Chakwera’s head is empty – Mutharika

Advertisement
Lazarus Chakwera
Peter Mutharika and Lazarus Chakwera
They never cease attacks on each other.

Malawi leader Peter Mutharika yesterday hit back at leader of opposition Lazarus Chakwera accusing him of having an empty head.

Speaking at the opening of the new Reserve Bank of Malawi branch in Mzuzu, Mutharika clearly indicated that he was unhappy with Chakwera’s remarks at Parliament that the State of the Nation address he made in Parliament was empty.

“Sometimes when your head is empty, you see everything as empty,” said Mutharika.

In his address, Mutharika also ignored the leader of opposition by not mentioning him in the salutation.

Chakwera said that President Mutharika’s SONA was empty and a bedtime story.

Advertisement

433 Comments

 1. Malawi coutry we do about Agricutur but why we buying Feltelizer with koponi you can talk and talk but this is the thing we need to talk about it koponi achose apange mutengo woti mulimi aliyese atha kukwanisa kugura. K20,000 bag ra feteriza limozi nanga mumphawi ungakwanise Amalawi tiyeni tiganize bwino kodi chimene chinapangisa kuti apange K1000 yogwirana ndichani kwenikweni,kubwera kwa koponi kunawonogesa zithu zambiri muziko lathu nanga bwanji akulephera kulipira kapane yopanga feteriza kuti atipangire mopanda koponi.Amaba ndalama zose ndi kulephera kulipira kapane yopanga feteraiza kenaka amatimata phura kumaso ndi koponi

 2. Malawi coutry we do about Agricutur but why we buying Feltelizer with koponi you can talk and talk but this is the thing we need to talk about it koponi achose apange mutengo woti mulimi aliyese atha kukwanisa kugura. K20,000 bag ra feteriza limozi nanga mumphawi ungakwanise Amalawi tiyeni tiganize bwino kodi chimene chinapangisa kuti apange K1000 yogwirana ndichani kwenikweni,kubwera kwa koponi kunawonogesa zithu zambiri muziko lathu nanga bwanji akulephera kulipira kapane

 3. wat I knw we pple alwz blame wat others r doing en those holding position never respect other pple ‘s viewz, onse ndmbuz bax, palibe angakoze dzikoli anthu anzeri anapita! ngakhale mukawapingapinga anthuxo ndnu ovuta

 4. The only time you hear Chakwera or Uladi Mussa is when they are responding to APM. These guys are ever behind Peter. They aren’t vigilant as to be ahead of APM. Just trudging behind mkolokolo wa Peter, aphwitsilidwako kumbuyoku awa, ndiopusa. Shameful opposition, can make a story of their own musemuja kumangoti Peter, Peter Peter iwowa akutani?

 5. That’s the problem when you don’t know that you don’t know. …. that you’re the one who’s heard is dumb

 6. Dziko la malawi likusoweka usogoleri wa mphamvu ngati wa malemu Bingu,dziko silingatukuke ngati msogoleri alibe experience yoendesera dziko.katundu wambiri wofunika pamoyo wa tsiku ndi tsiku wakwera mtengo mu nthawi ya bambowa.Tivomeleze kuti kusowa kwa mvula kwabwelesa njala koma bambowa alibe njira zothandiza kuchepesa njala.joyce banda zinangovuta kuti amaendesa boma ndi magamba komba koma mmai uja anali ndi mtima wofuna kutukula malawi.Boma ili presdent ndi vice wake ndi madolo odziwa masamu a kabedwe,mulungu thandizani a malawife tikuvutika chifukwa chosowa asogoleri angwiro.

 7. oooo!paja munthu akamakula amabwerera kuumwana eti!zoona munthu anganene kuti mmutu mwa munthu mulibe kathu?ubongo umakhala kuti?kapena chakwera amuchotsa ubongo mmatsenga?takulani.

 8. Ku Katolika a Nsembe akatenga njira zawozawo zosemphana ndi zimene analumbira, ubongo wao siumaganiza bwino komanso palibe china chilichonse chimene amapanga cha nzeru. Zimenezi ndizo mphamvu za CHAUTA ndipo ndizimene zikuwaonekera a Lazarus Chakwera ndi chipani chawo.

 9. Politics is a dirty game, my advice to Lazarus chakwera, wait for your turn if there is than saying bad comments which are confusing people who are already confused. There’s no man who is perfect, kamuzu did his part, we can see good things he did although he had a weakness, along came bakili who also did his part and he had a weakness also, bingu also and now peter is on, let him also do his part.This is like soccer , one or two touches or dribble then you pass the ball, my point is stop your criticism but lend your helping hand inorder to succeed.

 10. Hahahahaha!, whose head is empty?, Albinos are being killled everyday and you are failing to stop that malpractice with words only. Foolish APM

 11. vuto anthufe sitikudziwa dziko komwe likupita ai tikuona ngati zinthu zuzakharanso mwa kare ai mavuto sari kumalawi kokha kuno ai zambiri zikuchitika mmaiko ena komanso amalawi sitichedwa kuiwara komwe tikuchokera mavuto enawa sakubwera ndi president ai ndipo mavuto ena analekereredwa kare mavuto enawa ndipo timkadziwa koma kumangozisiya pano zinthu zafika nkhosi tikufuna zithe msanga msanga ai sizitheka ndipo peter sasova mavuto athu onse ai chifukwa zina zikuyenda ndi bible malembo ake or atabwera wina panopa president sakwanitsa kusova zonse ndlama zikubedwa osachitapo kanthu ndipo peter dziko lino analipeza muri mavuto ambiri vuti kumalawi kuno ndale zathu ndi zasanje otsutsa kwawo ndikuononga president chabwino choipa zonse amatsutsa ndipo saganizira anthu kunjaku ndipo otsutsa safuna kupereka maganizo abwino kwa president amaona ngati amumenyera kampeni omwe uri umburi munthu ukapereka magaizo abwino anthu akuona azakuvotera coz amalawi apano anazndikira ndipo wanzeru ama amudziwa pano!

 12. Truth hates but one thing is certain is that even if we try to talk as if things are ok we are same people to suffer at the end of the day….What is good governance if the gorvernment is failing to provide solution to the problems its citizen are facing????? Ur busy polishing those that are using our tax revenues for their personal gains munthu akamalowa m’boma kumamuona ali wosauka kapunthabuye koma after just a short period of time munthu wamela mapiko kulemera kuposa aliyense pamene anthu osankha anthuwo mumaudindowo akukhalira Zikhawo ena kumfa kumene ndinjala…. mumamva bwanji mukaikila kumbuyo anthu andale mbamva pamene abale anu kumudzai akumfa??? Ukakwera pamsana pa Njobvu usamati kunja kulibe mame muli ndi mwayi oyankhula coz inu muli ndipogwira koma mudzimuganizila munthu wakumudzi yemwe amavutika kulawila m’mawa kukaima pamzere kukavota with an intention kuti mwina zinthu zingasinthe, kuti mwina angasiye kusaukila mankhwala muzipatala,,,,Ambuye adzikukhululukilani anthu adyera inu ongofuna kukhutitsa mimba zanu

 13. Ndale.. Chasowa .. matafale and the likes are gone coz of this shit..you live on less than a dollar in a week… you are told to vote for somebody.he wins.. he gets millions of kwachaz …you are still there starving…. wake up guys…

 14. Palibe wanzeru kuposa mzake pasziko lapasi so lets wait end see kut yesu abwera liti osamangolimbana apa pamene mitsonkho mchikwezereni malipilo ndomwe aja,katundu mchidulileni, mkumati zidzakhala bwino antill when? To other side ngat akuona kut president walephera ndipo mu speech yake ili empty iwowo apangapo chani kut zili mu speech yakeyo zilongosoke? Ngat zinthu zikuvuta its thier time now kut azithandiza mumene mukuvutamo ndizithu zawo lather than kumangoti icho ichi mmalo mopanga mavoti amawa

 15. Kodi chakwerayu adathawa chiani Ku mpingo wakewo? Kodi ntchito ya mulungu adamaliza kapena akudelera chomwe mulungu anampatsa? Bwanji ngati Ali wa chilungamo and o wopa mulungu bwanji sadalingalire malemba akuti” be satisfied for whatever God gave you!” Koma kumakalowa ndale kusiya ntchito yomwe mulungu adamuyitanira. Sheeem amalawiiii dziko lathaaa.

  1. Mulngu mukunena inuyo ndi was aliyense. Ingakhale President peter nayenso ndi wake koma munthu was mulungu oona sanga manene anzake choncho. Izi nzooneka ndi mask kuti chakwera anathawa nkhosa sake ngati yona emwe ana thawira Ku ninive. Malamulo khumi akuti maka maka mwa limodzi( u satumikire milungu ina koma one ndekha) kunena kuti sungatumi kire ndale ndi mpingo nthawi imodzi kenakono udzataya mulungu ndikukonda ndale. Ndiye a chakwerawo ataya mulungu kukatumikira ndale momwe multi, mabodza, umfiti, kuba , kuphana ndi zina zotero zomwe mulungu yemwe mukunena inuyo Adana Nazi. Mnkhristu oona amapempherera adani ake ndiku wa nkhululukira osati kunyoza ngati momwe akuchitira achakwerawo mukuti a president a chipani komanso wa assembles of God church.

 16. Ntchito za msogoleli zizioneka, osati mukatupidwa wine kumanyoza anzanu ai. Chiyambileni kulamula boma palibe chikuoneka! Bola bingu anali bho osati pitala wanuyo ai.

  1. Oyo mukuti bola anali bhoyo ndimayesanso anthu munakuwiza achoke achoke mpaka munamulengela imfa? kkkk ine anthu sindimakumvetsani abale, ok.

 17. Achakwela kunyoza sikungasinthe zimthu kom kukambilanalana ndikupeza njila yochepetsela/kuthetsela vutolo kapena achakweza mukuganiza kt mukanyoza ndiye kt anthu akhalambali yanu,musatelo onetsan mzeru zanu zothandiza kutukula amalawi osat kusaukitsa.

 18. Achakwela kunyoza sikungasinthe zimthu kom kukambilanalana ndikupeza njila yochepetsela/kuthetsela vutolo kapena achakweza mukuganiza kt mukanyoza ndiye kt anthu akhalambali yanu,musatelo onetsan mzeru zanu zothandiza kutukula amalawi osat kusaukitsa.

 19. in the 1st place Chakwera was not supposed to talk like he was born yesterday! he was not the right candidate to accuse anything to Peter because it took 31yrs for MCP to achieve what they are talking about,in those days they were using pipo like slaves,so chakwera wadziputa dala,its not even 5 yrs wayamba tukumu tukumu ngati ukubayidwa ndi tsingano bwanji? The man(Peter) is not talkative yes but it does not mean he is empty,bwanji kodi Amalawi. kodi nthawi ya MCP tikanalemba zomwe tikulemba apazi,,,,

 20. in the 1st place Chakwera was not supposed to talk like he was born yesterday! he was not the right candidate to accuse anything to Peter because it took 31yrs for MCP to achieve what they are talking about,in those days they were using pipo like slaves,so chakwera wadziputa dala,its not even 5 yrs wayamba tukumu tukumu ngati ukubayidwa ndi tsingano bwanji? The man(Peter) is not talkative yes but it does not mean he is empty,bwanji kodi Amalawi. kodi nthawi ya MCP tikanalemba zomwe tikulemba apazi,,,,

 21. Eyaaaa! Ndimadabwa kuti mr president muzayakhako liti coz otsutsawa amakuonaningati opusa ayiwalakut anayimanawo pachisakho iwowandikuluza bt makani ngatialindizelu

 22. Eyaaaa! Ndimadabwa kuti mr president muzayakhako liti coz otsutsawa amakuonaningati opusa ayiwalakut anayimanawo pachisakho iwowandikuluza bt makani ngatialindizelu

 23. Bwana President musamalimbane ndi mbuzi zausongoleriziyi. Munthu wanji osiya zamaphero kukayamba zachikunja? Ife timaziiwa kuti munthu umasiya zachikunja kuyamba kutumikira MULUNGU mwa mphamvu.ndiye musiyeni amene uja wayamba kupenga sakumamva bwinobwino. Alapa pompano. Ochakwera ingolapani simuyaluka sitikusekani.

 24. He (muthalika) should be the first n most stupid ever failing in many ways to develop the country to stop issues of killing albinos robbery in country n many more bout very busy indeed in a fighting n insulting innocent pple what sort of president is this I can’t even define u sir ! Why don’t u focus on developing the country?

 25. He (muthalika) should be the first n most stupid ever failing in many ways to develop the country to stop issues of killing albinos robbery in country n many more bout very busy indeed in a fighting n insulting innocent pple what sort of president is this I can’t even define u sir ! Why don’t u focus on developing the country?

 26. kkkkk guys do you know how much we are buying a bag of maize now? every where the price has short up at this time of harvesting, are we going to reach december? what about february next year. Its high time you should hav stopped mudslinging and come together as one and build our beautiful Malawi but if you can’t adhere to one another then Malawi is doomed and any leader in the future wont excel becoz of this attitude, its only Dr H Kamuzu Banda and atleast Bingu who excelled. The duty of building this nation is for all of us and not Peter alone let’s help him let’s leave our egoistic thinking and get uniteD we stand and devided we fall , we are all sailing in the same boat if it is sinking every one will cupsize !Lol!

 27. kkkkk guys do you know how much we are buying a bag of maize now? every where the price has short up at this time of harvesting, are we going to reach december? what about february next year. Its high time you should hav stopped mudslinging and come together as one and build our beautiful Malawi but if you can’t adhere to one another then Malawi is doomed and any leader in the future wont excel becoz of this attitude, its only Dr H Kamuzu Banda and atleast Bingu who excelled. The duty of building this nation is for all of us and not Peter alone let’s help him let’s leave our egoistic thinking and get uniteD we stand and devided we fall , we are all sailing in the same boat if it is sinking every one will cupsize !Lol!

 28. inenso ndikutha kuona kuti akulu amenewa mmutu mulibe kanthu sindikukhulupirira kuti ali ndi ubongo ayi.Dzaka ziwiri ali learder of opposition koma kumangonyoza speech ya president basi.A President kulakhula zomveka ndipo zotukula dziko iwo ndemanga mkumangoti the speech was empty how?Udzakhala otsutsa mpaka imfa yako.Bola A Tembo aamayamikirapo zina koma izi dzoipa mitima kuposa satana iiiiiiiiii kodi paja mwati adali atsogoleri ampingo uti?samaba za mbale awa?panopa ndazindikira kuti sadaitanidwe ndi Mulungu ayi koma ndalama

 29. inenso ndikutha kuona kuti akulu amenewa mmutu mulibe kanthu sindikukhulupirira kuti ali ndi ubongo ayi.Dzaka ziwiri ali learder of opposition koma kumangonyoza speech ya president basi.A President kulakhula zomveka ndipo zotukula dziko iwo ndemanga mkumangoti the speech was empty how?Udzakhala otsutsa mpaka imfa yako.Bola A Tembo aamayamikirapo zina koma izi dzoipa mitima kuposa satana iiiiiiiiii kodi paja mwati adali atsogoleri ampingo uti?samaba za mbale awa?panopa ndazindikira kuti sadaitanidwe ndi Mulungu ayi koma ndalama

 30. President Peter Mutharika is the first to rule Malawi in the most difficult times. If we are failing to appreciate his efforts Malawi’s woes wll continue tormenting poor Malawians. Muthalika has one Head and Two hands. Plz it is upto 17 million heads and 34 million hand to Join Mutharika’s Head and 2 hands to turn around Malawi’s economy. Otherwise, divisions wll only cage us in rags.

 31. President Peter Mutharika is the first to rule Malawi in the most difficult times. If we are failing to appreciate his efforts Malawi’s woes wll continue tormenting poor Malawians. Muthalika has one Head and Two hands. Plz it is upto 17 million heads and 34 million hand to Join Mutharika’s Head and 2 hands to turn around Malawi’s economy. Otherwise, divisions wll only cage us in rags.

  1. Things can’t move if he only listens to his inner-circle which is interested milking government coffers and not advising him when he goofs. Things will continue to get worse because of his “laissez-faire” style and ndilibe pulobulemu attitude. At least late Bingu was able to talk hard and bite. Even in a classroom situation if you don’t accept and correct your mistakes you are doomed.

 32. No one is full head.
  Beside that why can u open MALAWIAN FACTORIES FOR US TO WORK.

  WE ARE TIRED OF UNPROFESSIONAL BUSINESS

 33. No one is full head.
  Beside that why can u open MALAWIAN FACTORIES FOR US TO WORK.

  WE ARE TIRED OF UNPROFESSIONAL BUSINESS

 34. Kodi alipa pachiongolero ndani ? Paja tu wa pakeliyala sayimba belu. Opanda nzeru ndiyemwe walephela kutsogolera dziko .

 35. Kodi alipa pachiongolero ndani ? Paja tu wa pakeliyala sayimba belu. Opanda nzeru ndiyemwe walephela kutsogolera dziko .

 36. Chimanga chikukwera every day kma atsogoleri athu mukungogemulana zoona?

 37. of the two some1 is really has empty head! sam1 who has led this government to go astray, alot is being mishandled , no funds to hospitals for more than two months, who is who?

 38. of the two some1 is really has empty head! sam1 who has led this government to go astray, alot is being mishandled , no funds to hospitals for more than two months, who is who?

 39. Kwene Kwene Ochakwela Olibedi Mzeru,,ogooo,,oli Mmutu Ngati Mbuzi Ati? ,okapitiliza Kutsutsa Mwaumbuli Sodzauwonaso Mpando Umenewu Chifukwa Anthu Omasiku Wano Odapenya Omafuna Action Osati Mfundo,,,,,

 40. Kwene Kwene Ochakwela Olibedi Mzeru,,ogooo,,oli Mmutu Ngati Mbuzi Ati? ,okapitiliza Kutsutsa Mwaumbuli Sodzauwonaso Mpando Umenewu Chifukwa Anthu Omasiku Wano Odapenya Omafuna Action Osati Mfundo,,,,,

 41. Kodi mungolimbana ndi anthu andale mmalo moti mukhale busy kusaka ganyu mudyetse ana anu mungobeleka mwa uchitsiruwo, kaya muti Ibu sakuziwani or mutafa lero maliro anu sazadziwa kuti kuli Namachende wamwalira uku ai .Koma ndinu anthu omvetsa chisoni kwambiri anthu mukuwachemelerawo akukhuta mimba zawo zikungotuluka pamene inu ana anu yekha kwashiokor, marusmus ati busy kuchemerela apm mbuzi za anthu dzimveleni chisoni

 42. Kodi mungolimbana ndi anthu andale mmalo moti mukhale busy kusaka ganyu mudyetse ana anu mungobeleka mwa uchitsiruwo, kaya muti Ibu sakuziwani or mutafa lero maliro anu sazadziwa kuti kuli Namachende wamwalira uku ai .Koma ndinu anthu omvetsa chisoni kwambiri anthu mukuwachemelerawo akukhuta mimba zawo zikungotuluka pamene inu ana anu yekha kwashiokor, marusmus ati busy kuchemerela apm mbuzi za anthu dzimveleni chisoni

 43. Kodi mungolimbana ndi anthu andale mmalo moti mukhale busy kusaka ganyu mudyetse ana anu mungobeleka mwa uchitsiruwo, kaya muti Ibu sakuziwani or mutafa lero maliro anu sazadziwa kuti kuli Namachende wamwalira uku ai .Koma ndinu anthu omvetsa chisoni kwambiri anthu mukuwachemelerawo akukhuta mimba zawo zikungotuluka pamene inu ana anu yekha kwashiokor, marusmus ati busy kuchemerela apm mbuzi za anthu dzimveleni chisoni

 44. Kodi mungolimbana ndi anthu andale mmalo moti mukhale busy kusaka ganyu mudyetse ana anu mungobeleka mwa uchitsiruwo, kaya muti Ibu sakuziwani or mutafa lero maliro anu sazadziwa kuti kuli Namachende wamwalira uku ai .Koma ndinu anthu omvetsa chisoni kwambiri anthu mukuwachemelerawo akukhuta mimba zawo zikungotuluka pamene inu ana anu yekha kwashiokor, marusmus ati busy kuchemerela apm mbuzi za anthu dzimveleni chisoni

 45. Chakwera can’t understand what these geniuses are doing, that’s why from the whole speech he only tries to find where to oppose as he is the opposer. Akuchepadi

 46. Chakwera can’t understand what these geniuses are doing, that’s why from the whole speech he only tries to find where to oppose as he is the opposer. Akuchepadi

 47. Chilungamo ndi choti amene ali mphawi azakhala ndi umphawi mpakana kale ndipo amene ali ndi chuma azingopitilirabe kukhala ndi chuma, a malawi tisayembekezera kuzakhala ndi mtsogoleri yemwe angakonze mavuto athu, atsogoleri onsewa ndi chimodzi modzi amangofuna kukhutisa mimba zawo osayang’ana mavuto amphawi tiyeni tingolimbika kugwira ntchito zathu osayang’ana kuti wina akupangireni zinthu

 48. Chilungamo ndi choti amene ali mphawi azakhala ndi umphawi mpakana kale ndipo amene ali ndi chuma azingopitilirabe kukhala ndi chuma, a malawi tisayembekezera kuzakhala ndi mtsogoleri yemwe angakonze mavuto athu, atsogoleri onsewa ndi chimodzi modzi amangofuna kukhutisa mimba zawo osayang’ana mavuto amphawi tiyeni tingolimbika kugwira ntchito zathu osayang’ana kuti wina akupangireni zinthu

 49. Having Big Head Doesnt Mean U Are Good At Solving Problem..But U Are Gud At Heading Bags..Pliz Lets Respect #Peter For His Job.

 50. Having Big Head Doesnt Mean U Are Good At Solving Problem..But U Are Gud At Heading Bags..Pliz Lets Respect #Peter For His Job.

 51. Kungoti Chilungamo nthawi zonse Chimawawa, Sindikuchiona chifukwa choti Chakwela anyozedwele coz zimene Analankhula Chakwelayo ndikukhulupilila kuti aliyense oukonda mtendere atha kukhala mboni yake kuti panopa palibe chanzeru chomwe chikuoneka, ndipo ngati mumatha kunyoza chonde muziona nkhani zonyozazo komanso sibwino kukamba nkhani zoti simukuziziwa, ndipo kunyoza kumene mukunyoza apa muziganizile Kaye kuti mutakhala inu wina nkumakunyozani mungamve bwanji?

 52. Kungoti Chilungamo nthawi zonse Chimawawa, Sindikuchiona chifukwa choti Chakwela anyozedwele coz zimene Analankhula Chakwelayo ndikukhulupilila kuti aliyense oukonda mtendere atha kukhala mboni yake kuti panopa palibe chanzeru chomwe chikuoneka, ndipo ngati mumatha kunyoza chonde muziona nkhani zonyozazo komanso sibwino kukamba nkhani zoti simukuziziwa, ndipo kunyoza kumene mukunyoza apa muziganizile Kaye kuti mutakhala inu wina nkumakunyozani mungamve bwanji?

 53. what chakwera said is just very true,the only problem is dat he ddn’t provide solution to the problems,koma APM has failed malawians,do not hide the truth coz ndinu alomwe,be honest plz

 54. what chakwera said is just very true,the only problem is dat he ddn’t provide solution to the problems,koma APM has failed malawians,do not hide the truth coz ndinu alomwe,be honest plz

  1. get the argument clearly….what is true? That the state of national address is empty? Wht is to be empty? Kkkkkk my friend your statement is fallacious…bring your premises together and see if your conclusion follows neccessarily.

  2. get the argument clearly….what is true? That the state of national address is empty? Wht is to be empty? Kkkkkk my friend your statement is fallacious…bring your premises together and see if your conclusion follows neccessarily.

  3. yu sound empty like Chakwera himself,they say “if yu can’t bring a solution to any problem then yu’re part of it “that’s what #Chakwera’s doing,so what’s da truth there ?akulu amene aja ali ndi Njala yolamulira kwabasi…

 55. Chakwera was saying de truth, kungoti anthuwa akumunyonza coz akhuta chimanga tangokolora kumenechi, ena chitha mwezi uno ndipamene muone kut this mbuzi also known as Ibu z toothless

 56. Chakwera was saying de truth, kungoti anthuwa akumunyonza coz akhuta chimanga tangokolora kumenechi, ena chitha mwezi uno ndipamene muone kut this mbuzi also known as Ibu z toothless

 57. Ndale pamalawitu zimatero opposition imapanga campaign kuchokera tsiku lomwe president walumbiritsidwa. Achakwera akufuna apange dzina kuti 2019 adzapambane motero adzingosankha zofooka za anzawo nkumatiuza. Chifukwatu munthu wanzeru zaumunthu komanso yemwe timakhulupirira kuti ndi opemphera sanganene kuti speech yonse ija inali empty. Zikuonekeratu kuti ndale zapamalawi ndi zaumve, dyera komanso kudzikonda

 58. Ndale pamalawitu zimatero opposition imapanga campaign kuchokera tsiku lomwe president walumbiritsidwa. Achakwera akufuna apange dzina kuti 2019 adzapambane motero adzingosankha zofooka za anzawo nkumatiuza. Chifukwatu munthu wanzeru zaumunthu komanso yemwe timakhulupirira kuti ndi opemphera sanganene kuti speech yonse ija inali empty. Zikuonekeratu kuti ndale zapamalawi ndi zaumve, dyera komanso kudzikonda

 59. If APM has knowledge, he shouldn’t be arguing with the opposition because he is wasting time. The opposition are giving him a wider view of the happenings in the country and his focus should be how to turn things around.

 60. If APM has knowledge, he shouldn’t be arguing with the opposition because he is wasting time. The opposition are giving him a wider view of the happenings in the country and his focus should be how to turn things around.

 61. Anthuwa ndichimodzimodzi angosiyana maina tikalimbana nawo tingotaya nthawi basi iwe ndi ine bola kukacha tiganize kuti tidyanji basi

 62. Anthuwa ndichimodzimodzi angosiyana maina tikalimbana nawo tingotaya nthawi basi iwe ndi ine bola kukacha tiganize kuti tidyanji basi

  1. Aise zomwe akuyankhula abusawa zopanda mutu zenizeni amenewa bola abwelele Ku church ndalezi simbali yawo it’s like boys doing mens job

  2. Aise zomwe akuyankhula abusawa zopanda mutu zenizeni amenewa bola abwelele Ku church ndalezi simbali yawo it’s like boys doing mens job

 63. If the president claims to have knowledge it should show on the ground not just the war of words between the two. Malawi was united during one party system than it is now in this multiparty democracy and this leads one to think then that Kamuzu was right to oppose the new system.

 64. If the president claims to have knowledge it should show on the ground not just the war of words between the two. Malawi was united during one party system than it is now in this multiparty democracy and this leads one to think then that Kamuzu was right to oppose the new system.

  1. Mmmm ine ndikuganiza kuti gulu lina lake la anthu asatanic mdzikomu likufuna lichititse manyazi mkuluyi ndi boma lake lamuonelela kufooka penapake, ok.awo ndimaganizo anga chabe mwina anuwo nkukhala olondola koma pangatalike choona chizadziwika ndithu ambuye ndiwabwino kkkk

 65. achakwera ndnu afodya m ‘malo mot muthandize nzeru ngat mukuona kut boma silikuchita bwno,kom bas kulongolora ndnu opusa ndpo muli nzeru,ungosiya ukapitilize ubusa

 66. achakwera ndnu afodya m ‘malo mot muthandize nzeru ngat mukuona kut boma silikuchita bwno,kom bas kulongolora ndnu opusa ndpo muli nzeru,ungosiya ukapitilize ubusa

  1. Makape mukuona ngt kuendesa dziko nzofanana ndi mabanja anu et… Development imayenda step by step and moreover anapeza zinthu masteni atawononga kale, … Simunayendeseko even shop ndye apa mutibowe…. Go to hell haters

  2. After all he is dull but he is a president..inu amnzerunu ndinu ayani.Taziwerengani malemba inu kapena kut bible kut linati chani za masiku omaliza.Zinthu ena anaononga ndiye mufuna zikozedwe lero ndi lero,chomsecho tikukambatu zoyendetsa dziko osati galimoto..Ai inu ena akadzakutchulirani makolo anu mau mwanenawa musadzamve kuwawa

 67. better to be empty head bkoz he full up with the needs of malawian than that of already water fulled head u discards the needs of people concetrating on biasing people through threating them ur head is full of water that disolved the needs of people fuck u pitala, ur’e just busy thiefing money in country instead of sustaining development instead ur’e developing killing albinism its all about ur fuckin incapability of ur head.NONSENSE PITALA.

 68. better to be empty head bkoz he full up with the needs of malawian than that of already water fulled head u discards the needs of people concetrating on biasing people through threating them ur head is full of water that disolved the needs of people fuck u pitala, ur’e just busy thiefing money in country instead of sustaining development instead ur’e developing killing albinism its all about ur fuckin incapability of ur head.NONSENSE PITALA.

 69. Malawi cannot develop if our leaders keep on insulting each other instead of putting their heads together to find solutions for the hard times we are sailing through. Its a high time that leader of opposition should also realise that his responsibility is not only to criticise the incumbent head of state but also to appreciate if something good has been done and give solution to other problems.

 70. Malawi cannot develop if our leaders keep on insulting each other instead of putting their heads together to find solutions for the hard times we are sailing through. Its a high time that leader of opposition should also realise that his responsibility is not only to criticise the incumbent head of state but also to appreciate if something good has been done and give solution to other problems.

  1. Chakwera can’t give advice 2 gvt, mcp failed 30years ruling Malawi NO university in de north, his head is just full of criticism.

  2. Chakwera can’t give advice 2 gvt, mcp failed 30years ruling Malawi NO university in de north, his head is just full of criticism.

  3. Mutharika sangakhale olakwa muzonse,pena pake timawalakwitsa ma leaders athu maka a oppositionwa ndife tomwe anthu masapota, kupsepsezela or kukolezela moto kuti adzidana ndi atsogoleri omwe akulamula pa nthawiyo mchinkana a oppositionwa amatsutsa nzopusa zomwe.

  4. Mutharika sangakhale olakwa muzonse,pena pake timawalakwitsa ma leaders athu maka a oppositionwa ndife tomwe anthu masapota, kupsepsezela or kukolezela moto kuti adzidana ndi atsogoleri omwe akulamula pa nthawiyo mchinkana a oppositionwa amatsutsa nzopusa zomwe.

  5. Kkkkkkk Mr Enock musatero Kamuzu adayesesa mbali yake koma vuto ndiloti alowammalo ake Mr Zenus JT ndi Mr C. ndi atsogoleri ankhwizi.kkkkk

  6. Mr B.W mwanena zoona zake ntheradi atsogoleriwa nthawi zina amamwera thiyi limodzi koma ife owasatira kumakhapana ndi kumatukwanana.

 71. Kod Si Mr Ibu Omwewa Amati “Lets Join Hands To Develop Malaw Than Kumakangana?” Ndie Chakwela Walakwitsa Chan Kukakhala Pa Mwambo Wa Boma Ngat Umeneo? Peter Iweo Ndi Amene Uli Empty Chifukwa Siukufuna Umodzi, Kulimbana Ndi Oposition Mmalo Mopanga Chitukuko, Ithink Enawa Ndi Manthanso Mr Ibu!! Na Ine Vote Yanga Siudzaiwona 2019 Munthu Opanda Khalidwe Ngat Iwe

 72. Kod Si Mr Ibu Omwewa Amati “Lets Join Hands To Develop Malaw Than Kumakangana?” Ndie Chakwela Walakwitsa Chan Kukakhala Pa Mwambo Wa Boma Ngat Umeneo? Peter Iweo Ndi Amene Uli Empty Chifukwa Siukufuna Umodzi, Kulimbana Ndi Oposition Mmalo Mopanga Chitukuko, Ithink Enawa Ndi Manthanso Mr Ibu!! Na Ine Vote Yanga Siudzaiwona 2019 Munthu Opanda Khalidwe Ngat Iwe

 73. I hate your silly & stupid talks Mr A.P.M watikwana with your unwelcomed leading.I can’t waste my time to drop my vote to you. 2019 Chakwera azawina kale unless uzabereso ma vote. Chakwera 4 my life but you called A.P.M kagwere kutaliko i don’t want you to be seen on my sight

 74. I hate your silly & stupid talks Mr A.P.M watikwana with your unwelcomed leading.I can’t waste my time to drop my vote to you. 2019 Chakwera azawina kale unless uzabereso ma vote. Chakwera 4 my life but you called A.P.M kagwere kutaliko i don’t want you to be seen on my sight

 75. Ndipo tikati empty mumvese ndichachabechabe olo mnchenga mulibemo mbuzi yamunthu ndipo asamalote kuti angazalamule mulomo ngati bakha

 76. Ndipo tikati empty mumvese ndichachabechabe olo mnchenga mulibemo mbuzi yamunthu ndipo asamalote kuti angazalamule mulomo ngati bakha

 77. No ibeg to differ those points he said definitely his head cant be empty,no body slept during his presentation,he gave facts upon facts ,solutions and suggestions he gave you,its only that you have chosen not to take them

  1. Our opposition team is also a reason to our woes,they make their minds dull before the presentation even a day before, its a shame.

 78. I agree, the head is empty that’s why he left the floaks and join politics.

  1. Propaganda tu iyo panopa akugona kuti ayankhule chonchi? Let him show us that he has knowledge by changing things than just talking and arguing with the opposition.

  2. Propaganda tu iyo panopa akugona kuti ayankhule chonchi? Let him show us that he has knowledge by changing things than just talking and arguing with the opposition.

 79. Aa apm You are late iknew before You that chakwera is empty no wonder a kudwala nzeru tisiileni ife nkhondo njinthu imwe pangani waka maplan ya kutuvyila inse tamalawi dpp woyeeee

  1. Road traffic ilibe vuto lililonse kumbali yanga,thats what is happening all over even ku SA you can not get a driving licence without going in class,so pezani ina njira yonyozera,

  2. Road traffic ilibe vuto lililonse kumbali yanga,thats what is happening all over even ku SA you can not get a driving licence without going in class,so pezani ina njira yonyozera,

  3. Kd makape inu mukuona ngt kuendesa dziko nkophweka..? Munthuyu walowa dziko lili m’mavuto ndikale, so, who is to blame…? Do you expect to see immediate change in our country…? No way, development is a slow process, maybe mukyankhula coz simunakhaleko pa udindo waukulu. Be patient nanu Mulungu azakupasani udindo waukulu muzanyozedwanso m’mene munyozera anzanumu mpamene muzazindikire bt that will b too late.

 80. Mmh!full headed president unable to deliver coz the head is exhausted with tadpoles.Blessed are those that are admits to be despised fate to those that don’t.Mr president I plead with you to change leadership styles.Malawians are really suffering interms of having basic necessities,medicine education,agriculture and too the killings of albino.Concentrate much on this otherwise u fail to convert the country into the real expected life.

 81. Kuyankhulana kotere sikwabwino pokhala nonse ndi ma president a zipani. palibe kanthu wina akulamula. Above all diginity is required. war of words are not necessary here.

  1. Nawo anthu aku jhb akuthawila ku america,canada n uk, ndiye muzifunse kuti ndindani yemwe azasintha ziko poti izi zili kuno kwathu kuno zili paliponse

 82. Was Chakwera wrong,when questioned the said sona?let’s be honest please.He asked if there is any change in lives of common Malawians in all aspects of life? is there any change at government hospitals? small scale businesses? education sector? etc…and one comes on to scream publicly that economy is ticking?

 83. The thing is that Chakwerah has lust for that position. He thinks that Malawians are fools. But we are not.He shuld be helping his frnd instead of making silly criticisms. He suld be told the truth. Now people have lost thier trust in him,,,,,,,,,,,,,,,,,,,, How can I waste my vote on an idiot like Chakwerah… He opens his mouth as if he has no brain,,,,, atleast u shuld have shown us that u want to develop Malawi not to use us so that u can get rich………………………………………… we aint in those yrz where u used to tell us kti ” Mwaona mu nthawi ya Peter Mutharika Mvula simabwerah yambri, kma ndikangokhala president mvula ixigwa” anthu anaseguka maso ndipo tikuona zikuchitika #GGMU

  1. Kodi iyeyo ngati wa opposition wapangapo chan chanzeru kupatula kupanga criticise zomwe akupanga anzake? Who said kuti munthu akakhala wa opposition ndiye kuti azingotsutsa …..chakwera open your eyes and seeeeeeeee if you really want t become a leader one day…..

  2. Kodi iyeyo ngati wa opposition wapangapo chan chanzeru kupatula kupanga criticise zomwe akupanga anzake? Who said kuti munthu akakhala wa opposition ndiye kuti azingotsutsa …..chakwera open your eyes and seeeeeeeee if you really want t become a leader one day…..

  3. di maria angakhale ngati iwe kapuku wa mbewa like u:tell ur mutharika is the only best failure i have ever seen,hell is waitng bullshit pipo like u

  4. di maria angakhale ngati iwe kapuku wa mbewa like u:tell ur mutharika is the only best failure i have ever seen,hell is waitng bullshit pipo like u

  5. Chikondi U dont understand me,,, am not saying that Mutharika is doing something great here but they shuld work together for the development of our nation

  6. Chikondi U dont understand me,,, am not saying that Mutharika is doing something great here but they shuld work together for the development of our nation

  7. Amenewo ndiye amalawi…president angabwereyo azakhalabe oipa. But kunena chilungamo chakwera kumpatsa udindo tikhoza kubwerera paukapolo wakale uja…..He really seems deaperate

 84. Yaaaa sure Mr President you light for that and I observe it but you must watch him is planing some thing at you.they are fishing you they try they fail,they are planing another open you will see.

 85. Ngati munthu wazelu kuenela kumanga chitukuko osamalimbana ndi mzake

 86. thats true he is still thinking of last elections and has bad advisors who are not guiding him

 87. That’s tr true Mr President! This pharisee is just lost. He is still obsessed wth the 2014 elections’ hangovers. He doesn’t realise that this is 2016 & that elections were held 2yrs ago! That’s the reason why he criticizes evrythng from the govt wthout bringing in tangible alternative solutions to the problems the country is currently facing! Did he really hav tym to analyse the SONA or he was just overwhelmed by his usual desire to always criticise APM? learn to be human sometimes mr pharisee!

Comments are closed.