Anthu awiri amene amapha anthu ndi kuwadula ziwalo zawo zobisika kuti akazigulitse, achoka ndi chimwemwe kutsaya pamene anatengeledwa ku Khoti mu boma la Nkhotakota.
Malinga ndi ma Lipoti, abambo awiriwa anamangidwa atapita kukatsatsa malonda awo a ziwalo zobisika kwa mkulu wina wa malonda mu boma la Nkhotakota lomwelo.
Mkuluyi atachita mantha ndi malonda amatsatsidwawo akuti anakanong’oneza Apolisi kuti anjate njonda ziwiri izi.
Apolisi anagwila njondazo ndipo anazipeza ndi maliseche a anthu.
Chodabwitsa, atafika pa bwalo anthuwa agamulidwa kuti akakhale kundende zaka zisanu zokha basi ngakhale a Polisi akuganizila kuti anthuwa amapha anthu ndi kuwachotsa ziwalo.
Awiriwo ndi Bambo Lazaro Alfred a zaka 28 ndi Bambo Robert Banda a zaka 40.
Anthu amenewo niopusa zedi ofunika nawo kuwadula ziwalo amve kuwawa
Chifukwa chake anthu amatengela lamulo mmanja mwao what poor leadership
Oweluza abwelele ku school
Amalawi ndichani chomwemukuchita mpaka 4 yrs kuphamunthu simaseweraayi. akanakhala ku prison moyowonse
Zovetsa Chisoni Zakazo Zachepa Chifukwa Chake Anthu Ena Amadzilangila Okha.
the z nosense hw cn u hv ziwalo xa mnthu osanaphe munthu guyz let us understand about life ts once in life time mmene munthu wakufa amapsera basii wina amupha iweyo busy kuchosa ziwalo wake up on your day dreaming ts good indeed to kill who found with killed somebody. Just because going to court z nosense akuzwana .
Ma Jadge Mwina Simulandir? Mwaonjez Okuba Mbatata Zaka 18 Okupha Miyez Inay Kod Mungamve Bwanj Atadulidwa Ziwalalo Mwana Wanu? Muziganiza. Ngat Simulandil Nenan Dziko Lidziwe
ine ndinaripo ndipo anthu awa amangowaganizira ndipo zikuoneka kuti ndizabodza pali munthu wina wapangitsa kuti anthu awa apite ku ndende
Nyirenda uli vuto lakumva eti akuti ziwalo za munthu osati khumba unatolako ziwalo zamunthu iweyo.zoti wena anaphedwa kuti papezeke ziwalozo sukuganiza ayi uli ndi ubongo wa pusi kapena
Sanaiwale ndiyekuti iwowa amadziwa kuti ku nkhota-kota ndikumene kumachokera zomerazo
Kkkkk amalawi 4m joz
Kodi inu oweluza mirandu???? Sukulu yanji mudapita??? Mungauzeko fuko la Malawi, pakati pa mulandu okuba nkhwani mdimba ndi mulandu okupha kusiyana kwake???? Kodi mzimu wa munthu ukulemekezedwa pamenepa????? Kodi nanga kwa anthu amene ali pa ma programmes okadulanso ziwalo angasinthe??? Nchitidwe umenewu????? Kapena mwatuma????
Gayz izi zatikwana anthu ngat amenewa amafunika kuwamanga moyo wawo onse osati mbwerera zomwe akupangazi…akagwidwa kumangowaotcha basi….
Gayz izi zatikwana anthu ngat amenewa amafunika kuwamanga moyo wawo onse osati mbwerera zomwe akupangazi…akagwidwa kumangowaotcha basi….
iwe judge ziwa kuti patsogolo pako pali judje yemwe adzakugamule nawe chonch zindikiranso kuti unfumu wa mulungu wayandika uzaziona ndakwiya nawe kwambiri.
iwe judge ziwa kuti patsogolo pako pali judje yemwe adzakugamule nawe chonch zindikiranso kuti unfumu wa mulungu wayandika uzaziona ndakwiya nawe kwambiri.
Ali limodzi ndi boma awa musadabwe
this is not enough plz
Judge Wagamula Mulandu Umenewu If Its True Mboli Yake
tawanthu tikuthawila kuno ku joni kuopa ndende ndiye wakupha kumutchaja zaka five zachisoni kwambiri malawi pamane ogwililira 14 years tibwela tikangoyamba yogulitsa ziwalozo
Amenewa Ndiofunika Kuotcha Bas.Majaji Amenewo Ndizitsru Zomwa Madzi Ometera.
Mudzina LA yesu mulungu wayakobo mulungu wa mose mulungu wa Abraham ndikunenesa anthu ameneya 5yrs akamatha azakhala aliku manda .
Boma zmene rikupanga sizabwino koma ifetokha tkamgwira wachifwamba kungomuphabasi osat kuitana police or amfumu ayi moti kuno kunkhata-bay ayamba kumaodira m’makhomo usiku ukaturuka kukuveka waya kenaka ndi imfa. Tisamareso potuluka
Kumangootcha basi court too late
Mbuzi yagamula mulandu umeneu mbale wa sanaphedwepo nd zifwamba akanaona mmene zimawawira, munthu kuphedwa imfa yowawa Akanawajaja moyo onse agalu amenewa. Conci tkawigwira tokha ndkuotcha tilakwa mxii ndakwya nawe judge
Thats why we malawians tikapezano anthu oterewa komanso akuba tikumangoowaotcha basi bcz boma silikuthandiza anthufe koma akuzithandiza okha kumipando kwawoko.
Tikumana 2019 Manganya akubwera
kod mesa wakupha ndi life in prison??
ndekut anadulidwa ziwaloyo sanafe et?????
Amenewo akhale zaka 5 koma atadulidwaso mavalo awowo
Waweruza .mulanduwo sadziwa aziona akadzadulidwa wachibale wake
Y 5 yrs. It should have been life sentence. The person has killed pamenepatu
Ma mafia ndi ma Big what do you expect opedwa alive ufulu it is what it means here
God is watching. Aaaa! A Malawi.
Khotilo lalowa ziwanda
Mabwaro akumalawi sindimawamvesa kaya àmakhala asuta chamba akamawereźa milañdu. Muthu yemwe waba njinga mukuti zaka 15 kupereka phunziro kuti ena asazapangenso. Opezeka nďi źiwaĺo 5 what you mean for this? Pameñepo ndiye ena a khalidwe lomweri aziti chani? A malawi tikapeza anthu otero tizingowapha çoz makhotiwa satithandiza
Is beter anthu amenewa akapezeka ndiziwalo kumangowapha basi
Thats Why Anthu Akumati Akagwila Wakuba Masiku Ano Akumangomuveka Mateyala Kumthila Petrol Kenako Kumuyasa Moto,anthu Odula Ziwalowanso Akangogwidwa No More Simpathy Awotchedwe Basi.
ZOONA
So bad, broken judge in a brocken country! Lawless xem!
Nkona Tikumalanga Tokha Boma Fulishi.
Kumangootcha kulangilatu basi
Akapezeka tizingopha tokha basi.
Ndiye takalanga tokha muzitidandaula
@ Nyirenda; Kapena iwenso malonda ako ndi adziwalo? Kapena wasowa comment? Ma Jaji ngati ndi ziwanda ziwani kuti tikukuonani ndipo tithana nazo mothandizana ndi Master Jesus
INU MAJAJ-NU MUKAMAGAMULA NKHAN KOD MUMAONA KHOPE OR CHAN.IWE WAGAMULA NKHANIYI WHAT MO KT ZIWALOZO ZINALI ZAM’BALE WAKO,UKANAGAMULA CHOCHO?IWE NDE SIJAJ,SIYA NTCHITOYO KAYAMBE YOJI-ILIRA MA MIN BUS.
Inu a Nyirenda comment yanuyo ndiyopititsa patsogolo mchitidwe wonyansawo, munthu akapezeka Ali ndi chamba amamuyimba mlandu wofanana ndi amene akulima chambacho. Ndiye leniency izikhala pamunthu woti wapezeka ndi ziwalo zamunthu, ngakhale muwayikile kumbuyo anthu woterewa dziwani kuti pamaso pa Mulungu namalenga sipadzapezeka wodziwa malamulo,mudziwe kuti gahena iliko ndithu ndipo mulungu adzaweruza ndithu ndithu….
Only 5 yrs, kupezeka ndi ziwalo zobisika zamunthu. ‘Ndalama ikalankhula chilungamo chimakhala chete’
Athira macobill awa dziko lidayanja achuma ili ife apa kugwira Bere mzimayi uva 14 years imprisonment while murders 2 years
Amadyela limodzi ndalamazo xmass yubwelayi awakhululukilanso.bola akanangowawotcha isaaaaa
Kugamula mwa umbuli,ofunika kudzaphako mwana wanu nkudulako dziwalo simwayamba ma 5yrz ?.choncho nde olo opanga bznes ya ziwalowo angasiye ?,kmanso bwan’noni ameneyo anakaphunzila xul yakut zaujaji zakezo ?aaaaaa ungandichimwitsepo apa
Kugamula mwa umbuli,ofunika kudzaphako mwana wanu nkudulako dziwalo simwayamba ma 5yrz ?.choncho nde olo opanga bznes ya ziwalowo angasiye ?,kmanso bwan’noni ameneyo anakaphunzila xul yakut zaujaji zakezo ?aaaaaa ungandichimwitsepo apa
Izizi ndaona kut kumalawi ma khoti ambri ndalama patsogolo mlandu pamumbuyo mwina tiziti samalipidwa zokwanila ndalama akhotiwa nanga chayani ichi ku malaw kadziko kosaukitsitsa kaja tikukaonongaso tokha pls pls musamatero inetu kamba koti ndnaba guava munda then kundigwira ndiye anazandiuza zaka seven poti tinawaonetsa kochepa then ndinazakhala 2yrs plus 5 month, chiphuphu 2 much kumalawi kwaipa kaya tisiziona ngat kutani kuno kwathu manda athuso ali konkuno ndiye jst c.
That’s why pple they just kill and burn when they caught these kind of pple. ! Don’t worry tiyamblanso zootchanazo nanga sinsimukufuna chilungamo .
Amenewa akanangowatulusa titane nawo mob justice is more educative not that
Izi ndiye zibwana tsopano 5 only wa Kuphawo?
Opha Mzake Nayeso Aphedwe Bas Kapena Angowapanga Zina Ndi Zina
Kugamulako mwatelo powona kuti busness yaziwalo ingasike pasi eti?mwina muli limodzi
Ndikuvomereza nawo mob justice is the best solution
Ma judge please muziganiza kt moyo ndiwofunika bwanji.Nanga akadakhala kt mmodzi mwa m’bale wanu anali mu gulu lophedwa munakamva bwanji. Reality is that ,ur affected with those kind of busineses
thats true
kumazimvesa zamalamulo ndibwino kwambiri usanayankhepo. Anthuwa akuwazenga mulandu opezeka ndi ziwalo zamunthu osati kupha munthu
Ndiye ngati wapezeka ndiziwalo ukuso yeza kuti unapha munthu
ziwalozo ndi zawo? eni aziwalozo Ali moyo? Iwowo anangozitola panjira? Kuli shopu yogulitsa ziwalo za anthu Komwe Iwo anakagula. kuganiza moperewera ngati mabjudge naweso.
sichoncho atha kupezka nazo ziwalo koma sanaphe ndiyeyo anthu .ni makhuluku masiku ano
Ada Nyirenda talembani zenizeni apa mwina ndi achibale anu?Apezeka ndiziwalo ndiyeno 5yrs?Amapha okha,ngati samapha ndiye ndiye amatuma anzao kukapha mlandu umodzi okupha.
A nyirenda, inunso mukuyenera kuka seva nawo sentence ya 5 years koz zkuonetsa kut nanu ntchito yanu ndi yomweyo. bwanji mukuganiza moperewera??
ndiye inuyo mukaganize kuposa omwe adàpanga malamulowa ndi oweruzayo? ngati ndichoncho pangani anu tiziayendera
wakuba mbuzi akumupatsa 6 years akuti kupangira kuti asapangeso ndiye wakupa azipangabe…..
This is nonsense. They deserve life in prison
Akachoka akaphe mayi ajajiyo alandila zaka zochuluka
Jaji ndi munthu.simamutengera zomwe zinamuyenda muntu mwake.akachezera kumwa mowa wa kadatsana amapanga zake.osaganizira ubwino kapena chilungamo mm
Boma Likuziwapo Kathu Pa Nkhaniyo,
Malawi
Zovuta
ine ndinakuwuzani kale amene akupanga malonda aziwalo ndi akuluakulu amuboma,amabizinesi a ndale ndiye pazakhala povuta kuti zinthu zimenezo zithe ooo Malawi shame
ndiponsi
Akuziwana amenewa
Malawi wasauka mpaka VAT pa ziwalo zobisika kkkkkkk
Tidzilanga tokha basi…..iyaaaaa
Corrupt Judges it started with Late Marxon and other Judges to pick One APM as …..
Koma nde apa aliyense asamale ziwalo yekha ndithu
Kupeza odula ziwalo , wakuba ndi wakupha nayenso adulidwe ziwalo kapena aphedwe ndi anthu osafunikira mdziko
Ndichifukwa Amalawi tikumathawila mayiko ena kuthawa kuphedwako
The only solution is mob justice once caught should just be stoned to death coz police & courts are biased
Zomvetsa chisoni kwambiri funso nkumati Ziwalo adapezeka nazozo ndiza anthu kapena chiweto? ndakhudzidwa mmoyo wanga Mesa apatu ngati anthu ngati apezeka Ali ndiziwalo za anthu zikungotanthauza kuti wina wake kwina kwake tikunena pano Ali mmanda analuza moyo wake chifukwa chkudulidwa ziwalo, nde funso langa nkumati mesa kuli lamulo lokuti wakupha munthu akakhale kundende moyo wake onse? mmmm Guyz apa chilubgamo chasowekapo ndithu wokuba nkhuku Zaka teni pamene wochosa moyo wa munthu zaka 5 mmmm koma malamulo anuwo muwawinikenso mwamva zandikhudza
Munthu wogwilila dzaka 12 ndiye mwati wochotsa /kudula ziwalozo ndiye dzaka zingati? Palibe chilungamo pa dziko
Kodi democracy is only exercised ndi odula not odulidwa ziwaloyo eeeshi!!! Think about it ma judge
Mw watani ? kutuma asilikali azunze mulimi ndi wogula mbewu koma ogulitsa ziwalo kukhala pa ufulu, pano sopano M’Malawi Mtendere Mulibe.
A judge kudulidwa mwana wawo angagamule zaka zisanu zokha? Masende yanu nose ma judge
thus y mob justice is high now Coz of these unjustice
I remember shoot to kill by rate mutharika,rest n peace zinachepa
Last day
Chamba etii
kkk zko ndi anthu ake,,
Alipo oweluza olungama ndiye Mulungu !!!
ndichifukwa chake anthu ambili amalanga okha mabwalo anthu ndi akatangale kutengera munthu ku police ndokutaya nthawi
Am gree with you men
Mob justice is fare than courts nowadays.
Pakufunika kumudula ziwalo zake yemwe wapereka 5yrs jail term kuzimbalangondo zimenezi
Kungotentha M’moto basi
Fuck jugment
Inenso ndakhumudwa ndi chigamurocho.Munthu ngati wapezeka ndi ziwalo ndiye kuti anapha munthu ndiye why sentence him zaka zochepa choncho?
Koma atagwira munthu ataba mwanapiye ungova 18 years in prison
Osawadula ziwalo nawoso bwanj coz akatula azapitilza pomwe analekela
Kd Panopa Anthu Akuphanabe Mkumadulana Ziwalo Mkayesa Mumat Mcp Ndiimene Imapha
Eshiii
Correction; number ya magistratem
ine nde ku malawi kuno ndinatopa nako amwene, ot kupeza mwai opita dziko lina kumalawi kuno ndizabwera maliro kapena ntembo…… dziko lopanda mutu lino!!!!!
Chonde wina atandipatsa ya magistrate-wo kuti ndiwafunse kuti apatsidwa zingati.
Tizingothetha tikawagwira
Ngati adapha munthu ndekuti akudikira mlandu WA murder omwe ndi Moyo onse my ndende, NDE palibepo chimwemwe chilichonse
Paja2 mbalame zofanana mawanga zmaulukila limodzi
MUNO MALAWI VUTO NDI AKUAKU AMAPEZAKO NDALAMA KUDZERA ZINTHU NGATI ZIMENEZI.
kumangokonza akagwidwa basi
Mesa ndanyamata otumikila akuboma ndemumat awapatse zaka zingati?posachedwa mwaona akuyenda ntown.nde ulamulilo wa petulo umenewo
Shaaa
Amawothawa amakana zimenezi
Dziko la mw ndilabwino bt cashgate 2 much, mlandu ngat uwu umaenela 100yrs osati manyaka a 4yrs wo mwina tiwamvetsetse paja akagulitsa amalipira msonkho no wonder nazo izi komanso tikadakhala ife taba nkhuku imodzi zaka 25 mu jail kma ku mw eeeish
Dziko la mw ndilabwino bt cashgate 2 much, mlandu ngat uwu umaenela 100yrs osati manyaka a 4yrs wo mwina tiwamvetsetse paja akagulitsa amalipira msonkho no wonder nazo izi komanso tikadakhala ife taba nkhuku imodzi zaka 25 mu jail kma ku mw eeeish
kodi akadakhala kuti ndi mwana wa ogamulawo zikanakhala zaka zingati, anthutu mumawaputa nokha kuti azitengela malamulo mmanja mwawo. Zilibetu maintanance zimenezija
mtsika uli ku boma komweko
Vuto ndi democracy muno munalibe izi muno munthu opha mzake lamulo linali loti aphedwe
Za masiku osiriza chilungamo chizachoka pa mpando ndipo n’chinyengo chomwe chizalamulire….no wonder
ngati mungakumbukile billy kaunda anayimba nyimbo yoti akakhala pa mkhate khoswe sapheka masho atatchuka ndi malonda aziwalo mu mthawi ya abakili muluzi ndipo mashoyo anali wa chipani cha udf kwa amene akukumbukila atsogolera azosezi ndi andale tikuwawonawa
zopusazopusa ,,chinyengo basi wadyamo uyooooo
mde zili kutiko ziwalozo
Laine ndinachita kugula la brandnew la nylon tyre ndikugula 5lt ya petrol iwe! Samala
Anywhere is the world governments responds to people’s concerns much quicker if they protest.Not violent protest.
ACB take action this magistrate is corrupted many people are going to be murdered
Iya,anayener kukakhala kundende moyo wao onse,cz akusowesa mtendere anzao
Tizilango ngat iti nditomwe tikulimbikida mob justice. Mot simukuziwabe zimenez? Nde mukungot tithana ndi mob justice pomwe tizilango kwa olakwa nditofewa. Mukuganixa kut abale aodulidwa ziwalowa or kukamuona munthu uyu aftr 4yrs zikatha bwino? Tamaganizan amakhothinu please aaa
Ndiye chifukwa chake kubvekana matayala kukupita patsogolo ndipo anthu adakatenthana sanati
sad development
THS is a mockery…..May they not come out of jail alive to proceed with their evil deeds.
Tingowatchola makosi kundende komko
That’s the wish of the government. They should come out quick business isayime
Business pa moyo wa anzawo…..
Why 5??????
Theirs no justice on this matter nde pot malawi walero ndiwokonda corruption mwina ogamula mlandu adalandilapokena shame
za chisoniii
mwina angowalawitsa zazikulu tikuvabe tidikire
Ndizambili zimenezo musazichepetse
udzaziwona zikadzachitikila wachibale wako kuti kani kuwawa kwake ndikumeneku
Anthu akuba ndalama zambilimbili m boma koma osawamanga pamene awa amanga zaka Five zikukwanila chilango ndichachikulu kusiyana ndi amene akuba ndalama zambilmbili koma osawamanga
mwina angowalawitsa zazikulu tikuvabe tidikire
Watumidwa ndiakuluakulu opanga malamalo mawa mukumana naye
anthu amene amawatuma ndi atsogoleri andale chifukwa ndi amene amadziwa kumene kuli misika osayila masho mzake wa bakili muluzi amkachita zomwezi
Bomaili likuvomeleza muchitidwe wumenewu etichifukwa chaniakumatere
tsopano mumafuna akafere kundende ali ndi ma banjatu anthuwo omwe akusowa chitsamaliro chawo
Bola akanadula zako
U pussss
Ufiti chani??
USATICHIMWITSWE AISE
U r fucken mad thy need to kill yo relatives you see how pain is
U r fucken mad thy need to kill yo relatives you see how pain is
udzaziwona kuwawa kwake akadzapangidwa chipongwe m’bale wako
amene aphedwawo alibe mabanja ?
mwina ukuziwapo kanthu eti?
Akuziwapo kanthu uyu ofunika afufuzidwe basi
The most stupid comment I have ever read since I joined Facebook.
Yeyo Mukt Ali Ndibanja Loti Azikasamalira Anthu Akumadulidwawo Ndiwosafunika #pasadi? Sunaziwonepo Kapena Ndiwe M’modzi Mwaiwo Eti? Awatulutse Akaduleko M’bale Wako Udzaone Kuwawa Kwake Ulibe Chikondi
Ndiwe mumozi wa iwo
Adulidwe akewo
Apa Fanz Mwaonetsa Moyo Wosakhululuka Moti Mukanakhala Mulungu Ambilibe Kulibe Chonsecho Mumafuna Yehova Azikukhulukilirani Anu Machimo Mukachimwa Koma Chonsecho Mulibe Ntima Wokhululukira Anzanu Apapa Muiwale Zoti Mudzakhululukidwa Machimo Anu Never Mpaka Ku Moto Basi
Stupid comment.those victims alibe ma banja?
Akukhulukire. Mwin moyo pt ophedwawo alibe mabanja
machenda ako ukuyankhula ngati ukunyela bwanji ukuona ngati anthu akumaphedwawo alibe abale kapena ma banja
mbolo yamako
Koma Anyamata Ndakuputani?
Watiputa kumene,awachepesa zaka zokhazo basi,mwina nawoso akanangowadula zawozo basi asaaaaw
Zachamba who.told them to kill someone are u mad?
Kodi zigawengazi mumazisekelera chifukwa chani ?
kawiri kawiri mkati mwa nkhani ngati zimenezi mumakhala anthu andale ndiwomwe amawatuma musayiwale mthawi ya bakili muluzi kunali masho ponda apa nane ndipondepo wa muluzi
haaaaa dziko ndianthu ake.
akudziwa chomwe akuchita. ndidziko la malawi lokha lomwe silikhala serious pazinthu zofunikira munthu kuba K2000 ndi fone ya Itel akutchajidwa 10yrs with hard labour wina kupezeka ndimlandu okupha just months ndikumpatsaso bell. kod zimenezi zikuchulukira cifukwa chan??ndalama zikuthawitsa chilungamoso mdziko lamtendere lija eish
Apa nde bola mob justice tu.
mwina poti ziwalo agwidwanazo siza ma albino..kkk
Malawi wa lero… the innocent face though jail time while the guilt still roam in our streets….
Kodi mwati Nkhotakota eti kwawo kwazomera mwina tingati wogamula mmlandu adaiwala
Ine ndimadabwa kuti chifukwa chiyani samaulula kumene kulimisikako kuti tithetse malonda amenewo
atsogoleri amalonda amenewa ndi andale mukuwawonawa musayiwale masho anali bwezi lake la muluzi nkhani zake zomwezi
Fishy
ixi ndiye zachibwana
Koma odulidwayo kukhala m’balewanga tingadulane ziwalo mu court momwemo ndithu.
Apondiye tidulanadi ma pieces or italira ndilibe nazo ntchito
Nanga chifukwa cha umphawi tizingodulana ziwalo? boma lingolamula kuti na opeza asinjidwe pompo mpaka afe. ngati mmene anapangila mugabe ku zimbabwe kuti mkazi aliyese ominula agwililidwe palibe mulandu eee azimai anasiya kuminula.
Zaka zisanu zokha basi? Shaaaa!!!
But why
Koma wakuba nkhuku ndiye zaka zaka
kma mlandu wakuba nkhuku nde 15 years