Atolankhani a ku MBC aswedwa makofi ndi oyang’anira akaidi, a bungwe anyangala

Advertisement
Malawi prisons

Bungwe loyang’anila ufulu wa Atolankhani mu chigawo cha Kum’mwera kwa Africa, koma la mbali ya ku Malawi kuno, la MISA Malawi lati ndi lokhumudwa.

Bungweli lati ndi lokhumudwa kuti ogwira ntchito awiri a nyumba youlutsila mawu ya MBC anamenyedwa pamene amakatola nkhani ya zionetselo za oyang’anira akaidi.

Malinga ndi chikalata chomwe watulutsa nkhalapampando wa bungweli, a Teresa Ndanga, a MISA ndi okhudzidwa kuti Atolankhani anachitidwa chipongwe akugwira ntchito.

Iwo ati izi ndi zoika pa chiopsezo ufulu wa Atolankhani ndipo sizikuyenela kumakhala choncho.
Mtolankhani wa ku MBC, a Patrick Dambula anamenyedwa limodzi ndi ojambula zithunzi wa ku MBC ku Maula komwe amakagwila ntchito.

Iwo amakajambula za kunyanyala ntchito kwa oyang’anira akaidi.

Advertisement

204 Comments

 1. Musasiyile Pompo,,,,, Mumenyeso Prezdent Wawoyo!! Amene M,mati Pitalayo. Zintax AchebeMan Wa Zintambira Fätsäñï Fäxýbwõï Rüssïæn Birdman Lpsgc MW TinTin Vynteen Chifu Stevie Di Biest Nkhata Zintax AchebeMan Wa Zintambira Man Fedzy Wa Undiscovery Kholowa Ç Ger Mashini Misslinah Mzumara Mathews Troopad Nkhata

 2. Awachepesa tikati tamvela zabwino pa mbc zizikhala zanyengo basi ikakhala mbctv ndiye ali busy ndi program ya malata ndi cement ati osika mtengo,,, thanks for MACRA popeleka ma certificates kwa ma mbc ozindikila,,

 3. Thats being savage…violence isnt a solution…its not a part of self help remedies kaa….now the grieved p/warders myt be facing battery charges

  1. Nanga kumenya atolankhani ndiekuti wina Ku mati achita bwino atakhala iwowo kuti amenyedwa angave bwanji vuto ndiloti tikumalowetsapo ndale pena paliponse tieni tizitsata chilungamo cha zomwe zachitika

 4. Both Sides Are Offside:journalists You Communicate With A Spokesperson Dont You? What Were You Doing With All Guards? To The Guards:do You Go To Church And Learn About A Great Command That God Gave Us? (Love Your Neghbour mt 22:39]Ok:who Is Your Neghbour? Your Fellow Civil Servant,how Come That You Slapped Him? Demons In Malawi Are Tormenting!

 5. This Malawi24 reporter seems very happy while MISA Malawi is disappointed with the Warders savage actions. Was there no better words than “aswedwa makofi”?.

  1. Chikufunika simatchulidwe amau koma ntchito imene oyang’anira ndende agwira or akanati aphikidwa,atibulidwa,means kumenyedwa basi kkkkkkkk ndipo ma reporter a mbc tsiku lina azatikitidwa pankhani zandale this is the first stage

  2. Poti zomenyedwa kapena kuphedwa ndi zomwe Atolankhani amakumana nazo, nzosadabwitsa ndipo onse amayembekezera zomwezo, imanena ndi nthawi.

  3. sanati azitibulidwa amenewa chifukwa cha ukadeti wawoo,kkkkk,paja ma journalists azawonso a ku times anawatibula a mbc times itatsekedwa you remember joe west? hahahaaa

  4. Kondwani, can we for once admit that we copy everything we will never understand for the sake that we are Africans.

 6. Vuto lilikwathuko eti atolankani A MBC ndioimira chipani cholamula boma ntawi zonse, MBC sibungwe loima palokha ai limaulutsa, kapena kutora ndi kulemba nkani zoyamikira boma limene likulamura, or zintu zikuonongeka mbomamo, amangoti zilibwino, ndibungwe laboma ntawizonse

 7. Pamenepo M pamene paonetsa kuchepa mzeru kwa ma prisoner warder wo fukwa nkhani yamalipiro mtolankhani sizikumukhudza,speaking frankly your all stupid,ndipo mmene mumka vomereza malipirowo simadziwa kt azanu mwawapezawo amafanana Kapena kusiyana malipiro ndi apolicewo?nthawi zina osamangothamangira kuti bola ndalembedwa kma kumaonanso ma benefit kuti akuti bwanji?mkumasaina bwino,mavuto ngati awa bwanzi kulibe kma kumenya atolankhani ndiumbuli waukulu sitingasekelere

  1. Point of correction,,,Mw Prison Service,Mw Police Service n Immigration Department are all under one umbrella bwana,Ministry of Home Affairs & Internal Security.Masalary samasiyana zimafuna ziyambike panopa.Hope u have been cleared.we dnt condorn ths behaviour of manhandling reporters is wat is being discussed here osati kuthamangira kutukwana musakudziwa chilichonse.

  2. Ndiye kuti mukuikira kumbuyo kumenyedwa kwa atolankhaniwo,fukwa ngati zasintha panopa kma poyamba amalandira zofanana akuyenera kutsata njira zoyenera osati kumenya atolankhani,kuotcha mateyala,imeneyo si strike kma demostration yoononga zinthu

 8. Awachita bwino atolankhani a MBC auchikape munfinyenso bwana wanuyo kenako musegule makomo onse andende akaidi abalalike ngati nkhwali mu udzu

 9. Apo inu akumaula munalakwa mtolankhani sakweza malipilo amunthu munapanga zosakhala bwino munaphwanya ufulu waa mzanu osamatero

 10. Anakaputa njuchi zawana mmm kkkkkk kkkkkk anaishosha hhhhhh kkkkkkkkk Munyanya a MBC kkkkk zilindi ukali zimenezo samala

 11. KKKKKKkkkkkkkkkkkkkk MBC is loosing credibility now kkkkkk propagandas will take u no where. Akanamudula ziwalo Philip Business kkkkkk

 12. ndipo awachita bwino kwambiri,kkkkkk,azanu ma radio ena akuwapatsa mpata ndipo akumapanga report bwino bwino,why only you akuswani makofii? mudzifunse? anthu anakudziwani pano kuti a mbc ndinu zitsiru,kkkkkkkkk.gd job,mukanakhala kuti munakwapulakonso filipi bisinese …

 13. #Afusidwe basi.
  # kumeneko ndikuphwanya ufulu wa atolakani ngati ulibe choyakhula kapena choyakha ndi ufulu wako kukhala chete osati kumenya.

  1. Yes!!! amadziwa malile atchito yake ,ndimene amadyera patchito yake .Ndiye mukuwona ngati mutapanda kumuyakha mafuso akewo angakumenyeni?

  2. Inu fillip yo anakuphwanyirani ufulu wanji?osamalowetsa ndale pamalo poti sipandale,ngati madana naye fukwa inu mmatsatira chipani chosemphani mchimene iye akumachiyankhulira sizikugwilizana ndiapa kwa Mmalawi okonda mtendere komanso omadziwa kuti tonse tinalengedwa ndi Mulungu mmodzi sangamati achita bwino kumenyedwa mkupanda umunthu

  3. zikukoma kt izi zikuchitikira adani amajority,,,ngtatolankhani ama media houses ena akuwapasa interview ndekt awawa ndunena aumbuzidwawa alindivuto,,,thibulani onse mosava chisoni cz mafunso amene angakufuseni ndioti ena achita kuwapangira,,,pondani aliyese kaya mwqngokumana naye mumsewu or sali paduty thibulanibe aphunzire ulemu

 14. Kkkkkkkkkkkkkakakkakakakakakakakakakakaakekekekekekekekekekekekekekekekeahahahahahahahahahahahahahahahah mukadapha phillip Business an2 aukape kkkkk mukadaswedwa makofi nxt kungowaznga mitu

 15. Atola Khani Athubula Funn M Lusaford Merrie Wa Nole Banda Zoon Kasani Evangelist Abel Angoni Kavala Payere Payere Christopher Chris Tuluka Wina Kakobwe Pelekamowawamalilo Kalebe Banda

 16. Nawoxo asalimbane ndi atolankhan akadango tsekura ndende n setting all prisoners free zawo zinatheka in tme.but to act againest media will endup to no solution.

 17. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk…….great news, munakammenya kwambira Philip Bussiness, amafusa mafuso and kuyakhula zopoyira zokomera ku chipani basi, ameneyi munakamubura koooooooooooooooopya?

Comments are closed.