The Malawi Government says it is conducting a feasibility study on the secure amount of money to be given to the elderly as allowances.
Chief elderly programs officer in the ministry of gender, children, disability and social welfare Steve Vinkhumbo said government has put in place measures to see to it that the elderly are protected.
”We are working on a feasibility study on the secure amount of money for the elderly aged 60 and above and once we are done then we will see to it that the elderly start receiving their pension fee,” said Vinkhumbo.
He added that government has developed a national policy which is a guiding framework for developing interventions to improve the lives of the elderly.
Vinkhumbo further said the ministry is conducting campaigns to create awareness to the public and the elderly to know their rights.
Meanwhile, some elderly people in the country have been facing a lot of violence as people accuse them of being wizards.
Ndikutha kuwona kuti pang`ono pang`ono chitukuko chikubwera izi ndi zina zomwe zikanayambika kale kale.big up boma la APeter
It sounds good
Anthu opusa allowance ya ana aku university yowathandizila in their education life achotsa ija akapeleka kwa nkhalamba?kkkkk zitsilu ngat izi sinawonenso what kind of corner stone are they going to build by giving allowances to the old Aged? Are they going to benefit Malawi in two or others ways? Stupid leadership ever
Anthu opusa allowance ya ana aku university yowathandizila in their education life achotsa ija akapeleka kwa nkhalamba?kkkkk zitsilu ngat izi sinawonenso what kind of corner stone are they going to build by giving allowances to the old Aged? Are they going to benefit Malawi in two or others ways? Stupid leadership ever
What??? Instead of funding education ali busy kukathandiza nkhalamba
What??? Instead of funding education ali busy kukathandiza nkhalamba
The begining of cashgate, mukufuna mube ndalama za misonkho yathu kunamizira elderly allowances. Mulunu akuona
The begining of cashgate, mukufuna mube ndalama za misonkho yathu kunamizira elderly allowances. Mulunu akuona
Kumeneku nde kuzama pa nzeruko kumeneku. Nkhani yabwino tiziyamikila komano zizikwaniritsidwa
Kumeneku nde kuzama pa nzeruko kumeneku. Nkhani yabwino tiziyamikila komano zizikwaniritsidwa
Thats great
Uuuum! kwacha yake iti? Tisanyenganepo ndi chala apa.
Avery good idea
Aaaaaaa za chani, a Boma mungofuna Cashgate..et?????
Inu palibepo chitasinthe apa zili ngati makoponi ndangati omwe amapindula ndindomeko imeneyi? Apa angofuna polemelelapo basi iziti tikuwapatsa ndalama azigogo zazi 500 taganizani akagula chani poti katundu nde eee wakwela mumtengo wa pine angopanga zinthu zoti zipindulire amalawi fundo izi zinayenela jb fundo zachikazi zoyendetsela dziko fotseke petera
Easier said than done, lets wait and see
Easier said than done, lets wait and see
Donor will welcome it. They enjoy supporting non developmental projects. I hope the govt has all citizens got IDs. Ghost elders, fraud and corruption excites donors. Hand to mouth kind of support was engineered to imprison the poor in the york of the affluent
Donor will welcome it. They enjoy supporting non developmental projects. I hope the govt has all citizens got IDs. Ghost elders, fraud and corruption excites donors. Hand to mouth kind of support was engineered to imprison the poor in the york of the affluent
The west has nailed it. Western donors prefer supporting non development projects. I guess the govt has finished with ID first. Corruption and fraud also pleases western donors. They will enjoy hearing about ghost elderly receiving million. Poverty is the only way they can contain us in their your.
The west has nailed it. Western donors prefer supporting non development projects. I guess the govt has finished with ID first. Corruption and fraud also pleases western donors. They will enjoy hearing about ghost elderly receiving million. Poverty is the only way they can contain us in their your.
It sounds bo!.
its really a gud move fo mdubs bt it beta not be njira ina yobela cush!!
welcom move
It is a good policy but Malawi Government cannot manage to implement it due to economical crisis.
Ndizeru koma apange ma ID kwa anthu omwe azilandila nthandizoli munthu akalandila adzidziwika
At long last we have this scheme, make sure there is transparency, they should have bank accounts or through airtel money or mpamba
Oo
Nzeru za bho,koma b sure kut zithandized okalamba mbali zonse za zikolino not kwa okhao anakuvoteran kapena komwe kuli MP wanu,that our tax money siza dpp
good…..Study in Belarus
good…..Study in Belarus
Mfundo yanyatwatu iyii
Mfundo yanyatwatu iyii
Aliyense akuyembekeza kuzakalamba,koma ine mfundo iyi sindikugwirizana nayo,ndipo uku nkufuna kungowalemeretsapo a nduna chabe.Why am saying this? Kuli ma nurses amene sanalembedwebe ntchito koma xool yawo anamaliza kale kufufuza zifukwa akuti boma lilibe ndalama.Akakhala mphunzitsi nde ena mpaka 3 yrs asanawachite post.Why not think of them first?How many elderly pple that we have in Malawi?Then where is the money that u r planning to pay them as allowances?Achinyamata akuvutika ma certificate akungokhala lero mukuti ma allowance kwa okalamba? Mulibe maganizo eti?Kapena mufuna mupeze pobera ndalama anthu achabe oganiza ngati anyani inu,mxiiiiiii
Maganizo abwino koma boma silingakwanise zimenezo ngati akulephera kuwanisa makoponi wogulira feteleza anthu amene anagwira ntchito mboma ena akulandira K3,000 pa pa 14 ndipo mpaka pano sitinalandire ndalama zanthu za pa 14 march
Good development
Nice joke
….That’s Better…
Boma lodziwa mavuto awanthu osat kumangopanilila ndalama thumba ngat boma lakale.
I think its a good idea, there’s so many old people who are suffering outside there. And Sad enough some have got kids who are ignoring to support them. So keep ahead with your plan Government.
Panganid zomwezo okalamba akuzunzik
That’s money laundering using the elderly we are not blind shut up!!
Zitatheka izi,ayi zikomo
Do not cheat elders plz
ma plan abwino koma chonde musapezeleponso mwayi olemerelapo please . kumakhala ndiumunthu.
Khani yabwino koma mvuto ndiloto afisiwa amachulusa ziphuphu even now my grand ma samalandila makoponi chinyego chachuluka fuck them
Ambili timadziwa kutukwana Boma apa muli zii 2019 DPP Boma
Good Strategy
ngati zingathekedi iyo yokha ndiyo mfundo yanzeru m’boma la ntate chakanika
Bullshit government instead of creating jobs n reduce high rate of unemployment, uzipeza kuti ndalama zopatsa nkhalamba zopusa basi
Good idea indeed
so great
Quite a good development lets put this in practice not just in words
atikwezerenso misonkho ku salary ndi katunduka sifika 60% VAT mwati…………………
So Far Sor Good
Don’t just promise.
Don’t just promise.
Only chawa people wil benefit frm it
Only chawa people wil benefit frm it
Kikikikikikikiki someone is either joking or bluffing the ignorant majority who always vote ignorantly. If government is failing to employ teachers, doctors etc, failing to pay good salaries to civil servants, where is the money going to come from to maintain and pay welfare
Kikikikikikikiki someone is either joking or bluffing the ignorant majority who always vote ignorantly. If government is failing to employ teachers, doctors etc, failing to pay good salaries to civil servants, where is the money going to come from to maintain and pay welfare
chamzelu chapanga Boma ndi chimenechi pa 2 years
chamzelu chapanga Boma ndi chimenechi pa 2 years
u shud 1st fulfil what u promised us n den u come up with dis political move. adaliponso ena adatero kut awaphimbe anthu kumaso koma adayaluka nazo zawo zopentapenta mpaka pano saoneka. pangan kaye zot kwacha ipeze pa malawi kut anthu athamange mosavuta ,agogowo ndi athu tikawapatsa ndife kut nawonso adye thukuta lawo.muziwe kut mphamvu zawo tdawononga ndife amene tkusowa chochitafe,ndiye ife tizawapatsa liti ? inuyo mutatitchingira kusogolo kapena azit inu abwino?
u shud 1st fulfil what u promised us n den u come up with dis political move. adaliponso ena adatero kut awaphimbe anthu kumaso koma adayaluka nazo zawo zopentapenta mpaka pano saoneka. pangan kaye zot kwacha ipeze pa malawi kut anthu athamange mosavuta ,agogowo ndi athu tikawapatsa ndife kut nawonso adye thukuta lawo.muziwe kut mphamvu zawo tdawononga ndife amene tkusowa chochitafe,ndiye ife tizawapatsa liti ? inuyo mutatitchingira kusogolo kapena azit inu abwino?
Let It Be Transparent. I Smell 60% Corruption, it will take centre stage. no doubt about that.
Let It Be Transparent. I Smell 60% Corruption, it will take centre stage. no doubt about that.
Good News.
AND THE UNEMPLOYED
Muza ona kolandila ndalama kuchuluka achinyamata akumati agogo ndiokalamba kwambiri samayenda angondipasila id liliboza
good move! mwina angasiye kupempha m’ma PEOPLEs shops.
Bola osazapeleka kwa afiti coz azagula nyanga zanyowani kkk tizalozedwe mmizimu
Nice i dea Mr APM
Kagwere uko nawe iwe agogo anu anakusamalani inuso kuti muwasamarem mkudikila boma kuti likudyesereni mbuli inu
The idea is good. For once, however, let me be labeled a doubting Thomas on making a reality this idea. The million kwacha question is WHERE WILL THE MONEY COME FROM? Govt is failing to address pertinent issues due to lack of funds, for instance,govt is failing to recruit people it has spent a lot of money on their training,people who would contribute to economic devpt. This, we are told, due to govt’s lack of money. So where will money come from? Am very skeptical. I ll clap hands when the idea is actually effected……..
Boma likamatelo ndiye layamba zanzeru, chifukwa ambiri achinyamata amathamangila ku south Africa ndi cholinga choti mwina angapulumutse azigogo awo pamavuto, ndiye kwanilitsani muzawona mavoti azakhaladi Ali anuanudi.
Yes pitala uli boh osamagoti aojedzere malipilo anu naeso gogo apedzeķo yasoda
That the best news coming from home
It’s a good idea as long as selection of beneficiaries is transparent and not politically motivated. Otherwise it shouldn’t be another outlet for embezzling taxpayers’ money, because I can notice that some departments are creating their ways of cashgating…..
Sometimes z better to support brilliant idea like dis one. At R S A they started long time ago bravo govt don’t allow any one to discourage this idea.
kufuna kuba dzina la athu okalamba tsopanoo
Nanga amachedwa kuti?
Mukungofuna njira yobera ndalama nsete. You’re failing to chiefs stupid government
Nkhan yabwino kwabasi carry on
Mulungu dalitsani malawi,maganizo abwino
.
Chiyambire chijaaaa chanzeru ndichokhachi basi…
very good idea, I support it. in SA any one who is 60 and above is getting about R1 500 every month which is about 70 000 kwacha
Nkhalamba (pesionair) akumalandira R1,330.00 ndipo ana ang’ono akumalandira R330.00
kkkkkk ndipo mwanisuska chomene nkhanira pa gulu la wanthu
Chilowereni Pitala m’boma Mfundo yomveka ndiyokhayi basi
Agalu a Malawi kwawo kutukwana basi,machende awo
Amalawi ndi agalu alibe pabwino machende awo
gud move
[READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS.
Good opinion mr president
That’s a gud dvpt, keep it up, enanu mulibe azigogo eti??? Ndadabwa nanu
Nanga tikabeleka mwana mwanayo azilandilanso kkkkkk ulesi
Ya good thinking bola ena asalemelelepo plz
Thats good news bola otsutsa asatsutse wokwiya amadya matewela.
gud develpment! Bravo govnmt
Azigogowa mmesa anakhalako anyamata bwanj sanapange tsogolo lawo?
i dont agree with this, if de government is failing to raise salaries of civil servants, whats the need of giving money to unproductive
people….dont be fooled with the UK or other super rich countries who implemented such program… the best we can is empower workforce not someone whp is producing nothing for the country.
Apatseni okalamba di muchita bwino
iyi nde mzeru pokhapo mwamuposa kamuzu
U want b like RSA but ziyambisa kuba
Yaaaa!!! maganizo abwino atleast tidxitha kuwona msonkho wathu ukugwira ntchito!!!
chomwe tikuyenera kudziwa ndicgakuti wina aliyense ngati munthu amayembekezera kudzakalamba nde ndikudabwa kuti ena saakugwirizana ndimfundo imeneyi maybe simukalamba pazifukwa zomwe mukuziziwa nokha,komanso munthu akamakalamba mphamvu zigwirira ntchito zimachepa and kwathu kuno anthu omwe alipa pension fund ndiwochepa so guys lets think of our future and that of our friends.We are malawi and together we will build a nation free of jelousity.
I can see many graduating into the category. Sad
Paja kanyuzi aka nkamabodza! Boma lake liti? Lomwe likulephera kugula mankhwalali? Pano ma pensioneer mpaka press release, makobili palibe. Fodya, chani?
Gud idea.but where will u get de money .don’t misuse our taxes.we need salary increament to meet de cost of living.we really that u will politicise de programme in order to be fame to ur stronghold areas
Selfish you Thomas.
Selfish you Thomas.
Such kind of allowences to the elderly does wonders here in SA so let it be in yr land too. U will rejoice.
What i need is transparency & it should based on merit,not only de grandparents of zea party members
Zili bwino tidzilandila kangachepe
Koma amalawi,tisamangotenga ma policy omwe ndi abwino koma oti sitikwanitsa.Inu boma limalephera kuwalipira anthu ogwira ntchito molongosoka,otinso akuthandiza a zigogo awo ndiye akanene zopeleka ma allowance??? Malawi wafika pamenepo? kuyambitsatu zinthu zoti ena angotitama sibwino.
Kkkkkkkkk
Nice move azigogo athu akumvetsa chison plz!
I think economists in the civil service have now started thinking in line with their profession
Ndalamazo agwilitse ntchito potsisa katundu,kugulira chakudya,mankhwala mzipatala ndi zonse zofunikira pamoyo wamunthu imeneyo ndie mzeru yabwino.
Zachuluka ndalama zo
if it’s a fight.. what kind of the Battle is this? Malawi government
The decision is just very good , but let us see who is going 2 benefit from such a project . surely the relatives of those who wili be running this r the ones who wili enjoy these salaries ,leaving poverty striken elders in our villages
Pamene mutazaluzire ndipamenepa mukuyamba zosatheka konzani kaye zithu zomwe zikulakwika this move is just to blind people anthu akuphedwa anthu akuzunzika ndi njala dziko lili pachilala ili mukanayamba kupulumisa miyoyo ya amalawi just be gratefull anthu anakuvoterani awonesereni chikondi anthu a dziko mwanu
Thats gud idea but the problem akapitawo kuba
Mwapeza imenei njira yoti mubereno. I can’t support this initiative completely doubtful and the truth z malawi can’t, will not manage to do and fulfill the promise. Osamanamiza munthu wakhate sapato, leave the elders alone mukupempha matsoka.
Really? Nganga zinenepe
Ndalama zake zizichokera kuti?musatitolepo utsilu apa tikudziwa kale kuti inu mulibe problem munanena kale.
For someone to be elderly means he was young also.
They have done a lot to develop our country and they deserve this package.
Some are not comfortable with it because they are young
Think twice next ndinu you will not be young forever mudzakalambaso
Big hand to Gvt
Mwayaganizira Makora magogo uko. .
Mukulephera kulipira maphunzitsi ndiye ndalama za okalamba mukatenga kuti? Mukulephela kugula chimanga nkuika m’ma admarc, zoonera sizabwino, anzanu ali ndi njira zopezera ndalama osati Zopempha.
sitingazikwanitse as of now, osadikila bwanj, thats why apm is a dull president of all time. Apm equals jb in his thinking capacity
Well done in advance
kulota saletsa paja
Ndimfundo yabwno,koma osangoyamba dzinthu zoti sitingazikwanise th way hw i know malawi, full of ziphuphu.
Ndimfundo yabwno,koma osangoyamba dzinthu zoti sitingazikwanise th way hw i know malawi, full of ziphuphu.
Where will this money com from don’t forget the primary teachers.
Tax dont b selfish for grannies hey.
Thank you thank you thank you that’s a way to go……..
Fundo koma imeneyi, koma kusakhale kozembesela ndalama.
Now if it is like this Malawi government is getting strong and is going to build Malawi energetic.
bola musalowetse ndale,
chamba et kodi akuvutika ndi okalamba okha angakhale kuwapasa nthumba la 50kg sangadye mwez chifukwa kwa omwe akuwathandizaoso ali ndi mavuto anjala gogoyo sangapangile mithulo olo muwapase ndalama palibe chothandiza
fantastic! !
asaa!kma anthu ndi zitsilu kwabas mmene amavutikira anthu okalamba chilichonse kumangotsutsa basi aaa!kutsutsa kwinaku ndi ufiti!!!!
That’s gud move coz thse erdels akuvutika kwambili monga ena alibe munthu otiziwayang’anila komaso ena ndiwolumala naoso a kufuma chithandzo ,& am happy the way the Govrt is planning
BIG UP MALAWI
MORE THAN 50 YRS FREEDOM ITS NOT EASY.
Great move.
nkhani ya boh
Mwaganiza bwino kwambiri
this government just focusing on votes rather than on Malawi’s health, we are in economic crisis what will this going to help boost our economy back on track….. heal our economy first Mr Presdent because charity works will take us no where…. find other means in helping them not allowances….. and to look deeper into the root of this initiative, somebody just wana root something….. i dont trust these politicians any longer
That’s true.
good point!!
good point!!
But please don’t support to my area,our chief is greedy he will squander all the money,even the coupons he writes people who have already passed away,so if u can come with this development hopefuly magogo will not benefit at all
with what money
Mwachulutsa mbwelera…anthu oduka mitu….!
Am supporting the idea well done mr president
lets clapp hands for govt for gud idea……
big up ndichokhacho chandisangalatsa. but ikani ma tall gate kuti mwina mupange improve miseu
But it is wise to solve financial crisis in the country than to put politics on centre stage
bola zisalowe ndale potimulowetsa ndale penapalipose
Exactly, who are the elders who will qualify for this? Who will identify them? Who will be collecting the cash on behalf of those who will not be able to reach the collection point? Who will be entrusted with reporting of deaths? Is cash for this available or will the programme be externally funded?
Thus stupid,alot of people are jobless and yet gvnt is planning abnormally aaaa if jobs can be available then people will help their grandparents not wat gvnt is thinking
Ndagwirizana nazo kwambiri. Good move.
dats welcm idea,in developed countries anayamba kale,kuganiza kwabwino!!
zabwino kumayamikila
muona anyapapi ena akutsutsa ngat alibe ambuyawo,ufiti bax,kkk
ngati pali chanzelu chomwe boma lachita since i waz born nchimenechi. alibe agogo amenewo
Ngati boma likulephela kuyendetsa ntchito zake kamba kosowa ndalama ndiye ganizolo litheka?mmmm tiwona.
Koma Mukwanitsa???? Kapena muzichita kuyang’ana Nkhope?
Bola musayendere za chipani
Just to gain morality. Muzitenga kuti ndalama zake?
Ndalama muzitenga kuti ?????????
dont forget my elder mum kkkkkkk
If you do that Mr president maybe you win over again our trust nice move
njira zobera money……politicsatitsbest
same jonz kuno amamangira nyumba zabwino
Bola mukwanitse ngati akukanika kulandila anthu oti akugwira ntchito ndiye kuli bwanji amenewa?
That’s the way to go
Bravo gvmnt
Nkhani yabwino koma musadzalowetsemo katangale.
Ndizabwino koma allowanceyo isakhale increment yanga. Ndisamve kuti andionjezera zochepa.
Nonstarter this one!
Thax for that God bless u peter ,,,,nxt tym weed free education plz
Nonstarter this one!
please agogo anga anachisale musawaiwale kuno kumulanje .kodi nanga ndalamazo azikatengela pa khoma(atm) kapena mkati chifukwa masiku ano saonetsetsa
Is this for real?
Azilandira ndi mafumu ndi azibale awo ndalama imeneyo
I don’t support this coz politics will take center stage on our taxes , look wat happened to Mbuzi, nyumba, n this malata things!
only those close to politicians benefit ifeyo achina Kafamsiyanji nde zero misonkho paliponxe!
nurse, doctors, graduates r not being employed despite need to increase workforce, no funding to institutions!
m
n now this? after chiefs honouraria?
Kkkkkkk trying to please some hungry crowd out there. Good move, but make Malawi an overflow of maize again and pliz don’t skip civil servants salaries
Inu tamayamikani plz,mfundo yabwino iyi anzathu anayamba kale kupanga zimenezo:tiyeni tiziyamikira zinazi
sndimasapota ndale koma ngat aganiza choncho ndekut zilibwno kwambir izi ndizomwe timadikilira kut tsiku lina kudzapemzeke mtsogoleri wachikondi chonchi coz maiko amzathu ochitaso kubwino kuposa ifeyo amaganizira nkhalamba, osauka , azikazi amasiye , odwala hiv /aids , ose amalandira kangachepe kutha mwenzi uliwose …south africa dziko lolemera ku africa kuno amaganizla anthu awo ovutika so why not malawi??? zina kumayamikla guyz osamangokhalira kutsutsa
Komabe suzawina pa 2019,
Bola ikhale yosachepela 20000g
Imeneyo ndiye dhilu
Good news
good dreams mr peter
Ok, mutiuza mukayamba
Ndakaika ngati anthu akumpoto will get access to this
How much?
I think this will be the only right thing Malawi will do, since I was born.
Thats good move,i wonder if they wil afford because even civil servants struggle to get paid sometimes
Maiko anzanu anatopa nazo zimenezi inu mukuziyamba lero ..? Kwa okalamba / amasiye ndi ana obadwa kwa amayi kapena kuti atsikana okanidwa or bambo osagwila ntchito ayenela alandire
Even the deceased will be getting paid via ghost names!!„„„
Guys anthu ena ndi afiti basi.Chomwe amaziwa nkunyoza kokhakokha.Nkhani yabwino ngati imeneyi wina nkumatukwana why?Ngati agoogo any munawapha ZANU izo.Boma lanzeru ili.
ena anayamba kale,koma bola asalowetse ndale
Ena anthu mzibekete kkk
kkkkkkk
Boma lake liti,anthu akufa ndi njara ,kumati eti azigogo aziwapatsa kangachepe.
Ndipo kodi ndi azigogo angati omwe angathe kumalandila nawo ndalamazi??…..ukamalankhula uziganiza……izitu zinayambila mu nthawi ya amayi dipo zimachitikadi koma vuto lomwe linalipo ndiloti mudzi omwe mumapezekamo nkhalamba zokwana 30 omwe amatha kulandila ndalamazo ndi nkhala zitatu zokha kodi nanga enawo amati adzilandilira kuti???..nanga adzayamba liti???
Ndipo kodi ndi azigogo angati omwe angathe kumalandila nawo ndalamazi??…..ukamalankhula uziganiza……izitu zinayambila mu nthawi ya amayi dipo zimachitikadi koma vuto lomwe linalipo ndiloti mudzi omwe mumapezekamo nkhalamba zokwana 30 omwe amatha kulandila ndalamazo ndi nkhala zitatu zokha kodi nanga enawo amati adzilandilira kuti???..nanga adzayamba liti???
komatu…heee
kkk koma photoyi,thats good gud development but osamawabela anthu okalambawa.
Dpp is gaining ground light at end tunnel
Good move
Dzithekadi izi koma ngatizili choncho zitha kukhabwino
Let’s wait and see
Ikukanika free education ndiye izi zitheka ?
Uziti akukanika kwalipila mafumu + ma civil servants… Alandira kwa miyezi iwiri kenako ziyambanso kuvuta
Goodmove bt involve political ppo in the system of chosing the needy use nuetral ppo
Zikanatero bola kusiyana ndi kuwaganizira ufiti.
thats great god bless our nation, give peter long lyf and protection. Dpp woee timafuna zimenezo kumizi anthu akuvutika
osalowetsa ndale apa,its malawi govt nt dpp govt
That a stupid idea……where are you going to get the money? If you are failing to fund the current budget…
Even Mocambique they do so
Believe me,it wil start wth pple frm Thyolo Thava or else Senior Ngolongoliwa’s area…….
welcome development!
koma osati mk 20 000 koma mwina kakhale ka mk30 000 kupita kusogolo
vuto nilakuti azipasa okhaokha a Dpp azipani zina i think cant get a chance for allowances it iz gud most
The one who comes with this idea my God blease him. thats the best 4 our poorest country .
thats good move to help them bikoz ana awo anawathawa kalekale
Great
Zofunika nanga opunduka amene sangangathe kugwira ntchito
Boma koma limeneli Hahah #Dpp
Koma zinazi cash yake mukaiba kuti bodza!
Akukanika kupatsa ana phala kuti azipita ku xul. Nde mukapatse azigogo dola.
I really agree wth that.
Welcome move
At last.
that will be good!
let’s do this plz:therefore it means we are moving forward.In some other developed nations such as Libya,South Africa,they do the same
Oky
Goodnews
thanks thanks thanks Government
This is a very noble idea if it is to be sustained. If not then its not good to start at all. But the question is who will foot the Bill. The number of the employed who would support this social security venture is shrinking by the day as companies have embarked on mass retrenchments due to the poor economic enviroment. I hope govt is not looking at some donor who can later frustrate the project which has good intentions. We know how our donors behave just as they know us.