Rabs Processors
Rabs Processors
TNM 4G Lite Flash
Old Mutual

By November 9, 2016

Fresh from claiming a double in the Urban Music Party (UMP) awards as best reggae dancehall artist and for album of the year, Malinga Mafia has untied his tongue on his relationship with female singer Sangie.

The Archaida boss commented on the issue in a radio interview when he was hosted by Joy Nathu on radio 2 FM, in Made on Monday program.

malinga-mafia-sangie

Malinga Mafia and Sangie in ‘I Love you’.

Nathu who was also honoured for his contributions in the country’s entertainment industry as a radio personality, asked the reggae dancehall Mafia if he is an item with Sangie.

But Malinga said he believes in making matters of his love life private as such he could not comment anything on his relationship with Sangie.

However the award winning recording artist went on to describe the songstress as one of the baddest female singers in Malawi. Malinga revealed that they have worked on a number of projects together, a factor that continue to raise questions.

This means Malawians will continue speculating on the pair’s relationship. However a good number have been convinced the two are lovebirds due to the high level of proximity between them.

A romantic delivery in I love You video, exposed feelings towards each other but being a created art where people can act, gave people a reason to accept the visuals as they are without making conclusions.

However one wonders as to why it was so hard for the reggae dancehall icon to give a simple yes or no to the straightforward question on whether the two are an item or not.
265 Comments

 1. amuna okhaokha atengana sindikutha kusiyanitsa

 2. Hehe, levos to dis ting VS ili busy,,,wat a nyc couple!!! Big up braz malinga umatiimilila

 3. Nthawi yonse Ija simumkaona kut Sangie ndiwakuda?. Hahaha kulengezaku mkoyambaaaa. Iwe umkangohopera kom Malinga wakwanitsa kumuuza mawu akukhosi kwake…… Big up guys….nothing can take you down. A nsanje akamba mkutopa….keep de bond tight and real. Mulibe problem

 4. All the best ts god gven

 5. Chidodo chandipweteka sangie ndi ma hop anga,,,,,,,,,,koma ndiyesabe mwayi mwina angasinthe maganizo ngati all the best

 6. nice pair

 7. All de bst guyz….

 8. Amene munyozanu koma mwaziona bhobho inuyo umalawi ukukusowetsani mteñdele…mvuto siinu koma umalàwi uli mumtima mwanumo..ñsanje mudatani iñu agulugufe bax mene ķwachela busy ķumangokamba ya ena bwanj osamakambà zakwañu ndi kachimbuďźi kogumuka kaja iyyàaaa shupiteeeeee long live gyz o da best #malinga.sangie

 9. Who Jaah has blessah no man can curse

 10. Best wishes guys

 11. asiye atokote iwe zako zili bo watenga

 12. Zayambaso liti?? source nyimbo ija….ya love yapalimozi!!

 13. read “Marriage is a private affair” by chinua Achebe

 14. Agie Tiza says:

  Bobo,Phyzo ndi Ruth bwa.zimatheka

 15. MALINGA NDI Best Artist OF THE YEAR Musyen Mukangova Yoyoooo! Ma Haters Ose Kubisala Mu Salu And Malinga Ndi Sangie Ndi More Palibe Asyen Please

 16. Kane Faife says:

  Asiyen azigonana inu mukuona zachilendo ayamba samenewa zikuchitika kaya aphane bas akufuna abale mwana oimba chamba cha matenda

 17. Uka dissa nde ukangoona ziii jst rememba levels aint da same lov u sangie n malinga mafia.

 18. Zilibooooo

 19. angotengana onyasa okhaokha, kufuna kunyasisa ntundu wa a malawi chani?

 20. Wapeza dona amakhala kt wapeza a gud ting wel done mafia

 21. Mistake,mamusician On Friendship?Shame.

 22. zilibwino kwambiri go ahead,enawa ndi obwebweta 4give them,tikufuna weniweni wodalitsa tidzabwele,sangie osataya bomwetamweta Mulungu wapatsa malinga,monga muja zilili Dan ndi Emmie zabwinotu kobasi,all the best guys.

 23. Nthawi yawo guys bwanji kodi aliyense Ali ndichokonda chake

 24. zao.zimenzo let them be its there private life,

 25. kod guyz anthu amenewa supachibale koma? coz kunyasaku nde akufanana bwanj

 26. Nyc all the best

 27. Ndie Mmalawi ameneyo kuvuta kuyamikira nzake eish guys

 28. Man malinga mafiya mbambad mundisamale izi ndinakuuzan kale koma mumakana apapokha tisapezane ngat ule ndo uja kkkkkk mwandipanila chik yanga tionana kkkkk. Gud wish bro kip on loving each ada

 29. Zilibwino ngati iron monky

 30. If u feel like don’t have comments its better to be silent rather than talking nosense. Don’t u feel ashamed that u r there embarrassing yourself with such comments u make? Turn back and luk the dates u have made.were the beautiful as poshy cars?

 31. #_Mafia #sangie do wary wt wat pipo r commenting jct mek up UA love healthy bad #man

 32. Zilibho guys mahaters mupange zanu tikuonelen mazoba inu et? Kuzolowera ku header mmisikamu ndimma deport mzanu akasankha chakumtima kwake inu ku phwisila agalu , sangie vs malinga mumakwana kumpanjeko love u all

 33. Mmmmmmmn Malawi ndi chani??(akazi timawakondera zifukwa zambili( not only body ndioonda kapena onenepa?? No!!!)paja pali mau oti kukuka mphono sikuziwa kumina >> pot is inside not out side, kungokhala ndi mtima ngat sabola Malawi why?? Nde munyatu adzanu akondana hehehe ng’ombo!! Nditoesa anatokukana eti?? Kapena hule iwe Malinga mafia anakulumisa chakuda eti?? Big up ( I.L.O.V.E > utWo

 34. My best artist malinga mafia

 35. Sono mimba adataya ija

 36. As we all created n God’s image we r all beultiful people… Malinga z handsome & Sangie z beultiful.. Others says Sangie ndiwakuda don’t u know dat we r Africans , we r black we r nt American s…..keep loving..Jealous z nothing..

 37. feelings of black people always being the sme: akondana basi asiyen;koma malinga umazembera beb yanga.kkkkkkkkkk?

 38. #Ndangozizidwaine

 39. chikumbutso chitsundi

 40. Dont say “saggie wapanga chani amuna onsewa ” ukamuonesetsa saggie ndi oneka bwino ?

 41. zikhoza kutheka kuti malinga ali nawo angapo dats y akulephela kuyankha zomveka chimodzimodziso sangie. omukonda sitimubisa man up n tell the world the truth.

 42. Koma fanz tili ndinsanje kkkkkkkk

 43. The comments though

 44. bola osakayalutsana mukadzathana zilakolako zanu

 45. PHWANYIKE vs GUMUKANI…in love.com

 46. #malingayo akamdyetsa chani #sangie dollar alibe timashow tomweti basi muvute nato tima award topanda ndalamati kkkkkkkkkkk tiona mmene zithere

 47. Joe Munlo says:

  Kkkk km mkazi ameneyu ndiye waonjezanso kuda kuneku

 48. She is not beautiful at all anyway thats love keep on

 49. Mukukhala osasiyana sound yanu timayifila heve

 50. Ka slim man ndaku fila Malinga ulemu wako

 51. mabanja alero. kkkkkkk!

 52. Mukhale rihana ndi chris brown next year pabwera drake azakhala gibo lantos kuzamulanda malinga…!!

 53. Who cares?to me it’s like 2+2=39

 54. Size ya bho.

 55. mmmmh zilibwino malinga

 56. ndichifukwa kumalawi oimba achitsikana samapita patsongolo nalo lutso lawo akangochuka pang’ono basi apanidwa akatelo basi ziiii kuimba kose balalala lol hahahahaa malo moti apitilize kuimba bwinoko busy basi nkhani zake izi shame on Female malawian Artists!!!

 57. Ben Phiri says:

  Ine Ndiye Zisandikhunze, Mwamva?

 58. Mimi Stark says:

  Koma ma comments ali apa.. anthu ena mukamayankhula ngati mukuthokera ku buya.

 59. aaaaaaa kukongola kumapha wachita bwino size yako imeneyo unakagwira okongola anakakulanda kalekale mbalamezi poti masiku ano love ndi thumba what are you doing? osaputira makolotu izi

 60. FIRST LET JAH BLESS YU ALL ,Mr , Mrs , nkhani yabwino mwakula in music mission timalimbiktsana kuti tidzikhala ndiokondedwa modzi monga chitsazo chanthu Adamu & Hava , chifukwa pali mawu amati wapedza kadzi wapedza chinthu chabwino , dzilibwino tiyeni timutsiye m’lengi ankhale nkhoswe ndi mboni padzonse , monga ife ana A baba jonai maina anu music industry uko ndiudzeni ,Dzina limodzi lomwe likuimirira nonse I yu hear mi kno ryt kno , Jah bless yu all again mi say

 61. nanga pot mkazyo amangodyesa

 62. Big up

 63. all the best

 64. Alick Wadi says:

  nafeso tili mchkond chovetsana kukoma ngt chanucho

 65. agogo says:

  guys majelasi ayi asiyeni antu awili akondana basi

 66. Zili bho bwanj…manyaka okhaokha…kutengana…ine ngakhale atandilozetsa mfuti mmutu…sindinganyenge…mkazi ameneyu…taona akazi ife osat akaipa dziwa nyimbowa..shit..

 67. nsanje iyayi mupange zanu

 68. ife zaakazi tilibenazo ntchito ,mawa zikavuta mudzatiuza kuti chain? Music yanu timayikonda kuopsa!!!!!!!

 69. Tripie Jay says:

  Ndikhale mbuli ine

 70. Malinga maluks ali~poor

 71. One ndnango3la sound yanuo basi osat nyasi zanuzo

 72. All Di Bst # Couplez

 73. Go to hell

 74. mwana wanu azakhala ng’ona sinanga nonse ndinu manyaka

 75. Niribe polobulemu.

 76. Those days during tsado ati secondary level we use to say let the child be nyani weni weni

 77. Anakana kugwira tsuna yaboo Malinga akuopa anthu angamamdyere sinanga iye ndi sangie onse ndimanyaka

 78. oyimba amenewa amandiyimbira boo sangie ndimankhumba heavy kkkkk

 79. angokumana khwangwa zokha zokha mwachita bwino mwatengana, koma kumbali ya sound inuo!! mumatha osanama

 80. Hahaha Sangie! Sangie! Ndichani Iwe Sumawuona JOE GWALADI. basi makonda ~ makonda

 81. Christopher martin vs cecile… Nzabhobho..

 82. Keep it up mumakhalana wasanje akakolope mu lake chirwa

 83. Nsanje anyapapi inu hiyaaa ….all the best my old classmate mphatso mbekeyani(sangie)

 84. Zili bwino guys

 85. Amos Mtawa says:

  Muzasiyaliti nsanje gwirani wanu wama looks

 86. Sangie ma looks ndi 0 pa 100 akaz osewa naweso malinga akupepetula mkaz ndi onyasa uyu unamuona mzako Gwamba chick ali nayo ija yolozeka not Sangie….mkaz obhowa Sangie si mkaz kkkkkkkkk

 87. mmmmm chomwecho panspano

 88. chodandaulitsa ndi chani apa?onsewa ma luks alibe ndiye pali nkhani apapa.kutchuka kumakongoletsa basi nkhwanga zithanepo bwa?!!

 89. ndinamvaa kut malingaa sali,,,,,,,,,,,,,,,,,kkkkkkkkk sinatchulee kanthuuu

 90. Louis Mgawi read for me the post n all the comments

 91. realy masuna osewa

 92. Osewo palibe oneka bwino

 93. Zili bho akawonaso kuti sizikuyenda tibva kuti ayamba kuyenda mun’dima ajoina ya Babylon

 94. phwanga daily kulemba nkhani zosamaliza bwanj??? utseke ichi ngati suzimaliza nkhani…. shupitttttt

 95. kkkk ndakomoka

 96. ma swazie okha okha awa. wina amasowa mkazi, wina amasowa mamuna

 97. Timadabwa ife…… Wayitha malinga koma mfana ulowa umphawi naye ameneyo kkkkkkkkkkkk

 98. mmmmmmmmm komaaaa

 99. Kugwilira kuchuka haha koma the fact is Sangie ma looks ndi 0 pa 1000

 100. Manje????

 101. Admin mbuzi ndakupatsani mbuzi yamunthu inuyo admin

 102. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk km yaaah

 103. Nkhwangwatu iyi kkkkkk

 104. umakwana malinga panse pa centre azawona ngati umangotha kuimba kokha

 105. Kkkkkk some comments thou

 106. Xiwanda za satana ixi

 107. Let God Guide Them All

 108. Ndumwa frozy ine

 109. Achamba okhaokha hehe

 110. nde olo munyoze chisinthe ndi chani??they are in love bas asiyenika…….all the best #malinga and #sangie

 111. weh we deh…..bodza anthu nsanje mudatani osangoyamikila bwanji ndr olo

 112. muthu uzikoza tsogoro rako malinga adakoza tsogororake nanga iweyo udakoza tsongoro rako

 113. zili bho guys musapange za CB n Rihanna koma tikufuna kuphunzira painu love yonjeyesa.pill and potion copied n pasted on #Sangie n #Malinga iwo kumati I. L. O. V. E. Me lv me lv…single imandiwaza imene ija….then #Sangie I ll do it 4 ur Love unayimba kunatha.

 114. Asibweni APA mwawelawaka kkkkkk

 115. gun boss woza!!

 116. Uuuuuuuuu

 117. Zkumuwawa azlume kusana,, salute gun boss umatiimirira jah bless u

 118. Zaziiiiiiiiii

 119. Apatu ndi amuna okhaokha zoti wina ndikazi ndakaika, mkaz uyu ndi mavukuvuku kkkkk kazi oti olo nyama alibe angot sololo kathupi kuuma ngat usipa wa dzuwa

 120. Guys kuyamikirana ndi bho penapange nzathu akapanga zabwino,,Malinga ulipo work hard kuti ansanje agonje ndili mbali yako

 121. chikazatha muzaneneso

 122. Nyc couple

 123. Akumana majombo oka oka,apa ndiye kuzikwatira.mpakana family kut. Tiri ndapongozi shemeeee

 124. chani this iz un educated union

 125. Alibe ndi otchi yemwe ,,akutayitsa thawi……

 126. chani this iz un educated couple

 127. Kodi Ka Malinga ko chipanda kuimba sibwenzi kali ka gule kapena kolima fodya kameneko..Sangie ndimwana okulira BT

 128. Kodi Ka Malinga ko chipanda kuimba sibwenzi kali ka gule kapena kolima fodya kameneko..Sangie ndimwana okulira BT

 129. Bola ngat munayezetsa magaz pot oimbanu mumangopisa pisa.

 130. sangie and Malinga? amatani anthu amenewa? sindikuwadziwa2

 131. ma jamaican nokhanokha all the best mumatha

 132. Kungotengana oyimba abwinoabwino okhaokha n’kukwatirana? Kkkk, all the best

 133. Ndie ife titan?? Kaya amakwerana kaya ai, kaya amaswana plain zawo zimenezo,ifenso tili nawo achikondi

 134. lol Martha Mandiwa

 135. #Sangie ndichani amuna onse ati mbwee awa kukakhala paubwenzi ndi #Malinga? Hehehee chimanga chiloradi opanda mano eti

 136. Tmadabwa msanje Sagie

 137. Muna bonzana kale basi vuto palibe.

 138. sono iweyo chibwenzi chako chija uchipanga chani ????

 139. #Lol…. bt nyc

 140. That is a good decision

 141. Kodi mukutiwonesa oyimbawo nanga tipindulapo chiyani

 142. hahahahaha aMalawi nsanje bwanj?

 143. Nt supporting this at all y my sangie!?? Y????

 144. My Advice,,chonde Mukayesetse Paja Maceleb Uhule Too Much,,,, Maceleb Akumalawi? Kkkk

 145. Big Up To Sir Malinga,ndiye Yake.

 146. Malawi24 Malinga finally speaks on his relationship with Sangie Fresh from claiming a double in the Urban Music Party (UMP) awards as best reggae dancehall artist and for album of the year, Malinga Mafia has untied his tongue on his relationship with female singer Sangie. READ MORE: https://malawi24.com/2016/11/09/malinga-finally-speaks-relationship-sangie/ Malinga finally speaks on his relationship with Sangie | Malawi24 – All the latest Malawi news malawi24.com

 147. Malawi celebrities kkkkk, tamalembani zopindula dziko admin.

 148. Munakayezetsa Kaye?????

 149. Paja amati celeb za ma looks zilibe flop kma ,,,mmm

 150. Enanu envy !

 151. malinga ndindan nanga amatan ???

 152. Amakwaña

 153. Malinga wasamba liti kodi? ana a mu 18 onunkha thukuta.

 154. level yabho malinga

 155. Eee Mahope Apitaso

 156. Koma ma celeb adziko losauka

 157. mmmmmh no commentoo

 158. Tinaziwa kale oimba inu kkk paja ndinkamfuxani mmabixa zchani?

  • nde anakanatu #Sangie kunena chilungamo pa touching base…mmm big mwandikumbusa ku home country ndilibusy kuonela mbc TB kwabraz after tym imeneyi muden masten alibe kalikose.God is great.

 159. Zosakongola zokhazokha

 160. Zosakongola zokhazokha

 161. amat chan ife tili pa free data tu

 162. Omega Bema says:

  Mwati ma celeb aku Malawi awa

 163. IFE TINAZIWATU ANAYAMBA KALE AWA

 164. wowww

 165. kkkkkkkk oyimba adzitengana oyimba okha okha

%d bloggers like this: