Bwalo lisekelela odula ziwalo zobisika: awagamula zaka zisanu zokha

190

Anthu awiri amene amapha anthu ndi kuwadula ziwalo zawo zobisika kuti akazigulitse, achoka ndi chimwemwe kutsaya pamene anatengeledwa ku Khoti mu boma la Nkhotakota.

Malinga ndi ma Lipoti, abambo awiriwa anamangidwa atapita kukatsatsa malonda awo a ziwalo zobisika kwa mkulu wina wa malonda mu boma la Nkhotakota lomwelo.

Mkuluyi atachita mantha ndi malonda amatsatsidwawo akuti anakanong’oneza Apolisi kuti anjate njonda ziwiri izi.

Apolisi anagwila njondazo ndipo anazipeza ndi maliseche a anthu.

Chodabwitsa, atafika pa bwalo anthuwa agamulidwa kuti akakhale kundende zaka zisanu zokha basi ngakhale a Polisi akuganizila kuti anthuwa amapha anthu ndi kuwachotsa ziwalo.

Awiriwo ndi Bambo Lazaro Alfred a zaka 28 ndi Bambo Robert Banda a zaka 40.

Share.

190 Comments

 1. the z nosense hw cn u hv ziwalo xa mnthu osanaphe munthu guyz let us understand about life ts once in life time mmene munthu wakufa amapsera basii wina amupha iweyo busy kuchosa ziwalo wake up on your day dreaming ts good indeed to kill who found with killed somebody. Just because going to court z nosense akuzwana .

 2. Ma Jadge Mwina Simulandir? Mwaonjez Okuba Mbatata Zaka 18 Okupha Miyez Inay Kod Mungamve Bwanj Atadulidwa Ziwalalo Mwana Wanu? Muziganiza. Ngat Simulandil Nenan Dziko Lidziwe

 3. ine ndinaripo ndipo anthu awa amangowaganizira ndipo zikuoneka kuti ndizabodza pali munthu wina wapangitsa kuti anthu awa apite ku ndende

 4. Nyirenda uli vuto lakumva eti akuti ziwalo za munthu osati khumba unatolako ziwalo zamunthu iweyo.zoti wena anaphedwa kuti papezeke ziwalozo sukuganiza ayi uli ndi ubongo wa pusi kapena

 5. Kodi inu oweluza mirandu???? Sukulu yanji mudapita??? Mungauzeko fuko la Malawi, pakati pa mulandu okuba nkhwani mdimba ndi mulandu okupha kusiyana kwake???? Kodi mzimu wa munthu ukulemekezedwa pamenepa????? Kodi nanga kwa anthu amene ali pa ma programmes okadulanso ziwalo angasinthe??? Nchitidwe umenewu????? Kapena mwatuma????

 6. Gayz izi zatikwana anthu ngat amenewa amafunika kuwamanga moyo wawo onse osati mbwerera zomwe akupangazi…akagwidwa kumangowaotcha basi….

 7. Gayz izi zatikwana anthu ngat amenewa amafunika kuwamanga moyo wawo onse osati mbwerera zomwe akupangazi…akagwidwa kumangowaotcha basi….

 8. iwe judge ziwa kuti patsogolo pako pali judje yemwe adzakugamule nawe chonch zindikiranso kuti unfumu wa mulungu wayandika uzaziona ndakwiya nawe kwambiri.

 9. iwe judge ziwa kuti patsogolo pako pali judje yemwe adzakugamule nawe chonch zindikiranso kuti unfumu wa mulungu wayandika uzaziona ndakwiya nawe kwambiri.

 10. tawanthu tikuthawila kuno ku joni kuopa ndende ndiye wakupha kumutchaja zaka five zachisoni kwambiri malawi pamane ogwililira 14 years tibwela tikangoyamba yogulitsa ziwalozo

 11. Boma zmene rikupanga sizabwino koma ifetokha tkamgwira wachifwamba kungomuphabasi osat kuitana police or amfumu ayi moti kuno kunkhata-bay ayamba kumaodira m’makhomo usiku ukaturuka kukuveka waya kenaka ndi imfa. Tisamareso potuluka

 12. Mbuzi yagamula mulandu umeneu mbale wa sanaphedwepo nd zifwamba akanaona mmene zimawawira, munthu kuphedwa imfa yowawa Akanawajaja moyo onse agalu amenewa. Conci tkawigwira tokha ndkuotcha tilakwa mxii ndakwya nawe judge

 13. Thats why we malawians tikapezano anthu oterewa komanso akuba tikumangoowaotcha basi bcz boma silikuthandiza anthufe koma akuzithandiza okha kumipando kwawoko.
  Tikumana 2019 Manganya akubwera

 14. Mabwaro akumalawi sindimawamvesa kaya àmakhala asuta chamba akamawereźa milañdu. Muthu yemwe waba njinga mukuti zaka 15 kupereka phunziro kuti ena asazapangenso. Opezeka nďi źiwaĺo 5 what you mean for this? Pameñepo ndiye ena a khalidwe lomweri aziti chani? A malawi tikapeza anthu otero tizingowapha çoz makhotiwa satithandiza

 15. Thats Why Anthu Akumati Akagwila Wakuba Masiku Ano Akumangomuveka Mateyala Kumthila Petrol Kenako Kumuyasa Moto,anthu Odula Ziwalowanso Akangogwidwa No More Simpathy Awotchedwe Basi.

 16. @ Nyirenda; Kapena iwenso malonda ako ndi adziwalo? Kapena wasowa comment? Ma Jaji ngati ndi ziwanda ziwani kuti tikukuonani ndipo tithana nazo mothandizana ndi Master Jesus

 17. INU MAJAJ-NU MUKAMAGAMULA NKHAN KOD MUMAONA KHOPE OR CHAN.IWE WAGAMULA NKHANIYI WHAT MO KT ZIWALOZO ZINALI ZAM’BALE WAKO,UKANAGAMULA CHOCHO?IWE NDE SIJAJ,SIYA NTCHITOYO KAYAMBE YOJI-ILIRA MA MIN BUS.

 18. Inu a Nyirenda comment yanuyo ndiyopititsa patsogolo mchitidwe wonyansawo, munthu akapezeka Ali ndi chamba amamuyimba mlandu wofanana ndi amene akulima chambacho. Ndiye leniency izikhala pamunthu woti wapezeka ndi ziwalo zamunthu, ngakhale muwayikile kumbuyo anthu woterewa dziwani kuti pamaso pa Mulungu namalenga sipadzapezeka wodziwa malamulo,mudziwe kuti gahena iliko ndithu ndipo mulungu adzaweruza ndithu ndithu….

 19. Kugamula mwa umbuli,ofunika kudzaphako mwana wanu nkudulako dziwalo simwayamba ma 5yrz ?.choncho nde olo opanga bznes ya ziwalowo angasiye ?,kmanso bwan’noni ameneyo anakaphunzila xul yakut zaujaji zakezo ?aaaaaa ungandichimwitsepo apa

 20. Kugamula mwa umbuli,ofunika kudzaphako mwana wanu nkudulako dziwalo simwayamba ma 5yrz ?.choncho nde olo opanga bznes ya ziwalowo angasiye ?,kmanso bwan’noni ameneyo anakaphunzila xul yakut zaujaji zakezo ?aaaaaa ungandichimwitsepo apa

 21. Izizi ndaona kut kumalawi ma khoti ambri ndalama patsogolo mlandu pamumbuyo mwina tiziti samalipidwa zokwanila ndalama akhotiwa nanga chayani ichi ku malaw kadziko kosaukitsitsa kaja tikukaonongaso tokha pls pls musamatero inetu kamba koti ndnaba guava munda then kundigwira ndiye anazandiuza zaka seven poti tinawaonetsa kochepa then ndinazakhala 2yrs plus 5 month, chiphuphu 2 much kumalawi kwaipa kaya tisiziona ngat kutani kuno kwathu manda athuso ali konkuno ndiye jst c.

 22. Ma judge please muziganiza kt moyo ndiwofunika bwanji.Nanga akadakhala kt mmodzi mwa m’bale wanu anali mu gulu lophedwa munakamva bwanji. Reality is that ,ur affected with those kind of busineses

 23. Jaji ndi munthu.simamutengera zomwe zinamuyenda muntu mwake.akachezera kumwa mowa wa kadatsana amapanga zake.osaganizira ubwino kapena chilungamo mm

 24. ine ndinakuwuzani kale amene akupanga malonda aziwalo ndi akuluakulu amuboma,amabizinesi a ndale ndiye pazakhala povuta kuti zinthu zimenezo zithe ooo Malawi shame

 25. Zomvetsa chisoni kwambiri funso nkumati Ziwalo adapezeka nazozo ndiza anthu kapena chiweto? ndakhudzidwa mmoyo wanga Mesa apatu ngati anthu ngati apezeka Ali ndiziwalo za anthu zikungotanthauza kuti wina wake kwina kwake tikunena pano Ali mmanda analuza moyo wake chifukwa chkudulidwa ziwalo, nde funso langa nkumati mesa kuli lamulo lokuti wakupha munthu akakhale kundende moyo wake onse? mmmm Guyz apa chilubgamo chasowekapo ndithu wokuba nkhuku Zaka teni pamene wochosa moyo wa munthu zaka 5 mmmm koma malamulo anuwo muwawinikenso mwamva zandikhudza

 26. Mw watani ? kutuma asilikali azunze mulimi ndi wogula mbewu koma ogulitsa ziwalo kukhala pa ufulu, pano sopano M’Malawi Mtendere Mulibe.

 27. Inenso ndakhumudwa ndi chigamurocho.Munthu ngati wapezeka ndi ziwalo ndiye kuti anapha munthu ndiye why sentence him zaka zochepa choncho?

 28. ine nde ku malawi kuno ndinatopa nako amwene, ot kupeza mwai opita dziko lina kumalawi kuno ndizabwera maliro kapena ntembo…… dziko lopanda mutu lino!!!!!

 29. Dziko la mw ndilabwino bt cashgate 2 much, mlandu ngat uwu umaenela 100yrs osati manyaka a 4yrs wo mwina tiwamvetsetse paja akagulitsa amalipira msonkho no wonder nazo izi komanso tikadakhala ife taba nkhuku imodzi zaka 25 mu jail kma ku mw eeeish

 30. Dziko la mw ndilabwino bt cashgate 2 much, mlandu ngat uwu umaenela 100yrs osati manyaka a 4yrs wo mwina tiwamvetsetse paja akagulitsa amalipira msonkho no wonder nazo izi komanso tikadakhala ife taba nkhuku imodzi zaka 25 mu jail kma ku mw eeeish

 31. kodi akadakhala kuti ndi mwana wa ogamulawo zikanakhala zaka zingati, anthutu mumawaputa nokha kuti azitengela malamulo mmanja mwawo. Zilibetu maintanance zimenezija

 32. ngati mungakumbukile billy kaunda anayimba nyimbo yoti akakhala pa mkhate khoswe sapheka masho atatchuka ndi malonda aziwalo mu mthawi ya abakili muluzi ndipo mashoyo anali wa chipani cha udf kwa amene akukumbukila atsogolera azosezi ndi andale tikuwawonawa

 33. Tizilango ngat iti nditomwe tikulimbikida mob justice. Mot simukuziwabe zimenez? Nde mukungot tithana ndi mob justice pomwe tizilango kwa olakwa nditofewa. Mukuganixa kut abale aodulidwa ziwalowa or kukamuona munthu uyu aftr 4yrs zikatha bwino? Tamaganizan amakhothinu please aaa

 34. Theirs no justice on this matter nde pot malawi walero ndiwokonda corruption mwina ogamula mlandu adalandilapokena shame

  • anthu amene amawatuma ndi atsogoleri andale chifukwa ndi amene amadziwa kumene kuli misika osayila masho mzake wa bakili muluzi amkachita zomwezi

  • kawiri kawiri mkati mwa nkhani ngati zimenezi mumakhala anthu andale ndiwomwe amawatuma musayiwale mthawi ya bakili muluzi kunali masho ponda apa nane ndipondepo wa muluzi

 35. akudziwa chomwe akuchita. ndidziko la malawi lokha lomwe silikhala serious pazinthu zofunikira munthu kuba K2000 ndi fone ya Itel akutchajidwa 10yrs with hard labour wina kupezeka ndimlandu okupha just months ndikumpatsaso bell. kod zimenezi zikuchulukira cifukwa chan??ndalama zikuthawitsa chilungamoso mdziko lamtendere lija eish

  • Nanga chifukwa cha umphawi tizingodulana ziwalo? boma lingolamula kuti na opeza asinjidwe pompo mpaka afe. ngati mmene anapangila mugabe ku zimbabwe kuti mkazi aliyese ominula agwililidwe palibe mulandu eee azimai anasiya kuminula.

%d bloggers like this: