The Presidential Cup semifinal between Blue Eagles and Nyasa Big Bullets on Wednesday at Nankhaka ground has grossed money up to MK8.1 Million from gate collections, Malawi24 has learnt.
The Peoples team beat the Eagles 5-4 on post matches penalties after the two sides settled for a goalless draw after 90 minutes.
According to authorities the two teams shared MK1.6 Million with the the Football Association of Malawi (FAM) getting MK1.1 Million and the other stakes for other expenses like security.
Bullets now have completed the quarterfinal list and they play Kabwafu on dates yet to be named.
FULL FIXTURES TO COME
Presidential Cup QUARTERFINALS :
Epac F.C vs Moyale
Kabwafu F.C vs Nyasa Big Bullets
Be Forward Wanderers vs Max Bullets
Dwangwa United vs Mafco F.C
Kkkkkkkk anthu ena kumva kumawavuta ndithuuu nanga apaso pali nkhani yoti munyozere team apa aaaaa ayi
Atibera kunali gulu ma pin pagate
Mpira upitilirabe kubeba mu chikho chimenechi chifukwa eni ake mpira onse awiri adakali mommo.
Kodi game ya Neba ndi karonga utd, gate collection anapeza ndalama zingati?
Semifinals really??? What a mess eish!
Palibekanthu ndufe agalu komamabe tawina 5/4 aaaaa neba yamikaaa
ooooops!!!!!semifinals???? malawian journalists
kodi mpirawu mumasera ndiife neba ndinu agaru nonse ku teamko mwava.
kodi mpirawu mumasera ndiife neba ndinu agaru nonse ku teamko mwava.
kodi mpirawu mumasera ndiife neba ndinu agaru nonse ku teamko mwava.
Kodi Mwat Mpira Wa Dzulowo Unatha Bwanj?
It was abg game no doubt about that
It was abg game no doubt about that
Ma admin ambiri England ndi mbora kkkkkkkj Kananji style
Ma admin ambiri England ndi mbora kkkkkkkj Kananji style
Pakhomo ngati ndi 1000 ndiyekuti amalawi tilipo ofunika tizilela m’manyumbamu
Pakhomo ngati ndi 1000 ndiyekuti amalawi tilipo ofunika tizilela m’manyumbamu
Out of the total amount, teams shared Only 1.6. and FAM pocketed up to 1.1, what for? And we say we want to develop football in this country. I dont see the decision coming to fruition. Teams were not supposed to share such a small amount.
Ngati ndi malamulo ake, lets revise them.
Zambodza semifinal palimbe wamenya ya cup imeneyo
Abale mesa mawu oti #learn amatanthauza kuphunzira, nde malawi 24 has #learnt akutanthauza chani. Ma journalists amafuna azitiona pang’ono eti!
Abale mesa mawu oti #learn amatanthauza kuphunzira, nde malawi 24 has #learnt akutanthauza chani. Ma journalists amafuna azitiona pang’ono eti!
blue eagles atidyetsa udzu,,u had all to kill these fools
blue eagles atidyetsa udzu,,u had all to kill these fools
Pspa mbale mudyabe udzuo
Pspa mbale mudyabe udzuo
Ati “maule ndi nkhani ina neba ndi mwana” ii koma abale, tamuudzeni olembayu aditha kulemba chichewa mwina ena mudzinvensa. Dzikugwiridzana bwanji dza ndalama dzopedzeka dzulo ndi Neba? Mmmm Malawi nzxanga tangosiya ngati sunanve icho chinenedwa.

semi final yake it? koma do u kno zomwe ukulemba iwe mbuli yophunzira?
semi final yake it? koma do u kno zomwe ukulemba iwe mbuli yophunzira?
Kkkkkk maule ndi nkhani zina neba ndi mwana
Kkkkkk maule ndi nkhani zina neba ndi mwana
Kungoti Mbava Zinali Kuntchito, Likanakhala Loweluka Akanapeza K2 Million
SEMIFINAL CLASH?. K5kkkk
Why are you misleading people you Malawi24? the game was not semifinal please be accurate when giving information.
Ndalamazo zapezeka pabwalo laling’ono komanso anthu ambiriso sanabwere poti ena anali ku zintchito zawo ena ku maphunziro, nde funso nkumati zikuvuta pati kupeza ndalama zoposa apa pabwalo lalikulu la kamuzu stadium pamene anthu amabwera mwaunyinji masewero akakhala pa tsiku lopuma?
Koma ground ili limandibowa koopsa kukangoonerera kuukonda mpira dzulo ndithu.
Oky ndye zimakhala zovetsa cison nakhaka ground lalng’ono grosses that amout Kamuzu n Civo maxmam 5mita
Kwapita munthu wankulu kuzidziwika basi
Koma yeah why dont u let ozitsata write da story or just ask if u r not sure of facts n details. Firstly da game wasnt a semi final and secondly it will b kabwafu vs bullets not what yo saying
kkkkk FAM mpaka K1.1 Million koma yah mateam akumalawi adzikhala wosawuka because of this development
Basi?
It’s Bullets which qualified not Blue Eagles as you are saying
Round Of 16 Not Semi-final Nyasa BB Not Blue Eagles To Meet Kabwafu