya atolankhani ndiekuti wina Ku mati achita bwino atakhala iwowo kuti amenyedwa angave bwanji vuto ndiloti tikumalowetsapo ndale pena paliponse tieni tizitsata chilungamo cha zomwe zachitika
Both Sides Are Offside:journalists You Communicate With A Spokesperson Dont You? What Were You Doing With All Guards? To The Guards:do You Go To Church And Learn About A Great Command That God Gave Us? (Love Your Neghbour mt 22:39]Ok:who Is Your Neghbour? Your Fellow Civil Servant,how Come That You Slapped Him? Demons In Malawi Are Tormenting!
Bravo Prison warders! Had it bn kut waswedwayo ndi uja wa tsitsi phwii pachipumi uja, Filipo, nkadakonza phwando.
This Malawi24 reporter seems very happy while MISA Malawi is disappointed with the Warders savage actions. Was there no better words than “aswedwa makofi”?.
mwina adakati awaphaphalitsa ndi makofi etii? kkkkkkll
Chikufunika simatchulidwe amau koma ntchito imene oyang’anira ndende agwira or akanati aphikidwa,atibulidwa,means kumenyedwa basi kkkkkkkk ndipo ma reporter a mbc tsiku lina azatikitidwa pankhani zandale this is the first stage
Poti zomenyedwa kapena kuphedwa ndi zomwe Atolankhani amakumana nazo, nzosadabwitsa ndipo onse amayembekezera zomwezo, imanena ndi nthawi.
kapena akanati awapumphuntha????
kkkkkkkkk aswedwa
Mmmmmm, Hara?. You know, there are certain comments befitting certain names.
sanati azitibulidwa amenewa chifukwa cha ukadeti wawoo,kkkkk,paja ma journalists azawonso a ku times anawatibula a mbc times itatsekedwa you remember joe west? hahahaaa
Kondwani, can we for once admit that we copy everything we will never understand for the sake that we are Africans.
copy everything like what in this case joe?
You see, hear nothing & close to nothing.
Fellow journalist writing like that? Malawi 24? Mmmm
#mmmmmmmm_mothermalawi_
Asiyen adzikwapulana amenewo kkkkkk!!!
Awaphetemula kkkkk
Kkkkkkkk koma mpakana ma mbama
Vuto lilikwathuko eti atolankani A MBC ndioimira chipani cholamula boma ntawi zonse, MBC sibungwe loima palokha ai limaulutsa, kapena kutora ndi kulemba nkani zoyamikira boma limene likulamura, or zintu zikuonongeka mbomamo, amangoti zilibwino, ndibungwe laboma ntawizonse
kkkkk akhoza makamaka aku mbc nde yake kkkkkkkkkkkkk ine kunva kukoma!
Mbuzi izi zokokedwa pachingwe kkkkkk atsala a galaxy kkkkkkk mbava
Pamenepo M pamene paonetsa kuchepa mzeru kwa ma prisoner warder wo fukwa nkhani yamalipiro mtolankhani sizikumukhudza,speaking frankly your all stupid,ndipo mmene mumka vomereza malipirowo simadziwa kt azanu mwawapezawo amafanana Kapena kusiyana malipiro ndi apolicewo?nthawi zina osamangothamangira kuti bola ndalembedwa kma kumaonanso ma benefit kuti akuti bwanji?mkumasaina bwino,mavuto ngati awa bwanzi kulibe kma kumenya atolankhani ndiumbuli waukulu sitingasekelere
Point of correction,,,Mw Prison Service,Mw Police Service n Immigration Department are all under one umbrella bwana,Ministry of Home Affairs & Internal Security.Masalary samasiyana zimafuna ziyambike panopa.Hope u have been cleared.we dnt condorn ths behaviour of manhandling reporters is wat is being discussed here osati kuthamangira kutukwana musakudziwa chilichonse.
Ndiye kuti mukuikira kumbuyo kumenyedwa kwa atolankhaniwo,fukwa ngati zasintha panopa kma poyamba amalandira zofanana akuyenera kutsata njira zoyenera osati kumenya atolankhani,kuotcha mateyala,imeneyo si strike kma demostration yoononga zinthu
How I wish akanakhala philip Business
yeah mwaitha ndipo pano ndikukulamulani kt mupite kwa timpuza mwasambo mukamufotokezeko nayeso excersise imeneyi isamupitirire
Ndi ana a munthu mmodzi asiyeni athana okha onse
Kkkkkkkkkk
kkkk zamnyumba eti??? kkk
Kkkkkk pepani ukongwa
Awachita bwino atolankhani a MBC auchikape munfinyenso bwana wanuyo kenako musegule makomo onse andende akaidi abalalike ngati nkhwali mu udzu
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Hahahahaha!!! Kkkkkiest
Kkkk koma adha inunso
Kkkkkkk koma inu ndi more
kkkkkkkkkkkkkkkkkk
Kikikkkkkkkkkkkkkknaneso ndaseka Nawomwekkkkkkkk koma abale nde mukusekesa bwanjkkkkkkkkk ah!
Apo inu akumaula munalakwa mtolankhani sakweza malipilo amunthu munapanga zosakhala bwino munaphwanya ufulu waa mzanu osamatero
…,,,,,,……
Iyi Ndi nkhani yosangalasa popeza amenyedwawo ndi atolankhani aku MBC omweso ali a DPP
Gud newz
A teacher quits teaching,a doctor quits treating patients kikiki a prison warder beating up a journalist hahahaha mbuli
I thought these people are being identified by their IDs???? kkkkk someone was sleeping on duty i guess,,,,,ndiye poti ndimbuli zisiyeni zikhare mbuli.
Kkkkkkkkkkkkkk a MBC?? aaaaa hahahaha
kkkk ukamananazo anthu okondera awa
Anakaputa njuchi zawana mmm kkkkkk kkkkkk anaishosha hhhhhh kkkkkkkkk Munyanya a MBC kkkkk zilindi ukali zimenezo samala
acita dala anadziwa kuti always mbc is pro govt, mbc siingasapote stilaka imeyo
Ndiye zafika pa mwana akana phala kkkkkkkkkkkkkkk khofi ilo! Mmmmm sanafufume ngati chimutubi?
Muziwatero m’mbuyomu bwenzi nkhani zawo n’zosakondela. Akabwelaso akwapuleninso
MBC inatha kale Palibe amavera olo mukanamaliza ndi kuwakomora sitikanadandaula.
Meydey meydey over!….tcheeeee…bad signal…
Awachita bwino amenewo,
Akanangowatsekela basi…kkkkk
Kkkkkk that’s good news
Amenyedwe kumene,tsopano otamika ndi mateagas sanabwere kuzaphulitsa?.akanapezeka nawonso apasidwe makhofi.
Eee Ku Malawi Kuli Bwino,kuchama Basi
KKKKKKkkkkkkkkkkkkkk MBC is loosing credibility now kkkkkk propagandas will take u no where. Akanamudula ziwalo Philip Business kkkkkk
kkkkk*mpaka ziwalo**?
Kkkkkkkkk afela nchito
anakanangowapha basi
Kkkkkk Kkkkkk chokomenta chagwera mkat.
Good job
ndipo awachita bwino kwambiri,kkkkkk,azanu ma radio ena akuwapatsa mpata ndipo akumapanga report bwino bwino,why only you akuswani makofii? mudzifunse? anthu anakudziwani pano kuti a mbc ndinu zitsiru,kkkkkkkkk.gd job,mukanakhala kuti munakwapulakonso filipi bisinese …
Kkkkk awachita bwino
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk ndye mwat awatan ahahahaaha achte nawo bac
kkkkk mwanyanya kujijirika nanu atolankhani penapake isaaaa!!!!!!!
Ok….chabwino tamwa.
good job kkkkkk
Awatuwisa ndi makofi? Hahahahahahaha!!
#Afusidwe basi.
# kumeneko ndikuphwanya ufulu wa atolakani ngati ulibe choyakhula kapena choyakha ndi ufulu wako kukhala chete osati kumenya.
Filipi Bizinezi amadziwa ufulu wa amzake??
Yes!!! amadziwa malile atchito yake ,ndimene amadyera patchito yake .Ndiye mukuwona ngati mutapanda kumuyakha mafuso akewo angakumenyeni?
nawonso ma warden ndimene amadziwira ntchito yawo,thats why awapambadzula ma cadets a mbc’wo
awachita bwino ana opusa amenewo, next time akazabweraso muzawamenye zolimba mpaka mano muzagululemo kt kwaabwanawo akanene zoona
Inu fillip yo anakuphwanyirani ufulu wanji?osamalowetsa ndale pamalo poti sipandale,ngati madana naye fukwa inu mmatsatira chipani chosemphani mchimene iye akumachiyankhulira sizikugwilizana ndiapa kwa Mmalawi okonda mtendere komanso omadziwa kuti tonse tinalengedwa ndi Mulungu mmodzi sangamati achita bwino kumenyedwa mkupanda umunthu
Adakapheratu Zikadakhala Bwino.
iwe chipirilo koma.ma cadeti aja akakhapa anthu kumisonkhano ndye umunthu umene uja????
zikukoma kt izi zikuchitikira adani amajority,,,ngtatolankhani ama media houses ena akuwapasa interview ndekt awawa ndunena aumbuzidwawa alindivuto,,,thibulani onse mosava chisoni cz mafunso amene angakufuseni ndioti ena achita kuwapangira,,,pondani aliyese kaya mwqngokumana naye mumsewu or sali paduty thibulanibe aphunzire ulemu
a MBC siatolankhani, they can be anything but journalists
ndi ma cadets ,kkkkkkk
Kkkkkkkkkkkkk
Ma prison awards bwerani mumuthibunso uyu ali mbali ya Cadet mwawatibulawo
100% ndilimbali yawo ndikulakwa kumeko awuze abwele.
ngati nd philip achita bwino
Kkkkkkk aitha heavy boma lingogulisa mbc alibe phindu
Kkkkkkkkkkkkkakakkakakakakakakakakakakaakekekekekekekekekekekekekekekekeahahahahahahahahahahahahahahahah mukadapha phillip Business an2 aukape kkkkk mukadaswedwa makofi nxt kungowaznga mitu
Ndiye akubweretselani nkhani ndani poti atola nkhani ana thidzimura
Kunyanya nanuso ngati mumadya kamera bwanji? Zinazi kumaonera patali anzakulira inu muwatolenso?
That’s good news
Atola Khani Athubula Funn M Lusaford Merrie Wa Nole Banda Zoon Kasani Evangelist Abel Angoni Kavala Payere Payere Christopher Chris Tuluka Wina Kakobwe Pelekamowawamalilo Kalebe Banda
kulakwa
Solution ndikungotulutsa akaiziwo basi nawo ankhale mfulu basi
#Malawi24 is nxt on the line
Amalengeza zabodza amenewo
Kkkkkkkk dziko ndiantu ake
kkkkkkkkk
Next FRANK KANDU
Ndie military imeneyo
Well Done Our Officer Even If You Shoot Them
Man, Malawi 24 are you reporters or jokers. mumangogemula zilizonse. i am sympathetic.
Zakhalaso buanji mesa paja mukuti Peter Mthalika ndiye wabwino, nanga zafika apa chifukwa chani?
Kkkk size ya boooh..angawone ngati moyo ngophweka….
Kkkk size ya boooh..angawone ngati moyo ngophweka….
Nawoxo asalimbane ndi atolankhan akadango tsekura ndende n setting all prisoners free zawo zinatheka in tme.but to act againest media will endup to no solution.
Achita bwino Kuwatibula Kkkkkk ine ndakondwa kwambiri
Kenako nose a ku MBC mudzaona zakuda ndithu!
Zitsiru zimenezi. Zibulidwe basi.
Ndimakape samati athawitsa akaidi?ndiye bwanj ma kiyi awasowa?ife timadikilira kuti abale athu atuluka
Makape ndiatiwo???????
Kkkkkkkkk fantastic news
Kkkkkkkkk fantastic news
Awakhuntha pang’ono amenewo
Vuto MBC ndi ya DPP amapangilapo campaign awachita bho hvy
kkkkkkkkkkkk nkhani yabwino kwambiri, akanawapheratu kkkkkkk
Kkkkkkkk anakawalandaso ma camera wo ndikuphwanya, then ndikuwa tsekera mu prison muja kuti akhaule hvy adyedwe mathanyula mmenemo!
kkkkk akanangotero zofuna zawo might be solved in tm.
kkkkkk kma ndeee mpaka manthanyula
Kkkkkkkkkkkkkkkk eya ka, asamayese ka!
Awachita bwino akazitape a boma ameneo
Good. They deserved to smarsh on there faces. How can one rejoice while the other one is crying. Akanawatchola miyendo kumene
Kwachema!!!!!
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk…….great news, munakammenya kwambira Philip Bussiness, amafusa mafuso and kuyakhula zopoyira zokomera ku chipani basi, ameneyi munakamubura koooooooooooooooopya?
Aziphikidwa kumene haha nkhani ya bho
Frank kandu joy nathu patrick simango and dj love osawa menya ndizabweza ine zachamba ay
Kkkkk koma Philip Business?
kkkk bola asadzaiware ma ID mugalimoto.Kkkk.
Sakulakwsa Awapangre Zmene Akufuna
kkkk no comment
azidyedwa makofi choncho maybe they can learn thru such.
Thats great news…. Im glad to hear that. Keep teaching them a lesson big up
awachita bwino sinanga makape amenewa ndiomwe amanamiza athu kut boma likuyendesa bwino zithu
So sad{Mwasala inu.}
Awa chitabwino amapusa, MBC imayankhula motumbwa.
Achita bwino kuswedwa
So sad{Mwasala inu.}
Sam Banda wa Blantyre Synod …azamenyedwaso nd ma coach coz amafusa mafuso achodziwadziwa
Achitabwino Kuwamenya Ndiyekuti Amafusamafunso Opoira
kkkkkk mwina amafusa mayankho,
Amafusa mowonjeza nde anthu ake azropewo
kkkkkkkkkkk MBC okha bwanji? Zodiak inali konko koma osaswedwa bwanji?
Awachita bwino 100% excellent, azichejera mpatowunitu pano, kuzolowera ma propaganda basi
kkkkkk anyanya mafunso aduka mutu…mapama ministries
Achita bwino kkkkkk
Anakawaswa mabhakera cuz makofi sawawa modetsa nkhawa
kkkkkkkk nde kut amafunsa mafunso Opusa
Ntchito dzina zophwetekesa