Letsani mitala ndipo pasapezeke obeleka ana oposa awiri – Phungu auza boma

Advertisement
Maize scandal

Phungu wa dera la kumadzulo mu boma la Nsanje, a Chidanti Malunga auza Boma kuti likhazikitse lamulo loletsa a Malawi kubeleka ana oposa awiri.

dr-joseph-chidanti-malunga
Chidanti Malunga: Anthu asamakhale ndi ana oposa awiri

A Malunga anauza wailesi youlutsa mawu ya boma ya MBC kuti boma likuyenela kuchitapo kanthu kuti achepetse chiwelengelo cha anthu mu dziko muno.

“Anthutu tikuswana ndipo ngati sitichenjela, tikhala pa mavuto adzaoneni,” anatelo a Malunga.

Iwo ananena kuti pofuna kupewa mavuto amene angadze ngati a Malawi angapitilize kuswana ngati ngumbi, Boma likuyenela kukhazikitsa lamulo loletsa anthu kukhala ndi ana ambiri.

“Tikati banja lizikhala ndi mwana m’modzi basi ndiye ilakwa, a Malawi ambiri savomela. Koma tinene awiri, anthu asamakhale ndi ana oposa awiri,” anatelo a Malunga.

Iwo anaonjezelapo kuti Boma lionjezelepo poletsa mitala.

“Mamuna azikhala ndi mkazi m’modzi basi. Osati uku mkazi wina kukabeleka ana kumeneko, uku wina kukabelekako ana,” anatelo a Malunga.

Advertisement

682 Comments

  1. Sizona Zimenezo,poti M,malawi Akazi Ndi Ambili Kuposa Amuna Ndiye Ngati Sipakhala Mitala Akazi Enawo Azangoffelamo Osalawa Mwamuna.Mukati Tisamabeleke Ana Osaposa Awili Dziko Tiligonjesa Poti Baibulo Linati Tibelekane Ngati Mchenga.

  2. Singing…..mawu awa tidzawakumbuka …tsiku lina kutsogoloko ……kkk now despite kut umabereka omwe utha kukwanitsa kuwasamala komabe mbuli ndizambiri kuno ku nyasa zomwe zikungoswanana mwaumbuli…..ngat cpangakhale lamulo tidzalira kutsogoloku ndithu…..

  3. Ine Koma Ndikadakonda Kupanga Lamulo Lomanga Kapena Kulipiritsa Anthu Awiri Amene Apatsana Mimba Yapatchire..Coz Ndi Ana Apatchirewanso(opanda Dongosolowa) Kwambiri Amene Akuchulukitsa Chiwerengero..Tianyamata Ndi Tiatsikana Tongoziwa Kugonanati Koma Osaziwa Kusamala Tikhoza Kuona Polekera…

  4. Uyu asandilankhulise pambali uyu. Aliyense amabeleka malingana ndi mmene angakwanitsile kuthandiza family yake. Iwe ndindani kuti ukakambe nsete ngati zimenezo? Litakhala boma la southafrica mwina ndi pomveka chifukwa mwana aliyense yemwe amabadwa amalandila thandizo R335 yomwe imapanga close ku 40pin yamalawi pamwezi kuchokela kubadwa mpaka 16 to 17yrs. Now iwe ndi ndani ndipo mmapangapo chani ndi boma lanulo pothandiza ana omwe akubadwa? Mosakunyengelela ndingoti #pansana pambuyako ndithu nana iwe.

    1. C aliyese man….come here in lakeshore areas akaz ambili alibe mabanja bt ali ndi ana odutsa awiriwo….on a sad note…akaziwa alibe pogwira …do u think anawa asamalidwa bwino?mbava zamtsogolomu…. U nid to digest his idea mr man.

  5. MWATOPAKO KU PARLIAMENT KO?BWELANIKONI.MWAIWALA KUT TINAKUSANKHANI NDIFE LERO MUKUTIIKILA ANA MALIRE MUMAWADYETSA NDINU?ZACHIBWANA AI.INU MULI NDI ANA ANGAT?NGAT AKWANA 4 ENAWO APHENI NOKHA AGALU.THATS SENSELESS.

  6. Awa ndiodwala akusanje awa asawona angati chani zoposa zofoirazi.Olo munthu usakwatire mitala mkazi wachiwiriyo sazakwatiwanso?

  7. Iwe ndiye ndi wa wachitatu m’banja lomwe udabwadwa, had it been so dat tym bwez ulikut iwe????? Nanga omwalira azimwalira angat bwana MP???

  8. Koma mukuti ndindani kapuku akunena zimeneziyu asatiyakhulitse pambali pamene pakati tikupaona pliz ndipo ndisamveso nkhani ngati imeneyi ndindanii yemwe safuna kukhala ndi ana pamoyo wake kodi malemba ndekuti akwanilitsidwa aja anati tichulukane ngati ntchenga aja hey wena pasop uzofa wena sathana

  9. Akulephera kuchita chitukuko wayamba zimenezi eti. Mmalo mopempha boma kuti limange mseu ochoka paboma kupita ku Marka akupempha zautsiru. Ma MP anzako akuchita zitukuko koma iwe ayi tionana 2019

  10. ine nkhanii palibe icho nduvupo coz sukulu nazo munakweza ndichifukwa chake anafe sitikumachedwa kulowa mbanja nanga tsono tilekelenji kubeleka ana momwe tingafunile chonde malunga muganize bwino

  11. Ask God for wisdom,,,, we are not wise enough to tell God what to Do,,,, Some of the rich people are suffering from diiseases like cancer, docctors told them to wait for the day of their death,,,, do not guide God but God must guide us

  12. I don’t depend on government I work hard my self who is that phwala to stop people from having more than 2 children anthu anakusankha kuti uzipanga chitukuko not to talk sh**there

  13. kuda unada tima umene chisulu kutengela kugwa papaya eti bible limati tibelekane ngati mchenga ndiyeiweyo zopusa zakozo wazitenga kuti.kusanje munabeleka satana ,basi munthu kuda nditima umene,kkkkkkk mbuzi

  14. Trump adakamba kale za ife ma Africans, timakonda izi zikutibeleketsa ana popanda plan, kubeleka ana ngati mbewa. UYU NDI PHUNGU WANZERU KWAMBIRI. Chilengedwe chikuonongeka chifukwa cha kuchuluka kwa demand kuposa zomwe chilengedwe chingakwanitse kutipatsa. Dziko lathu likungosaukabe chifukwa tilibe population control policy yothandiza. Pokhapokha boma litachitapo kanthu pa nkhani ya kubelekana ngati nkhumbaku, sitidzatukuka olo ndi pang’ono. Ngakhale titasintha olamulira motani, mtsogoleri aliyense adzakhala olephera. Kaya chipembedzo ngakhale wina aliyense, palibe nzelu pakumafuna kuti anthu azibelekana mwachisawawa.

  15. Zautsiru Bas ngt dziko likukanika kulitukula ndiye anamizile ana mmm asowa zochita eti mm ife zotinyasa ayi pano inu mukudya money muli phee bas mzinyumba zanu ndiye kumayankhula mbwelera zoona

  16. mmalo mopempha chitukuko kut boma likupangileni kudela kwanuko basi just wasting time for nothing. u r so stupid, amzanu akumapempha zipatala, misewu, maschool. misika yabwino, ndizina zambili, basi inu ndikachaso wanuyo wa misonkho ya amphawi nkumalankhula mbwelela zenizen. shame on u

  17. Afufuze kaye ngati iyeyo bambo awa anangokwatila mayi awo asapangako chibwezi ndiwina kod mitala inabwela ndindani mitala imabwela munjila zosiyanasiyana ena amakwatila pofuna kuthandiza azimayi ena ndiovutika ena ndiamasiye komaso chiwerengelo chazimayi ndiazibambo ndichosiyana akazi ndi ambili azibambo ndiochepa ndiye choletsela mitala ndichiyani

  18. kwa amene akudzwa blive ya msanje mp sanalakwe km ngt muli nazo dzwan kt mene ana anu adzadutse pa awiri muzakhala mulibe palibe chosatha ndbwnokuganiza b4making dsion take care

  19. Mukuletsa mitala koma muzikhala ndima side-girlfrends, imeneyo ndiye mitalayo! Think wisely musaiwale kuti kuli ufulu wachipembedzo

  20. Ngati ukulephela kuwasamala azibale ako zako zimenezo ife tibeleka 8 wanva achina pina akuvutika uko koma osawsamala ndie uziti ana awili machende ambuzi

  21. Kunotu ndiku Africa ukati tidzibereka ana awiri NDE kuti chani inukwanu mudabadwa ana a ngati?aliyese alindiufulu kukhara ndi ndi ana ambiri cox ariyese amasamara ana ake akha ,iweo ukupanga lamulo limeneri ulindi ana a ngati???zaziiiii

  22. Komanso Akupanga Zopoira Waona Kut Alndi Ana 4 Iyeyo Ndiye Akufuna Apoilise Ife Otsalafe Nanga Akwawo Avomera Ammutsidyao Koma Shaaah Guyz Mkaz Wake Classmate Wanga Wakwa ngabu Chkwawa Eeeh Mlungu Dalitsani Anthuwa Asiye Kuyankhula Mau Onyansawa Coz Munat Tiberekane As Mchenga.

  23. Aaaaaaa uku nde kusowa mfundo, mulesa bwanji mitala as if anthuwo muthandiza ndi inu? and mukalesa mitala akazi mmebe achulukiramu akwatiwa ndi ndani? mapeto ake moyo wa zibwenzi uchuluka which will result in high population yo plus HIV AIDS and poverty.

  24. ZOPUSA BASI !Mumatithandiza kutidyetserera ana ? Kulimà chakudya mumatithandiza ? Ngati Penis yanu yagonja chifukwa chobwinda ma Secretary anu zanu izo

  25. we can’t agree to have two children here in maawi…this is because child mortality is still here therefore low chances of those two children surviving…

  26. kkkkkk ana 12 anyumba imodzi mwayamba kuwakana after akupatsani mavote, lero wakana mawa tsiku lija la 2019 ndi 2024 udzawafuna utisiye tikazibelekana chakudya chako chili n’chiwelengelo chathu.

  27. Kuyankhula ngat ukumagawa ndalama bwanji anthu opusa inu chonsecho mu nyumba ya malamulo ndinu abububu mumangoganiza zokuba chithandizo cha anthu ovutika zimenezo zako iwe ndi akazi ako kwanuko chifukwa ndi amene amadya zako

  28. Takambilanani zanzeru osati zopusazo.we have big problems in Malawi like kusowa kwa madzi kuvuta kwa magetsi.misewu yoonongeka and poor education facilities, poor health facilities. Fix these things first. That’s what we want you to discuss there

  29. Ana awiriwo muziwayang’anila ndinu? Mukakhala ku paliyamenti kwanuko muziyamba kaye mwafunsa anthu amitu yakuthwa bwino.
    Munthu uli ndi ndalama zambirimbiri mwayi wa ana ulipo, ungalephere kubereka? Kuganiza kosapititsa dziko patsogolo. Ngati akukuvuta kusamala anawo iweyo, sikuti aliyense zikumuvuta!

  30. kodi iyeyu kwawo anabadwako angati,nanga iyeyu alindi ana angati? mupeza kuti alindi ana kuvibwezi kokha 50 pakhomo 12 ndiye lero azikati ana awiri mwayamba kutsutsana ndi MULUNGU kodi yemwe anati tibelekane ngati mchenga,abwana phwando la u mp lakoma mpaka mwayamba kumwela zikho za YEHOVA kodi? ayi akungopenya posachedwa dzanja lake lilemba khoma bachitani chimkondwemkondwecho tiona mathelo ache.

  31. Yamake ka MP kameneko!! ieo ndiwa number chiani kwauko??? ieo ndimkhiwa?? Tamuuzeni kuti zamanyizo kuMalawiko aiii, ndikabwera ndikapha ameneo bcz akutsutsana ndi BIBLE! Bible says”chulukanani ngati nchenga wa panyanja”! Ieo akutsutsa mauo? watisie ife tidakali ndimphamvu.

  32. Mwayamba misala inu kwanu mulipo ana angati tamangodyani ma allowance si dzachambazo malo mokamba mfundo zotukula Malawi bansi zokamba zimenezo May God Forgive You

  33. Iwe ndimwana wanamba 4 kudadwa m’banja la ana 7, panthawiyo pakanat papezeke munthu oiwala chomwe akufuna kuyankhula ngat iweyo nde ukanabadwa?

  34. Midoli Yamupweteka Eti,moti Azikhala Busy Kukambilana Kt Chuma Cha Malawi Achitukule Bwanji,kumangoganiza Zakuchipinda Basi,,,,anao Azikadya Kwao??

  35. Midoli Yamupweteka Eti,moti Azikhala Busy Kukambilana Kt Chuma Cha Malawi Achitukule Bwanji,kumangoganiza Zakuchipinda Basi,,,,anao Azikadya Kwao??

  36. Komanso nanga akazi otsalawo azichita uhule?? Ndee bola akhale pamitala kuopeza uhule omwe umasokoneza ma banja a anthu…… Panopa pa anthu 10 aliwonse mmodzi kapena awiri ndi mamuna enawo akazi …… Ndee akti mitalanso ayi akufuna akzi otsalawo azisokoneza ma banja aeni???

  37. I agree with you honourable. With the population explosion and the dwindling of basic resources we are encountering in Malawi there is need to reverse the trend otherwise poverty will cling to us like leprosy. Ndipo anthu omwe amabereka ana ochuluka nthawi zambiri amatero podalirira thumba la wachibale amene akuchita bwino because of his/her responsible parenthood. Umbuli ndi matenda owopsya ndipo osachiritsika.Check the multibillionare Bill Gates the number of children he has. But you wonder the poorest people having unnumbered children. Bomalo litilera mpakana liti? Let’s be responsible a Malawi.

  38. Dont forget during elections you need more people to vote for you, arent you? Therefore talk of development especially in education, farming and health.

  39. Nanga popeza nanenso ndiwachitatu pobadwa kubanja lakwawo akadaganiza mopanda nzerumo makolo ako bwezi ulipo iweyo zopusa basi wasowa mfundo zachitukuko eti

  40. phungu ofoila uyu iwe uli ndi ana angat kwanu ena obelekela mahule otaya nde osanena tikuonela 2019 uchite kuda ngat usiku 5 kopanda magesi ndi mwez

  41. uzinena bwino 2019 yafika kale anthu amene ukuti ali nditiyana tambiri wafuna komanso sitipempha ufa kwa iwe kapena umagwetsa mvula ndiiwe anakamkala kuti mai ako anabeleka ana awiri iweyo unabadwa mutu kuda ngati kazizi waba zambiri ndalama eti tikuchotsa chaka chibwerachi

  42. Mmmmmmmkkkkkkk Koma Mp Ameneyu Waganiza Bwanj Chfukwa Pali Anthu Ena Amabeleka Ana 4 Mapasa Nthaw Imoz Or Mwna Atatu Monga Mene Mulungu Wapelekela Mphatso Zawo Ndye Bac Iyeyo Wakut Pasapezeke Obeleka Ana Oposa Awiri Sopano Zkhala Bwanj Kwa Amene Akumabeleka Ana 4 Panthaw Imozkkkkk Aganize Bwno Mp Ameneyukkkkk Iye Sakuzwa Kt Kubeleka Nd Chsis Chamulungu Kkk

  43. Nkhani yabwn cz tiyeni tione mmene zinthu zikuendera pn kale2 zinthu zinali bwn makolo athu amabeleka ana ambili nanga pn mmm ayi inafe tikuonjezadi kukhala ndi ana ochepa ndikuwapitisa ku xool komanso utha kuwasamalira bwn enanu mukuti nanga akafa mmozi chabwino nanga mutabeleka ana ambili inuyo ndikumwalira zikumathekanso kt osamala anawo alinso ndi ana ake ambili motero anawo akumakhala paumphawi tiyeni tiunikilanepo apa bwn sizotukwana km kuthandizana mzeru

    1. Anganga,kaletu anthu samasolora ngati m’mene anthu akubera since Udf from 2004 mpaka pano. Iwowo akuba ndalama zomwe zikanatha kutukula dzikoli,akutenga ma tender oti anthu wena osati am’bomamo bwenzi zitapindulira ambiri koma zonse amaphangila,ndalama ikupindulira omwewo dzaka dzaka dziko litukuka bwanji? Ndiye mukati tisabalane kwambiri zitathauzanji? Iyeyo akuthandiza angati anthu apadera osati abale ake dera la kwao?

  44. Kusowa mfundo kodi?
    Kapena kupekewera nzeru ,
    Mabvuto onse omwe Ali kumalawiwa zolankhula mfundo zake zimenezo?? Ndinu ndani kuti mulese kubeleka ana oposa awiri

  45. Iwe Malunga,dziko lapansi ndi lako?mesa mulungu anati tichulukane ngati mchenga?ndiye ukutsutsana ndi mlengi wako? Akutukana aja acìta bwino ‘ndife mbumba ya Adam zizukulu zake za Abraham’ ngati mabatiri ako atsiya ku tchaja undilembe ganyu ndizikubelekera ana mnyumba mwako wamva? Mukufuna muzitiphera ana mzipatalamu eti? Lamulo limenelo kwathu ku Machinga lisafike lizakhale ku Nsanje kwakoko,galu mphaka iwe.Anthu akachepetsa ana nde Malawi kuzabwera mgodi wa siliva ndi golide? Feteleza azatchipa,magetsi sazizathima? President,nduna ndi aphungu azaleka kuba ndalama za boma ana akamabadwa ochepa? Wamisala iwe eti.’Malawi akusauka kamba ka umbava m’boma osati kuculuka kwa anthu’chitsiru cha satana mufuna muzibaya azikazi athu ma jakisoni achabe? Azimayi chenjerani mzipatalamo nkhaniyi ndiyowopsa muzandivomereza tsiku lina

  46. Awapangire plan athu angat amapasa soap ofuna mitala azipanga osakufuna samapanga galu wake mwati ndani wslakhula zimenezi kamuwuzeni musunu wakewo

  47. A mp WO alindi ana awiri? Zopusa eti maximum izikhala 4 and uzibeleka according to ur pocket if u can financially support 4 etc bereka hahaha

  48. Mmalo mopempha zitukuko kudela kwanuko basi busy kukamba nkhani zopanda pake,mfundo imeneyi ndiofunika kukhazikisa pabanja lako ndi onse amene amadalila thumba lako muuzane osamangopitilako zibwana kumeneko

  49. Akuluakulu I was there and Honorable Chidanti Malunga Sadauze Boma Zimenezi koma amauza atolankhani in his “Opinion” as with regards to how we can control the over growing population that is in turn exerting pressure on the environment. He said this in Zomba During the Lauch of ASSETS findings Research Project that was done by LEAD. So save the anger, the honorable MP was speaking his mind. We cannot all be Chidanti Malunga.

  50. Iye Ali ndangati???? Ngati Ali ndioposera awiri atiuze enawo tinyonge akhale NDA awiri, ngati alibe ilo ndivuto LA mchiuno mwake apondeponde, ine sindidaati kubereka ndikuberekesa, bwanji mufuna kutilakwisa berekanani muchulukane ngati ………………….wapadooko

  51. China did it and it worked for them . Malawi however isn’t ready for such . 2 children maximum would be good. It would make sense economically. Malawi talks of development but she is not ready to pay the price of it.

    1. Ife kwathu tilipo ana 12, sitinabadwire ku China. Funsani chiwerengero cha China? Nanga anthu angati ali pa ma Arv mdziko muno? Tiyeni tiziganiza 20years later osaganiza za pompo

  52. Iweyo uli ndi ana angati? nanga ku ku zibwenzi zako kuli ana angati onse pamodzi? kapena ukutengera kugwa mpapaya kwakoko eti? mbuzi ya munthu! wasowa mfundo eti, nanga bwanji osangokhala chete, tamuoneni nkhope ngati loweruka.

  53. Akunena zoona cz amalawi umphawi wachuluka xinthu zikusintha daily Mabanja amene sakulimba zikupedzeka kut mai alindiana 5 koma akusamala yekha zosakhala bwino kuzunzisa ana maphunzilo palibe owathandiza ine mfundo imeneyo ndikugwilizana nayo

  54. Kumangokamba Zopusa Basi Anayesanji Anakuvoterawo Munthu Opanda Mfundo Iwe Iwe Pamene Wasiya Kuberekapo Ukufuna Uwakhomerere Amzako Pita Uko Ndimfundo Zako Zopoirazo

  55. Wat i learnt is that in other richer countries the gvt takes action on bearing of kids,which makes anthu have smaller number of kids in their families kut atukule dziko lawo.n if old ones who can’t tukula dzikolo achuluka,families r told by the same gvt to bear mo kids kut ther Should b more energetic young anthu to tukula their country,that’s generations gap.whilst here in maiko osauka yes gvt can say have smaller number of kids,but many times it can’t work cz many anthu av no other things to do than making babies since ther are few jobs n zochitika zna for munthu to be doing n sizikhala zodabwisa to c anthu having more than 3kids in their families.but we really can make a change cz kudalira kwachuluka kwambiri. Its a welcome development.

  56. Fundoyi Ndiyabwino Kwambiri Ngakhale Ena Mukulesa Vuto Mukabeleka Ana Phwi Ngati Ankhanga Njala Ikafika Mumatukana Boma Ndi Mabungwe Kuti Sakuthandizani Ngati Bomalo Ndilomwe Linakutumani Kuti Mubeleke Anawo Ana Ambiri Koma Polima Mulibe Muziwapasa Chani Anawo? Munthu Akazi Atatu No Chochita Zachamba Bas

  57. Bwana mp, msatangwanike ndi zozila,kumbukani mmalawi muno muli mavuto ambili, kusowa kwa mankhwala okwanila,kukwela kwa katundu,kusowa misika ya mbewu,kosowa kwa mijigo,masukulu abwino,miseu ndi zina zotelo.Mr mp simnasakhidwe kukamba za mitala,yomwe inayamba pachiambi aAdam ndi Eva atachimwa.

  58. that’s why Malawi is poor, timasowa zonena zaphindu mmnyumba yamalamulo ana ndiomwe akukanika kutukula dziko? or anthu andalenu mukamaba ndalama zaboma kupepela madazi petupetu ati amthu amzeru chonsecho mmitu mulibe aliyense wake up man, talk of something very concrete

  59. What a rubbish proposal iwe ukuziwa kuti for every 100 children born 70 are girl 30 are boy ukaletsa mitala akazi osala 40 akwatiwa ndindani ? Iwe ndi amene umalimbikitsa same sex marriages eti satanic uzikapangila kunyumba kwako osabweretsa zimenezo Ku nyumba ya yamalamulo.

  60. Choyamba sakudziwa birthrate difference between girls and boys, Chachiwiri awapezere mabanja akazi amene samakwatiwao, Chachitatu iye siamene amadyetsa mwana wachitatu kapena wachifolo mmabanja ayiniakewo

  61. Mr MP I support by 100% chifukwa pamene Ali pano Malawi we are Les that 20 million ndeno tikafika 2 year s next ndimavuto opanda owathesa, this man he is right

  62. Niopusa….mkesa mukukula mimba nindalama zathu izo mulandira…..nimpando wandale uwo…kalankhulani zanzeru….iwe uli ndi ana angati….ngati ubala kwakuvutani…khalani chete…..mp….opanda fundo….no sence….

  63. APA tikungoyankhula zambiri koma nkhaniyi ndiyofunika kuyiganizira bwino aliyense malingana ndimapezedwe ake u can have ten children koma kulephera kuwasamala sizabwinoso kale ndi pano ndizosiyana, of course primary school ndiyaulele koma pali school fund just imagine upeza mwana walephera kupita Ku school becoz of school fund ndiye atati ayambe kulipira fees zingakhale bwanji? Tiziona mbali zonse zonse APA zinthu zikukwera tsiku ndi tsiku komanso zikusintha tsiku ndi tsiku munthu akhale ndi ana oti akwanitse kuwasamala

  64. Mukutsutsana ndimulungu musatilankhulise pambali.kodi mwazindkilaliti kuti anthufetikufunika tikhaleochepa.pachinachilichonse mulungu alinachondicholinga.kodi ndibwino kumvera munthu kasiyamulungu? Asatipusitse azunguwa chifukwa chaumphawi ikani maso patsogolo osasiya kutamandamulungu

  65. nonse amene mukutsutsa pa nkhani imeneyi mulibe nzeru, atsogoleri ngati amenewa ndiwomwe akufunika kulamulra dziko, muganidzre mene chwelengero chilili panopa and think of where we are going, kod mukuganidza kut umphaw umenewu udzatithera? ma resources amene tlnawo pano ndwochepa kwambri so tyeni mudzngoswana ngat makoswe choncho!

  66. Fodya wamukulu umamupweteka musiyeni nzelu zamuthela akuona nga ndi UDF et wayiwala kuti ndi DPP think twice b4 published hakwee

  67. That’s the way to go!! We’re too may and with our myopic politicians Malawi will always be poor and poorer

  68. This is absolutely nonsense. Why do you say parliament must approve a death penalty for those who steal government money? You want to tell us that all these problems in our country are coming because people are having more than two children? If a government official steals money from the government, is it because we are having three or four children? Let us look at our economy from the time of Dr Kamuzu Banda up to the present then we can have a better solution, we shall find out that Malawi can depend on its on. Find out the population of Lagos city of Nigeria. Always our leaders just think of punishing Malawians with stupid laws

  69. This Mp wanyasa ndimtima omwe ndithu.
    This fool’s of member of parliament must fall in 2019.
    Iyeyo ndiwaNumber 7 m’banja labambo ndimayi ake.
    He must know God, stop copying everything that fucken white people are doing.
    This rule belongs to your family only.
    Rubish

  70. I 2nd de point coz mmalawi muno anthu tikuonjeza kuswana..bolako mmataunimu,but mmizimu eeehh upeza kut munthu akakhala ndi ana ochepa ndie kut ndi 6

  71. Did you know that African population is very small compared to all continent and the higher the population the higher the continent is developed?eg Asia /China?

  72. A gogo ako anali ndi 10 square km of land. Koma anabereka ana 10. Mwana aliyense anatenga 1square km. A mayi ako nawo anapasidwa 1square km. Inu munabadwanso 10. A mayi ako anagawa aliyense 0.1 square km. Ndiye iwe ubeleke 10. Kodi anawo azagawana bwanji ka 0.1? Kuganiza ndibwino.

  73. Government must create more jobs, enawa amakhalira kugona kamba kakuti alibe chochita, kenaka basitu chaka mwana chaka mwana

  74. Since r still in financial crisis as a country, i request government to introduce fast fees on primary education and hospitals. Increase fees in secondary as u have done in colleges. Please fasten the national IDs to for easy implementation of these things. It when pple who need 20 children will realise the vital of having two children even one.

  75. l think all of you giving comments here are ignorant and you lack understanding and critical thinking. You need to analyse the statement before you comment to avoid the display of your foolishness and ignorance. Do you really know that the world is changing ? Lack of education is something I think is missing here. I would rather prefer if the government comes up with civic education on this topic so that some of us will be able to understand what the MP is trying to put across rather than giving stupid comments which lack understanding of the topic.

  76. Mbuz ya MP zokamba zinamusowa ngat iye akaz ake anasekesa or iyeyo sabeleka akhale choncho ife ndanyamata aphavu sitinanthe or mwana wake wamkaz tikhonza kumgwila ntchito galu nsena önyela mmadzi iwe ife tinakaswana ufune usafune wamva ukambe zina kaya ana 100 ndi anga bola ndiasamale bac anawo amadya kunyumba kwako usamaletu ndi malakhulidwe ako oyipao chisiru iwe undilakwisa bac

  77. If Malawi palament has one idiot member is this Chidanti Malunga. He is paramount idiot of all idiots in Malawi. Anthu aku Nsanje anabeleka satana in the name of this fucken son. Kuipa nkhope kofanana ndi mtima wake omwe

  78. Mr malunga anthu Malawi sadaphunzire mokwanira mmene angagwiritsire ma natural resources kuti apange cuma koma mosamala cilengedweco inu ndi anzanu mutere mucite kafukufuku 1ikani maphunziro one opindulira Malawi mchichewa adziva mosavuta 2mukhazikitse bungee lomwe lidziphunzitsa amalawi zacuma ndi kayendetsedwe ka bizinesi mchichewa 3english idziphunzitsidwa payokha as communication language China, Russia,India amaphunzitsa nzika zake mziyankhulo zawo koma ndiotukuka cifukwa cigulu cimamva ndikutsata zinthu 4aphunzitsi aphunzitsidwe mwaukadaulo kuti adziphunzitsa masayansi subject practically cifukwa colinga cophunzitsira nkuti akapange apply luso lomwe apeza kutukulira miyoyo yao komaso dziko most Malawian teachers are exam oriented as a result we fail to produce and export.chidant we are now friends.

  79. I think he’s mad he knows that ladies are too much than men if we don’t marry mitala where they gonna get husbands?this is malawi is not china

  80. Ngati mungayambe kuthesa mvuto laufiti kaye ndikhoza kugwirizana nanu. Poti munthu azunguwa akabereka awo awiri palibeso zoti mwina kubwere mfiti kuphera anawo , ndiye Malawi amene ndimaziwa ine azakuphera tomweto tiwirito ndiye mabvuto abale.

  81. APHUNGUNU ndamene mumakwatira AKAZI AMBIRI ndiye mudzitani AKALETSA????KUMENEKO NDIYE KUGANIZA MOPEREWERA,Mmalo mopempha CHIPATALA/NSEWU/SUKULU/MIJIGO ETC zothandiza kudera kwanuko MUNGAMAPEMPHE ZIMENEZO??????

  82. Kusakhala Ndi Nzeru Phungu Ameneyo Mmalo Moti Mzikambirana Zothetsa Njala Ndi Umphawi Kumatha Alawansi Ya Boma Kumakambirana Za Mitala. Mwina Shaft Ya Phunguyu Yilibe Mphamvu. Asiyen Akutha Kukhala Ndi Mitala Azitero

  83. kodi mp ameneyo ,ndiwachipani chanji abale,chifukwa wa MCP sangayankhule zopusa ngati zimenezo?do you know that prisoners staff are on strike? solve those problems

  84. Last time I checked phunguyo ngwa chifive mmbanja mwa kwawo nde tiziti he is too much greedy mpaka kunena kuti osaswana ngati mphemvu. Aaaa my foot zimenezo

  85. Mr mp ngat mwatopa ndikumulelera ana awina wake ingomuuzani zoyeneleka kuchita osat zikhudze gulu.

    Mzovuta wina wake kuti mumuuze pazakuchuluka kwa ana chikhalirenicho thandizo amasaka yekha

    Nkhani ngat zatha zoti mutha kumakambirana ndibwino kumasiyanapo msanga kusiyana ndikutulutsa ma bill okut sangatheke,cos aliyense amapanga maplan ake malingana ndimmene akumzimvera kapena kuganizira as long as he can afford for the basic needs

  86. Koma mbalame zinazi! Kuyima mkuyimako basi? Next term anthu ngati awa don’t vote for them. Kumangomadya misonkho yathu ya ulere.

  87. Africa Ni Africa Nkhani Yobala Ndiye Moyo Kwao Ndiye Kukamba Kwa Uyu Phungu Acita Monga Watukwana Koma Nizanzeru

  88. Bwana MP,, before you speak please understand peoples actions towards what you talk, implementing this law, it will have a positive and a negative impact towards the population and as well a sin against God, I can give you an example of china, the chinese government implemented this law 20 years + ago if am not making mistake and recently they are trying to revisit the law, because most of the children being born are girls, which is out numbering the population of men in china. So the motion in the house of common was that they should kill a girl child just born.

    Bwana,, it is good for we Malawians to remain as we are or try civic education campaigns about the demerits of having a big family towards social, economic and other services.

    I believe in Holy Bible and Qua ran there is no law which says ” you should have two children”,, as both muslims and christian believes that God told Abraham or Ibrahim to make his name father of many nations, it simply tells us to multiply as we can.

    Bwana about your point, many Malawians I dnt think will tolerate it to pass.

  89. Hahaha so shame on u !! Why dont u come with another wise topic, not this one its everyone’s right to be in polgymmy or no as long as he will manage to support them and a number of kids he agrees with the partner not coming With ideology like this, and people never voted for u to come with that nonsense like this, ask government to rescue people from porvety and youth unemployment not that rubbish u talking here

  90. ndkanakondwa kt bill imenei iduse. an2 tikuonjeza, infact, akanat m’modz like CHINA. an2 tikukhala ngat as if we r COMPETETORS kt tikufuna tiwine LOTTERLY.

  91. If government support the children,go ahead.. Otherwise you are challenging God..moreover how many children do you have..Think before you talk..

  92. Malawian reasoning !!” what about if one dies” mmalawi sazantheka. Umphawi basi tizafanawo!! Botswana only 2 million population. Ndalama yawo it’s almost 1 Botswana pullar to 50-60 Malawi kwacha. Malawi population almost 17 million now!!!

  93. That’s very good plan,kuifunira ubwino dzino.Mulungu anati ngati diso likukuchimwitsa ichotse kuti usachimwenso..Mulungu anati berekanani ngati mchenga koma ngati tikulephera kuwasamalirira ndibwino kubereka ochepa.Look Botswana as a country ndiku desert but ndiyochita bwino chifukwa population ndiyochepa.Tonse timadalira boma kuti mmabanja mwathu kuti ziyende,kwenikweni kuno Ku Malawi.pali zitsanzo zambiri zomwe timati boma timaidalira.

    1. Penapake osamangotchula dzina la Mulungu pachabe. Inuyo muli ndi ndalama zambirimbiri mwayi obereka ulipo mungalephere chifukwa cha boma?

  94. Wasowa chonena kape ameneyu,amene Anatilengayo anati Tiberekane tichulukane,iwe ndiye ndindani kuti ukatsutsane naye sample mayankhulidwe ako,komanso Palibe angaletse misala,siinayambe lero

  95. Umatilelera ana ndiwe,pita ukasambire mushire ngati wasowa chonena kudya ndalama ndi zamkutu.amvekele ndikuyimilira anthu amdera langa,bola kuimira makoswe kuti asaswane mnyumba mwako.

    1. akulakwitsa zinthu ndiwowa. kumamgoba ndalama zaboma nde ndkumablema anthu wamba whats that for. ana omwe sadabadwe akhala bwanji vuto. ana omwe alipowa mukuwaphunzitsa umbava ndinu akumaonera inu mmene mmabera mubomamu. nde pajatu nkhuku imaoneravmake kunyera mnyumba. ngakhale mukut pakhale lamulo loti aliyense azikhala ndi ana awiri awiri, koma ngakhale litakhalapo koma ngat mukupitiriza kuba mdalama zaboma mukuganiza zngasinthe? go to america kulibe lamulo lotero koma ndidziko lolemera, Russian, Arab countries ndmaiko olemera koma chfukwa kuli malamulo oletsa chinyengo omwe samaona nkhope mmaiko a Aluya ndchfukwa mulungu adawapatsa chuma. muyambe kusintha ndinu

  96. Ndiopusa uyu chosecho kwao anabadwa ana 9 nbanjamwao lelo nkumanena kuti pasapezeke munthu obeleka ana oposa awili zakumachende

  97. Yemwe sanasosoleletuyo zake.zimayamba chonchi tivomereze.gwirani ntchito mzipindamo ili lisanakhale lamulo amayi ndi abambo.mwamva?????

  98. People are a source of market for our produce, a source of labour for our production, among others. I think we dont have to blame people for the poverty we are in, blame government for not having good use of the growing population. Such policies are violations of human rights. Atleast try to invest in education for girls

  99. Inu madala mulibe nzeru mukutilesa kubereka ana opitirira 2 koma inu zibwenzi 5 anaso bwee! Ndiye mukuyankhula chani kanundu et

  100. Kkkkkkkk iyi nde timati Fundoless
    Kuli anthu mmanyumbamu akubeleka ana adzigololo mpaka ana 7 wina aliyense bambo wakewake nde ukanene zoletsa mitala kkkkkk zangovutapo panyasaland Lol

  101. Uchitsiru Sudzatha Amalawi. Anthu Osauka Osawa Pogwira Ana 10 Koma Anthu ozindikira Ndi Ochita Bwino Ana Awiri Basi. Kodi Mwana Kut Akule adziimire Payekha Mumaluza Chuma Choluka Bwanji? Ndiye X10, Mukanakhala Ndiawiri Better. Mufufuze China, Israel, America, Egypt Etc Anayamba Kale Iwe Ndiwe Ndani Kt Utsutse
    Awiri Bas Maganizo Abwino Zedi. China Chisatsutseso

  102. Malunga ndi MP opusa kwambiri iye waswaiswa ana Midzi kunsanje kwAkeko ndiye aziwamphwanyila ena ufulu imeneyo ndimbuzi Kwabasi olo boma Litavomeleza ine sindingasiye kubeleka Chifukwa chameneyo anawo amadyesa ndiiyeyo? Mphwala lake ameneyo

  103. Mr MP can you justify this with valid reasons of why this should be happening.

    Increasing in the population is very important Mr mp bcoz its a way of increasing HUMAN RESOURCES in the country which somehow is very important for the development of this country.

    Don’t worry with the increased number of people in this country, I blv you don’t know that God created natural ways of controlling this..

    If you think the increased number of people is the only reason of creating future problems in this country, then mmmmmm I think you have to revisit ur dictionary..

    The problems you and ur fellow MPs are enough to cause hefty or future problems than the number of people amene sanabadwe….

    How can the un born people create problems in the future while they are not yet born.. This is ridiculous…

    You may never know that out of many unborn people, one will be the person to come and rescue this nation.

    Solve the problems within the available population.

    You have to do a critical COST BENEFIT ANALYSIS, Then come back ok

    1. At Mr Justice G. Mikili even if u have 1 or 2 kids in Malawi, that can not be a solution to feature problems. There are a lot of factors to be considered, but not only overpopulation.. Suppose you have 5 kids, r you telling me that ur kids will be a problem of Malawi? Have many as long as you know that you can manage to manage or raise them, there I don’t see that can be a problem kkkk

    2. @ Beatrice that is also a big problem, you always expect to be employed…. Why can’t you think of doing something and then u shud be the one employing others… Be an entrepreneur!!!!

  104. I support him ine i only have two kids(girls) and there is no reason to go beyond that,what for?i will concentrate on the two invest for myself and for them…….. ana ambiri achiyani olo mpaka 4 mmmmmmmmm i dont care about having my name as most do for having boys after all i would be dead and am not sure what becomes after,as long as i grow my daughters in good spirit education and run business i would die a happy father period…no reason to chase for a boy child and in the end have 6 kids kkkkk

    1. I dont care of the name i will not be there after all my brothers have male children the name will be of them……. will i know whether my name is there or not when am dead noooooooo atleast i have a well established business well in my name thats a better thing to leave behind other than several children

    2. noel kp it up bola kuzawasiya ana akaziwo pabwino ndi chuma and ma future anyatwa than kuwasiyila dzina la nkhoma basi. enawa akazafa azasiya ana mbwe mbwe akukanganilana dzina lawo basi

    3. Kufuna kunditapa mkamwatu phungu ameneyo.

      The reasons for bearing a maximum number of two children is what I call (((Bombo craaaaat ?)))

      Funso loyamba:…
      1. M’bele mwanu ana mulimo angati?
      2. ………

    4. I support dis idea.mulamu wanga has 2wives.my ccta 6kids+10kids for the sekond wife.coz akufuna azasiye dzina.guys worysome.

    5. Zachamba basi pamafunika kumakhala ndi ana ambiri zoti ukadwalamo azikwanisa kusonkhelana ndalama mkukwana transport ya kuchipatala, and zokhuza kudyesa kapena kusamalira zimenezo amaziwa ndimulungu palibe angazitame kuti ine ndimaziwa kudyesa zonama amadyesa ndiyekhayo MULUNGU wathu, ndipo apapo ndili ndi ana 6 ndikufunaso 7

  105. Aphungu anthu mwatibweresera ufiti woopya muno chfkwa cha zokagula na Zanu zoti ufiti kulibe. Nde lero mkuona anthu abereke ana awiri nde fiti ziwatafune. Anthu andalenu ndamene mkutembelera Amalawi Kukhala pa malawi amoto

  106. pepi mr mp ngati mukuona kuti zikolathu tachulukana kulibwino muuze a p m f kuti akuombeleni ma mp nose kuti tichepeko koma osatiphela ufulu anafe ngati ndi satanik mualuka

  107. ameneyu. ndamene akulankhula zanzeru,, caz kumalawi kuno anthu tikuberekana kwambiri,, as aresult ana chitsamaliro chimachepa, @ pano dziko linasintha kubereka ana ambiri zichepe,

  108. Matako yinu ineyo ndibwereka mmene ndingafunire nobody can stop raggie apart from my wife and i mama and i

  109. School ku primary yaulere,zipatala zaulere,nthawi zina zikativuta ma bungwe komanso maiko akunja amatipatsa chakudya chaulere ndiye mpovuta kwambiri kuona ubwino okhala ndi ana ochepa ndipo zizatitengela nthawi kuti tizasinthe kuteleku wina akumutukwana munthu woti apeleka maganizo abwino koma nayenso achepetsa bolani anakakhala 4 kkkkkkk.

  110. Wachita Chita nao azimai wakwana nao nde uletse anzako!!!!! Anthu amvekere phungu wathu ameneyo kutiimirira, abale nde bolanso wa chamba ujatu, koma uyuyu mbola basi

  111. I feel sorry for my own country for lack of understanding, it’s so sad that many Malawians are shortsighted, though they have eyes but can hardly see it’s sad

    1. that iz true m’malo moganiza chuma nd chakudya ali bzy kunyoza chosecho ana ake ali nd umphawi kuxowa fees km akufuna kutchuka kt ngoberekaa

  112. Iyeyo anabereka angati? Asatikhomelere . Bola akananena kt awachepesera ndalama za salary, allowance komanso fuel apunto azigula ndalama zamthumba mwawo, zikanamveka

  113. How many children does he have? We have never ever even visited his home to ask for a help for our children. Stupid. coming 2019 he will need many voters. stupid again. You also have out side children I know

  114. Akadati boma ikupeleka chithandizo monga ndalama every month kwa ana ngati maiko ena tikadati mzotheka. Akulu amenewa ndi amisala asowa chonena ndi ana angati amene iye chiloweren m’boma athandiza ku dera la kwawo?

  115. Ine ndili ndi ana akadzi okhaokha awiri nde uziti ndilekeze pompa tsopano akadziwa aziwateteza ndani? Ndikuyenela kuyesanso mpaka ndipeze wammuna zimenezi zichepe mmalo Malawi muno ndi ambiri tibelekane Basi tizaze zimenezi osazakambanso takana kkkkkkk

    1. I support him ine i only have two kids(girls) and there is no reason to go beyond that,what for?i will concentrate on the two invest for myself and for them…….. ana ambiri achiyani olo mpaka 4 mmmmmmmmm i dont care about having my name as most do for having boys after all i would be dead and am not sure what becomes after,as long as i grow my daughters in good spirit education and run business i would die a happy father period…no reason to chase for a boy child and in the end have 6 kids kkkkk

    2. mukitero chifukwa mudaninkhidwa azimayi okhaokha ndiye nanga mungalankhule bwanji mwinaso kuyesera munikhidwanso azimayi omwewo .what kind of business she can run while she is at her husband place?

    3. Herbert Mtambalika iweyo ndi amene ukuganiza mwangozi wamva? Nkhani ndiyokuti ife tibelekabe Kaya ana 20 bola ngati Ndalama zilipo to support my kids tamvana???

  116. Ganizo lopanda mnzeru, amitalawo abwera kunyumba kwake kuzapempha ya soap? Kuchuluka kwa ana zimukhuze iyeyo ngat ndi banja lake? Chambachi kaa mapilisi muzisuta bwinotu

    1. Alibe mfundo ameneyu,akamufunse mzake uja,mayi wophoda monyanya uja,ndiye anayambitsa zopusazi kupaliamenti kuti kodi ndi chifukwa chani anayisiya nkhani imeneyi?

  117. Aphungu ndiwo amatiyimilila ife kunyumba ya malamulo ndipo amati amakamba zomwe tawatuma.

    Mtakufumsani bwana …. Kodi zimenezi ndizomwe akutumani bwana ku dela lanuko? Tiziti kumeneku misewu iliko yokwanila? Ana asukulu akumwa phala mammawa?

    Zoti amzanu mtukula pakhomo anawapondereza kudera kwanuko mukudziwa?

  118. Kkkkkkk iye wabereka ten mayi ake anabereka 12 gogo ake 14 ndiye afuna ife tibereke awiri? Tamulakwiranji

  119. Zizingateke mwina mtown ko mmizi amafika amenewo angazakwanitse kuyendera komo ndi komo? or atakambirana Ku parliament but they can’t eliminate these practices

  120. Nanuso mwati mutchuke?bwanji osangopeza nkhani ina yotchukira.mbuzu yamunthu,ungandiuze kuti amayi ako anaswa ana angati?

  121. Kupuxa Eti Iyeyo Chidant Yo Ali Ndi Ana Angat Aziti Atatu Bola Siku China Kuno2 Ndi Mw Paja2, In Stead Kt Zinthu Zixinthe Kaye Osat Zopanda Mutu Zomwe Akutiuzazo

  122. Mphungu opandachitukuko amakamba nkhani yopandanzeru not izimenezo chitsilu iwe amako anakubala iwewekha kwanuko

  123. iyeyo ndiwachingati pobadwa, enafe ndi a number 9 zikanakhala zimenezo enafe sitikanabadwa akapange lamulo limenelo mnyumba mwake sizophwanyilana ufulu obeleka ndikubadwa masiku ano,olo ubeleke ana 50 bola ukuwasamalila basi.

  124. Mmalo mokamba nkhani za nzeru kunyumba yamalamulo ukuzesa nkhani ya cisokonezo. Ndiwe udyesa anawo kapena amabwela koxadikiza kwanu. If u dnt hv anythng to sy in parliament its better to be quite.

  125. Bolako uyu amayankhula koma MP wakwathu chimusankhireni sanayankhulepo ku Parliament amangopita kukamwako tea nkulandira ma allowance nkumabwerako. Ngakhale ka point of order kapena kutsokomola ayi ndithu. Akafuna kutsokomola amatuluka panja akuti mantha. Nthawi yakwana ma MP athu ayambe kumayankhula chichewa mwina wathuyi nkumvekako mawu.

  126. mp ameneyo zomwe akukamba akukhala ngati mutu sukuyenda bwino,kuno kuminzi tiliko anthu ambiri ophunzira koma tikamafunsa ntchito amatenga abale awo ndiye mutititanipo ife,iwesungatipangale ma budget munyumbazanthu ngatitafuna kukhala ndi ana 5tinkhala nawowamva.

  127. Ndetu ku breaker record ya ma mp opanda fundo ndi nzeru zomwe mp ameneyu…ukaletse anthu kubelekana anawo amazadya kunyumba kwanu… Malamulo amenewo uziwuzana iweyo Nda akazi ako ndi Ana ako..chifukwa ndamene amadya zathumba mwako…. Ma rubbish

    1. Mr paul Mwalusatu kkkkkkkk…..u jst hv to luk beyong one’s family wen giving a comment…ts partly helpful on one side of t n not fair to those with enough resources to support more than 2 kids.so ndzabhobho

    2. very useless comment…., anawo mukabeleka azizapita ku xul yanu, chipatala chanu, magetsi mudzapanga anu, misewu yanu etc? U have to kno that a person doesn’t only require food to survive.

    3. Aaa nanu munakali nawobe moyo odalila…. Masiku ano kuli ma private school, private hospitals…. Ukanakhala malamulo amenewa anapangidwa mbuyomo iweyo sukanabadwa coz ati Ndiwe wa number 5 banja lakwanu…nde osawaphela ena ufulu obadwa

    4. nde ndikanapanda kubadwa pali vuto lanji? U mean the world wld hv stopped coz ine sindinabadwe? The millions of sperms that r potential pple do not end up forming human being, does the world then stop?

    5. Thats why xul ndiyofunika, it helps in reasoning. A person who understand things wouldnt waste his time typing nonsense like this. You are cursing your brain mr man

    6. Thats why xul ndiyofunika, it helps in reasoning. A person who understand things wouldnt waste his time typing nonsense like this. You are cursing your brain mr man

  128. Even utabereka ana ambiri koma kufa kulibe ixo coz onse akhoza kumwalira nkukhalanso opanda ana ndechongofunika nkuunika bwinobwino mlingo Wa ana omwe banja liyenera kukhala nawo basi. Mundikhululukire ngati penapake ndalemba mosakhala bwino

  129. fodyayu kumazimitsirako..
    vuto siiweyo koma komwe ukuchokera.
    siumadziwa kuti ndi plan ya zibambo aliyese kupanga chisankho?
    kapena ukufuna unene kuti Boma lidzika likupelekaso thandizo kwa mabanjawo?

    kweni kweni ukufuna utiuze kuti chani?

  130. Kuletsa kwabwino mulimbiktse sukulu …chifukwa mwana pomamaliza ku college, amatanganidwa ndi zina osati zopanga ana …zoika lamulo ndizokomela ochepa …Osaiwala bwana malunga paja timabeleka ambili kuti adzatigwile pankono.

  131. Mzeru zopusa kwambiri,anawo ndiako ndpo uziwadyesa ndiiweyo? Wandikwiisa kwabasi ukanakhala pafupi nkadakukhadzula khazula, usamale nd pakamwa pako ponunkhapo

  132. u r ryt Mr mp, muona chitsiru China chitukwana popano apa Kkkkkkkkk ,kwathu kuno zikuonjeza heavy kumwera paka ana full lineup ya flames koma akut ndiamunthu modzi kkkkkkkkk

    1. Kklkkkkkkkkkkkkkkkkkk bwana khalani serious mukuonjezeraso ,mukut mateam awiri pano koma chosecho bambo modzi maiso mozi paka ma team awiri ,osatero Kklkkkkkkkkkkkkkkkkkk

  133. Do not bring dictatorship into the country. If one has resources and able to support three children or more let them bear more. But for those who can’t afford to support themselves let alone their children maybe its applicable to have two as maximum number. But just don’t dictate about two. My opinion

  134. Ine Ndi Wanumber 4 Kubadwa M’banja Mwathu… Ndiye Makolo Anga Adakati Atsatile Njira Imeneyi Kalelo Sibwenzi Ine Ndilipo! So In Short I Can Say That, I Cant Support That! Its Foolish Decision And Even Bible Says “mubelekane Ngat Mchenga”…. So Who Am I Amene Ndingasinthe Chikonzelo Chamulungu? Ndikabeleka Ana Ambiri Ndidziwadyetsa Ndekha! Ndilibe Problom Ine

  135. Ndiwe wautsiru etiiiii?If you said 4 maximum I would agree with you, but imagine you got one child and that child die while already over the age that you can’t make any child what will you do? Who will enherit your worthy or what you have? Think b4 you bring this to publish

    1. Think b4 you coment mamen we went to school we know what we coment he is ngumbi ya ngumbi does it give sense munthu ukhale ndimwana m’modzi,for what????? We already know mavuto munthu ukakhala ndi’na ambiri Simeon Hassan Namputu I think rather not coment if you know that your point is senseless

    2. man ndmaona ngat mkamba za nzelu. infact i wud wish akananena m’modz, vuto amalawi we beliv so much in CHIGOLOLO.

    3. Kkkkkkkk mpakana mwana modzi ada? Bolani akanati awiri or atatu choti tidziwe munthu timayenda ndi imfa nde ndikalanba ana mwana uja atamwalira atazagwire pamkono ndaniii? ?? Mungomo Foster

    4. When U’re Starting Business, Don’t Thnk Of Th Loss Bt How U’ll Rn It In Th Same We Should Nt Talk About Death When Bearing Children Even 1 child can survive at th same time even 12 Can Die& Remain 2(Wife& Husband)

    5. what the meaning of chigololo? because chigololo ndikugonana kwa anthu omwe sanalowe mkwati.ngati akwatilana sitimatinso chigololo ai. ine anga alipo kale 3 two boys one girl if possible ndingofuna modzi basi ndatha uyo safuna ana akhale basi

    6. Zopusa zimenezi zimafunika ma country ochita bwino osati Malawi that’s a fact Iwo atiuze zoti abweresa ma company tilowenawo ntchito Ife tidyese ana ambiriwo basi

    7. Sometimes you need to findout before you comments because this issue is very sensitive! Look China now, amene aja bwez ali olemera kuposa maiko onse! Koma chifukwa chakut they adoptet this policy thats why they can’t!!!

    8. Kkkkkkkk! Ine ndijuberekabe ndikufuna akwane 8. Pano alipo asanu, atsala atatu. Ndimawadyetsa ndekha ndipo ku chipatala ndimakalipira ndalama zanga osati za kanyimbi wina wake ayi.
      Iye ngsti ali ndi bvuto la m’nyumba sikuti atipatse chipsinjo chakecho ife ayi.

    9. ichi ndiye chamba cheni cheni mix dzuwa kwawoko,ana alakwa chani? amadyetsa ndi iyeyo? iyeyo ali ndi angati? akulephela kuchita chitukuko kwawoko ndiye wati ayambe imeneyi?Atiuze kuipa kokhala ndi ana ambiri ndizosatila zake,ndiyeno anthu azisankha okha kukhala ndi ana omwe angathe kuasamala,koma osati kuika nambala ya ana pa family,kuno siku China ayi,uku nkususana ndi mau a Mulungu,ana tiabelekabe basi tikafa ifeyo asale iwowo.( don’t dare to attack me with my comment) 48 hrs non stop revange will be applied tirelessly!

  136. NGATI ANASIYA KUCHINDA NDIZAKE ANAWO AZIWADYESA NDI IYEYO?…IYEYO ALINDI ANA ANGATI? NANGA KWAO KUNABADWA ANA ANGATI?…MUMUWUZE IFE SITILORA…MULUNGU ANATI TICHULUKANE NGATI MCHENGA

    1. Iwe DPP inakulakwila chani? Look how small Malawi is, but compare our population with our neighbouring countries like Zambia, Zimbabwe and Mozambique. Are we not ashamed kuti we dont have land, ngati sitisamaba ana mukulililawo tizawasiya pa mavuto koopysa Gomiwa Mlomwe Mbwiyee. Whether phunguyi ndi wa DPP or any other party but I support him. Malawi will be like China very soon.

    2. Even if DPP fall today, nothing will change, tivomereze kuti yangokwana nyengo koma tikuyenela kuchitapo kanthu, put all yo God in prayer.

    3. Ayi poti kunali anthu ambiri sindinathe kukuonani koma ndikukumbukira kuti munali pakalikiliki kukopa anthu kuti adzavotele DPP

    1. generation come and go if we can not produce children then who will see next generation???? do not course someone blessed by Almighty be a fool pls

Comments are closed.