A Malawi apemphedwa kuti akhale anthu omvetsetsa pa nkhani ya lamulo lokhudzana ndi kuchotsa mimba.
Malingana ndi mkulu wa bungwe loona kuti palibe kusiyana pakati pa akazi ndi amuna, la Gender Coordination Network, Mayi Emma Kaliya, a Malawi akuyenela kukhala anthu olola kuti lamulo limeneli liikidwe.
Pakhala pali mpungwepungwe pakati pa a Malawi pamene ena akufuna kuti amayi aziloledwa kuchotsa mimba koma ena, maka atsogoleri a mipingo akukana kuti ayi. Iwo ati chifukwa kuchotsa mimba ndi kupha.
Koma onse ogwilizana ndi kulola kuti amayi azichotsa mimba ati dziko silingamalamulidwe ndi malamulo a Chalichi. Enanso akuti mchitidwe ochotsa mimba umachitika ndi kale koma mwa njira zosayenelela.
“A Malawi akuyenela kugwilizana ndi lamulo lovomela kuchotsa mimba ili kuti titeze amayi ndi asungwana amene akufa Kamba kochotsa pakati,” anatelo a Kaliya.
A Phungu a kunyumba ya malamulo akuyembekezeka kukambilana za nkhaniyi.
Ndipo ndizisilu zenizeni.
Palibe kanthu chosan tu
Nanga kachaso. ? win, ponda mx shooter ?
tayankhani funso la malume chisomo kajorijo khonje, watipemphayo ndani, ndikufuna kumudziwa nane
mwayambako kuganiza ngt ziweto kumeneko eti?
Dziko la satanali latsaladi pang’ono kuwonengedwa,dzowonadi amalawi kuvomeleza muchitidwe woyipawu? Izi ndizomwe ananena yesu kut mumatsiku womaliza muzawona ndi kumva zinthu zowopya.
amalawi nkhaza zimenezo.
Bola mukuziwa kuti mukuchosawo ndi moyo mukayakha ndithu
Chamba eti mukufuna jaja atikwiire?? Mufuna mulungu ationonge zitheratu
Amene atipemphayo ndani?????
Mupite mukafunse kwa amene anakulengani ngati angalole mutha kumachita . mbuzi zolumpha popanda dzenje
Akanachotsa mimba yako mayi ako iweyo bwezi palibe pa fb
kukafune kooangira zapusa zanuzi not mudziko lathu labwinori
Ochosayo nayenso azichosanso moyowake
where iz world going on,,,,here in s africa ziliko kale amachta encorage kuchosa mimba uuu kaya
I mean that’s foolish thing coz simukuganiza et bwanji zotere zikabwera musanabadwe bwez mulipo imu enanutu mukuyakhula zopusa enanutu munabadwira kuchigololo chif
Zopusa zinezo! !!!!
A Malawi ake atiwo munena inuwo ?,zopusa eti za usatana ife ayi.makondomu ntchito yake ndi chani ?,kungozolowera kupha basi ifeyo makolo athu akanaganiza zopusazo kapena inuyo makolo anu bwenzi muli pamenepo nkumayankhula zauchitsiluzo ?,.
Dziko lalephereka basi.
Mabi awa wayambitsa ndani kuputsa eti
Wapemphayo ndani?
kkkkkkkkk wayambitsayo mapaz Ake
Subhaanallah
Ineso ndkut mulungu achte nawo
Zopusa
Inject men to produce weak aperms.
#katemela_wamumchele kungodya za nchele wapha Ngozo
Nkhani ndi yoti nthawi yatha pangatalike maka Zizacitika by force cox tixasowa cinacake nde pofuna kuthandixidwa tixasainilana basi poti tikufuna thandixolo kma pamaso pa Mlungu ndi tchimo ndithu musaganixe kti Malawi axakhalaso wabwino ayi apapa tikukwanilisa malembo basi kwabwino kukonxeka basi
Pasavute anthunu ayambe iyeyo kapena ana ake basi
God will punish u soon just wait n see,Do u think ur clever than God? 2 Timothy vs 3 (zoipa zoopsa masiku osiliza )
Shame Malawi
Zachibwana ife sitifuna.
Respekt to my mother’s womb sananganize zopusazi
Wat a lyf dis world iz going to an end dis truuu heee kupha ayambaso kuloleza God must 4 give who have come wit dis plan ok and dziko ili panopa lili mmanja mwa satana devil iz controling dis world masiku osilizadi pakana pamenepo ayi iiiiiiiiii
Mayi kaliya mulungu akuyendeleni mwapadeladela ndima followers anu onse chifukwa mukuganiza mopusa ngati ana .
Mmmmmmm wapephayo ndani kma anthu inu zooona anthu simukuopa Mulungu mukungopanga zinthu zanu muli pheee dziko la mkaka ndi uchi ija lero ikupita kuti,,,mmmmm am ashocked
OMG, This is killing mwaganiza bwanji
then murder should not me a crime
Seals of times
Zaugalu basi, makolo anu anakati achotse mimba yaiwe oganiza mopusa bwezi ulipo iwe. Kuchotsa mimba kugwiritsa ntchito condom konseko ndikupha basi. Ukalangidwa
Amalawi munalolora America kuti ilamulire dziko lathu la Malawi ndizimenezi
Sizoowona kutero
Zamanyi zimenezo
Koma Azimai ena ndi zitsiru. Zoona mai weni weni angamanene zimenezi. End time.
So you mean evry stupid gallons who open legs should terminate.Iknow why pple are pushing for this cz we are a cursed generation.Kupha mwana wolumala ndmulandunso cz evryone has the right to live..who should decide this one shud live o die
ABALE AMENE WAYAMBITSA MAGANIZO AMENEWO MULUNGU AMUKHULULUKIRE NGATI LILI BOMA LINGOYITANITSA MAPEMPHERO A DZIKO LONSE KWA 1 WEEK ANTHU TISALE KUDYA ( prayer and fasting) MULUNGU ATIKHULULUKIRE KUTI MVULA IGWE BWINO NGATI KALE
Satanic fruits
Nosense
Tifune or tisafune, tizalamulidwa ndi oipayo
Wanena ndani opusayo
SHA!! Amw anzanga tisamale tili mthawi yakumapeto.tiyeni tipemphele kwambil.
Koma mmene ilili photo mwaikai ingachoke pha imeneyi?nde kubelekatu osati kuchotsa
pantundu panu nonse musamayambane
chomwe ndaona anthuwa akufuna magazi ndie njira yopexera magaxio yawasowa ndie ndichifukwa akukamba dxinthu zopanda nxeruxi kodi iwowo anakakhala kut mai awo apanga ximenexo anakapexeka dxiko lampasi?? Dziko ngat ngat lakukanikani ndibwino kungovomereXa bass
mmmm mudzasowa chowilingula Amalawi
nde mwabvomereza?
That’s Devilish
Ndani akutsutsana ndimulunguyo zachambaizi
ndiyetikamanena anthuwopusa matitalowetsa ndale ayi koma kulikondadzikoli apapatiyeni tivomele kutitikusoweka utsogoleli chifukwa tsogoleli akanakhalapo sakananenazimenezi ndichimodzimodzi kunena kuti amalawi tiyeni tiziphana palibekusiyana komadziwani ichikuti chilichose chikuchitika chotsutsana ndi mulungu mukayankhamulandu pamasopake pamulungu
Inu amanu akanachosa bwenzi mulipo?opani Mulungu
Mukanalrmba kuti; aMalawi apemphedwa kuti azimayi azipha ana awo asanabadwe
A Malawi ake ati ine ndakana
Do that , but remember hail iz waiting
Ndakana agenda yawoyi muwauze, ayambe akonza magetsi kaye
God forbid
Ndimabwerezabwereza kuti ngati dziko lithe msanga liyamba laku malawi kutha chifukwa anthu ake amakhala ngati ndi ophuzila koma taaaa mbuli zokhazokha zitsilu
This is a very big sin before God! The Bible says Do not kill . NDE inu mulorelanji mchitidwe wakuphawu?? A Malawi think twice…..
Apemphedwa Ndi Ndani?
Signs of the times. Ngakhale apolisi asakumangeni pamene mukupha ana osalakwawo, koma kwa Mulungu mulandu wanu ngwachikhalire ngakhale pachedwe bwanji mukayankha ndithu because whatever you are doing here is accurately recorded in heaven and you will never escape this unbiased judgement. A creature becoming wiser than the creator. Cursed be all of you advocating for this foolish idea. Advocates of the devil.
Read Exodus 20 Vs 1-12 Anthu Oipisisa Inu.Cenjelan,mvekan Padziko Lapansi Lino But Judgement Day Is Upon U.Mudzafa Imfa Yowawa!!!!Mzimu Wa Mulungu Ukudzudzulen.Repent And Be Babtised In Jesus Name,EMEN
Ngati akufuna kuchepetsa chiwelengelo osadanda tingoyitana boko haram kapena alkaida adzachite nafe pang’ono olo tikangoyiyambitsa ndi mozambique tichepa nthawi yabwinoso
Zichepesani mtunduwanuwu mbuzi inu muzatha sure
Zachamba ayiiii
ZAUSILU .AKAMWALILA MUJA!!!
Total Evil….
Malo moti muzipempha mulungu kt dziko lanthuli liziyenda bwino km nlkhani zake za zoduka mutuzi kumbukilani kt ndinu olengedwa ndi mulungu
Mutatha Kupha Pochotsa Mimbazo Nanunso Mfumu Yesu Adzachita Nanu Pa Judgement Day.
Kodi..tiziti mwasowa ..zoti..mungatiuze.!!!
Kapena ndi kuchuluka nzeru mopusa.
Mmalo moti..mupeze njira yothesera mavuto omwe.!!
Tili nawowa ndipamene..mukuonjezera mavuto ena.!!!
vauchindere ivo mwayamba wamalawi mwasowa vakuchita ataseeeeeeee
Fools!!! rather beg them to Avoid sex!!!
Osayiwala kuti mau amati, masiku omaliza anthu adzakonda zoyipa. Ali ndi maso, mapilikanilo, azigwilitse ntchito ndikudziwa chochita ekha.
Ndakwiya nanu anthu opusa inu,zoona tivomere kuchotsa mimba? Ine musandiwerengerenso ngati Mmalawi Nosense
.
.
Murdererz, promoting abortion in a peaceful nyasaland
Tosefe Tidakhalako M Mimba Ya Amayi Athu Maganizo Awa Ndiwopusa Kodi Tiziti N Chifukwa Cha Ndalamazo?
Demeti!!!!!!!
Vuto ndlakut amene anabwelesa #democracy sanatiunikire bwno nde pano zimalamuro zomwe zikubwer pano nd zosusana nd #mulungu waku mwamba, kuphiphlisa kwake akut nd ufulu wathu, at kuteteza amayi mwanayo ai,muthu wazeru kumenyela ufulu ma #hule mot athandze ana oyendayenda town mu km ndkumakawathamangisaso #ndakwiya~nanu
Zoputsa kuchosa njara osati mimba
inuyo amayi anu aķanatelo bwedzi mulipo eishi ambuye pelekani chilanģo kwàanthu amenewo, ali ndimagañidzo ñgati amenewa
FUCK YOU,WHAT IF SOME ONE ALLOWED, HELPED YOUR MOTHER KUCHOSA MIMBA YAKO,WUD YOU BE SAYING SHT LIKE THIS,WE GOT PROTECT OUR UNBORN BABIES
Ukadachotsedwa iweyo sibwenzi nditakomenta
ndalilira dziko langa Malawi watayika
Ndikanakonda anthu amene akufuna lamulo limeneli akanafa mwachangu asanapange lamulo laolo. Chifukwa angayambe kutichimwisa. Akufuna adzitenga ana omwe achosao ndikukakhwima
Eyi zopusa zanuzo kwathukuno ayi ufiti eti kukanakhala lamulo limenelo munaka badwa inu zopusa basi shit
Endytme
Kodi amapempha zimenezo mkukhala galunji? zili zonse basi kumangoyendera maganiza america
amene akutipemphayotu amayi ake sanawuzidwe kut amuchotse iyeyo…mchifukwa chake lero iyeyo akuti pempha kut iyeyo akhale omaliza ku mtundu wa anthu…nanga amene azawapemphhe amalawi pathupi azisamalira azachoka kwayani?
Zautsilu Et. Akukatengela Ya Chiani Mimbayo. Kumanga Nyumba Kukapasula Ndi Chamba Chmenecho. Amenene Akapezeke Wochotsa Mimba Apolice Amumange
End times
Legalising murder, eish!
masiku otsiliza akugwla ntchto mofanana ndmaulosi a baibulo
Uchembere wabwino ndiye ulipati?
Mukuthandauza kuti sumakhala mulandu padziko pano koma tsiku lachiweruzo ndi wachikhalire mulandu.
Zopusazo Nde Zmenezo Kupusa Bas Alla Iwo Pompwalana Sakuziwa The End result?Wapemphayo Mazira Ake
Koma zowona munthu wa mzimu waumunthu nkumapana maganizo upusa ngati amenewa? chonde amalawi anzanga tiyeni timuope Mulungu osati mzungu..
Foolish mimba akazi akumachosa daily
Zopusa zimenezo
Ndiye anthuwo akutengelanji mimba uyu ndiye timati #fodya wa mkulu wa #Nkhotakota akulamula but anyway God is watching u #Malawians
Ndiye anthuwo akutengelanji mimba uyu ndiye timati #fodya wa mkulu wa #Nkhotakota akulamula but anyway God is watching u #Malawians
Jabulos At Work, paja Ndalama zikamalankhula chilungamo chimakhala chete, but what I know is kwa Mulungu kulibe kubisa kalikonse , inu amene mukupanga malamulo opusanu Amai anu akadaganiza zokuchotsani musadabadwe mukadakhala mulipo inu? Mukunena kuti ayi dziko osamaendetsa ndimalamulo Atcharitchi mmmm Shame on you! The Bible Said Akapanda kumanga Dziko Yehova Olimangayo angomanga Dziko chabe, Mukufuna kundiuza kuti inuyo Ndi Mulungu wanzeru ndiinuyo? Oimba wina wake adaimba nyimbo akuti Ena akaphunzila Sukulu yomweyo Amasanduka nayo Mikango nkumapha Anthu nde mwaoneka yapa mfiti za anthu mikango yolusa, ndalama zake ziti? ndipo Sukulu Yake iti? mwandinyasa kwambiri . Musamutenge Mulungu ngati James, kapena ngati Amalume anu, Milili ili mbweee mukufuna kuonjezela ina? anthu inu mumauluka ndithu kutamba Mulungu Achite nanu ndithu Ndipo akuonetseni polekela!!
Kodi Azimayi Mumasangalala Mukamabeleka?
Zoophya
Nde tidzimphanasotu
Umeneo ndiye utsiru okumwa mkodzo wanu omwe amene mukupanga ziganizo zopusa zanuzo
malawi has no any president anymore
No not at all
Hillary Clinton and Obama supported this shit. Trump akukaniratu nyasi izi. Ma NGO amene munapeza mgodi pa nkhani ya abortion, gay & lesbian rights munyera funding simuyiona. Trump demurs this shit.
Dziko ndi zintchito zake.
Lero m’malo mowauza anthu zinthu zomwe zili zolondora mwati ai kma tingowapotozeratu.
M’malo mowalangiza kti asiye chiwerewere mwati ai kma mukapezeka kuti mwatenga mbimba inu kaichotseni.
M’malo mowalangiza atsikanawa kuti say no to sex b4 marriage inu mwati ai kugonanako vuto kulibe kma mukapezeka kuti mwatenga mimba kaichotseni.
Anawatu ngati akusongonekera vuto ndinu.
Chovuta ndichani kuwauza zoona zeni zeni atsikana athuwa.
In as far as I knw,atsikana athuwa kuwauza kuti tsiyani chiwerewere ndiye kuti tikuwalakwira,this is nature and u cnt run away from this fact.Kma atsikanawa akuyenera kuuzidwa kuti kugonana mukandali ang’ono,kapena kuti musanakwime sikwabwino.
Mkuwapasa sizanso zomveka bwino monga,,,kutenga mimba ya patchile,zomwe mapeto ake ndiye kuti mwazionongera nokha tsogolo lanu,kutenga matenda zomwe zosatira zake ndi imfa.Kusiyira xul yanu padela zomwe zosatira zake ndi ndizokuti mwazionongela nokha tsogolo lanu.
Atsikana athuwa akuyenera kuuzidwa zoona zeni zeni zokhuza kugonana.Akuyenera kuuzidwa kuti u can only enjoy this thing wit ur husband and by then sizakhala kuti zikuchitika the way God Almighty intended it to happen.
pangani koma muzakayankha kumwamba
oky mluņğu wanga sazalola zoopsaź zicitike .kd asogoleli moźiganza musanayakhĺu .ngat simubeleka inu zanu .ticulukane ngat cenga
Thawi yayandikira amene apirire ndiwo ana wake, ziyenera zikwaniritsidwe pakuti mawu ake sabzapita pachabe ,
eeeeej,koma yah!mulungu akanthadi,ndiyo mwapeza njira yachidure yochepetsera chiwerengero cha amalawi?zopusa basi akadakuchotsani inuyo mukadakhalapo?stupt,kukwatirana amuna okhaokha tidakukanirani,kugwiritsa ntchito macndm sizikuyendaso swt mpepala,mwayamba kugawa macndm kwa ana asukulu aprimry takukaniraniso tsopano mukuwuza amalawi kuti aziphana,cholinga chanu ndichani?vuto lokhala ndi atsogoleri osapenphera ndilimeneli.
Lord have mercy
u mus knw that its win nd loose a life for women moyo ulipachiopsyezo chachikulu basi
Ambuye mulikuti tsopano apa nthawi yathadi
Izi ndizomwe tiyenera kuzimva ndipo sizinati uku ndikuyamba chabe,wamzeru samachotsa mimbayo,chifukwa ndikupha komwe Mulungu akudana nako.
Ndipo amene wabweresa nzeru, ndi maganizo amenewa aona ukali wanamalenga kumwamba ndithu; ntawi yakusodom ndi gomola mulungu ananyekesa mzinda cifukwa camacitacita asatana devil, ngati amenewo, Ndipo ndikucita kuonerathu kuti akufuna kuthesa cikristu kuti Satanism ilowerethu msanga kuti magazi aana osabadwa zikhale nsembe kwa mbuye wao satana kuti aapase zimene Yesu anamkanila kumpembeza or kumgwadira, Maufumu ndi maulamuliro ampamvu zakumdima ngati zimene tikuziona ndikumva apa lerozi.
Inu amalawi 24 ndamene akulakkhula zopusazi palibe wayakhula zimenezi anthu wopusa amalawi 24
Tikanakhala kuti timaopa mulungu,sibwenzi ganizo limeneli litabwera.tchimo likamachitika kwambiri tikumafuna kulivomereza ndilamulo. Amene sakumafuna kukhala oyembekezera azipewa kapena asamapange.kugonana kumasowa kumasowa kukhala responsible.
Tikanakhala kuti timaopa mulungu,sibwenzi ganizo limeneli litabwera.tchimo likamachitika kwambiri tikumafuna kulivomereza ndilamulo. Amene sakumafuna kukhala oyembekezera azipewa kapena asamapange.kugonana kumasowa kumasowa kukhala responsible.
Street Love.+ dating.+making love+…………….now let them complete the gap.mbado wawuchimo ndiifedi.
Ndizoona zimenezo anena anzangawa mufuna ufumu walou muukhalile nokha basi
Sindupanga nawo
Kwatsalaku Tizadzamva Kut Amene Wapereka Mimba Aphedwe, Wake Up Mw, Wea Iz Faith? Land Of Peace
Malawi uja ine Clinton pompopompo
acahalichi kunena chilungamo sayenela kulowelela zandale potidi nkhaniyi siyachalichi koma yaomwe amayendesa dziko…nde achalichi sayendesa dziko koma andale….achalichi udindo wawo ndiwowuza anthu awo kuwawuza zomwe zikhulupiliro zawo zikunena pankhani yakuchosa mimba…ndipo izi zizapangisa kuti ochosa mimba achepe poti alichikhulupiliro chachikulu…..kwaine kulakwa kuchosa mimba koma anthu akuchosabe…izi zandale avomeleze akane kuchosa mimba kulakwa ndipo sasiyaso kuchosa mimbazo….ndipo kufa sasiya poti ku SA kuno amalola koma nako amafasa kamba kakuchosa mimba.
Kupempedwa ndi boma kuti mtundu wa amalawi aziuthera m’mimba shame!!! Boma lopanda nzeru sindinalionepo ngati limeneri.
Machendewo nde amenewo ,,,zaku mtumbo kwa mapwala achitete ,,,,,
Stop this nosense can u accept it in your own house fools.
Ndikunenetsa kuti amene avomereze zopusazo ndithu kumwamba kulowerelepo,kotero kuti thambo lakuda ligwe pa iye,ndikupemphela ndimphamvu zochoka kumwamba
Shut up your smelling mouth, iye anabadwa bwanji?
sodomu ndi gomola malawi wafika pamenepo
akayambe Kaye amai ake a amene wapemphayo kuchotsa mimba ya iyeyo,akakamuchotsa iyeyo nde abwere ku Malawi adzatiuze tidzichotsa mimba…atleast I’ll be convinced
Boma lopusa .mukati athu azichotsa mimba NDE chan? Bwezi iweyo uripo
.auzen athu za kuipa kochotsa mimba
Pang’onopang’ono satana wayamba kuyenda ndi mwendo yonse ngati dziko la SA zovetsa chisoni kwambiri,Mulungu tithandinzeni
Wapempha zamisalazo ndani?mmene anthuwo amatibulana zotsatira zake samadziwa kt ndi mimba mwasowa chopempha eti
Walamula ndi Trump??
I will say something on this anyone who share blood GOD HE will punish him so if u want punished with GOD you can do it you people of GOD this is what devil want he want all of us we mast go to heaven he want to go with us to hello but we got choice so make your choich in JESUS NAME I PRAY amen
manyi amenewo ayi kuno iweyo adakakuchotsa bwenz uli ndi mpata omayakhula manyi amenewo iwe pathako pa mbuyako ndi mbumba yayo yonse
kupha
Koma mukudziwa kuti kunja kuno kuliMULUNGU amene anatilenga?
Amuthalika.muziganiza bwino2, akanakhala amayi anu analola kuchosa mimba ya inuyo kodi mukanafika pamene mulilipo .Kodi koma simukudya chamba? /nyaupe or pinch……….
President of the USA, Donald Trump is saying, no, to abortion
haha nde yake mwina naneso ndikhoza kuphulisa aft akachotsa
palije zeru.in malawi w hv rght 2 lf sono abotion z nt violtng ths rght?cz abortion z killing of un born baby may b unborn baby hasn` t any rght.to me ndi ngazomera yayi.
vuto ndiloti azimayiwo azichotsa mimba za ana ot akanazakhala azitsogoleri abwino aphindu pa chitukuko cha dziko lathu ndikumasiya mimba za ana osalongosoka mbava komanso zitselekwete ngati azitsogoleri alipo lerowa
kusowa dzocita mlungu anat usaphe welenga pamalamlo omwe ananen. kucit kupang budget amakumvutitsan cithandzo? akanakhal amai ako akanapha ie bwedzi thandizo akulipedza? asa
Wapemphayo ndi ndaninso kodi?
iyi ndinthawi yomwe mdyelekezi akugwilisa ntchto luso lake kt achimwise aliyense
Its sin be4 God, may be try injection, tablets or zija amati lupu/lupo
Akupha phani zonse ndi msogolo Amen. Asogoleli mukufuna kutukwanidwa eti dikilani bwanji mkachotse makolo anu mimbazo
Azayambe kuchotsa ndi mayi Calista Mutharika ndimamene enawo azizaloledwa nawonso kuchotsa
Zapambwindilo zazii,osangonena kuti tidziphana!
Chifukwa chake amalawi sizatukuka mlungu atilanga.
Stupid idiot mr Presdent
A Malawi apemphedwa kuti akhale anthu omvetsetsa pa nkhani ya lamulo lokhudzana ndi kuchotsa mimba.Malamulo ololeza kuchotsa pakati akufunika ku Malawi.Malingana ndi mkulu wa bungwe loona kuti palibe kusiyana pakati pa akazi ndi amuna, la Gender Coordination Network, Mayi Emma Kaliya, a Malawi akuyenela kukhala anthu olola kuti lamulo limeneli liikidwe.Pakhala pali mpungwepungwe pakati pa a Malawi pamene ena akufuna kuti amayi aziloledwa kuchotsa mimba koma ena, maka atsogoleri a mipingo akukana kuti ayi. Iwo ati chifukwa kuchotsa mimba ndi kupha. Koma onse ogwilizana ndi kulola kuti amayi azichotsa mimba ati dziko silingamalamulidwe ndi malamulo a Chalichi. Enanso akuti mchitidwe ochotsa mimba umachitika ndi kale koma mwa njira zosayenelela.“A Malawi akuyenela kugwilizana ndi lamulo lovomela kuchotsa mimba ili kuti titeze amayi ndi asungwana amene akufa Kamba kochotsa pakati,” anatelo a Kaliya.A Phungu a kunyumba ya malamulo akuyembekezeka kukambilana za nkhaniyi.
Abale malawi ndi dziko lowopa mulungu why doing so?yehova mulungu wanga menyani nkhondo anthu mdziko muno akanali mnthawi yakusadziwa.
zopusa zimenezo,,,akachotse kaye yaiyeyo
dzimen mkupang ndzanu, mzapedza kt wacotsa mimbayo unali ndi mwan yokhay amene watay. abale inu ndzoona kumalimban nd mlungu? lnenso ndkupemphela kut mlungu yemwe ndkumziwa akukanthen.
Zoona mulungu awakanthedi,akutionjeza kwambiri,asakambilaneso nkhani ngati zimenezo,kod akufuna azikambilana zichani?zopusa!
now you are coming with shit stories,stop misleading people.
uwu ndi mwikho
Ndi ufulu wamunthu even kuno ku south africa akuchosa mimba basi and amachita kukhoma ma poster
ooooh my God mchifukwa chake chichonse chilichovuta mdziko lathuli mvula kuvuta njala yosatha umpawi wadzaoneni chifukwa chamachimo….Malawi walero wavuta basi
Zopusa zimenezo bwanji osangosiya kukwerana bwanji
Tilimunyengo zowawitsa
Ambuye azitithandizira
Amalawi ake ati
Iphani ana anu omwe akanakusungani patsongoro nanutso aboma kuikila uboni zimenezo cholinga chanu chili chani
akupemphayo ndindani? mulungu amukhululukile
Kodi inu @malawi24, sukulu yake munapita ndi iti mukulephera kupereka uthenga osakwanira komanso ofuna kusokoneza anthu? Nkhani ndiyokuti akufuna kuvomereza kuchotsa mimba mwa malamulo osati azilola amayi kuchotsa mimba ngati anthu ndikale lonse samachotsa mimba.
komanso bwanji osangopewa kulekana ndikutaya ana osalakwa?
Kodi ndidani akuyambitsa nkhani yoonyasayi Malawi wavunda
Bullshit
Ndiye tilemera?
Asilu Inueti Amayiwo Si Amalawi?
Wayambisa ndani bwanatu ulendo wanu womwe mudapita ku usa wayamba kutiophya kenako tinva zoti ana nzimayi akachila ana aziwasiya kuchipatala ngati kuno ku joni akatelo aziwaika ziwanda ife ayi takukanani kupha toto kabwezeni.ndalamazo
Inu zisiru kwabasi zikusiyana bwanji ndikuphana,kodi amalawi mukufuna dziko lanulo lifike pati pati kweni kweni,inu zoona mungamalankhule pamaso pa mlungu kuti anthu azitaya mimba.Mwa ndi lirisa ndipo ndikupempha kwa mlungu achite nanu moyenelera nonse amene mwatengapo gawo pankhani yokupha ana osaziwa kanthu ndi osalakwawa Dzikomo
I like your coment bro,that’s true speaking
Ndizokhunza kwambili kwa munthu amene amaopa mlungu braz
akanakhala 100 anthu ngati inuyo chimwene wanga Issa bwezi dziko likuyendako bwino.
Man mphatso zandikhuza kwambili chifukwa ineyo ndili ndi moyo makolo anga anakaganiza zokuti anditaye sibwenzi ndikuona zomwe ndikuona zokoma ayi
Ali ndi chibwana kwambiri aganize mozama bwino asakhotetse malamulo amulungu. mwayankhula bwino brother Isaa Gandi
Bro isah mulungu apitirize kukupatsani nzeru;amalawi taiwala mulungu zoona
Vuto ndiloti akamapanga ma decision Mulungu sakumamuikapo……….za usatana basi……. Let them achita nawo posachedwa!
Good point issah
Dzikomo anwene nyelere
Zizindikilo zamasiku osiliza izi anthu akumalolela kumachita chithu akuziwa kuti ndichilakwika chifukwa cha makobili.kodi kaliyayo mayi ake akanakhala ndi ganinizo lopusali akanakalankhulila kuti mbwelela zakezi?
Amen!
Achita bwino tachulukana maka chakumwera
Za ziiiiii zopanda nchele.
Kodi Lamulo Limenelo M Biblelo Lilimo?
Am not supporting this law kma kdi malamulo onse aja ali mu Bible?????
Musiye kuchindana
Kuteloko, alola kale chifukwa chandalama apasidwa ndi maiko ena, mabungwe ndi Papa. Boma linavomeleza Zamatanyula apa akuti kuchotsa mimba, mawa ndizina. mabungwewa afuna kulowasta zausatana kuno with exchang of money. wk up mw!
Amalawi tsopano asowa zoti apange ndiye kumangoganiza zomachotsa mimba.Nanga tingati pali zeru pamenepa Kkkkk kumaganiza mozama amalawi inu muli ndi moyo pano bwanji akanakuchotsani nthawi yomwe muli ndi mwezi maganizo amenewa mukadawatulutsa? Ngati kutenga mimba inuyo kwakutopetsani katsekeni osakhala kumawuza anthu nkhani zopusa ngati zimenezi. Palibe mimba yomwe imabwela iwe mwini usakudziwa,Ganizani zoti zitukule Malawi.Mukunva
Zoona madala akuganiza ngati anachita kugwa kumwamba aiwala kt akhalako mimba akufuna kuchotsa panozo. Chodabwisa akufuna azichotsa zaanthu ena ngati azimawo ndi azikazi awo angachotse
gyz kt zixakukhudzen jst get married bac
Pakuti chiuta walizomera kukoma namwe komani chiyeluzgo panthazi
ZAZIIII AMAYI AKOAKANAKHALA ANAPANGA ZIMENEZO BWEDZI IWE ULIPO
iiiiiiiiii paka pamenepo moto ulipondi kwa mulungu
abomination on abortion
Koma mmene yakulila imeneyi ndiye mpakana kutaya?
Zopusa zimenezo akuteroyo mwanayo amalenga ndiyeyo zochitsilu basi Malawi sazathekanso kumangomvela zilizonse zoti munthu akamachotsa mimba amatha kufa simudziwa zamanyi basi
Kod kumalawi kuli ndende zakazi?? Koma akanakhala amuna bwezi kulikumanga Malawi yose, pumbavuzenu!
amabugwe ife2 zochotsa mimbazo ximatinyasa,zamathanyura ximatinyasa km yesetsan kt frozy timweso
Nyasalnd ndi fck , kungokulisa chiwelengelo chauhule bas
koma zafikapo kutha kwa ziko,anthu asiya kuopa mulungu koma kuopa lamulo shaa!
Mawu mawu sister
Eeetu,,,,,End times
end time
kuchotsa mimba ndi ndalama yomwe papa wapereka ku dziko la malawi zikugwirizana bwanji pamenepa?
Mukamati akuloredwa kuchotsa mimba amakaniza ndindani popeza zake zonsezi anthu mimba akhala akuchosa alipo anamangidwapo BLM NTchitoyake yaikulu mesa ndiimeneyi nde mufuna ukambachani apa
Kod inu kholo lanu likanaganiza zotaya mimba mukanabadwa? Mukalemba muziganiza kaye
Satana watha mantha chomcho mpaka akupempha anthu kuti azitaya mimba(azipha ana) kapena walamula ndi Tramp
kuchita kupemphedwa ?
Nosese
palibe zochotsa mimba anthu akamakwatana amakhala akudziwa kutii akhoza kupatsana mimba.paliibemimba yobwera mwangozi ndie kungosiya kukwatanako,fwetseki mutitukwanitsapo apa.
Choka limeneri ndilo khalidwe lako lotukwana usaname apa,chilungamo ndichimene ukunenacho.
kodi kukwata mkutukwan?
Musapemphe amalawi kma mupemphe mulungu…….musakakamize kut tikuthandizeni kuchimwa inu Ana a njoka! !
Chfukwa Cha Umphawi Bwanji Mumangovomera Zilizoxe? Ma Injection Akulera Dzibayani Pamene Iwo Sabaya?
Kma Kumalawi
Mmmmm dziwanda tsopano ku Malawi dzayambika
ubwino wake milandu imeneyo muakayankha nokha kwa mulengi
Zayamba!Muganiza Papa Ndikumuziwa ineyu!Angapeleka Chithumba chamakobidi opanda profit yake’kkkk Muyenela Kupeleka sembe ka. Nde Malamulo Amakatenga Kwa papawo Ndamenewa Zina zikubwela apa mphoyambila chabe.
Sure
If this issue of abortion is supported by the Pope let God himself punish him BUT if You statement is false what do you think will happen to you?
I wowo akanati awapange zimenezo bwezi akuyankhula zokhuta ngati zimenezo?
only God knowz ….
Wayambitsa Zimenezoyo Mgalu
Mmmmm inde mayiko ena amavomeledza koma kumalawi kokha tisavomeleze zimenezo.Kuchotsa mimba ndi tchimo.
Palibe chanzeru pamenepo
Zapansi pa nyanja ayiyayaayiyaya…
koma kumalawi kuno 666 wayambika basi
Kuchotsa mimba? Jesus plz come quickly. All things that you said don’t do, one by one are now changing in favor of the devil not you. Very pathetic. God will judge you one day
Koma a Satanic mwafikapotu ndi mabungwe anuwa.